Тёмный

AMENYEDWA NDI MBAMA YACHIKWANJE KUMALO OBISIKA ndipo zadzetsa ulumari kumaloko. 

LIKI-LIKI TELEVISION
Подписаться 48 тыс.
Просмотров 51 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

6 май 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 226   
@gesinasutherland9241
@gesinasutherland9241 2 месяца назад
Mwenye ameneyo azkpita kwawo ndiwankhaza..kukanakha kuno ku South Africa akadapanga zonthekela kuti amuyimbe mlandu..koma Malawi mmmmm sadzantheka..amasamgalala ndikuti Malawi nzawo adzivutka....zomvetsa chisoni😢😢
@ChilpaKamcholoti
@ChilpaKamcholoti 2 месяца назад
Vuto ndi apolice sanagwire ntchito yawo mwadongosolo ngati anthu oti anaphunzila ntchito yawo bwino bwino.
@juliusnjerengo2610
@juliusnjerengo2610 2 месяца назад
Vuto si a police ayi, vuto ndi malamulo a dziko lathu. Zikanakhala kuti kuli malamulo kwathu kuno, kuyambira galu akumuti bwanayo ndi a police onse anapanga zimenezo bwezi pano atamangidwa onse.
@OwenJambo
@OwenJambo 2 месяца назад
@@ChilpaKamcholotimbuzi zap0lice kupha mbalewanga chifukwa cha mwenye that's bullshert
@doralinyenga9195
@doralinyenga9195 2 месяца назад
Ndipo apolice akuno amadana ndi anthu oyela khunguwa sangapange zimenezi kwa munthu wakuno nzawo
@user-og4oe5yp4w
@user-og4oe5yp4w 2 месяца назад
Amangidwe ameneyo
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 месяца назад
Akulankhula momvetsa chisoni kmso chilungamo chokhachokha ambuye a lowelerepo mmmmm😢😢😢
@mlfmalawi4393
@mlfmalawi4393 2 месяца назад
Let lawyer's fight for this man's justice, the foreigner and police men need to answer to the LAW. This is not acceptable, #Chakwera do something urgently. Owners of the land are suffering at the cruelty of foreigner's
@DanielJuly-dj2ji
@DanielJuly-dj2ji 2 месяца назад
Mayi walankhula chilungamo. Komanso banja iri Ambuye alikhudze mwapaderadera 😢🙏
@giftchale672
@giftchale672 2 месяца назад
Malawians please let's help our fellow brother
@marychilima1661
@marychilima1661 2 месяца назад
Exodus 14 vs 14 igwira ntchito pa moyo wanu mulungu akumenyelani khondo
@StelliaSangaya
@StelliaSangaya 2 месяца назад
Police ikupanga chinyengo yasiya kuona chilungamo chankhan ikufuna ndalama mbili yonyasa imeneyo
@user-qu9iu7hs8k
@user-qu9iu7hs8k 2 месяца назад
Ntolankhan ari bho kwambiri amafusa ma professional 😊
@BlessingsJames-yp6on
@BlessingsJames-yp6on 2 месяца назад
Amalawi please kaocheni company imeneyo basi thats too much 😢😢
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 2 месяца назад
Ulamuliro wa MCP muli nkhanza
@janetchinga695
@janetchinga695 2 месяца назад
Tikuthokoza maloya ozipeleka woo mulungu asogolele zonse ❤❤
@user-zy1br2fy6v
@user-zy1br2fy6v 2 месяца назад
Ku Malawi kuno kulibe apolisi A Malawi okhaokha kumazunzana chinchi Lord have Mercy on us
@DanielJuly-dj2ji
@DanielJuly-dj2ji 2 месяца назад
May God almighty bless Abel Zulanga. Mafunso akuya komanso kulondoloza nkhani mwachidwi.
