Тёмный

A Aisha Mambo Alandila 150 Million Kuti Asokoneze UDF - Evance Khaiya 

Nyasa VoiceBox
Подписаться 28 тыс.
Просмотров 12 тыс.
50% 1

On Nyasa VoiceBox, Evance Khaiya claims that Honourable Aisha Mambo, chairperson of the UDF convention committee, has allegedly pocketed MWK 150 million from the MCP to sabotage the UDF's political ambitions.
Pa Nyasa Voicebox, Evance Khaiya wati wapampando wa komiti ya chipani cha UDF a Olemekezeka Aisha Mambo ati apereka ndalama zokwana MWK 150 million kuchokera ku MCP pofuna kusokoneza zolinga za chipani cha UDF.
#malawi

Опубликовано:

 

28 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 80   
@MandalaChaona
@MandalaChaona День назад
Komanso UDF monga Chipani cha Opposition chikhalira limodzi ndi cholamula bwanji ? Pangani mgwirizano wo Koma MCP Will never rule again. God will save His people Mphamvu Zanu zingachuluke bwanji inu a MCP Koma simungagonjetse Namalenga. Lets wait and see.
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy День назад
Amen bwana ❤❤
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 День назад
Amen bro❤
@BrightZionga
@BrightZionga День назад
Kodi opposition ikhala bwanji ubale ndi MCP?
@HaroonSaidi-jv3ek
@HaroonSaidi-jv3ek 20 часов назад
Ku Parliament kuja amatani Always kuzuzula ma mp a opposition
@binalidjeyshabahzombamalawi
@binalidjeyshabahzombamalawi День назад
Osaculusa kuyankhula muzingotipasa uthengawo
@lucianogeoffrey4275
@lucianogeoffrey4275 День назад
Yes, please mukumamalizatu nokhaso nkhani yonse amatero?
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u День назад
Vuto lake Umphawi sizinthu muyaluka nazo Inoyo ndi 2024 osati make zana 1965 kunalibe ma phone 🤳 Facebook
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa День назад
AISHA MAMBO NDI GULU LAKO MUKATHERA KU CHIKANGAWA.BASOP!!!
@adamujosaya-q8e
@adamujosaya-q8e День назад
Aisha mambo pamodzi ndi agaru omwe mwawayitanawo mudzagendedwa nawo limodzi komaso kwabwino kumango njamuka kusayana mkuwononga chipan sha UDF please Aisha mambo pamodzi ndi agaru omwe mukut abwere wo Koma a MCP ndat mukufuna mufike 2025 please don't come there this is oning??
@paulnyondo7572
@paulnyondo7572 День назад
Chipani chamagazi achair anayankhula kale.then ndikuwaitana zowophyatu
@DysonTummiesSajiwa
@DysonTummiesSajiwa День назад
Ndachitsilu inu akayiya chifukwa chair ngakhale amati MCP sichipani chopanga nacho mgwilizano mwayiwala inu kut UDF idapangapo mgwilizano ndi MCP 2009
@NoohNowa
@NoohNowa День назад
Aisha Mambo ndiwadyela😢...amapanga zinthu Ngati sanatuluke kumatako Kwa anthu bwanji 😢😢😢
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani День назад
Ndimaiopa MCP kwambri kupha Chilima ngongole tho fertilizer otchipa chimanga chotchipa eeee MCP mbambande
@McfallenKayuni
@McfallenKayuni 23 часа назад
Kafufuka amene tapeza ndiwakuti UDF siyenda ndi chipani chimene sichili mboma
@AlickSylvester-ro3dd
@AlickSylvester-ro3dd День назад
Ma....activist azaka dzino osadziwa chomwe mukuchita hahaha
@ChrisEnos-to5uv
@ChrisEnos-to5uv День назад
Muthu sungapange dzokozekera ndi m'dani wako kalipokalipo aishawo asatinamize
@HaroonSaidi-jv3ek
@HaroonSaidi-jv3ek 20 часов назад
Indedi uyu analandira mmamuona ku Parliament kuja mmene amachitira she came from opposition koma amayimira mcp ndipo izi ndi zoonadi uyu analowa kale mcp kale UDF wangovala nsalu yo
@PatrickMangochi
@PatrickMangochi День назад
Inu ndale simukudzidziwa,kodi mwaiwala kuti ndi Chair emweyo anasankha Honorable John Tembo kukhala Presidential Candidate wa Mcp/UDF alliance?musamanamize amalawi apa.
