Тёмный

1.SYPHILIS_CHINDOKO CHA MMAGAZI 

CHE MANDOTA COMEDIES
Подписаться 123 тыс.
Просмотров 14 тыс.
50% 1

FOR QUESTIONS 0999374695

Опубликовано:

 

2 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 123   
@MussahHasayam
@MussahHasayam 8 месяцев назад
Km number yanupalibetu apa
@Mbozo_tv_2002
@Mbozo_tv_2002 8 месяцев назад
Kodi munthu wamkulu pa nkhani yokhuza masturbation kd zimakhala ndi effect yotani kuma sex organs and kt uzisiye zimatani plz help me l've been m*** for 5 yrs now l found that l have penile disfaction wht is the connection? Plz help me plz
@Abdurazaq2024
@Abdurazaq2024 9 месяцев назад
Thank you Mr .. koma enafe number yo pansipo sitinaione,, please tipangireni share
@samuelmabulesse1267
@samuelmabulesse1267 9 месяцев назад
Sabata yamawa bweletsani diabetes
@EnockJoseph-c9y
@EnockJoseph-c9y 6 месяцев назад
Bro ndimakunyadirani, inutu mwatithaza Mr
@mussanesterkapanda1417
@mussanesterkapanda1417 9 месяцев назад
This is a welcome development Doc. Nanga mpaka free consultation? You were born to serve and not to be served. Keep it on!!!! Next topic idzakhale ya mauka. I guess anthu akusautsika nawo matendawa.
@pscvideoz
@pscvideoz 9 месяцев назад
Kmano kukayezetsa syphilis voluntarily ananiuza kt sapanga wamba ku KCH,they said unless I'm referred to "the test" by the doctor after the doctor has seen or discovered that some of the signs and symptoms I'm showing are related to syphilis. So you can see kufuna tinali Nako km tinakanizidwa access to voluntary syphilis testing at the KCH as big as it is 😢😢 Don't know what to do know,,, kaya what can be your say doctor??
@blessingsjass9386
@blessingsjass9386 8 месяцев назад
Thanks Dr chikakuda
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 9 месяцев назад
Alhamdulillah taphunzira kwambiri brother Allah adzikutsogolerani ndi kukutetezani inshaallah
@vascowhite4515
@vascowhite4515 9 месяцев назад
Mwatilangiza biggy
@aishaayatu8653
@aishaayatu8653 9 месяцев назад
Ma shaa Allah brother zili bwino mupitilize basi
@jefreykazembe8691
@jefreykazembe8691 9 месяцев назад
Jamil ulemu wako.....God bless you
@BlendaMitambo
@BlendaMitambo Месяц назад
Komas pali zin ati chikaz chimatha kutuluk chachikas ndi zomwez kod
@NyoxyLeman
@NyoxyLeman 8 месяцев назад
Thanks for your advice
@MushychiujaMpaso-f6h
@MushychiujaMpaso-f6h 24 дня назад
Kod syphilis ndi gonorrhea ma sign ake ndiosiyana komaso inu mukugwila ntchito chipatala chakut ndimafuna ndizayezese
@PortipherDkzintola
@PortipherDkzintola 6 месяцев назад
Zikomo kwambiri brother taphuzila nawo may God bless you 🙏
@IsaacTwalibuWitika
@IsaacTwalibuWitika 8 месяцев назад
Thanks boss Che mandota
@MusaAli-pn5yg
@MusaAli-pn5yg 9 месяцев назад
Ndiye ukapezeka kut wachedwa ndiyayikulu mwaiona mochedwa akamalandila akayamba kulandila chithandizo zimatheke kuchila kapena zimakhala kut bas kwatha
@twitikemachangwa
@twitikemachangwa 9 месяцев назад
Kuyankhula momveka bwino doctor Kodi ndizotheka munthu oti akudwala nthendayo Kuti abeleke?