@user-gx7dq1bd2f
@user-gx7dq1bd2f 2 месяца назад
Mulungu ndiwoo khulupilika pemphelani machilitso ndikumbwezeletsa kwathupi olo mulungu apange upalechoni wakumwamba chachikulu tikupemphela moyo ambuye akukhuzeñi ambuye alimbaliyanu
@user-um6yo6nc3e
@user-um6yo6nc3e 2 месяца назад
Pepeni kwambiri Mr Felix ,Ambuye akukhuzeni ndi dzanja la machilitso....
@janetchinga695
@janetchinga695 2 месяца назад
Apolice njala ngaphe munthu wakwanu chifukwa cha mwenye kupusa police ziwani kuti mwenye simubale wanu ndichifukwa chake mumafa udyo muzi ntchito mulozedwa Apolice
@officemoyenda-rj2hz
@officemoyenda-rj2hz 2 месяца назад
I wish Bushiri could come in and assist this family for daily nsima so that the wife should not run away from this man
@marychilima1661
@marychilima1661 2 месяца назад
That's my prayer
@marychilima1661
@marychilima1661 2 месяца назад
That's my prayer
@PrinceThom-pe6ie
@PrinceThom-pe6ie 2 месяца назад
Anthu wosauka ku malawi alibe ufulu mmmm
@IshuAkibu-xl9ei
@IshuAkibu-xl9ei 2 месяца назад
izo nde zoona
@user-zl3ne5kv5t
@user-zl3ne5kv5t 2 месяца назад
Muthune ndikumalota ndili ku school pafupifupi tsiku lilonse Koma school ndinasiya 2019 nditalemba mayeso a4 anthu amati za school ndimadziganizira kwambiri komano sidziri choncho ndani Muthu angandimasulire maloto amenewa.
@marychilima1661
@marychilima1661 2 месяца назад
Spirit of demotion Just pray and fasting to rebuke that Spirit. Mapephero muli mphamvu khulupirani mutsutsane nawo mzimu obwerela zithu mbuyo
@user-ln5hn5kj8i
@user-ln5hn5kj8i 2 месяца назад
Iphani apolice onse apanga izi zimene zikuchitikazi sizabwino abwanaonso panga nawon zinthu
@JosephChitseko-ro9fv
@JosephChitseko-ro9fv 2 месяца назад
Good work Abero❤❤❤❤
@user-sz9uu2dm1o
@user-sz9uu2dm1o 2 месяца назад
Amabungwe Ntchito yanu imeneyo
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 2 месяца назад
Ambuye alowerere ..why police nkhaza izi mukuzitenga Kuti dziko lathu la ufulu ..Koma mudzayankha
@enocknkhata1001
@enocknkhata1001 2 месяца назад
Chonde if someone can help get justice for this man, wenela police imatchuka ndi nkhani za nkhaza....
@MzatiMkolongo
@MzatiMkolongo 2 месяца назад
Osauka alibe mawu 😢 ,ambuye odziwa kukhuza awakhuze Mr kachingwe
@samdiverson9733
@samdiverson9733 2 месяца назад
plesident akutipo chani azipita amwenye wa kwawo
@user-dn6ts5xe2j
@user-dn6ts5xe2j 2 месяца назад
This has moved me into tears 😭😭
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 2 месяца назад
Mmmm abale inu wosauka alibe mau, ndlama inamuphadi yesu, apolis akumalawi kufuna kupha malawi nzanu chifukwa chosusukira ndlama? Manyazi akugwireni ndithu ntchito yanu simukuyikwanitsa ndipo Mulungu akulangeni pamodzi ndi m'mwenye wanuyo bola zikanakhala kuti zinthu zo zabedwadi panali pombveka Mulungu akufungatireni bambo inu pamene mukumbva zowawazi muthawi imeneyi, Koma boma limene tili nalo panoli nde ayitu yohhh
@chiputulaerik-nx4hn
@chiputulaerik-nx4hn 2 месяца назад
Nthawi imakwana yomwe Mulungu amaonetsa mphavu zake ndipo zoti ndiwe wa Police sizioneka.
