Тёмный

ANTHU AMBIRI ADABWA NDIZOMWE WAPANGA SAMEER SULEMAN LERO KU CHIKANGAWA POMWE ANAFELA SAULOS CHILIMA 

Makosana
Подписаться 96 тыс.
Просмотров 41 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

23 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 210   
@JuniorHala-vf9ov
@JuniorHala-vf9ov 18 часов назад
Uyu nde munthu oziwa kuwawa kwa imfa god bless you big man
@chrisboyce2
@chrisboyce2 18 часов назад
Ife kuno ku Ntcheu Central kwawo kwa Biyeni💔 Tikunthokoza abanja la DPP kms Hon Sameer Suleiman kuti Mulungu akudalitseni maka polira nafe limodzi🙏
@lyiemax
@lyiemax 15 часов назад
I like Suleman much, munthu wanzeru, ozindikila and also with human heart ❤️❤️❤️❤️
@LuciusMowa
@LuciusMowa 19 часов назад
Pa ulemu wake zimakhala chonchi pa anthu omwe ali ndi munthu, osati Amcp sanaonetse chikondi Kwa vice pulezidenti
@VicentMalopa
@VicentMalopa 12 часов назад
Hon Sameer SulemanIs a Very Strong and Courageous New Generation Alpha Leader With Passion and Visitorn For Malawi 🇲🇼
@JibraanSharief-ol1yn
@JibraanSharief-ol1yn 17 часов назад
Uyu ndiye munthu woganiza mwa u munthu ❤❤rest in peace dr souls chilima
@LovemoreCathy
@LovemoreCathy 15 часов назад
God bless you Mr Suleiman chomwe mwapangachi sichinthu chapafupi ayi zaonetselatu kuti mwainu muli umunthu bwana..Ulemu wanu 🙏
@SaudhaKatete
@SaudhaKatete 19 часов назад
May Allah reward you Mr suleiman
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 13 часов назад
Imfa yowawa imeneija idakhudza anthu ochuluka a mcp sadachite bwino kupha poyera yera so touching.
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 19 часов назад
More fire Suleman
@AndrewjemesJemes
@AndrewjemesJemes 12 часов назад
Peter muntharika osamusankha vice mu2 uyu bwanj ? Ali mkuthekera kwakukulu God bless u boss let continue
@muhabaulen7912
@muhabaulen7912 17 часов назад
Allah wakbar my allah guide and protect sheikh sullaman🇲🇼🙏🙏🙏
@YassinAmbali
@YassinAmbali 16 часов назад
Bwana ndikanakhala woziwika ineyo ndikanati munditengeko 😢 Allah bless you always
@ImmanuelndagomaKondowe-n1v
@ImmanuelndagomaKondowe-n1v 18 часов назад
Uwu nde tmati umunthu, chifukwa olo aMANGANYA sanafikepo koma akufuna u president wa UTM
@VeronicaChirwa-ct4os
@VeronicaChirwa-ct4os 13 часов назад
Ndiponso inu
@JeanfatsanJere
@JeanfatsanJere 8 часов назад
Ambuye Akudalitseni koposa kamba ka mtima wanu❤❤❤ Addp🎉🎉🎉
@innocentmusuli7380
@innocentmusuli7380 18 часов назад
Kupawona pa chikangawapo mmmm ngati boza ndithu RIP SKC
@MariamAlabi-t3n
@MariamAlabi-t3n 18 часов назад
Jazzakallah may the Almighty Allah bless you my brother and the entire team
@BrightZionga
@BrightZionga 13 часов назад
Mr Suleman you are really cool leader ❤❤❤
@IssaLazack-ij1gf
@IssaLazack-ij1gf 17 часов назад
Izi zomwe zomafunika pa umuthu komaso monga tsogoleri wa bwino ❤❤❤
@Staphelsavimbindhlovu
@Staphelsavimbindhlovu 18 часов назад
That's good, may God bless you mr suileman
@KassimWilson-g6m
@KassimWilson-g6m 17 часов назад
God blesse you sulaimana
@cosmasnkanda8193
@cosmasnkanda8193 18 часов назад
Bravo bravo suleiman🙏🏾🙏🏾
@yassinn5634
@yassinn5634 17 часов назад
Pali gulu lina la Chisilamu (achikunja) amakhulupirira kuti akakapempha kwa munthu wakufa mzimu wake umapeleka madalitso ndiye sindikudabwa zikuchitika izi chifukwa chachisankho chikubwerachi. Wa nzeru wadziwa chomwe ndikunena akulimbikira ndi wa chipembedzo chanji?
@ShalomShine
@ShalomShine 14 часов назад
Our own MP more fire
@AkimumusaMusaakimu
@AkimumusaMusaakimu 19 часов назад
Tajambulani mtengo womwe unamenya dege uja please we want see that tree ..
