Тёмный

A Lyton Mangochi ajatu uku😂 

Malawian Cameras
Подписаться 17 тыс.
Просмотров 101 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

26 май 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 131   
@blessingsnyalo-rp9ko
@blessingsnyalo-rp9ko 16 дней назад
The dc mwana ooooooooooopysa kwambiri from njeza T/A mabuka mulanje 😂😂😂😂😂 inuyo ndiwaakulu
@mkhulukinyata5198
@mkhulukinyata5198 Месяц назад
Bwana Lyton apatu ndiye mwayalukatu kuposanso kuyenda mbulanda Inu zowonadi kuyankhula komwe mumayankhula podzudzula n'khanza za Tonse Alliance kuja kani inu ndinunso woyaluka chonchi kkkkk
@StevenMbama
@StevenMbama 29 дней назад
Mwayitulutsadi mwachangu guys eishiii uyuyu mukanamudikilila mpaka patsikulimenelo
@OdettaLowrence
@OdettaLowrence 17 дней назад
A Layton mango hi sindikukunxiwani Ndine mwana, kma pakhani iyi mboli zanu, mumve kumene muliko mwayaluka, Mr bornnnnnnnnnnn kalindoooooooooo, kawawa😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@greatalfredlaijah4474
@greatalfredlaijah4474 29 дней назад
koma pano bon kalindo alidi serious kuyimila amalawi, pano even bon kalindo atati ayimile u president ,akhoza kuligwesa boma lilipoli
@JohnRasheed
@JohnRasheed Месяц назад
Good work Mr kalindo
@user-pv9uk6sc3w
@user-pv9uk6sc3w Месяц назад
😂😂😂😂😂😂 wayaluka Mr.Mangochi, ndipo a Banda mwamutha Mangochi tathokoza.
@EmmanuelKalumbiology
@EmmanuelKalumbiology 18 дней назад
You are light people soon i will join you guys
@StevenMbama
@StevenMbama 29 дней назад
Chapusa chigawenga chija chachita kufotokoza kumene chimakonda kugona kkkkk tikachiphulitsile konko uyuu Nde tampeza kkkkkk
@samdiverson9733
@samdiverson9733 28 дней назад
Dccc the most dangerous child from njeza village
@stanleykaludzu-bm4pm
@stanleykaludzu-bm4pm Месяц назад
Ulendo wa ku 2025 ukunka nukomerabe....big up the DC
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Месяц назад
Lyton mau osasawo ngati wadya manyi ankhumba, watibowa hypocrite iwee, amalawi tinakutuluka ndipo sitizamvelanso ma VN ( voice noteless ) ako osasa aja opanda mchele ajaa
@user-xw6ic1gj1p
@user-xw6ic1gj1p 8 часов назад
Good work Mr kalindo ❤
@GrecianWyson
@GrecianWyson Месяц назад
Mwaitulutsa mwachangu audio mpaka akanakakumana athuwo Mmmmm zandiwawabwanji komabe tiyamikire Inuyo amene mukuima pachilungamo keep it up 🎉🎉
@YusufChipojola
@YusufChipojola 27 дней назад
Mwapupuluma bwezi titawona athu a mimbazawo
@alickkachepa3801
@alickkachepa3801 Месяц назад
Kkkkkkkkk kalindo eti ndi wowopya 😂😂😂
@MustaphaCassim
@MustaphaCassim 29 дней назад
Kodi chakwera ndi busa kapena wasataniki? Mc cathy chakwela mbuzi chilima mbuzi nduna zonse mbuzi imodzi imidzi..
@daviekamanga1417
@daviekamanga1417 29 дней назад
waboza aaaa iweee ukungonena sunaziwe yemwe amanena mugwa nayo boma silichoka ili 🎉🎉🎉🎉
@danielmwatchipitsa7442
@danielmwatchipitsa7442 27 дней назад
😢😢😢
@naniibrahim7774
@naniibrahim7774 4 дня назад
Wayithawatu za dola wakana kunena ife timadikila tinve nawo galu wachabe 😂😂😂 appreciate guys let,s be together ❤
@user-ui4ux5kc8d
@user-ui4ux5kc8d 29 дней назад
Mangochi mapolo akoo takudziwa ndiwe chitsiru ndi azimzako omwewo motii mmene tikumzuzikiramu iwe uzipanga zimenezi sure ambuye akukhululukire ndithu ndipo ngati ulindi mzeru usiya uchitsiru umenewu ndiwe galu kwabasi
@EvelynWilliams-ec5fx
@EvelynWilliams-ec5fx 28 дней назад
Mwayi umenewu mmaudandaula bwanj 😂😂😂😂😂😂😂 wina ampaseko ndalama inr
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 Месяц назад
Mr VP amalawi 1st a Masauko Banda zikomo kwambiri poima pachilungamo and inudi mwaima pachilungamo chofuna kuzaombola amalawi pamoto, AMBUYE TITHANDINZENI pantchito yomwe mukuigwira pamodzi ndi Borne Kalindo, AMBUYE amadana ndikukwiya nfi anthira kuwiri monga redson Munlo , ben longwe, lyton mangochi , mozes kumukuyu, chakwela , chilima, zikhale ng'oma , mkaka, chimwendo banda , marther Chizuma , simpulekisi chithyola, yolamu, ndi ena ambiri
@AiameAdamo
@AiameAdamo Месяц назад
Layton Mangochi ndi galu galu woopsa kwabiri.
