Тёмный

ABWANA PAULENDO - BLESSINGS CHIMANGENI 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 62 тыс.
Просмотров 42 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

11 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 224   
@FaroukSaliem
@FaroukSaliem День назад
Chikangawa ulendo, watsala chimwendo. Dzina langa ndine FAROUK SaLIEM. Kuchokela mu mzinda wa Lilongwe. Ku kasiya. Ondifuna ndilipo nditu. Thaxs
@brianjames211
@brianjames211 День назад
Those who live their life by the sword they'll die by the sword, God has said it all
@dalitson3558
@dalitson3558 День назад
God help us we’re going through a lot tikuvutika chifukwa anthu ochepa
@kennethnasteve4721
@kennethnasteve4721 День назад
This song reminds me BINGU once this song come out that means something big happens 😢
@MtendereChimbuto
@MtendereChimbuto День назад
It came out in 2007 0r 2008
@JemaxChibwanazulu
@JemaxChibwanazulu День назад
Exactly
@ellensambo6323
@ellensambo6323 День назад
😢😢 nyimbo iyi mmmmm Ambuye ankhuze Malawi
@kingstonekalonga8435
@kingstonekalonga8435 День назад
Achimwendo Mulipo koma kumeneko kkkkkkkkkk azanu oipa mtima ndamenewo ikwaswndera ifa 😂😂😂😂😂
@lawremmakanyenda3390
@lawremmakanyenda3390 12 часов назад
Manyazi bwanji
@kasimmussa-c5v
@kasimmussa-c5v День назад
Ambuye please tengeni satana ameneyuu 🙏🙏🙏
@victorauwana7258
@victorauwana7258 День назад
Komatu ndiye lelo ndilezela ,,, nananangati wafa mmmm ayi munthuyu wawononga ziko
@AmissKumakanga
@AmissKumakanga День назад
Ineyo panopa misoz yachimwemwe irimasaya mwanga murungu atimenyera khondo❤❤❤❤
@ronaldordinga6537
@ronaldordinga6537 День назад
@@victorauwana7258 anthu mkuyankhura ngati MLI ndi umboni oti munthu wamwalira bwanji
@wisdomsadyalunda2001
@wisdomsadyalunda2001 День назад
you can say that again umamwa chani ase kkkkkkkk
@benzobanda-ed8tp
@benzobanda-ed8tp День назад
@@AmissKumakanga kodi ndizoona zoti wamwalila abale
@OdetaGidypro
@OdetaGidypro День назад
Zoti akudwala ndizoonad, stroke. Ndaonera sabc news koma sanakambepo zot wamwalira ayi. Ndiye zinazi tiyen timusiye Mulungu akhale Mulungu basi
@PeterNamphwanya
@PeterNamphwanya День назад
Tivine kaye koma otsaiwala mother's day ikubwela🎉🎉🎉🎉🎉❤❤❤❤
@SamuelMtambo-p1z
@SamuelMtambo-p1z День назад
Straight
@BannetMwale
@BannetMwale День назад
I
@MoosaSidrick
@MoosaSidrick День назад
Komabe apete watikwana athu Akufa ndi njala usiku onseu ndimangopephe kuti apite ndithu tikapeza komweko achilima Ali paseu akukudila abwana
@RuthTimothyChirwa
@RuthTimothyChirwa День назад
I like this song keep it up my brother ❤❤
@EphraimNyirenda-e3s
@EphraimNyirenda-e3s День назад
Nyimbo iyiiiiii ikangolila ndkt China Chake chachitika😭😭😭
@BlessingsCperumal
@BlessingsCperumal День назад
Are u seriuos
@GraceMakawa-b8e
@GraceMakawa-b8e День назад
Ndipo zoona
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg День назад
Ambuye please chakwera mtengeni akuchinda akazi ayeni
@vanessachimbayo1247
@vanessachimbayo1247 День назад
Zoonadi mpaka pamenepo
@BlessingsTembenu
@BlessingsTembenu День назад
Kkkkkk koma ndaseka,ameneyu atsogole basi
@HawaMamo-q2v
