Тёмный

A MICHAEL USI AYANKHULA ZAMBIRI 🙌🙌🔥🔥LERO PA 4 August 2024 

HOT 265
Подписаться 82 тыс.
Просмотров 31 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 154   
@lastonekaponya7675
@lastonekaponya7675 2 месяца назад
Ameneyu asatinyase ndi WA Congress
@TrynessChirwa-qj5td
@TrynessChirwa-qj5td 2 месяца назад
Ufumu WA Mulungu uwonekere. Mau ogwira mtima. To God be the Glory and Honour
@RitaKainga
@RitaKainga 2 месяца назад
Suppoter #1 wa Chikangawa
@emmanuelchavula7144
@emmanuelchavula7144 2 месяца назад
Dear SKC wherever you are the guy you trusted is no longer value what you planned for young and old generations 💔💔 our hero continue resting well😢💔💔 if it means to take us to promise land through him then God forgive us 💔 you departed un-expectedly ndife athu nditha kukakhula or kuganiza zambiri 💔💔💔 komwe muliko SKC control us spiritually through God intervention. 🙏🙏 we missed you so much at least mukanasiya mau or umboni winawake kuzera mwa ena ake or mulungu oneserani mphamvu yanu potitengera kuchoona 🙏💔❤️🙏
@ChisomoBisani
@ChisomoBisani 2 месяца назад
Osamalankhula kwambiri.muzikumbukiraso kut Palibe amene anakuvoterani
@WisikiBlack-gj4gu
@WisikiBlack-gj4gu 2 месяца назад
Usi zautsilu ife ayi wamva, wayamba ndale kumene , ndalama yoseyi ikubedwa bomamu uzitiuza zakovidi ife ndiza kolela ife manganya ngati ulibe zokamba uzingosiya osamalakhula wamva usatinyasetu ifeeee
@RodgersMhango-ff2nu
@RodgersMhango-ff2nu 2 месяца назад
Zawuchisiru Basi, iwe Micheal usi sungandipange convince kuti ndikamuvotere chikangawa.
@yusufbreak905
@yusufbreak905 2 месяца назад
Iwe usamatchule dzina lachakwela pls ife sitikufuna
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 месяца назад
Koma zeru sizimenezi Big up VP
@JereEdwardMaxine
@JereEdwardMaxine Месяц назад
Mwalankhula mokwana Bwana
@SimonJesimani
@SimonJesimani 2 месяца назад
Kudyera mwazi wa SkC.
@darlingtonbarhazanhie6830
@darlingtonbarhazanhie6830 2 месяца назад
kodi anayikidwa kuti sadzamwalira SKCyo ifesotu tinkamukonda
@limbanikamanga7514
@limbanikamanga7514 2 месяца назад
Chipembezo will remain a potent weapon mu toolbox ya wa ndale wa mu Africa. No wonder, wandale and wamkachisi/wamumzikiti are always pachinzake. Akangosemphana, systems fall.
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 2 месяца назад
Ukurakwisa kumachura mr chikangawa please chonde inu simuntha kuyankhura
@kenmvula2123
@kenmvula2123 2 месяца назад
Inu mukanika kupanga type Chichewa yet you are criticising the VP. Shut up and listen.
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 2 месяца назад
Lamulo lalikulu pamalamulo 10 uzikonda mzako monga uzikondela ameeen ausi
@hazibatizoni9366
@hazibatizoni9366 2 месяца назад
Zanzi...palibepo chanzeru apa
@AndrewKadammanja
@AndrewKadammanja 2 месяца назад
Abale ndale mpaka mu church mupta nazo kut izi, Jesus Christ is the president of presidents, Judge of Judges, please, please 🙏🙏🙏. Muzwakonzera masku apadera anthu awa osamaphatikiza ndzaumulungu please let God be God
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 месяца назад
Chakwera My vote
@frezarphiri3480
@frezarphiri3480 2 месяца назад
Kodi uyu aziyenda mu BT mokha?? Or ngongoleyo azipeleka ku anthu aku BT okha ndiwo A Malawi??
