The purpose of of life is to find rest in him who so loved us. The purpose of this channel is to show the character of God as it is revealed in Jesus Christ
Maphunziro wo ndimawakonda kwambiri koma pemphe 🙏mudzikwezako mawu pang'ono I don't know ndi ndi chida chomwe ndimagwirisa ntchito chi kaya mumandimvekera mosika kwambiri
Palibe chimene mukudziwa inu, sabata, tithing, ndi miyambo ina zinali za ayuda, Yesu atabwera chili chonse chinatha, pitani mukwerenge Hebrews 7:10-14, ngati unsembe unasintha kuchoka ku fuko la Levi kupita ku fuko la ayuda, malamulo akenso anasintha, ndi zomvetsa chisoni kuti ambiri a SDA ali mukusadiwa koma amazitenga ngati odziwa ndi olungama kuposa aliyense. Inenso ndi wa SDA koma ziphunzitso izizi sizolondola ndi zina za ellen white sizigwirizana ndi Bible.
Tathokoza chifukwa cha comment yanu. Choyamba Ministry inoyo siyampimgo wina uliwonse timalalika Bible ndikusimikiza chowonadi Koma funso ndiloti mwaonella video Yonse Fukwa zomwe mwayika mu comment ndizomwe zilli mu video ndizosiyana! Zikuwoneka kuti mwangowona title ya video ndikuyankha ndi coment. Mulungu akudaliseni
@@edwardphiri6018 Uku ndi kuyankhula kopusa, kusafuna kusutsidwa, ngati simufuna kusutsidwa ndiye muuzane kuti musamayike ma video anu abodzawa. In the OT people rested on the sabbath day, in the NT Jesus is our rest (sabbath) unfortunately mpesa ukufuna utakhala israel pamene ali ma gentiles, ma israel ali busy kumeneyana ndi Hamas osati inuyo, inu ndi manyasa olo mutasunga sabata. Bible limanena momveka bwino kuti chilamulo chinathera pa Yesu. Galatians 3:23-24 [23]Before the way of faith in Christ was available to us, we were placed under guard by the law. We were kept in protective custody, so to speak, until the way of faith was revealed. [24]Let me put it another way. The law was our guardian until Christ came; it protected us until we could be made right with God through faith. Komanso Bible likufotokoza kuti Mulungu anakonza plan ya chipulumutso kusanabwere chilamulo kotero kuti chilamulo sichingasinthe plan ya Mulungu. Abraham analandira chipulumutso popanda chilamulo. Galatians 3:17 [17]This is what I am trying to say: The agreement God made with Abraham could not be canceled 430 years later when God gave the law to Moses. God would be breaking his promise. Lamulo linaperekedwa kwa Moses ndi ayuda chikhristu chisanabwere ndipo linagwira ntchito yake ndikukwanitsidwa chkhristu kapena mpingo wanuwo usanabadwe. Siyani kugona.