@patisonlufan2823
@patisonlufan2823 2 месяца назад
Amwenye ndi akhaza kwambiri
@user-tm9ro2sm6n
@user-tm9ro2sm6n 2 месяца назад
Ndipo mulandu uwu usaime pa njira ukambidwe ndithu ndiponso m'mwenye ameneyo anyongedwe ndithu sizoona katundu wake alipo okwana ndikumateronso hmmm ayi
@GiftMunyonga-ko9dz
@GiftMunyonga-ko9dz 2 месяца назад
Nanga ungasume kuti mathero ndi boma 💔🙌
@user-bw3qu2yt6n
@user-bw3qu2yt6n 2 месяца назад
Justice should take it's course.. plz legal aid ntchito iyooo
@hopemasango1260
@hopemasango1260 2 месяца назад
Apolisi aku Malawi kuno atha kukupha eeee🙌🙌. Ku LL kuno kuli apolisi aku area 3 eeeee🙌🙌🙌
@user-wm7vl4wp8v
@user-wm7vl4wp8v 2 месяца назад
It's bad that these kind of things are too much in Malawi since it's not new issue. Ambli akulavulazidwa kwambli nd apolis I think many they are not knowing their role
@user-ek3tm3su3g
@user-ek3tm3su3g 2 месяца назад
Nayeso aphedwe mwenye ameneyo ukuku ndikuphatu kudachitikaku malawi mmmm
@user-rg9zc6eo2q
@user-rg9zc6eo2q 2 месяца назад
Mwenye ameneyo aphedweso bas
@AkilenMussa
@AkilenMussa 2 месяца назад
Mwenye ameneyo ndiwankhaza choncho shop chamwenyecho chikuyenera kuwochedwa , Allah akale nawo koma nkaz yo ndi fiti ameneyo kwambir komaso ndi hule kumukana mwamuna wake chifukwa choti mwamunayo wafulala tipatsen njira yoti titha kuthandizila m,bale wathuyu kochepa kamene tingakwanitse bon kalindo alowe pasewo please president was amphawi mwenje ameneyo azowe
@BethsiderTavares-ug4sv
@BethsiderTavares-ug4sv 2 месяца назад
This is a very bad situation and their Asian bossis using the abuse of his power and it's a felony charges against this poor innocent man May the Lord heal him and have mercy on his soul.
@yamikanifischer
@yamikanifischer 2 месяца назад
Anthu kumeneko gwilanani manja kukaotcha shop ya mwenyeyo
@user-ml3ly8hh8y
@user-ml3ly8hh8y 2 месяца назад
Anthu akuyenela kuthandizidwa ma lawyer alowelelepo apapa munthuyu munamuvulaza kwambiri chipepeso chikufunika Cha nyoo
@user-kv4cs1ot3x
@user-kv4cs1ot3x 2 месяца назад
Nkhani yomvesa chisoni kwambili mulungu awayanganile Mr kachingwe pa mvuto lawagwela komaso a police onse ankhuzidwa pa nkhani iyi ntchito yawo inthe alandileso zilango
@RashidiJala
@RashidiJala 2 месяца назад
Malawi wachakwela anthu akuvutika😢😢😢
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 2 месяца назад
Ndipo kwerekwere mwenye ameneyo achoke kwathu kumalawi
@davismwale8602
@davismwale8602 2 месяца назад
Some of our police oficers are wicked..... Very unfortunate. I wonder the school they attend
@innocentsathasteven4093
@innocentsathasteven4093 2 месяца назад
zovetsa chisoni kwambiri...Police anthu sibwino kuthamangira kumumenya munthu pa ntchito yanu...aboma chilungamo chionekepo apa dyera a Police ndi ndalama tikamakupangani chipongwe midzimu mudzitiona ngati adani anu...siose apolice magwira ntchito mwachilungamo
@user-eh1mg3ww6d
@user-eh1mg3ww6d 2 месяца назад
Amwetu ndi athu akhaza kwambili amachoka kwaoko alibe kalikose amalemelela dziko lathu komaso ndikumatizuza Chocho mmm