@HawaMamo-q2v День назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂koma abale
@EstherMaonga
@EstherMaonga День назад
Ine ndimafuna asafe nsanga azamangidwe kaye ndikuyankhanso milandu
@HestingsChibalo
@HestingsChibalo День назад
Ndipo inu aaaa😂😂
@MarkManyowa
@MarkManyowa День назад
Akamwalira nanga ndalama asiila ndani🤦 Zimangoona kuvuta koma kuzikonda kuja nkosapindulitsa
@festongreston
@festongreston День назад
Let the will of God fulfill
@IdressaMussa
@IdressaMussa День назад
Chakwera 💔💔💔💔💔 ayende bwino 🎉🎉🎉🎉🎉anali oyipa ngat 🎉🎉🎉kambuku 🎉🎉🎉🎉🎉🎉 nyimbo 🎉🎉🎉🎉🎉ya chakwera 🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@TamaraSeleman-cl2fc
@TamaraSeleman-cl2fc 17 часов назад
boma ilooo ife sitikusintha boma nkhalamba ikagwere ukoo chakwera oweeer
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza День назад
Apule mungamuphe mzanu atagwira colona zoona? Colona ndi woopsa lero ndi zimenezi dzakutsatilani, ngati zikumbvekazi zili zowona
@RaheemNgoma-pk1ev
@RaheemNgoma-pk1ev День назад
Kamajete next
@mariamahamadu8402
@mariamahamadu8402 День назад
Nde Mene dzatelemu Dani Lu mukuti bwanji apatu nde ndalama dzija simudya kujijilika umakagwa matope mubwelelaso kwa Dade kapena Mwangi Taya thawi pachabe 😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@pemphokatembe443
@pemphokatembe443 День назад
😂😂😂😂😂😂😂
@rashidadan2533
@rashidadan2533 День назад
What goes around comes around
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 День назад
Iyi ndiye tiyivinadi 😂😂😂😂
@AugustineChimaliro-e5i
@AugustineChimaliro-e5i День назад
Achimwendo mwazukako bwanji nthupi
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os День назад
@@AugustineChimaliro-e5i kkkkk
@AngolanChinga
@AngolanChinga День назад
Kkkkkkk km guys
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 День назад
Paja amalondola misonkhano yanzawo tiyenitu ku chinamwali kuzomba kuli msokhano lero 😂😂😂😂
@fannyzimba149
@fannyzimba149 День назад
😂😂😂😂😂kamaliremba kkk ndi mzake Jezebel kkk
@TiwalumbeNathan
@TiwalumbeNathan День назад
Let GOD BE GOD
@thomluciouss7360
@thomluciouss7360 День назад
Oyenda ndilupanga azafatso ndilupanga,palibe wamuyaya pa dziko ask kamuzu Banda
@HassanSaid-q8q
@HassanSaid-q8q День назад
Yaaa pano ukuona bwanji kumene uliko..mulungu siosewela naye
@AdamuKasimu-x5o
@AdamuKasimu-x5o День назад
Kukhuyu mukumva bwanji tupimo😂😂😂😂😂😂
@omarajibu860
@omarajibu860 День назад
Very educative song
@ThomsonChipwele
@ThomsonChipwele День назад
Akafa tisangalala
@zelliachamboto5744
@zelliachamboto5744 День назад
😂😂😂
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 День назад
Tizika janza nyimbo yomweyo pa bingu stadium
@ChristophrMaiko
@ChristophrMaiko День назад
Nditangomva izi inenso ndimaiganizila nyimbo yomweyo eeee koma tivine kaye mowa uli pambalipa
@JosephHill-fy1bb
@JosephHill-fy1bb День назад
Commission of enquiry ija anakoza
@KettieNathaya
@KettieNathaya День назад
Chikangawa hoyeeeeeeeèe ukawapatse mon anthu 9 aja
@LameckNgwangwa
@LameckNgwangwa День назад
The more u plant the more u harvest
@JemaxChibwanazulu
@JemaxChibwanazulu День назад
Mau akulu akoma akagonera.
