Тёмный

ACHEWA AKU DOWA ASAMBWAZA EE!!🙌🙌 

HOT 265
Подписаться 82 тыс.
Просмотров 33 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

26 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 94   
@HamiltonwaNamuwah
@HamiltonwaNamuwah 2 месяца назад
Mtsogoleri akuyenela kukhala munthu oleza mtima. Osabwenzera choipa . Komano a Chakwela ngati mbusa ayi ndithu, zawabvuta ndipo sitimayembekezera kuti ulamuliro wao ungakhale oyipa moteremu. Chifukwa iyeyu amadziwa bwino lomwe za umoyo wa uzimu. Lero wasanduka wakupha . Anapha Sidick Miya komanso Saulosi Chilima ndi anthu ena omwe anali mu Ndege muja. Ifeyo tikudziwa zonsezo ndipo ma umboni alipo. Chakwela galu ameneyi , owona mizimu yonseyi singamusiye siye ayi imumzunza ndipo azunzika koopsya pansi pompano Chilango chake cha Mulungu asanachilandire galu ameneyi.
@VincentManyenje
@VincentManyenje 2 месяца назад
@@HamiltonwaNamuwahkoma awinabe.
@CoshantAsante
@CoshantAsante 2 месяца назад
@@VincentManyenje ndipo nkhan zaifa za anthu aja zisiyeni coz umbon mulibe kut anaphedwa nd munthu wina aiii... Mulungu ndamene akuziwa... ku Malawi vuto ndlimenero Kukonda kulenga nkhan
@RachelNkhoma-vn2jo
@RachelNkhoma-vn2jo 2 месяца назад
❤❤ochewa ozanga ozindikila Dpp oyeeeee 💥💥💯 ❤❤
@CoshantAsante
@CoshantAsante 2 месяца назад
Mbuz zimalakhur paja zja mpaka mun2 kumanyumwa nazo?... Evn kwao zngakope anthu😂😂😂😂😂
@marryphili5419
@marryphili5419 2 месяца назад
More 🔥🔥 adadi tikudikirani 2025 mwina moyo wungasitha 💃💃💃
@GanizaniCmbewe
@GanizaniCmbewe 2 месяца назад
Ichi ndi chathu ichi
@LexKatandika
@LexKatandika 2 месяца назад
Dpp,UTM,UDF,afford,,tagwilanani manja tichose amalawife Ku iguputu komwe tikumphula njerwa za moto
@PeterJanga-wv9nz
@PeterJanga-wv9nz 2 месяца назад
Munthu wakulu Brian Band mmmmm guys munthuyi akapangako kunali ntcito
@MasterMwandira-d3k
@MasterMwandira-d3k 2 месяца назад
Anthu awa akalamba asiyile achinyamata
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 2 месяца назад
Inenso ndi Mchewa koma palibe chomwe yapanga MCP. Panopa biziness ikukomera oremeretsetsa.
@StalloneButao
@StalloneButao 2 месяца назад
Wachikulire sakhala ndiphuma akukagona woyeee
@sirgiftedmagalasi22
@sirgiftedmagalasi22 2 месяца назад
Zizafika poti olo a pule azavotera APM....kkkkkk
@omarajibu860
@omarajibu860 2 месяца назад
Mwana wa pa Dowa kulankhula chilungamo
@ThumbikoNgulube
@ThumbikoNgulube 2 месяца назад
Dpp yomweyo
@JoshuaNyirongo
@JoshuaNyirongo 2 месяца назад
Vilombo vozindikila
@GumuleKandawala-g7k
@GumuleKandawala-g7k 2 месяца назад
DPP OUR LAST HOPE
@VincentBorrah
@VincentBorrah 2 месяца назад
Kkkkkkkk koma ochewa mukuithanulatu apa 😅😅😅
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 2 месяца назад
Brian wadzinvela wekha ndi a Malawi onse. Zinthu silibwino mu dziko.
@trickermussa472
@trickermussa472 2 месяца назад
Anaziwa adad kuti or achokepo ana awo sangamenyane
@WilliamkaipahKaipah
@WilliamkaipahKaipah 2 месяца назад
Powerful brothers
@VesterLuke
@VesterLuke 2 месяца назад
Tawina kaye...