@mercychinji3417
@mercychinji3417 2 месяца назад
This is sad...chilungamo chiyende ngati madzi
@marychiwowa1759
@marychiwowa1759 Месяц назад
Kangaude plz help him to get his justice
@esteryndau8546
@esteryndau8546 2 месяца назад
Kukanakhala kuno ku south africa akapha mu mwenyeyo
@StiveMatias-yp4zu
@StiveMatias-yp4zu 2 месяца назад
😢Mvuto apolisi aku Malawi ku konda ndalama kupotsa moyo wa munthu!! @meyo adzipita kwawo
@TadaDuncan
@TadaDuncan 2 месяца назад
Osauka alibe mau
@user-ch3eq9yx5w
@user-ch3eq9yx5w Месяц назад
This is sad😢 Amwenye nd anthu opoila 😞😤
@user-kw7wr4kq9w
@user-kw7wr4kq9w 2 месяца назад
Always is Blantyre why? We're tired of this please try other places gha
@lulumchizi121
@lulumchizi121 2 месяца назад
A police kukonda ndalama. Apapa Popat amutsegulire mulandu. Amwenye amazunza antchito kwambiri. This man has to be compensated. 32:38
@user-cw5pl1hq5f
@user-cw5pl1hq5f 2 месяца назад
😢😢eish koma zomvesa chisoni
@user-ce6hy6tp7e
@user-ce6hy6tp7e 2 месяца назад
Km abale zamasiku omaliza sizoona kumupanga munthu choncho mpaka kumuwononga munthu kumoyo zosakhara bwno ndpo inuyo apolice mulungu akukanthen inuyo musadzafe mulungu akuoneni poika kuvulaza Mala WI nzanu inuyo muli ndi nsambi
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 2 месяца назад
Amalawi okha okha kuphana cz chaminthu obwera ai zikomo ndithu
@user-bq1mb4fk1b
@user-bq1mb4fk1b Месяц назад
Mmmmmm kma gyz eshiii zamasiku itsilidza
@lillianmwanza4218
@lillianmwanza4218 2 месяца назад
#timothy mtambo ...mmwenye uyu nde ofunika mademo ajA
@marianamwanje8968
@marianamwanje8968 2 месяца назад
Anthu amenewa ndankhaza koopsa vuto amasekeleledwa ineyo ndiye nsaname ifeyo ndopusa kwambiri amwenye wo apolice wo ayankhe, justice should be saved, kukonda ndalama apolicewa
@CikumbutsoCitokire
@CikumbutsoCitokire 2 месяца назад
Umphawi sizinthu abale munthu walumala okula Kula abale 😢😢
@ibrahimalfred6539
@ibrahimalfred6539 2 месяца назад
😢😢😢 zachisoni kwambiri
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 2 месяца назад
Mayi inu musadandaule za mnyumba kuti muzitani kuchipinda dandaulani zamoyo wa amunanu lungalunga nkubadwa mayi
@NedsonBilly
@NedsonBilly 2 месяца назад
No sister amaiwa akuyankha funso momwe awapatsira not kut iwoo akuzifuna zakuchipindazo
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 2 месяца назад
@@NedsonBilly owoooo ndimaona ngatitu chabwino ndakumvani ndithu brother
@user-ci5nc7mm8w
@user-ci5nc7mm8w 2 месяца назад
Koma apolice elibe mzelu amalola kuwatenga athuwa kumakatsekela ndikunawamenya mpaka muthu kumuphulisa zithu kumalo obisika kuti awulule awulula chani muthu sanabe komaso okubawo anathawa sanabe kathu athu omwewo ndi omwe anaimba phone kwa bwana akanakhala akuziwapo kathu sakanaimba phon kwa bwana akanatha kungobwezelesa tikatunduto koma apolice ayi ndithu
@JustinLigomeka
@JustinLigomeka 2 месяца назад
Koma a Malawi tokhatokha tizizunzana chonchi? we are very vulnerable ku Malawi kuno mmmm Ambuye atithandize
@EreneoMchenga-ly5vq
@EreneoMchenga-ly5vq 2 месяца назад