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
ndipo mzimu wachirima ukugwira nthito mitu yabararika anthu awa tisaname sukuyenda vote yanu kuribe
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 2 месяца назад
Zazii nawo awa akafula
@AliceChipeta-pc3nb
@AliceChipeta-pc3nb 2 месяца назад
Inu zaboma ndi church zikungwifizana pati
@RowlandChimzimu
@RowlandChimzimu 2 месяца назад
Palibe chazelu chimene walankhula uyo
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
wabararikatu uyo vp chikangawa akusekerera kutcharitchi akumenyaso kapeni wabararika usi wamphetsa wathu imwekazitape
@giftkamwiyo9175
@giftkamwiyo9175 2 месяца назад
Mbuzi yamunthu
@TiwongeChikhoza
@TiwongeChikhoza 2 месяца назад
Kugoyakhula za nonense basi amalawi ukutipangitsa ndi uphawi ndithu ,coz palibepo chanzeru ayakhulapo apa
@Aisha-db6ds
@Aisha-db6ds 2 месяца назад
Inu ndiye aiso
@mikegobede3830
@mikegobede3830 2 месяца назад
Zaziiii
@LouisNgowera
@LouisNgowera 2 месяца назад
Koma zoti winawake anadzeetsa mavuto akuthawira Ku Nenevi mu sitima ukuzidziwa?Phepo NDI mafundo zidatha atamuponyera madzi kumezedwa NDI nsomba ukudziwa iwe Manganya
@VanPaul-sv9yx
@VanPaul-sv9yx 2 месяца назад
Waboma analenga dziko za nziiiii dziko ndila Mulungu ili
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
akufuna chakwera azimuyamikira uzavota wekha uyo
@PETERSINKADZIWA
@PETERSINKADZIWA 2 месяца назад
Mfundo zake zosagwira Mtima
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg 2 месяца назад
amanganya kampeni ndikutchalitchi komwe 😂😂😂 komatu inu muzindikila zomwe mukulankhulazo mutasowa nazo mayankho usi ulibe chikondi ndipo anthu akutukwanadi sunati
@DanielPhiri-u5x
@DanielPhiri-u5x 2 месяца назад
Vp u r really true 👍
@FrankChione-k6m
@FrankChione-k6m 2 месяца назад
Ndamuvetsesa Michael Usi kuti ndiwa MCP ati campaign kwa Chakwera, misala yake
@Alinafe-o1u
@Alinafe-o1u 2 месяца назад
That's why I like this man
@KHUMBOH
@KHUMBOH 2 месяца назад
Just the right person for the job in such times
@TrynessChirwa-qj5td
@TrynessChirwa-qj5td 2 месяца назад
Mau okoma,a VP Mulungu alandire ulemu ndi Matamando ukulu wanu Mulungu uwonekere ...mu Dzina la Yesu Khristu
@Shys-t7e
@Shys-t7e 2 месяца назад
Iyenso anagwilitsidwa ntchito ndi satana pomupeleka nzache chilima, ukuona ngt anthu sakudziwa, mbuzi ya munthu iwe
@HashoAlfred
@HashoAlfred 2 месяца назад
Kod akuti chani ameneyu?
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 2 месяца назад
Ndichifukwa mulibe manyazi kuti chilima anakupangilani chani komatu 2025 ili kubwela brother
@HenryManda-m9h
@HenryManda-m9h 2 месяца назад
Koma Utsi kunena zoona u vp sakukwana, zoona vp anganene kuti dzikoli eniache ndi ama church ndi boma uyudi bolaa drama aja amapanga koma za u vp ndiye panja angochitadi kumukokerapo
@josuasitima
@josuasitima 2 месяца назад
chikangawa ,kuvala chikopa cha khosa km ili mimbulu yoopsa
@ErnestChansa
@ErnestChansa 2 месяца назад
Tisamatukwane bwanji Kwa anthu afiti oipa mtima omwe anapha mzimu ya anthu osalakwa akuzuza anthu amoyo Iwo mabanja awo akusangalala pomwe ena akufa ndinjala ponyelela pa president chakwela mumuwuze
@SildaKatundu
@SildaKatundu 2 месяца назад
Bwanji sanamukonde Chilima chakwerayo ?