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 19 часов назад
Abale mtengo umenewo nane ndimafuna mtawuona
@AtupeleChitenje
@AtupeleChitenje 17 часов назад
😂😂😂ndipo😢
@ZaithwaMatchado
@ZaithwaMatchado 11 часов назад
God bless you sulemani
@EdenNgulube
@EdenNgulube 14 часов назад
Mall power Mr suleman God bless you
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt 16 часов назад
Uyuu chimenecho ndimuthu wabwino kwambili kusondera manda zikulakwa ayi achita bwino allah akudalisani moyo wotelo
@shayrafernandeslatif9556
@shayrafernandeslatif9556 11 часов назад
Wosatopa wosafowoka wosawopa,SKC MHSRIP 🌹
@happynsaku
@happynsaku 15 часов назад
Oooo our dad shud rise ,thanks my brother u welcome,we thank u
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 17 часов назад
God bless yu sir
@andreabanda7838
@andreabanda7838 15 часов назад
Bwana Suleman. Uyu nde Umunthu mwaonetsa. Kulira mzanu
@DoreenLivata
@DoreenLivata 13 часов назад
Mm mm mayesa amati sukungafikidwe ndi nkhalango yoopsa kma ambuye atitetezele kmabe chilungamo chidziwika ndithu
@ShaffiMilias
@ShaffiMilias 15 часов назад
Jah bless you mr sulamana
@dalisoulphiri3094
@dalisoulphiri3094 15 часов назад
Komano ase iweyo ukamapanga ma videos akowa umakhalanso ndi nthawi yowonela zomwe wapanga upload zo? Cuz zimadabwisa kuti recoder yomwe umagwilitsa ntchito ndi ya 19 chani fukwa umachita kunvekera pansi ndiye kuti ngati munthu akufuna kunvera zomwe ukuyankhula azichita kumangilira amplifier?
@KhanMuhammad-n2w
@KhanMuhammad-n2w 13 часов назад
Kwa Onse amene anadya ndalama kudzera pa imfa imeneyo Ali ndi tsoka Rest in peace
@ThokoMsonkho-hy4uc
@ThokoMsonkho-hy4uc 19 часов назад
Ndipo a DPP asasiye ku gwiritsa ntchito imfa ya Chilima ngati nyambo yowakolera a MCP. Ndenge inagwera pa ground la mpira iwowo kumapita kuthengo daladala zazi. Pamene panagwera panafera CHILIMA ndipoti titha kusewelerapo mpira wamiyendo si kuthengo ayi ife tili ku mpoto kokuno tinawonapo
@EstherZintambira-sq3yy
@EstherZintambira-sq3yy 5 часов назад
Mpa ground bwanji mesa tidauzidwa kuti ndimkhalango mkati kumitengo nde mpila mumanenyapo bwanji?
@IshmaelJerard-u9w
@IshmaelJerard-u9w 13 часов назад
May Allah bless you❤ mr suleman
@RodgerChaula-r5z
@RodgerChaula-r5z 12 часов назад
God keep guiding spirit for Chilima and others 8 Saul rest in peace
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 19 часов назад
God bless you mr sulemana
@EsauSimkoko-u3t
@EsauSimkoko-u3t 13 часов назад
Mr suleiman ulem wanu big🎉🎉🎉🎉🎉
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 15 часов назад
God bless suleman
@UnicekapachikaHanzwell-zz8te
@UnicekapachikaHanzwell-zz8te 19 часов назад
God bless you mr soremani
@WezzieChisi-e1g
@WezzieChisi-e1g 16 часов назад
God bless you suleman
@StanleyChabwera
@StanleyChabwera 13 часов назад
Uyu ndiye muthu wachisoni kwambiri. Enawa olo tsiku limodzi kupitako....
@yassinn5634
@yassinn5634 17 часов назад
Anthu ambiri aDPP ndi aku Ntchewu akupusitsidwa ndi ndizomwe akupanga zokhudza imfa ya a Chilima . Imfa imeyi aDPP akupangira campaign ndipo ndi zachisoni kuti DPP ndiyomwe imasangala kwambiri pa imfa ya aChilima anthu ambiri sakudziwa kuti imfa ya Vice president idzaiwalika chisankho chikangodutsa. DPP ndi imene inali mdani weni weni wa Chilima zonse akupanga a DPP zi ndi MISONZI YANG'ONA YOMATI UKU IKUDYA UKU MISONZI IKUTULUKA. WANZERU AMVE MAU ANGAWA OPANDA AKHALE.