@MichaelMpeki
@MichaelMpeki 22 часа назад
Ife chipani cha udf timachikonda koma izi zokhalira limodzi ng'onazi aaaa ndanyasidwa kwambiri. Mcp zoona? Mai ameneyu waganiza bwanji?
@IsaaczidanaZidana
@IsaaczidanaZidana 23 часа назад
Zimene amanena achair nthawi imeneyo MOTi akulu simukudziwa kuti ndiye ndala zakuno kumalawi?zoti nthawi ya achair ena anafa simukudziwa?matafale ndi ena anadwara nthenda yanji?iweyo ndiwe opusa asaye achipani apange zomwe akudziwa,osokoneza ndiweyo
@IsaaczidanaZidana
@IsaaczidanaZidana 23 часа назад
Now muluzi ndi waufulu chifukwa cha mcp,a dpp amamuzunza chair,sukudziwa iweyo,opusa iwe
@NolityKondowe
@NolityKondowe День назад
Zalowa personal tsopano.Mwina anakukani chibwenzi
@MussaChilembwe
@MussaChilembwe День назад
Nkazi ameneyi walandira ndlama zamagazi basi wasatanic imeneyi achoke basi sakufunika ku udf
@IsaaczidanaZidana
@IsaaczidanaZidana 23 часа назад
Ngati si iwe wandale siya zolankhura zandale uzipanga zako
@PatrickChirwa-cv5cd
@PatrickChirwa-cv5cd День назад
Inuyo akupatsani ndalama zingati a DPP? UDF anaipha ndi a DPP osati MCP kuti ikhale ndi ndi aphungu 7 okha out of 36 ku Eastern Region. UDF isaitane DPP ndi njoka.
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza День назад
Achotsedwe di adzipita Kung, ona ko okha, tengerani chitsanzo cha dpp anachotsa anthu wonse osokoneza
@BilaalLalie
@BilaalLalie День назад
I AM UDF MEMBER...AISHA IS ASTUPID LADAY YOU MUST GO AWAY AND IWEYO SIUWINA NEVER UNTIL YOUR DEATH....YOU SEE ZITABU ZIGWIRA NTCHITO PAIWEYO UDZIWANSO.THIS IS YOUR LAST TIME TO BE AN MP
@TwalibiArafred
@TwalibiArafred День назад
Hule ameneyo ngt walandiladi ndalama ku mcp aziwe kut malawi sii yambuye akhe..ife tikuvutika mziko muno UDF ndichipani chathu.iyeyo ndi uhule wakheyo akachitile kunja kwa UDF
@AnnieNyirenda-d5t
@AnnieNyirenda-d5t День назад
A phweka chikangawa aliyese akufuna mahule onse akupita nkonko ku mcp
@PaisonUmali
@PaisonUmali День назад
aisha ndalamazo kadyereni ku mcp komweko tulukan mwaulemu
@SammyChakwana
@SammyChakwana День назад
Achindidwa kangati kuti agulise udf ku mcp pantumbo pako nzimayi iwe
@rashidadan2533
@rashidadan2533 День назад
MULUNGU walinyanyala dziko la malawi chifukwa cha mcp
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma День назад
2019 mesa anaphatikizana lero mukut bwa aaaa muzipaganawo
@Fanzo-h2l
@Fanzo-h2l День назад
A UDF akuyenera kusamala naye nzimaiyu musaiwala kuti ku dpp analiponso anthi amena amasokoneza dpp Anankhimwa atalandira ndalama ku mcp kuti awononge chipani cha dpp a mcp mukhalike komanso Aisha angotuluka achisiye chipanicho iye apite ki mcp ko 150 million ndi chiyani kuti agulitse anthi a UDF ku mcp
@ChikondiChauma-ib9pg
@ChikondiChauma-ib9pg День назад
Koma Dani lu watukwanika pang'ono koma mayiwa mpaka awakumbusa komwe anatulukira ayi zikomo
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete День назад
Komatu ngati UDF yathu ikutha chotchi ndichifukwa cha DPP not MCP
@TwalibiArafred