@KhadijaMsosa-d7z
@KhadijaMsosa-d7z 9 месяцев назад
Number yanu bro sikuoneka
@TiyaMitambo
@TiyaMitambo 6 месяцев назад
# mukunenayo sikuonekatu
@kondwanjnrmadengu7752
@kondwanjnrmadengu7752 8 месяцев назад
Mwabwera Doc🙌🙌🙌 komatu # yo ndee sikuonekatu pa screen pa
@mandevukankoto7975
@mandevukankoto7975 9 месяцев назад
Kd syphilis umaitenga bwanji kudzela nkamwa?
@sylvesternamphungo9901
@sylvesternamphungo9901 9 месяцев назад
# mukukambayotu palibepo apa,,nde tipange bwanji?
@MphatsoIron
@MphatsoIron 9 месяцев назад
Natokotatu a dokuta napusila nitutu
@rashiddeula5715
@rashiddeula5715 9 месяцев назад
Apa tikupangani address Ngati Doc sopano osatinso Che Mandota. So next one should be Hepatitis....I think ndika silent killer nako kameneka
@FrancismaseyaMaseya
@FrancismaseyaMaseya 5 месяцев назад
Wawa chemandota 😁 ndimaonera lifidio lanu ku RU-vid yokhuza khani yamathenda a sifilisi ndapeza Kuti zomwe munanena zikundichitikira Moti panopa ndikumakhala ndivuto loiwara iwara komaso kubalalika ndimatuluka silonda Malo obisika Maka pachinena ndipo pakadusa thawi zimasowa zokha opanda kumwa makhwala aliwose komano ndili kutali sindikudziwa kuti palibe njira iliyose yoti ndingapezere thandizo.
@NkhataBayMusic
@NkhataBayMusic 9 месяцев назад
Wow Nice Lesson Mandota❤
@andymisempha848
@andymisempha848 9 месяцев назад
Umakwana
@YusutRashid-po8rm
@YusutRashid-po8rm 9 месяцев назад
Koma # sikuoneka
@ThandiefidesMwalwanda
@ThandiefidesMwalwanda 9 месяцев назад
Kuleka zausatana bas kkkk koma mandota zikomo potikumbutsa ambuye akudalitse
@HendrisonOffice
@HendrisonOffice 9 месяцев назад
Safeka mutuwakulu
@hamzastambuli9420
@hamzastambuli9420 8 месяцев назад
Muli bho Doc Zikunveka bwino kwambiri
@MuhireDominic-rw4vf
@MuhireDominic-rw4vf 9 месяцев назад
Doctor wina wake adandiuza kut ol utavala condom utha kupewa h i v km pali timatenda tina tolimbikira ngat chindoko gonorea nd tina tolimbikira tomwe ol utavala condom umatha kutenga zimatheka bwanj?
@PATIENCEMHANGO-zb6pk
@PATIENCEMHANGO-zb6pk 8 месяцев назад
Week yamawa mutiuzeko za chizonono pliz
@joeedward6545
@joeedward6545 9 месяцев назад
Number plz 😢
@englessanusa5250
@englessanusa5250 8 месяцев назад
Where is your number ,I can't see it
@ChisomoChidothe-fv7yf
@ChisomoChidothe-fv7yf 9 месяцев назад
Thanks mwatikumbusako coz tinaphunzila kale ku primary, timazitenga mopweka nthaw imeneyo
@ChindeChindenga
@ChindeChindenga 9 месяцев назад
Pitilizani kutiphuzitsa achimwene
@apatsakalonga7740
@apatsakalonga7740 9 месяцев назад
Yah mwaitha big mwaganiza bho pitilizani kutiuza za health zi 👍 2024 ma subscribers afika 100k 💪
@EnelessMunthali
@EnelessMunthali 9 месяцев назад
Dr. Chikakuda, ine ndikumangonda kuiwala maka kudzimitsa data ndie ndikufunika kuyedzetsa mwina ndi matenda omwewo 😂😂😂😂😂😂😂
@yammiemakwete
@yammiemakwete 8 месяцев назад
Thanks Doc, tifotokozereni Gonorrhea
@PATIENCEMHANGO-zb6pk
@PATIENCEMHANGO-zb6pk 8 месяцев назад
Zikomokwambili tadziwanawo zambili
@TiahChithope
@TiahChithope 8 месяцев назад
Mauka next wk
@robertmussah4268
@robertmussah4268 8 месяцев назад
Dr Chikakuda we are not able to see your # so if possible can you share it
@CHEMANDOTACOMEDY