@chilembwekanjirawaya4296
@chilembwekanjirawaya4296 16 часов назад
Imfa imawawa aisey akanakhala Bambi Ako mwina
@chilembwekanjirawaya4296
@chilembwekanjirawaya4296 16 часов назад
Iyi siitha mpaka wina azpenga
@SaeedMaunde
@SaeedMaunde 16 часов назад
Ku dpp anabwerako wa moyo ,mcp inamupha,pamenepo wabwino ndi ndani?
@AademMulla
@AademMulla 16 часов назад
Mwachitabwino Suleman akulephera achakwera kukafikapo bad man
@MathewsLongwe-ix8ps
@MathewsLongwe-ix8ps 19 часов назад
Good idea❤
@marryphili5419
@marryphili5419 18 часов назад
My god bless you bro ❤️❤️❤️
@MzikaPhiri
@MzikaPhiri 12 часов назад
God bless u Sir
@AlfredInocente-l9e
@AlfredInocente-l9e 18 часов назад
Nzimu wa my present chilima uwuse mumtendele
@TameeraInglis
@TameeraInglis 11 часов назад
Suleman may God. Bless you.
@GeorgeChikwesele-k2v
@GeorgeChikwesele-k2v 7 часов назад
God bless you
@BrunoChakukuma
@BrunoChakukuma 14 часов назад
God bless you Suleiman
@StevieTaiza-n9k
@StevieTaiza-n9k 15 часов назад
God bless you boss
@HopeMakoka
@HopeMakoka 19 часов назад
Wa camera sakundionetsa chimtengo chinakola khupe la ndege bwanji, nkumati kowirira uku?
@RuthMkangala
@RuthMkangala 19 часов назад
Kupatula za kampenizo mwapanga bwino mwatiphuzitsa kukumbuka zimene Muthu amapanga Ali moyo zikomo mulungu akudalitsen
@chimwemwechiundira6002
@chimwemwechiundira6002 17 часов назад
Umunthu nde uwu😢
@AgnessKalindo
@AgnessKalindo 19 часов назад
Iweso ndi gulu chifukwa chimene akuchitazi sidzaka mpeni ayi or iweyo okhoza kupita kukapephelerapo . Chifukwa amene anamwalira aja ndi abale anthu.
@chippakaribafox2865
@chippakaribafox2865 15 часов назад
Amalawi ndife anthu opusa kwambiri....anthu kumachita kuwawona daily omwe anakhapa anthu amenewa zowona nawonso osawatema....
@MussaAndreQuenessi
@MussaAndreQuenessi 16 часов назад
Allah akupaseni zabwino
@TracyCassim
@TracyCassim 3 часа назад
Masha Allah ❤
@PatienceMphuche
@PatienceMphuche 15 часов назад
Uku ndiye kukhala mulungu akudalitseni.Manganya sangachite zimenezo Ali ndi kuzungulira kusaka ulemelero
@HaroonSaidi-jv3ek
@HaroonSaidi-jv3ek 17 часов назад
Allah Akbar is one who knows what is behind This ain not repenterble
@BeautyMtambo
@BeautyMtambo 2 часа назад
May good Lord be with you all guys is not easy ❤
@InnocentBanda-ze8de
@InnocentBanda-ze8de 13 часов назад
RIP SKC and 8 overs❤
@eunicesaiti
@eunicesaiti 3 часа назад
Misozi ikanatsikabe ukaganiza ngati maloto, Rip 😢😢😢😢😢😢😢😢😢
@RichardChirwa-em6qj
@RichardChirwa-em6qj 18 часов назад
Pambalambanda apa posawirira nkomwe. VP n team anaphedwa ndi chikangawa party
@chiefmitengo
@chiefmitengo 15 часов назад
Apiteso pamene panafera Isa Njaunjo. Komaso Ku poly komwe kunafera Robert Chasowa.
@Randy-er2xo
@Randy-er2xo 19 часов назад
ALLAH AKBER
@jomochirwa
@jomochirwa 19 часов назад
Pemphero ndiye yankho la zonse,simudalakwe a suleiman
@DavidKanyemba-n2s
@DavidKanyemba-n2s 17 часов назад
O Chakwera even one day kukaonapo Panafera Biyeni😢
@AslamCassim-b7n
@AslamCassim-b7n 18 часов назад
Ameen ameen Allah reward u
@LaghtonMadeya
@LaghtonMadeya 16 часов назад
Ndie pamenepo ndipoti anthu angayang'ane ndege kwa ma minutes angati
@JibraanSharief-ol1yn
@JibraanSharief-ol1yn 17 часов назад
Ameen ❤
@ShillahLawrence
@ShillahLawrence 14 часов назад
Ndizabeino ,chifkwa pa chikhaludwe ndi pachipembedzo ,anayenera kupanga zimenezo akanakhala a Cha kwela poti anali m ng'ono wao
@MarryNyilongo-s5x
@MarryNyilongo-s5x 16 часов назад
Mulungu ndiye akudziwa zonse ndipo akuona ngay ali oti anachita kuha mulungu ationetsera ndithu
@ManuelKamba
@ManuelKamba 14 часов назад
Suleman waonetsa umunthu kwambiri
@ImraanKananji
@ImraanKananji 17 часов назад
Allah reward you
@ChatambalalaChatambalala
@ChatambalalaChatambalala 13 часов назад
Zonse akudziwa ndi mulungu,mzimu wa abale athu onse upitilize kuusa ndi mtendere osatha.