@TwalibiArafred День назад
amene akunenayo kut inu ndi a DPP ndichisilu komso galu pamozi ndi amakhe
@AchiwaNikisya
@AchiwaNikisya День назад
Ndi zoona a kunena akhayiyazi ine zinandiwawa pitilizani comrade
@Halima-i4x
@Halima-i4x День назад
Inde ayisha mambo achoke ku UDF ndi mayi oipa kwabas aaaa hijabu yabodza bas
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma День назад
Aaaaa ndiwe wabodza amadziwadi iweyo ndamenesudziwa Kodi mesa
@AdamYas-ec9oc
@AdamYas-ec9oc День назад
Ai sha mukunena dzoona akufuna kuononga chipani cha u d f 'choti titsiwe m c p sichipani chabwino chakupa kuba ndi kumangana
@StanelyPhiri-kg1ix
@StanelyPhiri-kg1ix День назад
Comrade you are not Worthy Freedom fighter
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza День назад
Ndalama ndi njoka yayikulu, inamuphadi yesu
@McfallenKayuni
@McfallenKayuni День назад
There is no permanent enemy in politics
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h День назад
😮 mayi uyu ndi galu kwambasi pa nyini pakenso apite Ku mcp galu ameneyu
@MosesTangwe
@MosesTangwe День назад
Mai oipa kwambiri ameneyu musamale naye
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma День назад
Mukunama Kodi audf mesa adpp anathawa.kuudf
@AlgentChilanga
@AlgentChilanga День назад
Iwe mayi ndiwe chidebe cheni cheni chobooka
@Bashir-g1t
@Bashir-g1t День назад
Achoke zachibwa sitikufuna 😡
@jamesbanda8602
@jamesbanda8602 День назад
Ufulu wakupanyo ulinawo iwe galu wamapolo panja
@JosephPhiri-z8b
@JosephPhiri-z8b День назад
Apange achokera limodzi
@AngolanChinga
@AngolanChinga День назад
Aisha mambo inuyo panyini panu pamodzi ndi amuna anuo mapwala awo
@chesterkumwenda
@chesterkumwenda День назад
mcp yisapite kumene tikayigendako
@ahmedmsume1489
@ahmedmsume1489 День назад
Ase umawelenga bwino kwambiri
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma День назад
Sanalakwe ai koma kuzolowera kutukwana
@MoreenHussein
@MoreenHussein 18 часов назад
Ndipo asakapezekekoso,akasonezako
@AlexBanda-d5v
@AlexBanda-d5v День назад
Ee koma achakwera atha Azeru tsopano
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 23 часа назад
Aisha ndi chitsilu cha munthu
@DicksonYohane
@DicksonYohane 12 часов назад
Money is a devil
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule День назад
Mayi ameneyo ndi wa MCP ndi galu
@ShaibuSmart
@ShaibuSmart День назад
Aishah Mambo Mai mulibe chison
@ChisomoBanda-jo4ix
@ChisomoBanda-jo4ix День назад
Nyini yake amenei Aisha ndi m c p yake
@AidantBwanali
@AidantBwanali День назад
Bambo ake analind udindo ku MCP
@UmariBashiri
@UmariBashiri День назад
Ayi MCP sitikuwamfuna
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj День назад
Mcp ndiye kuti mukuiwopatu
@EstherchavulankhomaNkhoma
@EstherchavulankhomaNkhoma День назад
Tadziwa kut ndinu adpp zako
@LoyidKarebe
@LoyidKarebe День назад
Komaanthu atopa tsopano
@bwenzilanga
@bwenzilanga День назад
Uchitsilu mayi inuyo
@McfallenKayuni
@McfallenKayuni День назад
Akutuma ndani?
