Тёмный

Akukamba zama passport aaah koma anthu awa ndi a mbwelera nthawi zina 

Malawi Trends TV
Подписаться 33 тыс.
Просмотров 8 тыс.
50% 1

Ma Ulemu kwa Mibawa pogwila ntchito imeneyi

Опубликовано:

 

9 июл 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 89   
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
Bingu Muntharika ndi Peter Muntharika anali akatundu owopsa zedi, zinali zotchipa komanso zimatuluka popanda nkhani iliyonse, DPP ndi akamuna zedi❤❤❤❤❤❤❤❤
@NescotNyamwela
@NescotNyamwela 16 дней назад
Makape
@brainsmkumbwa6267
@brainsmkumbwa6267 16 дней назад
Machende anu nonse aku Immigration,kunzunza amalawi basi,akafunsidwe kaye mafunso ndi Mr Brian Banda osati mafunso mukufusana apa apachibale chifukwa nonse ndinu a M.C.P
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 16 дней назад
I miss Peter and Bingu. Panopa ndikalangitsa ku Zambia. Ku Malawi kuli ma passport a fake.
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 16 дней назад
Boma la abwampini zitsilu za anthu zizeleza zenzen.
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 17 дней назад
zitsiru za anthu
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 16 дней назад
Awatso awa, kofunika kuwaitanila, anyamata ndi atsikana'aku Kenya, chifukwa kumalawi kuno titotoledwa kwambili.azangoyambila,pa ,bt kuwatibula,iyaaa.
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
Passport ukanyamuka ndikumabwezedwa kuti siili mu system 😂😂😂😂😂😂😂 koma abale MCP😂😂😂
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 16 дней назад
Kodi ndi zoona?
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 16 дней назад
@@GraceZumazuma Eyaaah Grace ndizoona kaaah anthu akubwezedwa koopsa zanga wina zamuchitikira ndi dzake akubwera kuno
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 16 дней назад
@@user-uc1pd1tc2x ndiye akungobela a Malawi ndalama tu
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 16 дней назад
@@GraceZumazuma Ndipo koopsa Ndizomwe akumachita kaaah akumangopusitsa anthu
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 16 дней назад
@@GraceZumazuma Kodi iweyo uli Kutiko panopa?
@tiyachisale9075
@tiyachisale9075 16 дней назад
Ngat cha mzika chaurere chimachedwa Ku Lilongwe nde kuli bwanji passport
@user-hl3st3cc4v
@user-hl3st3cc4v 16 дней назад
Koma Malawi mukutitola inuyo muzingowauza achakwera anuwo kuti thawi ikwana abwerera kokamvina zinyawu mwamva
@user-nq2ih6xl5z
@user-nq2ih6xl5z 16 дней назад
Bwelerani ku chipiku akulu ku Assemblies nso ai simukakukwanisa
@marryphili5419
@marryphili5419 16 дней назад
Mukunama panopa passport ya malawi panopa siyamphamvu yinali yamphamvu kale nthawi ya DPP
@user-lk8kj9zv6x
@user-lk8kj9zv6x 17 дней назад
Odi ndidutse ndingachimwepo apa
@HalisonSolomon
@HalisonSolomon 16 дней назад
Mbuzi za manu pansi a immigration agalu asatanic muchoke palibe chanzeru mukupangapo demeti
@jamesgama5489
@jamesgama5489 16 дней назад
Ku immigration ndi department ya boma yomwe kuli katangale wowopsya kwambiri
@bysongeorge3243
@bysongeorge3243 16 дней назад
Akuluwanso nawo kulankhula za mbwelera..palibe zachilendo apa, pokhapo pokachitira printing ku Lilongwe means no improvement in service delivery..kukhala backlog 10 days sizingatheke..
@MalitaKapesi
@MalitaKapesi 16 дней назад
Nkhani iyi ndiyosamveka kuti zina zipangidwe ku blantyre ndikukafikanso ku LL, passport imodzi yomweyo, ndibwino kunena kuti simunayambe kutulutsa passport.
@DeliaKaduya
@DeliaKaduya 16 дней назад
Ndili ndi mau oti ndiyankhule koma ndilibe kolowera ine 😢😢😢😢
@user-nq2ih6xl5z
@user-nq2ih6xl5z 16 дней назад
Koma mulibr manyazi kumakamba zopusazo, munapeza chili chonse chikuyenda chinachituka ndi chani kuti musokonezr
@user-nq2ih6xl5z
@user-nq2ih6xl5z 16 дней назад
Abwere amene akuziwa zakayendesedwe ka dziko , inutu palibe chomwe mukuziwa
@nafejonga972
@nafejonga972 17 дней назад
Machende anu nonse...manyi anu😢😢
@ConfusedAstronaut-qv6wq
@ConfusedAstronaut-qv6wq 16 дней назад
Tiwona kuti zitha bwanji,palibepo chabwino apa.
@stanleymollen7273