lawyer apapa agwire ntchto mwachilungamo mmwenye uyuyu adzipita kwawo
@DoriccahPhiri
@DoriccahPhiri 2 месяца назад
Iih ndanva chisoni 😭😭😭
@makomberodgers3791
@makomberodgers3791 2 месяца назад
😢😢😢 dziko lanthu lomwe kumazuzika
@user-nb7dp6pr9n
@user-nb7dp6pr9n 2 месяца назад
Kumuononga m'Malawi mzathu chonchi a Police ndinu zitsiru kamba ka ndalama🥸
@user-lx8ow6ek6k
@user-lx8ow6ek6k 2 месяца назад
Amalaw mmmm kukonda ndalama ngat salandila salary
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 2 месяца назад
Futi si yoopya pofuna, chilungamo,apa pali njila ziwili,amalawi,tiime kuthetsa, nkhani iyi.apolice,akayankhe,komaso,mwenyeyo atseke company yacheyo.waputa,kudabwe.
@symonmajir9470
@symonmajir9470 2 месяца назад
please tiyeni amalawi tikondane tokha tokha munthuyu ndi osalakwa nanu a polisi mmmm ayi musamatelo please
@thomluciouss7360
@thomluciouss7360 2 месяца назад
Bwana wa munthu ovulazidwai akuyenela kulandi ndalama zachipepetso chifukwa anamenyedwa ndi kumangidwa opanda chifukwa ndipo powonjezela apo palibe katundu yemwe anabedwa,a police ndi bwanayo onse amangidwe ndi kukaseva ndende
@user-uv1vu6ub5o
@user-uv1vu6ub5o 2 месяца назад
Apolice ndi inu nomwe omwe mwamudulisa mikono mwana uja akhala ovutika moyowake onse, langizo kwa apolice nonse ngati simusamalisa kumwamba chanu kulibe akakulangani kopsa
@WilliamHaji
@WilliamHaji 2 месяца назад
😭😭
@yanoh-hk5fe
@yanoh-hk5fe 2 месяца назад
a mabungwe please lowelelanipo po thandiza felix kut mwenye ameneyu amuliupile ndithu ndipo ndalamazisakhale zochepa chifukwa uku ndye ndikuphana komaso a police wo alanbdiole zilango
@user-rl2ow2qk7k
@user-rl2ow2qk7k 2 месяца назад
I even crie 😢😢😢😢
@PatriciaFast-gf7fc
@PatriciaFast-gf7fc 2 месяца назад
Km apolice aku malawi mukuwonjeza kukonda ndalama ,bwanji kd sizabwinitu izi akhala bwanji muthu pa ziko lapasi mutamunga khaza conci
@user-nm7mv3wr1s
@user-nm7mv3wr1s 2 месяца назад
Amabungwe loweleranipo apa sizoona izi chilungamo chiyende apa
@RobertGoliat-gt2qh
@RobertGoliat-gt2qh 2 месяца назад
Mbudzi za apolice akumalawi pansi pa achakwera kudzunzana okhaokha nkhani ya anthu obwera eeshhh chilungamo chiyende ndithu
@gladyschisomo4324
@gladyschisomo4324 2 месяца назад
A police amaikilana kumbuyo ipangeni follow up nkhaniyi please munthu wamwamuna nkumusi ndikutha kuona ululu omwe akudutsamo bambo athuwa
@user-ln5hw7dn9g
@user-ln5hw7dn9g 2 месяца назад
Sad development mmmm😢😢😢😢
@yassinn5634
@yassinn5634 2 месяца назад
AmaBungwetu apa zikanali zandale mukanaona kumachita kupikisana kuyankhula kuti atchuke ndicholinga chakuti apeze cholowa kuchokera kwa ndalewo.Koma apa zamunthuyu kuli Ziiiii.Akuti omenyera ufulu wa anthu bwanji osanena kuti omenyera mimba zao bwanji
@mariamwandwanga3035
@mariamwandwanga3035 2 месяца назад
Amabungwe athandizeni anthuwa ndithu ali mu ululu oopsa ndithu
@user-dx1ic4ij1v
@user-dx1ic4ij1v 2 месяца назад
Police yanji yokomedwa ndalama choncho 😔😔
@PiterDeleza
@PiterDeleza 2 месяца назад
Malawi Police sinasinthe olo amakamba zoti inapanga reform koma sizoona .
