Keep it up brother... True Malawian fighter... God bless you... Onjeza moto... Osabwelera kumbuyo...tiyenazo zigawengazi.... A Malawi timamva nkhwangwa ili mmutu.... Shame on Mcp and ur so called Tonse alliance... Dzidzete
Information yomwe imapelekedwa ina yasathandiza kwenikweni , anthu ena ali pa south Africa pompa adapita okha koma akuvutika kwambiri ndiye ife tisanamvere chisoni anthi omwe adapita ku Israeli iwo eni ameyenera udziwa kuti akuvutika
ine ndimafuna kuti mufufuze za ndalama zimene natasidwazo popeza kuti a mozesi nkunkuyu anati zithandiza zina ndi zina pa chitukuko za dziko! sopano afotokoze