@MauriceMukona
@MauriceMukona День назад
A Bakili Muluzi analipo ndi Tembo pa mgwirizano koma DPP idawagwetsa pano zichitikansi akalimbila mgwirizano uwu.ndipo tsopano udf iferatu
@IsaaczidanaZidana
@IsaaczidanaZidana 23 часа назад
Sukudziwa
@yassinn5634
@yassinn5634 День назад
Zikudabwitsa ndizakuti anthu onse akukuwa kuwa apapa si a UDF onsewa ndi ADPP. Nonsense nonsenu sindinamve mukusapota UDF amene timamudziwa kuti ndi sapota wa UDF ndi ABDUL basi .Leave UDF alone. Mdani wa UDF ndi DPP si MCP AYI. For your I.nformation mbuli iwe a Tcheya anapangapo mgwirizano ndi John Tembo chifukwa Bingu anaipanga chipongwe UDF. Ndiye DPP ndi mdani number one wa UDF. Usachimvera Chikadeti cha Dpp chimenechi.
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u День назад
Is better DPP than MCP Anthu zimene akufuna kuti azidya katatu osati zonsezo Mukakamba za Bingu ndiye muyaluka Bingu anachita kugula chipani chija chifukwa vice president analipo ndiye palibetso kuyankhula za Bingu Acheyawo dyera kwambiri
@LeonardChinomba-r5e
@LeonardChinomba-r5e День назад
Man ulemu wanu ine ndili kuno ku south Africa koma ndakusatani mu VN yanuyi u spoke well Aish mambo is eival wangovala buyi buyi koma ndi mfiti sakumva chisoni ndi anthu mene akuvutikila son beich
@IsaaczidanaZidana
@IsaaczidanaZidana 23 часа назад
Abro mwanveserayo ndiwamisala
@NolityKondowe
@NolityKondowe День назад
Koma 2009,Bakiri muluzi anapanga alliance ndi mcp.
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani День назад
Ndye zinatha bwanji taswera limodzi tinachangamuka pano ovota ndi anthu osati azavota yekha uyo wankhope ngt mamunayo
@ishmaelsiffah9900
@ishmaelsiffah9900 День назад
Ku constituency komwe amaimila Aisha ndikomwe kumachokera Abdul Lapken anaphedwa ndi MCP uja,zoona amai amenewa angamalimbe mtima kumaitana MCP kuzochitika za UDF zoona,anthu akudera lake azimuona ndidiso lotan maka maka akwachapola kwe Abdul Lapken amachokerako
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 День назад
Shame umunthu alibe ufiti koma eesh ndlama🙌🙌
Далее
Chakwera Will Not Win The Elections - Samuel Lwara
22:19
ДЕНЬ УЧИТЕЛЯ В ШКОЛЕ
01:00
Просмотров 910 тыс.
Se las dejo ahí.
00:10
Просмотров 1,2 млн
JUDICIARY OPEN DAY 2024 LIVE CHE MANDOTA PERFORMANCE
14:19
Moi Uhuru Endorsement
3:27
Просмотров 202 тыс.
Ine Sindingakhale Pamodzi Ndi MCP - Bon Kalindo
18:14
Просмотров 2,5 тыс.
ДЕНЬ УЧИТЕЛЯ В ШКОЛЕ
01:00
Просмотров 910 тыс.