@DavisKapenga
@DavisKapenga 28 дней назад
@FrankKambwani
@FrankKambwani 29 дней назад
Kuyaluka kuposa kugwidwa ufiti mayi busa😂😂😂😂
@Mickeykasambula265
@Mickeykasambula265 29 дней назад
Eish malawi uja
@user-gq1lj6nc8h
@user-gq1lj6nc8h Месяц назад
Mission failed 😅😅😅😅 mr mangochi
@user-ok7bq9es3y
@user-ok7bq9es3y Месяц назад
Mabodza ngati akazi kkkkkkkk, propaganda iyi yopusa galu Kalindo iwe
@Henry-vw2cz
@Henry-vw2cz Месяц назад
Lyton mangochi 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂kapolo galu
@harrykadango4871
@harrykadango4871 26 дней назад
We say Azaan not Muazzin. In fact, Muazzin is the one who calls people to prayers while Azzaan is the actual calling of believers to go to Masjid and offer their prayers.
@ChimwemwePhiri.1
@ChimwemwePhiri.1 26 дней назад
Ndikape Laiton Mangochi yu............
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x Месяц назад
Lyton tinakutuluka ndi mbava kuchita kukhala ngat simsilamu nayenso ndi mbava yotherati
@PhillipAcquaron
@PhillipAcquaron Месяц назад
Ati munthu woyipisitsa kkkkkkk
@PetroJack
@PetroJack Месяц назад
Kkkkkkk mangochi wayaluka😂😂😂😂
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 16 дней назад
Msu ndiye apita kale asasa koma ukufuna kusokoneza gulu,😅😅😅😅😅
@user-iw6cz5ft2l
@user-iw6cz5ft2l Месяц назад
Layton mangochi wathera pomwepo bas?
@williamsalexmbonga
@williamsalexmbonga 26 дней назад
Nde mijedu imeneyo azibambo akuluakulu ngati inu mupindula chani kodi nde maumboni anu alikuti timve kuti a Mangochi ananenadi zimenezo? Or mukupanga sewelo la Nyuwani?
@AchinaKellz
@AchinaKellz Месяц назад
Akulu akulu kuli mulungu osi milungu osayiwala
@erickhowoya9894
@erickhowoya9894 Месяц назад
😂😂😂😂😂 mangochi alibho, kumachenjera pa town
@JaneMoyo-ws2di
@JaneMoyo-ws2di Месяц назад
Wina ayipe koma zochitika nzimodz. Azbambo uthira kuwiri sumaakhala nza zimayi izi. Kumaona nkhani zokamba pa foni a Lyton
@kondwaniselemani8558
@kondwaniselemani8558 6 дней назад
Chakwera simungamukwanitse mwachepa muuzane nonse ndipo kongelesi ma vote ale ndi achikhalire
@IssahBannet
@IssahBannet 5 дней назад
Mboloyalo wanva napamnyelo iwe
@FauzaTabu
@FauzaTabu 6 дней назад
Muthu oyipitsitsa kwambili ndi ameneyuyu mukunena kalindo
@JosephKeneph
@JosephKeneph 25 дней назад
Awa ndie ma 3dom fight eni eni, not enawa angokula mazila nkabusula bas, mbambande The DC-BON KALINDO Mr President!!