@SaidSamuden
@SaidSamuden 2 месяца назад
Kod amanganya palipose chakwela mukutchule simungayakhule osanenapo za chakwela
@giftmasenti5732
@giftmasenti5732 2 месяца назад
Ma glass munagula nokha kapena munatenga Kwa malemu? Ngati munagula nokha munagula aakulu kaguleni size yanu😂😂😂
@GoodluckVithumbiko
@GoodluckVithumbiko 2 месяца назад
komaso ndi mbuzi yotherathu ndaramazo koma kunkhata ndarama kubomako abare
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 месяца назад
Kodi kungokhala osapanga comment ngati zithu zakunyasani bwanji koma kutukwana chingakupindulireni ndi chani chifukwa izi sikuti iwo amava zawo zikuyenda ntchito akugwila
@MpogoroMwikoko
@MpogoroMwikoko 2 месяца назад
Vito MALAWi sanje ndi kaduka musiyeni maiko usi naye akhale vp AAA MALAWi zosiyirana izi AAA
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 месяца назад
Michael usi amakwana
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 2 месяца назад
Amen dr usi
@LAZARUSCHAPAMBA
@LAZARUSCHAPAMBA 2 месяца назад
Kuyesesa kuzikokelera koma sizikuthekabe😂😂😂. Kodi unali ulaliki, kapena Nthawi ya zolankhula-lankhula?
@MasterMapira
@MasterMapira 2 месяца назад
That's ZEC My Church.... Very Beautiful ❤️... More fire 🔥🔥 Hot 265
@zondanitzulumusicfly.5202
@zondanitzulumusicfly.5202 2 месяца назад
The speech of supporting evil.
@ClementSakala-s2k
@ClementSakala-s2k 2 месяца назад
Manganya ponyankhula fundo zake zonse ndi drama poyankhula
@LindaNkwazi
@LindaNkwazi 2 месяца назад
Don't forget Chikangawa iwe
@EugeneMatope
@EugeneMatope 2 месяца назад
Ok! Chifukwa Cha chikondi ndiye ife tizikuyimnirani mmanja mukulephera kukwaniritsa zomwe mudalonjeza? Maganizo opepera ochokera Kwa vice president. Worry not one year remaining
@MosesSolomoni
@MosesSolomoni 2 месяца назад
Mukaitanidwa kuma Church osamakamba za boma kapena za chakwela ai
@PaulineKamwana
@PaulineKamwana 2 месяца назад
Uyu ndie ndi panja peni peni cx munthu sangamalankhule zopeperazi m church .anachimwa ndi chikangawayo posiya kutumikira Mulungu nkusankha ndale
@Kamwachale
@Kamwachale 2 месяца назад
Funso komwe akufunsa amalawi kuseriku nlakuti Kodi anthu omwe akukukondani inu a Michael Usi azapereke Mavuto Anu Ku UTM kapena Ku MCP yankho liri lonse lomwe mungapereke perekani zifukwa zake
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 2 месяца назад
Munthu samadedwa ndi anthu onse. Inu mutha kumadana naye Usi pazifukwa zodziwa inu. Anthu ena asadane naye chifukwa chakuti inu mukudana naye. That's life.
@tamalangoma2765
@tamalangoma2765 2 месяца назад
Zoonadi ,nsiyeni mulungu akhaledi mulungu, nasty politics won't help Malawian. Our VP said it all.
@ShillahChisi
@ShillahChisi 2 месяца назад
Ndale ku church mmmmmm mwaonjeza
@MoeshahIbrahim
@MoeshahIbrahim 2 месяца назад
He is a good guy only that his senior is the problem
@HaliJana
@HaliJana 2 месяца назад
KOMA USI MACHENDE WAKO WAVA IWEYO UKUMACHULA DZINA LA MULUNGU BWANJI MZIMU WA CHILIMA UKUZUZIKA IWE
@Martinmkapangakapanga
@Martinmkapangakapanga 2 месяца назад
anachimwa ndi chakwela anatenga boma mwakuba mulungu anakwiya
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg 2 месяца назад
mukungogawa ndalama 😂😂 koma guys
@HurmlysLangwan
@HurmlysLangwan 2 месяца назад
Anachimwa chakwerayo
@SamuelMthengo
@SamuelMthengo 2 месяца назад
Siza social media,muja achakwera ankati 2025 ndiyimanso chilima alipompo muja inali social media?iwe usatipusitse wamva!
