Тёмный

AMENE ATAPHONYE NKHANI ZA LERO ZAKE (NKHANI ZA LERO PA 9 AUGUST) 

Makosana
Подписаться 88 тыс.
Просмотров 28 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

9 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 33   
@IbrahimRamzy-s9i
@IbrahimRamzy-s9i Месяц назад
Kom Dr Chikangawa ai ndithu Mulungu asakusiye choncho ai
@guilty-rz3ek
@guilty-rz3ek Месяц назад
For the last day, the elders are getting to know each other😂😂😂
@allanchangalusa6662
@allanchangalusa6662 Месяц назад
Afika bwanji mdzikomo? Nanga Ngati Boma silinadziwe, ndiye Kuti tili sefe?
@user-ld8gb9xm7v
@user-ld8gb9xm7v Месяц назад
Wakasayina ninja kuti vibizi vinjile mu chalo chithu
@user-pg1kc5sg9w
@user-pg1kc5sg9w Месяц назад
Kupanda chitetezo kotani kumeneko dziko mwathu anadutsa Kuti
@user-sh6gi5uq3l
@user-sh6gi5uq3l Месяц назад
Pali zotukwananazo apa kukula mopusatu uku
@user-gs7wc3nx3q
@user-gs7wc3nx3q Месяц назад
Koma chakwera ukufuna uphe amalawi tose.ndeno uzaramurira ndani komaso anthu akumizi sangaziziwe ayi azingomwa makhwarawo azingofa
@giftbanda7690
@giftbanda7690 Месяц назад
Sopano makhwalawo aziziwika bwanji muthu muthu wakukudzi angaziwe za izii komatu ku Malawi nde sitili self
@user-ld2je1hn7i
@user-ld2je1hn7i Месяц назад
Clothes
@jescandimbo6030
@jescandimbo6030 Месяц назад
Ine ndamwako tu Amoxachikangawawo koma mtima zomwe umachita mmmhuuuuu
@AngellaMkata
@AngellaMkata Месяц назад
Yomweyo bwamtasa iwe😂😂😂
@JonathanMunthali-n3c
@JonathanMunthali-n3c Месяц назад
Waoder zimenezo ndani kufunakumaliza mtundu waamalawi
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 Месяц назад
Dziko lathu mulibe chitetezo, Nanga Mankhwala alowa bwanji mdziko opanda chilolezo cha Boma,, Chikangawa atimaliza ndithu!! Sakudziwa kuyendetsa dziko.
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np Месяц назад
Mankhwala alowa bwanji mudziko boma losadziwa?????
@evansjohn7766
@evansjohn7766 Месяц назад
Zomvesa chisoni kumva nduna ikulengeza tchonchi,kkkkkkkk.....manga Iwowa ndi anthuwamba angaziwe zamankwalao ndani?akuti ngosaloledwa nanga alowabwanji?very useless
@juniortsegula3847
@juniortsegula3847 Месяц назад
Mutipha a congress
@ChipiliroSpencer
@ChipiliroSpencer Месяц назад
Afika bwanji kumalawi makhwalawo pomwe ali oopsa
@madalitsomakawa9708
@madalitsomakawa9708 Месяц назад
Tasankhani background music yabwino amthuni
@THOCCOChimbali
@THOCCOChimbali Месяц назад
Koma mcp
@OmegaMussa
@OmegaMussa Месяц назад
Phatumbopanu nonse kumeneko
@TroubleMuthala
@TroubleMuthala Месяц назад
Tambala atipha uyu atimaliza
@user-vx5kv8dz3d
@user-vx5kv8dz3d Месяц назад
Tsono ka musiki kakubhowa
@SteviePatrick-g2p
@SteviePatrick-g2p Месяц назад
Waitanisa mankhwala ndindan
@FadweckLifa
@FadweckLifa Месяц назад
@user-vw7tj2ss3l
@user-vw7tj2ss3l Месяц назад
Yomweyo. Galu iwe
@user-mv1ho9pp7o
@user-mv1ho9pp7o Месяц назад
Komatu boma ili lititha tonse ndithu nanga mankhwala alowa bwanji dziko la malawi ndiyekut chakwela wapanga dala cholinga akhale yekha.
@ChimwemweBottomani-hc5ju
@ChimwemweBottomani-hc5ju Месяц назад
Cholinga achepetse chiwelengero chozabvuta chaka cha mawa.......wagwa nayo chikangawa
@ChimwemweBottomani-hc5ju
@ChimwemweBottomani-hc5ju Месяц назад
Sioneka ndalama imeneyi
@JanaMdala
@JanaMdala Месяц назад
Kwayipa kwathu ku MW
@FadweckLifa
@FadweckLifa Месяц назад
Atipha.
@user-ti9yk4eg2l
@user-ti9yk4eg2l Месяц назад
Zovutatu
@CatherineDesire
@CatherineDesire Месяц назад
🙄
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w Месяц назад
Pankholo panu nonse agalu
Далее