@stanleymollen7273 16 дней назад
Ma kadeti,a low poor quality passport. Kale linali bwino.. MCP OUT NEXT YEAR
@eunicemsuku-il2fd
@eunicemsuku-il2fd 16 дней назад
Mulungu akakuotcheranu chipinda cha nokha nokha anthu amabodza inu ndithu
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 16 дней назад
Ine ndimaganiza kuti ma passport ayamba ku printer ku blantyre koma zimene akunena Abambo awa sizikuveka kwa munthu wazeru akuti ma president kuchokera blantyre angolembesa koma print ndi ku lilongwe . Sitikufuna zimenezo ma passport azipangika ku blantyre komweko
@user-nq2ih6xl5z
@user-nq2ih6xl5z 16 дней назад
Koma mulibe manyazi olo potchula mitengo ya ma passport
@AllenBanda
@AllenBanda 16 дней назад
Zoboza basi Chakwela mmmm sazatheka
@user-ux8bc6wy1i
@user-ux8bc6wy1i 16 дней назад
Mboli zanu nose Zoona anthu azibvutika kufuna ma passport
@UsumanLuwayo
@UsumanLuwayo 16 дней назад
This is nonsense, mboma ili anthu onse nzeru zawo nzopanda nzeru kkkk anayankhula ngati nzanzeru ziki zopanda nzeru
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb
@ExcitedBreakingWaves-oh3zb 16 дней назад
Mukuwononga dzikolo.bodza lokha lokha.
@GraceZumazuma
@GraceZumazuma 16 дней назад
Akatelo mwana wa chakwera ma billion nthumba akupanga ma passport a fake ndamva zoti pa beitbridge sikutulutsa information ngati zili zoona mukulakwa
@FestonSaulo-iz9nd
@FestonSaulo-iz9nd 16 дней назад
koma nditukwana kwinako mpaka ku lilongwe 🙄
@LilianKachala-yz2xf
@LilianKachala-yz2xf 16 дней назад
Aaaaaaaaa abale ndiye mudziti mwatsegula ku BT pamene printing Ku LL Haaaaaaaaaaaaa abale
@marryphili5419
@marryphili5419 16 дней назад
Boma ili mmmmm🙌🙌 ndinambara one kulemphera tiyeni tizizuzika basi dziko ndi rathu nanga titani
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j 16 дней назад
Koma azikwanilisa zomwe akunenazo bvuto boma ili limanena Zina limachitanso Zina
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 16 дней назад
Zauchitsiru iziii nde ukufuna kunena chani?? Ma passport k320pin ena mpaka k400 pin usapusitse anthu bagamoyo💔💔💔
@willisphiri4035
@willisphiri4035 16 дней назад
Bodza lenileni ,kuti ituluke passport yako mpaka K500 000.
@jeffchikwapata6933
@jeffchikwapata6933 16 дней назад
Amibawa amenewo mafunso kapena kongokwanilitsa zimene mumadziwa kale, ndinu zitsiru kwambiri kodi mukuyesa amalawi ndi zigule eti akapoli inu
@user-nq2ih6xl5z
@user-nq2ih6xl5z 16 дней назад
Ndiye iwe ukuona ngati K50,000yo passport yatchipa? Iwe mbuzi kwambiri
@UseniMailosi
@UseniMailosi 16 дней назад
Amene atsunga MCP tsindikumali
@user-fh7sd6gp3f
@user-fh7sd6gp3f 16 дней назад
Kodi ndiye pamene mumangokhala osamatulutsa ma passport munali kulandira malipiro? Or mumangiwononga ndalama za boma?
@mollymasangano473
@mollymasangano473 16 дней назад
Kodi Amalawi amveziti akapita kuka wombora Passport yawo akumawauza kuti apereke ndamala zina kodi chilungamo chake ndi chiti K50,000.00 but people they are playing more than that advice your worrks not to do COLLAPUTION when people goes to collect their Passport PLEASE We Malawians were tired. STOP IT,STOP IT.
@user-nq2ih6xl5z
@user-nq2ih6xl5z 16 дней назад
Kodi osangonena kuti zakuvutani bwanji
@Faithnsini
@Faithnsini 16 дней назад
Ndingodutsa ndingachimwe
@lyiemanganjira9708
@lyiemanganjira9708 16 дней назад
Nanga ndi chifukwa chani inu ngati a immigration munthu kuti atenge passport koma apereke ndarama zoposa mtengo WA passport,, mwachuluka kuba nonse kumeneko muchoke basi sitikufunani mwationjeza
@chikaonekarh
@chikaonekarh 16 дней назад
Which means ngati udataya slip satha kupeza information yako mu data sever, koma abale zinthu zake zovuzedi
@braveglorymwanzagolah4899
@braveglorymwanzagolah4899 16 дней назад
Mwa panga angat lero
@Hopenandola-zg6kz
@Hopenandola-zg6kz 16 дней назад
Machende ake ameneyi
@sarahmphande6108
@sarahmphande6108 17 дней назад