@jennyx6914
@jennyx6914 День назад
kulsmkhula mwachikulu good msg like it ndipo ndskumva though ndine mtinga based in joburg
@rodgerstembo7866
@rodgerstembo7866 20 часов назад
Amen what you plant is what you harvest
@VeronicaKelias
@VeronicaKelias День назад
Mulungu salakwitsa watilanditsa ku mimbulu imenei ngat ndi zoona ai zakhala bwino akanatitha tose koma ambuye atilanditsa
@DanfordMkalimbaBanda
@DanfordMkalimbaBanda 19 часов назад
Kuthawa ntchito yamulungu, koma imfa siithawika
@EmmanuelNtago
@EmmanuelNtago День назад
Am enjoying reading comments than listening to this music
@nuhiabwanali-jo5eq
@nuhiabwanali-jo5eq День назад
That's true bro
@WisdomChimalizeni
@WisdomChimalizeni День назад
Nyimbo ilibwino iyi🇲🇼 oyimba analosera kale
@JeanKambala-gm1zr
@JeanKambala-gm1zr День назад
Wafa imfa yabwino ameneyo yosadulidwa miyendo muyende bwino ,,imfa yosavulidwa jekete ayi zikomo mngwilizano unja Kuno
@MemoryChaima
@MemoryChaima День назад
Ngati zili zoona ambuye kumwambako mwamva mapempelo akatolika tonse tipange mpwando anatimpela munthu wosalakwa mfiti imenei
@BonfaceMpokosa
@BonfaceMpokosa День назад
Ndikhale mbuli ine chete
@user-nt5yn2im6t
@user-nt5yn2im6t День назад
Thanks Lord
@ElizabethMajiga
@ElizabethMajiga День назад
Mulungu amava ndithu
@MustapherLino
@MustapherLino День назад
Get well soon mr chakwera,we still need u
@AliceGeorge-il6ig
@AliceGeorge-il6ig День назад
Oooh,Ambuye atiyankha bas,,Linali pembedzero langa la kolona
@trickermussa472
@trickermussa472 День назад
Or angoika komko plz
@PaulNyirenda-d7k
@PaulNyirenda-d7k День назад
There is no guarantee in this earth
@LonjezoChitseko-lx4qb
@LonjezoChitseko-lx4qb День назад
Akafa ntendere ufika mmalawi
@RoyTrading-b4x
@RoyTrading-b4x День назад
Blessings Chimangeni on repeat 🎉🎉
@AllenBanda
@AllenBanda День назад
Only God knows
@mariamahamadu8402
@mariamahamadu8402 День назад
Mmmmm chikangawa mudzimu yawanthu 9 ija ikukudikila
@nuhiabwanali-jo5eq
@nuhiabwanali-jo5eq День назад
Koma di azi pita, akayankhe zomwe ama phela anthu pa dziko la pansi osalakwa.
@ThomasChiwaya-qx9mf
@ThomasChiwaya-qx9mf День назад
Ndikufuna Charly patache choipa chisata mwini
@Mpungwe123
@Mpungwe123 День назад
Iponyedwa imeneyo bwana khalanibe pompa zitheka ndithu
@issahmaloto9141
@issahmaloto9141 День назад
Ndichita choyenda maliseche lamulungu lino
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os День назад
Mpaka kuyenda maliseche😂😂😂😂😂
@samchibenene4458
@samchibenene4458 День назад
😂,,,
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole День назад
Ukayamba ndi zomwezo umamaliziranso zomwezo,kuyamba ndege kuikwera eeeee mkutsazikana nayonso.
@KassimWilson-g6m
@KassimWilson-g6m День назад
Abwana paulendo akajele kumwamba ndrama zakubazo 😂😂😂😂
@meganabigail-ye7fw
@meganabigail-ye7fw День назад
Nyimboy simatuluka wamba ikatuluka choncho kumakhala kuti wina Akuonana maso ndi maso ndi anthu omwe anasogoza.
