Zikomo kwambiri Doctor koma ndili ndi funso (FUNSO LANGA NDI ILI) Ine ndimati ndikhakhala pa mtima panga ndikhala ngati kuti chinthu China chakundiphwinda kenako ndimayamba kuvutika kupuma ndima banika kwambiri ndiye chimakhala chili chani please Doctor thandizeni