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 2 месяца назад
Nayenso Chaponda wakalamba mpaka 81 kakaka
@MeliaMichael
@MeliaMichael 2 месяца назад
Achewa awa ayankhula zonveka kwambiri
@haroldmazombwe8081
@haroldmazombwe8081 2 месяца назад
Nganga bulawayo wakagona watopa, nkhalamba yachabechabe
@FrankMsiska-i9j
@FrankMsiska-i9j 2 месяца назад
Peter watopa koma tikanampumitsa 😢😢😢😢
@HendryChiwezo
@HendryChiwezo 2 месяца назад
Brian uwapusita achewa koma mchewa sangaone kuti akuwapusitsa kodi mafuso amenewa adawafusa choncho kufunsa anthu aku Tyolo
@DeniaKaunda
@DeniaKaunda 2 месяца назад
😂😂😂😂 kma Brian ukhalike
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 месяца назад
Onyamata odziwa kulankhula ndi ozitsata ❤❤❤
@FebbyPhiri-n7j
@FebbyPhiri-n7j 2 месяца назад
Eeeeee Koma Cathay ndi Brian kkkkkkk
@ChrisyMbewe
@ChrisyMbewe 2 месяца назад
APA ndiye.dzikundivekelabwino.Dpp.wooooyeeee
@JanetJamesMachila
@JanetJamesMachila 2 месяца назад
APM my vote ❤
@FrancisGama-qb7ze
@FrancisGama-qb7ze 2 месяца назад
Awa nde anthu ozindkira kwambri
@BillionChigwirionaires
@BillionChigwirionaires 2 месяца назад
@JeffreyKalepa
@JeffreyKalepa 2 месяца назад
DPP THE ONLY TRUSTED PARTY WHOLE NYASALAND
@MeliaMichael
@MeliaMichael 2 месяца назад
Kungonva kuti chatuluka mdabwe changa😂😂😂😂
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 2 месяца назад
Km Brian 🤣🤣Aliunena zoona
@sallyphiri-qz7if
@sallyphiri-qz7if Месяц назад
APM WOYEE
@PaulBexter-c4g
@PaulBexter-c4g 2 месяца назад
Zikhale chani kodi usiku umenewu
@FrankMsiska-i9j
@FrankMsiska-i9j 2 месяца назад
Koma chichewa chaku Dowa nchokoma
@GreyShadreck
@GreyShadreck 2 месяца назад
❤❤
@AlfredMatthew-v4h
@AlfredMatthew-v4h 2 месяца назад
MWAYENDA BWANJI ? TAKWERA MAMINIBASI😁
@TracyBanda-i2g
@TracyBanda-i2g 2 месяца назад
Kkkkkkkkkkk
@MACFARLANEMULENGA
@MACFARLANEMULENGA 2 месяца назад
🤣🤣😞😞 mchona wapita kukagona
@EvanceEdson-fz1vn
@EvanceEdson-fz1vn 2 месяца назад
Labourers work more than professionals, biggy amagona ndi kudzuka nthawi yabwino
@PiusFumulan
@PiusFumulan 2 месяца назад
❤❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@mcdonaldchakwira3145
@mcdonaldchakwira3145 2 месяца назад
Tumidala tovuta utu situkufuna kusiyira anyamata
@benjulius6070
@benjulius6070 2 месяца назад
Akut tawina kale 😂😂😂
@TimaNyirongo-jt5vy
@TimaNyirongo-jt5vy 2 месяца назад
Koma Brian anakonza
@FoxmanPhiri
@FoxmanPhiri 2 месяца назад
Woyeee
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 2 месяца назад
Dpp woyeeeee
@RiteRoderick
@RiteRoderick 2 месяца назад
Mbambande DPP❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@AgnessMwafulirwa
@AgnessMwafulirwa 2 месяца назад
God bless Malawi
@kennethkaunda3636
@kennethkaunda3636 2 месяца назад
Ndipatse number ya Brian Banda guys please
@FatimaUmali-pc8sy
@FatimaUmali-pc8sy 2 месяца назад
Nice one 😂😂😂😂❤❤
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 2 месяца назад
Brian Banda umakwana 😂😂
@MACFARLANEMULENGA
@MACFARLANEMULENGA 2 месяца назад
Chatopa chapita
@NizigiyimanaChantal-c2p
@NizigiyimanaChantal-c2p 2 месяца назад
Jerous people never winnnnnn!!!!!!
@RuthKaunda-tc5qd
@RuthKaunda-tc5qd 2 месяца назад
DPP wooooyeeee
@hourlyview4226
@hourlyview4226 2 месяца назад
Kulamudi dziko sikuyakhula bwino English
@SueWahna
@SueWahna 2 месяца назад
Ndipo thaw mkachitsirud 😅😅
@chifundoKaluvi-ey5uw
@chifundoKaluvi-ey5uw 2 месяца назад
Yakwani thawi
@RiteRoderick
@RiteRoderick 2 месяца назад
APM❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@thomluckson4557
@thomluckson4557 2 месяца назад
at fateleza
@AgnessMatchado
@AgnessMatchado 2 месяца назад
Dr chikangawa alibe mawu
@VincentManyenje
@VincentManyenje 2 месяца назад
Dr albino sangawine .