@patricksamson4852
@patricksamson4852 День назад
Tidikire ntanyiwa
@FlorenceDouglas-x5c
@FlorenceDouglas-x5c День назад
Koma ma comments ali apa mmmmm 😂😂, ine lelo ndiumwa mowa size kukana pati !!!! 😂😂
@JosephIsaac-s1c
@JosephIsaac-s1c День назад
Best song ever, once I hear this song I feel cry
@EsetaGerate
@EsetaGerate День назад
😂😂😂😂😂 komatu mukhalike Kodi chikangawayo wafa kapena chani 😂😂
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 День назад
Ineyo sindufuna afe,, koma akhale ndi moyo kuti adzazione ndi maso
@EsnartGirivin
@EsnartGirivin День назад
Rip chakwelq
@Richardbanda-hg6pt
@Richardbanda-hg6pt День назад
Let's pray for Malawi something happen
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn День назад
NDILI KU MSIKA NDIKUDIKILIRA CHI GALIMOTO CHA NKHUKU😂😂
@LameckLubanimbewe
@LameckLubanimbewe День назад
Palibe wa muyaya
@LinlyMatheweKufakwina
@LinlyMatheweKufakwina День назад
😂😂😂😂aaaaaa komatu Malawi muli ndi chipongqe iiiii
@KhadijaMsosa-d7z
@KhadijaMsosa-d7z День назад
Amalawi sititha kucheza😂
@NancyLennoh
@NancyLennoh День назад
Kmanso tili pa changu kwambiri 😹🙌🙌🙌
@AbdulrazaqHussain
@AbdulrazaqHussain День назад
Let's wait for news, no speculation, here,l love mpungwe pungwe coz only the truth comes out on this platform, so let's wait 4the updates
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka День назад
Mulungu salakwitsa kalikose akuwoneni pomuyika aliyese ukhudzidwa pa ifa ya chilima
@ChristophrMaiko
@ChristophrMaiko День назад
Ngati zili telo mulungu asakamulandile ai galu ameneyo watizunza kwambili
@EyobeAyala
@EyobeAyala День назад
Koma guys zoonad izi kapena ndikulota tandizuseni ine
@JrAlfeoLungu
@JrAlfeoLungu День назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂 ndipo isaphonye ikulondola ndiku garden city
@nuhiabwanali-jo5eq
@nuhiabwanali-jo5eq День назад
But guys tell us what's going on,, '" its. true story that president Chakwera died?"
@JuniorHala-vf9ov
@JuniorHala-vf9ov День назад
Osamasewela ndangoni amene anapanga nao program yokupha chilima paulendo bwezela agwile ntchito yake apa
@MonijaKataika
@MonijaKataika День назад
🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔🤔 😭😭😭😭😭😭😭😭😭 🤐🤐🤐🤐🤐🤐🤐🤐🤐 Whatever it is God save Malawi..
@dhaoudhiabedinegomaseko2363
@dhaoudhiabedinegomaseko2363 День назад
Ndi wamwayi amene amabwelako ndi moyo ku Galden city koma Mulungu akukhuzeni nonse omwe muli kuchipatalachi imfa siyabwino ngati kuli moyo.Moyo kunyenga nthawi yolapa inalipo koma chuma chimanyenga
@MarkManyowa
@MarkManyowa День назад
😂😂😂😂😂
@MarkManyowa
@MarkManyowa День назад
Imfa yanji yokondweretsa 🤣😂🤣🤣 Koma ngati sizitheka panopa His days are numbered for sure 😂
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z День назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂​@@MarkManyowa
@ElizabethMulinde
@ElizabethMulinde День назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂​@@MarkManyowa
@MarkManyowa
@MarkManyowa День назад
@@ElizabethMulinde 🤣🤣🤣🤣 Akanangopenga Misala onse omwe anatenga nawo mbali pa plan yozimitsa Chilima ndi ena onse aja
@adsonphiri6497
@adsonphiri6497 День назад
Guys kodi zikuti bwanji tiuzeni bwino
@MariaNyamwera
@MariaNyamwera День назад
Kkkkk kkk koma kumeneko chete ku ma stand
@JosterNgalawa
@JosterNgalawa День назад
Apaso chimwendo wasala ndi days yokha ulosi wanga watelo the 4th is kamajekete
@CameronVisser-k7i
@CameronVisser-k7i День назад
Pangani search manganya ma bodigadi ake kunyumba kwakwe kuli bwanji apo ndiye tidziwa chiona
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w День назад
Honest this ikayikidwa something happens
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 День назад
Okumpha nzake samwalira😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@samdiverson9733
@samdiverson9733 День назад
Koma ma trillion a malawi apitatu😢😢😢
@EnerstManess
@EnerstManess День назад
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉Fire 🔥 🔥 🔥 🔥
@DeborahChikumbu-c2v
@DeborahChikumbu-c2v День назад
Lero masanawa ndakumana ndi conivy ikuthamangira mulungu airport kaya sakukawatenga a bwana vp kaya.