@George-e6h
@George-e6h 9 дней назад
Mbava zokhazokha kuopa kuberana 😂😂😂😂
@islamaameen2177
@islamaameen2177 Месяц назад
Koma Malawi yoh
@GiiiKatekesa
@GiiiKatekesa Месяц назад
Ine ndimazifusa Kut Lyton agakhale ndi nzeru momwe amalakhula munja ngati sipika yalowa nchenga
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv Месяц назад
😂😂km abale
@thomasyohane987
@thomasyohane987 Месяц назад
😂😂😂😂😂😂😂
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv
@AbdulmajeedJbanda-oz3jv 29 дней назад
😄😄etidiyinu
@user-lz4kc5ob1t
@user-lz4kc5ob1t 27 дней назад
umenewo nde umbuli wa mangochi
@giftmandozamkwatula5032
@giftmandozamkwatula5032 11 дней назад
Life yabwanji iyi😂😂😂
@HAMISI265
@HAMISI265 14 дней назад
Munthu oyipisisa kwambiri 😅😅😅😅 koma mangochi
@shealtielmajawa8234
@shealtielmajawa8234 28 дней назад
Mafanaaaaa
@teezdada
@teezdada Месяц назад
Lyton Mangochi 😂😂 anthu amutsika
@Manuel-cm1np
@Manuel-cm1np Месяц назад
😂😂😂😂 malaw to the world😅😊
@user-ek7ny9wi4g
@user-ek7ny9wi4g Месяц назад
Mangochi ndichitsilu chamuthu moti ndakwiya naye
@FefieTenisha-du7ge
@FefieTenisha-du7ge Месяц назад
Great for debunking him... I wish you had maintained your patience until the big fish behind the scene was exposed by Lyton... Next time take your patience until everything gets exposed
@ChristopherMadulira
@ChristopherMadulira Месяц назад
Apap bas galuu wagwidwa app
@bakolomanyenje8360
@bakolomanyenje8360 27 дней назад
Kalindo ndiwachabe ,,, kalindo wants to be consulted,,,, ka share kake ,,
@user-gm9xj1wc2m
@user-gm9xj1wc2m 15 дней назад
Izi ndezachamba
@jamesgama5489
@jamesgama5489 Месяц назад
Lyton mangochi mbala yeniyeni wayaluka.
@simonabraham7241
@simonabraham7241 28 дней назад
How can I get in touch with Mr Bon Kalindo? From Zambia.
@user-zl9vj6hc6y
@user-zl9vj6hc6y 28 дней назад
Namachende kukonda ndalama 🤣
@EdwinBanda-ee1bz
@EdwinBanda-ee1bz 29 дней назад
Kkkkkk
@kelvindickson
@kelvindickson 29 дней назад
Amangochi apa ndye mwatikalkasa padazitu chifukwa cha ichi padakopako nkhope yophyanyikayo
@DawoodIssah-mp1yi
@DawoodIssah-mp1yi 29 дней назад
Malawi 1st You are true people to be followed thank you Mr president thank you Mr Masauko Banda and entire Malawi first organisation.❤❤❤
@user-px9jd9co3v
@user-px9jd9co3v 29 дней назад
DC for ReaL forever
@PatrickMlawe-we3ie
@PatrickMlawe-we3ie 24 дня назад
mangochi 😆😂
@Wilardmavuto
@Wilardmavuto 17 дней назад
@GavenElias
@GavenElias 17 дней назад
Andalenu mmmmmmmm mbava zachabechabe
@danielsulani8689
@danielsulani8689 Месяц назад
❤❤❤❤
@bakolomanyenje8360
@bakolomanyenje8360 27 дней назад
And kalindo was recording ndikuyakhura mwachocho ,,kuti aoneka ngt. Ali serious
@user-vu9rt8gj3o
@user-vu9rt8gj3o Месяц назад
Iwe mangochi ndiwee galu kwambiri
@user-ul1fb4yn5o
@user-ul1fb4yn5o 29 дней назад
Lyton mangochi apa ayaluka kuposa munthu ozikozera akuyenda
@HopeMakoka
@HopeMakoka 25 дней назад
Mangochi wakalambanazo izi kalime kumudzi aise amalawi atopa pano
@DaireMusopa-rh2cy
@DaireMusopa-rh2cy 27 дней назад
But why coming out this early with this info... Tinakaadziwa agalu akumpeza mangochiwo... Mwatilakwila
@AmaliYahaya
@AmaliYahaya 29 дней назад
❤❤❤👍👍
@AbuOsman-ts6ef
@AbuOsman-ts6ef 29 дней назад
Mwayaluka amangochi inu dyera lakuvutani usatana uwo
@user-ky4ce9gb6j
@user-ky4ce9gb6j Месяц назад