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 месяца назад
@@VincentManyenjeiwe pamtumbo pako Chakwera sangawine mistek yopha chilima ija zinalakwika pamene paja chomwe ungadziwe dziko lapasi limalamulilidwa ndi Roman catholic wekha malizitsa
@VincentManyenje
@VincentManyenje 2 месяца назад
@@Musa1828-l5d usavutike ndikutukwana koma ziwa kuti MCP ikupitilira ku lamura .sunga mawu anga.
@CoshantAsante
@CoshantAsante 2 месяца назад
@@Musa1828-l5d mpaka kumutukwana nzanu nkhan yake iti😂😂😂😂😂
@HaliJana
@HaliJana 2 месяца назад
INE NDAVOTA KALE DPP 2025 BOMA
@MACFARLANEMULENGA
@MACFARLANEMULENGA 2 месяца назад
Bola ngati sanagwe pa mpando
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 месяца назад
Olo atagwa mkufa koma muthu ozindikila sangavotere munthu opha mzake pamtumbo pakoso iweyo ndi chakwera wakoyo panyini pamanu nose
@spargomw
@spargomw 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂muuzen chilungamo ameneyu😂​@@Musa1828-l5d
@CoshantAsante
@CoshantAsante 2 месяца назад
@@Musa1828-l5d inu abwino mpaka kumatukwana anzanu... Namkhumwa my Vote
@CoshantAsante
@CoshantAsante 2 месяца назад
Mmmmmm APM wathawa kuopa kugona
@ShamilahSaizi
@ShamilahSaizi 2 месяца назад
Nde asakagone chifukwaaaaa
@CoshantAsante
@CoshantAsante 2 месяца назад
MLC anachezeratu
@ibrahimjackson-cg6tc
@ibrahimjackson-cg6tc 2 месяца назад
Waiopeladi 😂😂😂😂 koma alibho
@CoshantAsante
@CoshantAsante 2 месяца назад
@@ibrahimjackson-cg6tc kkkkkkk pamenepo
@limbanitambala3939
@limbanitambala3939 2 месяца назад
@@CoshantAsante Ndiye kuchedzera kwa Chakwera kunapangitsa kuti sugar atsike mtengo??
@noelmunthali3516
@noelmunthali3516 2 месяца назад
Walira mwana wapedegu 😅
@MACDONADLITIA
@MACDONADLITIA 2 месяца назад
Koma Malawi tinapusa kwa basi
@HamiltonwaNamuwah
@HamiltonwaNamuwah 2 месяца назад
Bwanjinso nanga
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 2 месяца назад
DPP ndichipani chafiko, chosapha,
@macleanwazalanyirenda4994
@macleanwazalanyirenda4994 2 месяца назад
Ma albino ajaaa zinali zinyama? achinyamata azathu anawaombela Ku Mzuzu pa 20 july ajaaa ndi nyama??
@limbanitambala3939
@limbanitambala3939 2 месяца назад
@@macleanwazalanyirenda4994 Ma alubino ankhaphedwa Chakwera nanu ali ku opposition pofuna kuyipitsa mbiri ya APM anthu 20 aku Mzuzu aja anaphedwa ndi apolice chifukwa after ma demonstration anayamba kumakathyola ma shop a wanthu osalakwa.
@ellensambo6323
@ellensambo6323 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂
@HopeMakoka
@HopeMakoka 2 месяца назад
DPP woyeeeeeeeeee
@DaveMukhova
@DaveMukhova 2 месяца назад
Apa palibwino
@SlindiryLoveness
@SlindiryLoveness 2 месяца назад
Koma kuthamawu sibwino ngati mukufuna kuvota kavoteni osati kuti muthemawu achonchi mawa tizakugunsani
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 2 месяца назад
Yawawatu poti amzanu alankhula😂😂😂m'mene mumanyozela inu muja bwanji mwayiwala😂😂😂
Далее
Только ЕМУ это удалось
01:00
Просмотров 969 тыс.
Китайка и Красивые Глаза😂😆
00:20
MK Party media briefing
18:57
Просмотров 16 тыс.
Только ЕМУ это удалось
01:00
Просмотров 969 тыс.