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani День назад
Guys maliro Achakwera alephereka ali moyo wapita ku Israel panop nkhondo ija yavuta anaivotera ija wapita koleresa ndthu usiku Lebanon yaphulisa Israel anthu awiri afa ndye Chakwerayo alikumeneko ndthu
@ShakiraJackson-x8w
@ShakiraJackson-x8w День назад
Ndikukagura sound music basi
@yassinn5634
@yassinn5634 3 часа назад
Anyamatawa ali boo chifukwa sanabise kuti iwo kuimba ndi business. Ndiye amene sakutha kuwamvetsa apite ku RUO azikagwira nkhanu
@AubreyNdeule
@AubreyNdeule День назад
Kkkk mwatibwanj ku chikangawa?
@MuhammadPyson
@MuhammadPyson День назад
Ammbuye tengen chikangawa
@MosesTangwe
@MosesTangwe День назад
Kanyimbo aka anakomza
@ChristopherMaulidi-m3v
@ChristopherMaulidi-m3v День назад
Good
@LawrenceBamusi
@LawrenceBamusi День назад
Ndee ena akuti Usi akungotola ma 3 points awulere😂😂😂😂
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa День назад
NDILI KWA TELALA KUSOKESA BLACK CHEERS❤❤❤❤❤
@GeoffreyBAyatuKazembe-q7u
@GeoffreyBAyatuKazembe-q7u День назад
😂😂😂😂😂😂
@MaryNyirenda-nq3mh
@MaryNyirenda-nq3mh День назад
😂😂😂😂😂😂
@zelliachamboto5744
@zelliachamboto5744 День назад
😅😅😅
@WisdomChimalizeni
@WisdomChimalizeni День назад
A St chikangawa mphakati akaphikira kuti kumene kukuoneka kuti kungakadyeke bhoo😂😂
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa День назад
Osayiwala kulongeza tsabola wa kambuzi okadyera nyama ku siwa ku kasiyaa hehehehehehe
@TonykalicheloKalichelo
@TonykalicheloKalichelo День назад
Chonde tithandezen mwachangu abale tiyambepo kulezela plz
@GoldenHappy-gt6ld
@GoldenHappy-gt6ld День назад
Ngati zili zoonadi Malawi wapulumuka
@AliceGeorge-il6ig
@AliceGeorge-il6ig День назад
Osasewela ndi kolona wa mkatolika
@WellingtonChipembere-l1i
@WellingtonChipembere-l1i День назад
No comment🙅🙅🙅
@JosephIsaac-s1c
@JosephIsaac-s1c День назад
What is going on here??????
@JOHNSANGWALI-n2f
@JOHNSANGWALI-n2f День назад
What is going on guys
Далее
Evance Meleka -Yashuta
5:10
Просмотров 38 тыс.
Seja Gentil com os Pequenos Animais 😿
00:20
Просмотров 5 млн
Zeni Zeni zake Zokhuza Chakwera
12:31
Просмотров 118 тыс.
Evance Meleka _Yashuta
5:10
Просмотров 7 тыс.
Chifukwa Chimene Anthu Amamudera Miracle Chinga
11:55
Chikuchitika ndichani Amalawi 🤔
2:21
Просмотров 60 тыс.