Ma boza okha okay, munayambapo mutatulusa passport munthu atapereka 90 thousand before ,after kupereka 90 pin ,mumademandanso 100 something mumunthu Osaka agalu inu,mulungu akulangeni , in our own country like passport amalawi muziweni mulungu ,coz passport it very important thing for residents mukut r50 pin 2 weeks wm ,maboza munthu akapita ku migration yenkha kopanda ma agents and anthu aku migration simumamuthandiza anthunu ummm only for passport please we ate all Malawian we have right to have passport please have mercy to us we don't have money to bride you guys,
@jackmambo2638
@jackmambo2638 17 дней назад
Sindimangidwa ndiyakhule?
@DeliaKaduya
@DeliaKaduya 16 дней назад
My question too 😢
@georgeabigailmaseko-ts3fq
@georgeabigailmaseko-ts3fq 16 дней назад
Panya panu zitsiru kwabas
@frankkaipa8925
@frankkaipa8925 17 дней назад
Dc chidindo cha boma kungoti nda kokha nayeso amafuna timupase zake chikhalilecho ndintchito yemwe analembedwa opusa kwambiri anthu inu
@TisopeChagala
@TisopeChagala 16 дней назад
Izi zisizo zenizeni
@eunicemsuku-il2fd
@eunicemsuku-il2fd 16 дней назад
Ku mzuzu mpaka liti ndi ma bodza anu inu?
@user-nq2ih6xl5z
@user-nq2ih6xl5z 16 дней назад
Mcp just pack and go
@user-zk7jw9up6m
@user-zk7jw9up6m 16 дней назад
Anthu akuba inu
@user-jl6sq3ph1b
@user-jl6sq3ph1b 17 дней назад
Mboli zanu inu mbamva zachabe chabe inu mukamayaķhulatu muziwona kumawa mapwala anu inu kod mukuyakhula zichani inu a migration print ku Lilongwe
@mussamapira801
@mussamapira801 16 дней назад
Pano passport kuti ulandile for 3weeks ikumadya ndalama yokwak350 ,000,00
@williamdaka79
@williamdaka79 17 дней назад
Agalu awa
@TopoTopo-bm4vw
@TopoTopo-bm4vw 16 дней назад
Zisilu ižiiiii zakuba
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 17 дней назад
Sisani kamtundu wose osati simene mukunenaso sopanda chito andiaku funaakdya sindi sisike anamachende iwe
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 17 дней назад
Ans the question yes or not.osati explain
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
😂😂😂😂Koma MCP abale mmmmmmm😂😂😂
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg 17 дней назад
❤❤❤❤
@NoelLangwani
@NoelLangwani 17 дней назад
Koma ndinu okuba Muthu wagula passport yake yatuluka mukufunaso mupasidwa ndalama yopotsa imene wadula 90 pin.... Mufunaso 200pin yokuba kuti mupeleke passport athu okuba inu 😭😭😭
@IshuBillalli
@IshuBillalli 16 дней назад
Koma muli ndi umunthu inuyo tizakumana or pangachedwe
@FoniyalaMthamulo
@FoniyalaMthamulo 16 дней назад
Ntengo udakwela munthu akumapeleka 300000 ,mukudziwa zimenezi
@WitnessPhiri-zr9uf
@WitnessPhiri-zr9uf 16 дней назад
Ndizoona ndithu ine ndinapangila mwana wanga 2monthy ago ndinapeleka koma paka pano siinatuluke ku Lilongwe
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e 17 дней назад
Mwati chasintha ndi chani pamenepo?
@MaryJefry
@MaryJefry 16 дней назад
Mmmm 😂😂😂😂😂
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 17 дней назад
Yankhani funso akulu
@bisciouspalima8626
@bisciouspalima8626 16 дней назад
Zosangalatsa ndithu
@BlessingShabalala-py7fl
@BlessingShabalala-py7fl 17 дней назад
Panyapanu ndi agalu Inu Kuba basi
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 17 дней назад
Agalu zaziii chatap
@CharlesKachipanda-jz9jv
@CharlesKachipanda-jz9jv 17 дней назад
Koma boma ili zawabvuta basi angabvomereza
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 17 дней назад
Musandichimwise ine
@CharityMhone-uk9ym
@CharityMhone-uk9ym 17 дней назад
Votsek😮😮😮 zaziii
@JafaBulhm
@JafaBulhm 15 дней назад
Mbolo yako
@frankkaipa8925
@frankkaipa8925 17 дней назад
Mupatibela kwambiri agalu inu paspot ikatuluka kuti titenge mumafunaso tikupaseni ndalama kuti titenge
@sarahmphande6108
@sarahmphande6108 17 дней назад
Don't ignore my comments please reduce bribe
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 17 дней назад
😂😂😂
@NescotNyamwela
@NescotNyamwela 16 дней назад
Mufuseni kapeyo kuti roll on wapaka akununkhatu.
@franknzerub6644
@franknzerub6644 17 дней назад
Za ziiiii
Далее
Wait for the BOWLING BALL! 👀
00:38
Просмотров 11 млн
Watch Donald Trump's 2024 RNC speech in full
1:36:20
Просмотров 1,6 млн
Donald Trump speaks at the RNC: FULL SPEECH
1:32:24
Просмотров 3,6 млн