And chimene tingaziwe Amalawi ndichakuti kumalawi kuli ma president awiri chakwera ndi chilima kulibe vice president kumalawi and ma president awiri awa akakumana pa ground you know sipangakhale bwino chifukwa ngati wina akufuna kuba k20 billion winayo sangalole kupasidwa k5 million afuna ndalama ifanane chifukwa izi ngakhale inu ndi ine tingapange chimodzimodzi nakonano zinthu zafika potelopa chifukwa kuti azilamula dziko anapangisa ndiwinayo igwilizano umodzi kwanvuta kumalawi utsi bho bho kwaipa sanatitu ma president awiri amenewa