MADALITSO OCHULUKA APITE KWA ANUWAKE SITE IYI.INEYO WANGA NDI UMBONI WAKUTI SINDIMAGONA TULO POGANIZA ZA KATUNDU UYU WA NYIMBO KUTI KODI NDIDZAMUPEZA KUTI.CHIFUKWA OLO PA INTERNET SAMAPEZEKA AYI.NYIMBO IYI NDIYOOPSYA PA MOYO WAMUNTHU YEMWE SAFUNA UPANGILI WA MAKOLO AKE.AMENI AMBUYE AZIMUDALITSABE M',KHASA.AMENI AND AMENI
December, 2003 when i was in Standard 6 is the time this famous album of him was released. Tigwilane Manja. I loved every track from this legendary album but this song still stands out above them all. My mom passed away and this song carried me throughout my school years. This song made me the man i am today. Ankasa pitilizani kuyimba nyimbo za malangizo chonchi. You are the best Mr, i love you.