@CHEMANDOTACOMEDY 8 месяцев назад
0999374695
@jamesjolichi2026
@jamesjolichi2026 9 месяцев назад
Nxt week mulowe ku chizonono
@asiyatujuma5507
@asiyatujuma5507 9 месяцев назад
Tayamika❤❤
@LindokuhleSongwangwa
@LindokuhleSongwangwa 8 месяцев назад
Program iyiyi ei ndiyabwino zed
@mayah_kandoje
@mayah_kandoje 9 месяцев назад
zikomo
@jonaspatel6225
@jonaspatel6225 9 месяцев назад
Zili bho kwambiri Dr Chikakuda, pitilizani kutiphunzitsa😊
@williammenard48
@williammenard48 9 месяцев назад
I Just support this idea braz pitilizani kutiphunzisa
@JohnMoles-e6h
@JohnMoles-e6h 9 месяцев назад
Zikomo bwana chi kakuda
@wilsonrajab1650
@wilsonrajab1650 9 месяцев назад
Ndazikonda
@kondwanibanda8838
@kondwanibanda8838 9 месяцев назад
In my phone I don't see the number you are talking about please share it
@ConnexManedza
@ConnexManedza 9 месяцев назад
Number palibetu apa Doc
@AhyamieChiwanda-zd1on
@AhyamieChiwanda-zd1on 9 месяцев назад
Doc ineyo Maka pankhani ya tizilondato tinandipangapo ndinagonana mosaziteteza and mapazi mate matentha ndeno ndingathandizidwe bwanji boss
@chiletsobisweck5007
@chiletsobisweck5007 9 месяцев назад
Matenda sachedwa kuwonetsa zizindikilo *timafinya* kwa amuna than akazi why?
@Pungwe123
@Pungwe123 9 месяцев назад
Doc tazakambani za nthenda ya gas ikusautsa nowadays😊
@lloydsimioneseveriano7496
@lloydsimioneseveriano7496 9 месяцев назад
Yah zoonadi
@sainetjackson6183
@sainetjackson6183 9 месяцев назад
matendawa ambil til nawo kma sitimaziwa vuto kuzilimbisa ndi kuopa ku chipatala am one of them , number palibepo tipeze thandizo apa
@samuelmabulesse1267
@samuelmabulesse1267 9 месяцев назад
Zilibwino kwambiri malume
@petermbisa2127
@petermbisa2127 9 месяцев назад
Tapangani ya ma STI onse basi
@JosephNanjala
@JosephNanjala 9 месяцев назад
Nambalayo sikuoneka
@amirirajab8005
@amirirajab8005 8 месяцев назад
Bwelesani ya zipere
@chinsinsimakhuwa1575
@chinsinsimakhuwa1575 9 месяцев назад
Number palibe2😔
@MirriamKalima-q4z
@MirriamKalima-q4z 9 месяцев назад
Mankhwala ake ndi chani
@tamarasibale8232
@tamarasibale8232 9 месяцев назад
Uku nde kudza tidziwe
@Musicfromstreet
@Musicfromstreet 9 месяцев назад
Week yamawa chizonono bwana ❤
@mphatsogregzamadenga5454
@mphatsogregzamadenga5454 9 месяцев назад
The number plz ife number sikutionetsa
@robertmussah4268
@robertmussah4268 9 месяцев назад
Good advice Doc koma # sikuoneka
@IssahMUHAMMAD-i9k
@IssahMUHAMMAD-i9k 9 месяцев назад
Number yo brooo
@LindokuhleSongwangwa
@LindokuhleSongwangwa 8 месяцев назад
Tigawireni Fon number
@BlendaMitambo
@BlendaMitambo Месяц назад
Number taponyan bwana,
@aminikondwani9361
@aminikondwani9361 9 месяцев назад
Zilibwino zimenezi ndipo zizibwera
@mimimangani1999
@mimimangani1999 9 месяцев назад
Zikomo tadziwa
@LaizTabu
@LaizTabu 9 месяцев назад
Nice bro
@OsmanKassim-ec1hu
@OsmanKassim-ec1hu 9 месяцев назад
Munyao opusira ziyan kunena ayaove, 😂🎉
@damuzeylaifos
@damuzeylaifos 9 месяцев назад
❤❤❤❤❤
@jamesjolichi2026
@jamesjolichi2026 9 месяцев назад
Big up bro, mwalongosola bwino!! Mulungu akudalitseni
@DykeMasho-u8g
@DykeMasho-u8g 9 месяцев назад
Boma iroooo
@realsu7816
@realsu7816 9 месяцев назад
Following 🔥🔥🔥 Tadzakambeni za matenda a NOMA.