@bysongeorge3243
@bysongeorge3243 2 месяца назад
A VP pitaninso ku Lilongwe mukayenderenso ma Church ndi Misika after that mupitenso mukayendere anthu ku Mpoto....kkkk
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 2 месяца назад
AKUONA NGATI KUPEZEKA KU CHURCH MULUNGU AKUKHULULUKIRANI MUTAPHA CHILIMA AGALU INU MANGANYA NDALE SIMBALIYAKO PITA KU TIKUFERANJI MFITI YACHABE CHABE IWE PETRO OMPEREKA YESU
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 2 месяца назад
Uyu alibe mzelu mbuzi ya munthu uyu mwamudziwa lero yohova galu wacheba cheba
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 2 месяца назад
Koma akulamulilabetu ngati sumufuna igosamuka pamozambiq mpafupi pitani
@darlingtonbarhazanhie6830
@darlingtonbarhazanhie6830 2 месяца назад
iwe unamva kuti samamudziwa Mulungu, Galu ndi iweyo
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg 2 месяца назад
ndikuona anthuwo akuyankha kut anachimwa ndichakwera pomuthawa mulungu simunati ndipo nzeru zikuchokani
@AlexMwambayiGriffin
@AlexMwambayiGriffin 2 месяца назад
Inu lakhulan zogwira mtimat,sanje zokha zokha bas
@HamidMasamba
@HamidMasamba 2 месяца назад
Ochimwa ndi chakwera yemweyo coz anasiya ntchito yake ya ubusa kukayamba ndale, nde mulungu wakwiya naye ndipo akufuna awonese ukulu wake pa chakwerayo. Iyeyo si mulungu ayi, komaso amalawi si ochimwa, mr chikangawa nde ochimwa
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 2 месяца назад
Woipa amabisala nchurch,usamànene za MCP NDI chakwera m'busa wonyenga wakupha.chilima,ndiwe amene chitsiruu Satanayo ndiwe galu.uku tenga za zisuzo kupita nazo ku church, mpamene uku mango imba nyimbo za kuthezo pa msonkhano mbuli mbuzi ya Munthu Iwetu si president adaku sankhula ndani?mbava inzako chakwera mu ulure amene adapha Chilima,ankhandwe Inu,mu charichi simo ya nkhula za m'boma Wanthu aSatana Inu,mu ulure za imfa Ku Chikangawa mbuzi inu
@MpogoroMwikoko
@MpogoroMwikoko 2 месяца назад
A dpp chilima amamunyoza kwambiri wamwalira ayamba kumuyamikira zichani zimenezo. Mukuwona ngati achina kabambe ndi a utm aja ndima supporter's a dpp kuyambira kale kale mumupase u president muwone mugulisa chipani
@arnoldsimfukwe-d5c
@arnoldsimfukwe-d5c 2 месяца назад
Uzilalikira za kuchikangawa
@BrightZionga
@BrightZionga 2 месяца назад
Kkkkkk Mr 1 and 1 chakwerayo ndi ndani achitsilu awanso paliponse ine ndi chakwera 1 and 1 meaning
@JimmyIsaac-xd4ef
@JimmyIsaac-xd4ef 2 месяца назад
Kodi amapitila ulaliki kapena ndale
@JamesIngeni-ku3qj
@JamesIngeni-ku3qj 2 месяца назад
Chikangawa 2
@SueWahna
@SueWahna 2 месяца назад
Kod mazenerawo amakhwepa😅😅😅
@JohnKaudzu
@JohnKaudzu 2 месяца назад
Likonzedwa dzikoli but not anthu Ake inu.Munthu sungasinthe zithu ngat iweyo sunasithe
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 2 месяца назад
Kodi ndikumapemphero,,osanenako zolimbikitsa anthu bwa,,mwapeza nyumba yaulere,,galimoto komanso ndalama,,mungakumbukenso komwe mwachoka