Anthu mukudyeleradi eti
@user-gt8nn5ic1v
@user-gt8nn5ic1v 25 дней назад
Mangochi ndiwopusa zedi
@IdressaMussa
@IdressaMussa Месяц назад
The DC ndikatundu wakulu simunthu wachibwan big up
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj Месяц назад
Vp nayeso ndi wadyela uyu anthu wa akufuna ndalama ndiye cholinga chawo
@IshmaelLifah
@IshmaelLifah 7 дней назад
Izoooooooooooo
@JohnOmar-mf2pu
@JohnOmar-mf2pu 29 дней назад
Aaaa!! Malawi wamoto anthu oipa sazatha pamalawi😢
@user-xe3xo5mu9k
@user-xe3xo5mu9k Месяц назад
Alytoni ndimunthu onvesa chison gyz😢😢😢😢 😂😂😂😂😂😂
@wangatawamilolic4140
@wangatawamilolic4140 11 дней назад
Akalindo alibe nzeru anangokula mutu
@AllanChabwela
@AllanChabwela 28 дней назад
Kuyankhula kwabwino
@user-gk6bf7xe9g
@user-gk6bf7xe9g Месяц назад
okay chabwino
@maggiemahewe2728
@maggiemahewe2728 9 дней назад
Muphana😂😂😂😂
@Wilardmavuto
@Wilardmavuto 17 дней назад
yaphedukadi kkkk
@GraceLimani-zw7dx
@GraceLimani-zw7dx Месяц назад
Munakadikila akumana ndi anthu odzaapereka ndalama wo mutaika camera pokumanapo kuti ayaluke zeni zeni mangochi ndi Ben zitsiru za anthu umphawi wapweteka
@user-ww7rx6ke4o
@user-ww7rx6ke4o 29 дней назад
Km nde yatonyoka osati masewera 🙄🙄🙄🙄awawa apwetekana🤔🤔🤔🤔
@BakaliPhili-es3xj
@BakaliPhili-es3xj 13 дней назад
Kkkkkkk yatonyoka? kkk
@user-vl5on2lj8b
@user-vl5on2lj8b Месяц назад
Koma iwe oola nkamwa layitoni usamatipute dala nkhati timakoboli tomwe unapasidwato tinatha usanakwanilise zomwe umafuna shauli yako iweyo ungamakope munthu oti akumenyera ufulu waamphawi? Ndalama zopedza mudzina lomenyera ufulu anthu osauka pomwe ukumenyera mimba yako siichedwa kutha komanso siimapindula tikukuchenjedza mangochi usiru wayambawo usiiyiretu komanso usiye kulimbana ndi president wathu bon kalindo ukuyiputayo ndi minyama pomwe uli waminyama kale .😂😂😢😢😢😢
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk Месяц назад
Nkhanga zaona
@BakaliPhili-es3xj
@BakaliPhili-es3xj 13 дней назад
Zawonadi patali
@user-dt8nr1zx6e
@user-dt8nr1zx6e Месяц назад
Mangochi ndi galu
@OwenNyangu-nv1yt
@OwenNyangu-nv1yt Месяц назад
Bola tadziwa kuti mukumagulidwa pansewu muzipita nokha
@alexgweje8610
@alexgweje8610 Месяц назад
Mangochi Eish mavuto a munthu
@gabrielmaluwa1038
@gabrielmaluwa1038 28 дней назад
Mangochi wayaluka
@JosephKuyeli-rc9on
@JosephKuyeli-rc9on 29 дней назад
Kodi muku jambula filimuu??
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi Месяц назад
The DDDDDDDDDCCCCCCCCCCCC 😂😂😂😂😂😂😂😂
@katalamajames4947
@katalamajames4947 Месяц назад
Layton mangochi ndi mbuzi
@lulukunkeyanih8271
@lulukunkeyanih8271 Месяц назад
Mangochi mmmm mbuzi
@user-ni4nw1ee2f
@user-ni4nw1ee2f Месяц назад
Makhanga zaona
@shonmike-su7qk
@shonmike-su7qk Месяц назад
Layton magochi ndi khuluku all
@emmanuelluhana8608
@emmanuelluhana8608 14 дней назад
All what is happening is Childishness. And taking Malawi as playing ground
@user-tn2qg1vs9j
@user-tn2qg1vs9j 24 дня назад
The dc
Далее
DRIEMO  - TRAILER (Official Music Video)
3:03
Просмотров 5 млн
skibidi toilet zombie universe 33 ( New Virus)
02:59
Просмотров 1,4 млн
Maloto A Bon Kalindo (Part 2) - Bon Kalindo
14:17
Просмотров 75 тыс.
Nzinvereni nokha Samuel Lwara kuseliku😂 😂
22:41
Просмотров 4,3 тыс.
Zomwe Zinachitika Kut Ndege Isowe
5:19
Просмотров 132 тыс.