@SelinaEfraim-hb4pk
@SelinaEfraim-hb4pk 9 месяцев назад
Ayi zamveka,zikomo kwambiri taphunzila nawo.malangizo a ulele kusowa,wakumva wamva osamva akhale❤
@qeavesting062
@qeavesting062 9 месяцев назад
Nde nanga utakhala nayo unga use makhala anji kapena ngatiso ukuzikaikira
@qeavesting062
@qeavesting062 9 месяцев назад
We need assistance please sir
@allimebhaissa2611
@allimebhaissa2611 9 месяцев назад
❤❤❤Mukukwana dr
@khaleedsaidi6232
@khaleedsaidi6232 9 месяцев назад
Ilove you mr chikakuda ❤❤
@frankkachigumba187
@frankkachigumba187 8 месяцев назад
Am gaining knowledge... Thanks DR
@IssahMUHAMMAD-i9k
@IssahMUHAMMAD-i9k 9 месяцев назад
Muli crear bro
@EvangelKautsi
@EvangelKautsi 9 месяцев назад
That's perfect may you explain about diabetes
@BrianMalindima-m4f
@BrianMalindima-m4f 9 месяцев назад
Thanks so much potiphunzisa,,, may the God Lord bless you all the time... Unfortunately number yomwe mukunenayo sitikuiona
@richardbinali9645
@richardbinali9645 9 месяцев назад
Now he is no longer Che mandota he is Dr J S Chikakuda. Iwe ndi dolo adha
@bridgetkaluwa345
@bridgetkaluwa345 9 месяцев назад
Magazi a pa chala nanga sapeleka ma accurate results or what? Please i really want to know
@Zaliro87_Frank
@Zaliro87_Frank 9 месяцев назад
Plz share the number, to my side I didn't see it, other than that thank you Dr
@jacquelinekhumbanyiwa296
@jacquelinekhumbanyiwa296 9 месяцев назад
Nice
@giftdzoole9721
@giftdzoole9721 9 месяцев назад
Thanks for this wonderful lesson Dc Chikakuda
@enockmsakatiza1683
@enockmsakatiza1683 9 месяцев назад
Zili bwino kwambiri tamvetsera mwachidwi. Next time dzakambeni za gas
@VictoriaNyirongo
@VictoriaNyirongo 9 месяцев назад
Ndathokoza man apa mwapulumutsa miyoyo yambili mulungu akudalitsen
@Thandez
@Thandez 9 месяцев назад
Ena amati akazi itha kuchoka yokha chifukwa choti Iwo amapanga ma period.nanga kugwira ma fluid ungatengenso?
@Tikos_Ishmael
@Tikos_Ishmael 9 месяцев назад
You're such a generous person
@CosamPhiri-d1z
@CosamPhiri-d1z 9 месяцев назад
Signs and symptoms of syphilis ?
@RahmaSiraj-ms9gg
@RahmaSiraj-ms9gg 9 месяцев назад
Chemandota zikom kwambili mupitilize kuunikila mtundu wa chimalawi mulungu azikudalisani inshallah
@shaik4123
@shaik4123 9 месяцев назад
Tikayezetsa basi ndithu
@muhammadackleen2487
@muhammadackleen2487 9 месяцев назад
Thanks ❤jameer😊
@vandaichande8294
@vandaichande8294 9 месяцев назад
Ine anandipezako ndi ya magazi koma treatment sindinamalize that time nde ndingatani?
@cyrusnamagonya3265
@cyrusnamagonya3265 9 месяцев назад
Nde mukutiuza lelo😔😔mwaona moyo wanu😂😂
Далее