@JamesSamison
@JamesSamison 2 месяца назад
Hy
@user-jp9sw8sl7p
@user-jp9sw8sl7p 2 месяца назад
Poor policing. Machende amayake mmwenyeyo ndiapolisi. Chakwera mboliyamake
@user-rg6hn7mt6w
@user-rg6hn7mt6w 2 месяца назад
Eshiiiii 😢😢😢
@InnocentGama-qz3xy
@InnocentGama-qz3xy 2 месяца назад
A Malawi ndchani makamaka ndichifukwa chani mumakonda athu obwera kusiya athu anu, ayi Boma lichitepo kathu ine kwanga ndkupepesa kwa bambowo pepani kwambiri😢😢
@user-xg5pq5ku4l
@user-xg5pq5ku4l 2 месяца назад
Ndipo dziko lathuli aaah,ku south Africa amakonda nzika zawo ndipo foreigner kujoni samamulabada.or kuwona mzungu sanjenjemera naye ngati mmene amapangira ku Malawi kuno.Malawi,,,changamukani,osamafera anthu obwera ayi,ndalama mukuyikonda kusiya kusamala moyo wamunthu.iyoh..Lord have mercie
@GrecianWyson
@GrecianWyson 2 месяца назад
Koma police yathu ya Malawi simukukhoza choncho sibwino tosefe ndife athu.ndikupepha mulungu wakumwamba alowerelepo mbali zose ziwili.inu a police officer munagwira tchitoyi yakumuvulaza muthuyu ambuye akudaritseni 😂
@bruhanhassan8494
@bruhanhassan8494 2 месяца назад
Kulakwa ndalama ndiwathu ziko ndiwanu
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 месяца назад
Amabugwe ntchito iyi ndiyosavuta akuyenera chithandizo
@kennedymakhula1203
@kennedymakhula1203 2 месяца назад
People are wicked, ntha kuwalodza ine apolisi amenewo
@EuniceBanda-pu6qp
@EuniceBanda-pu6qp 2 месяца назад
Mmmmm kulakwa
@ConnexMakande
@ConnexMakande 2 месяца назад
Kumalaw kulibe mtendere tikuphana chifukwa cha ndalama
@GiftMwasauka-uv6ql
@GiftMwasauka-uv6ql Месяц назад
Mtendele si Nsima #Malawi🤔.
@dicksonmwale8617
@dicksonmwale8617 2 месяца назад
Mbale wanga pepa koposa,zikoli silibwino.Boma liyenera lilipire
@shepherdmaseko3561
@shepherdmaseko3561 2 месяца назад
Uyutu ayiphula
Далее
NDIKUYANKHULA NDI MKAZI - Episode 165
16:03
Просмотров 35 тыс.
Your bathroom needs this
00:58
Просмотров 17 млн
Что не так с воздухом в Корее?
00:45
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH BON KALINDO
59:52
Просмотров 40 тыс.
Chikonzero chakaita kuti Baba Harare vatendeuke
45:03
Zikuchitika
1:13:13
Просмотров 14 тыс.
IMFA YA JANET ULENDO..kafuku-fuku oyamba..
43:15
Просмотров 41 тыс.
CRUISE 5   ELIYA NZERU WILLIAM
1:20:13
Просмотров 383 тыс.