@masianobrighton
@masianobrighton 2 месяца назад
Mulekeni micheal usi agwire ntchito yake musamupepuse umphawi amauziwa mkuluyu
@masianobrighton
@masianobrighton 2 месяца назад
Zotukwananazo enafe zatikwana ndipo sizingakonze zithu olo kumanga ziko kodi mukufuna chilichonse chiziyenda momwe mukuganizira inu mmmmm ai ziko sasenza limakuphinja
@estherkambewa7791
@estherkambewa7791 2 месяца назад
Tili masiku otsiliza, oipayo sagona tulo, kufunafuna oti amulikhwire
@AnnaPhiri-b8t
@AnnaPhiri-b8t 2 месяца назад
Awa ndie ayiso
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 месяца назад
Aaaa palibe chikumbvekapo apa maiko ambiri kunali cyclone sikuti ndi Malawi yokha koma maiko anzathu wo bwanji akuyenda? Muli pamaso pa Mulungu mudzinena chilungamo
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 2 месяца назад
Bolansotu Malawi kwinaku kulipepani
@ManMen-kp2ze
@ManMen-kp2ze 2 месяца назад
Koma ziliko , chaka chinoo, kodi ndi campaign kapena ulaliki, kapena drama?
@LindaNkwazi
@LindaNkwazi 2 месяца назад
Bwinotu bwino
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 2 месяца назад
Manganya siyani ndale mukapitilize zisunzo chonde kuti mukalowe bwino ufumu wakumwamba please
@edsonphangula5817
@edsonphangula5817 2 месяца назад
Wonderful speach akunena zoona
@HestingsZiba-d6k
@HestingsZiba-d6k 2 месяца назад
Mwapha chilima skc kuti mutole ufumu munya muwona zaboza basi
@wanangwamwafulirwa8839
@wanangwamwafulirwa8839 2 месяца назад
VP sakuziwa chomwe akufuna kunena.....fuduless, kumpeleka zake kut azanjoye ndiye pampandopo. Chiuta yekha abakwapulengi
@mikegobede3830
@mikegobede3830 2 месяца назад
Kumpingo mwapitisako ndale
@MichenkMalichi
@MichenkMalichi 2 месяца назад
Usi mapaxiako
@cassimyusuf6683
@cassimyusuf6683 2 месяца назад
I like kuti tonse ndife akuda ndilankhula chichewa
@GabiBanda-r3o
@GabiBanda-r3o 2 месяца назад
Iweyo sukarowa ndi chikangawa
@MabvutoMichaelPanagona
@MabvutoMichaelPanagona 2 месяца назад
Wabodza Michael usi ukupanga kampeni
@EmilyBanjachikwatula
@EmilyBanjachikwatula 2 месяца назад
Ochimwa ndi amalawi pomuvotela DR chikangawa
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 2 месяца назад
Ife sitinachimwe nawo
@Kenmoney-xp7tz
@Kenmoney-xp7tz 2 месяца назад
Chitsiru uyu okondedwa amakubela? Kodi galu ise ndalama zakuba zakupengetsa eti
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 месяца назад
Ndichisiru manganya chome wachabe chabe palibe chomwe ukunena apa iwe galu kwabasi
@BrianMakonda-bw2ux
@BrianMakonda-bw2ux 2 месяца назад
Manga kuyankhulapo
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 месяца назад
Kodi muli ku Church kapena ku zitsunzo
Далее
#kikakim
00:17
Просмотров 7 млн
Zifukwa zomwe Brian Banda anachoseredwa ntchito
9:55
Просмотров 145 тыс.
Malodza Akuchikangawa A Poem by Sir Michael Benjala
5:00
FREDOKISS KUYANKHULA MOSAOPA
12:33
Просмотров 9 тыс.
#kikakim
00:17
Просмотров 7 млн