@MagretSaizi
@MagretSaizi 14 часов назад
Pangatalike bwanji, chidzatera
@EmmanuelNgambi-y6h
@EmmanuelNgambi-y6h 14 часов назад
Umakwana suleman
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 18 часов назад
Zofunika kwambr ❤❤❤
@ChristinaLigomeka
@ChristinaLigomeka 19 часов назад
Ndipo usakayike kambani bwino report silikumveka ngati report ya school yakwacha kampeni ndimeneyi kumene onse otsutsa wo ine simpanga nawo zandale km imfayi inandiwawa koopsa
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 17 часов назад
It is only right🙏🏿🙌🏾
@MonijaKataika
@MonijaKataika 14 часов назад
n the president failed to passby like him... Shame on Malawian P
@ElliottBelon
@ElliottBelon 16 часов назад
God protect you suleiman
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 12 часов назад
Suleman munthu wandalama zake ndi wozichepesa God 🙏 continue bless you
@yassinn5634
@yassinn5634 16 часов назад
Pamaso pa mulungu moyo uli onse ndi ofana ma udindo ndi apadziko lapansi pompano ngatidi sulemani ali wa chisoni ndi imfa bwanji sanapitenso paja anthu 26 anapsera mini bus or mchipinda momwe Bingu anafera mwadzidzi? Akudziwa kuti izizi it's not trending. Ndipo musamatchule kuti Sheikh . Sheikh ndi title yakuti amapitira ku mapaphunziro achipembedzo.
@DamianoNombo
@DamianoNombo 14 часов назад
Kupatula kusemphana ku ndale siudani that's why udf inapangapo umodzi ndi mcp,manganya ,chakwera akhala akupita kumpoto no body stopped koma mkulu uyu wafika komwe asilikali sanafike mosaopa muyankha
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe 14 часов назад
Uko ndiye kumukonda munthu ndiponso kumukonda Malawi
@ambassadorsaul3980
@ambassadorsaul3980 18 часов назад
I wonder when people say nkhalango yachikangawa kunena apapa
@GiftNed-n2u
@GiftNed-n2u 15 часов назад
Amen ❤
@FrytonKampira
@FrytonKampira 15 часов назад
A chakwela ankat ndege inaomba phiri , komanso inagwela pakat pa phiri a Malawi taganizani pamene padagwela ndengepo pali phiri
@RAJABSTYLESTYLE-yi1el
@RAJABSTYLESTYLE-yi1el 12 часов назад
chikangawa ndimunthu woyipa
@MzombeDaniel
@MzombeDaniel 14 часов назад
Ndiwapoza uyu angofuna ma vote basi
@HajiraMustapher
@HajiraMustapher 14 часов назад
Amanganya muli pamenepo chifukwa cha chilima kod chimwalilireni nzanu chilima mwapangapo chani?taonani nzanu zomwe wapanga
@JafaliAkimu-ll1bf
@JafaliAkimu-ll1bf 16 часов назад
chakwera koma amapuma bwino pa moyo wake akaganiza za anthu anawaphawa
@benamos1058
@benamos1058 19 часов назад
Continue rest in peace skc
@AKMASEKO
@AKMASEKO 15 часов назад
Siyani kupanga compain mudzina la Chilama andale pepani sizikuthandizani pangani zoti zipindulire a Malawi DPP inaphanso akadili ndi Njauchi komanso UDF sitingayiyiwale Matafare n Chigawa namizani ana osati ife akale pepani
@JibraanSharief-ol1yn
@JibraanSharief-ol1yn 17 часов назад
❤❤
Далее
«По каверочку» х МУЗЛОФТ❤️
00:21
Please Help This Superhero! 🙏
00:48
Просмотров 2,8 млн
Ozoda - Lada (Official Music Video)
06:07
Просмотров 4,5 млн
THE DC BON KALINDO 24 September 2024
18:01
Просмотров 9 тыс.
TONDE WADULA DRAMA SERIES EPISODE 121
29:14
Просмотров 6 тыс.
Ditaba tsa Sesotho l 23 September 2024
24:36
Просмотров 3,2 тыс.