Тёмный

Anthu Awa Ayenela Ku Khala M'Boma 2025 Jaffa Mussa 

Nyasa VoiceBox
Подписаться 30 тыс.
Просмотров 1,9 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

25 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 29   
@mayesojameskatete
@mayesojameskatete 2 дня назад
Big Up brother true ❤
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt День назад
Yes us good nice brother mulungu akudalisene isi zilibwino kwambili ndasangalala naso tupere ❤❤❤ aford zoona kabzmba komaso nomary chisale zoona
@JohnJohn-og8rt
@JohnJohn-og8rt День назад
Atupere ndi boma🎉❤
@RiteRoderick
@RiteRoderick День назад
Anthu muli ndimoyo opusa zedi, aAtupere akudziwa chani za economy??? Kabambe mukumunenayo wapangapo chani mu economy ya dziko lathu. Anthunu ndiinu ogona zedi Amwene. Ndipo ngati mwadya dollar zawo kabwezeni coz mwawabera
@RiteRoderick
@RiteRoderick День назад
Inuyo sindikukudziwani koma ndiinu gona, Atupele wanuyo zoti akugulitsa chipani chake coz chokomedwa ndi ndalama simukudziwa??? No one will fit on Malawian president than APM boss. Mutu owopsa osakondera opanda nkhaza osakomedwa ndi ndalama not zanuzoyi
@GreshamKadzembe-tn8cq
@GreshamKadzembe-tn8cq День назад
Inutu ndi onama inu opanda nkhazazo ndani APM inu muli ndi chibwana kwambiri
@saidimwanyali8969
@saidimwanyali8969 6 часов назад
Atupele ndimunthu modzi amene tingapithule naye Mutharika tiyeni tipase ulemu basi
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Час назад
Atupele apo nde bodza nde Bola Kabambe or APM
@StevenGJohn
@StevenGJohn 2 дня назад
Akuti boma ndilomweli likupha anthuli
@staindulamanja1218
@staindulamanja1218 6 часов назад
Atupele akukanhikk kupanga chiganizo lero
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 Час назад
Iwe ndiwe wa UDF mjomba nchifukwa chache ukufuna Atupele Wanama Bola APM or Kabambe
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 2 дня назад
Atupere amachedwa kutenga action
@HassanTwaibu-c6h
@HassanTwaibu-c6h 2 дня назад
aaaaaa mulungu ndamene akusiwa basi
@YusufAjida-t8r
@YusufAjida-t8r 2 дня назад
Iwe boma ndilomweli lakwambuyako chamba eti
@Littlefair7
@Littlefair7 День назад
Akuyankhula zombwambwana mbuli uyu, Atupele sangayendetse dziko, pa youtube pano yasanduka platform yotankhula zoduka mutu.
@johnkambala692
@johnkambala692 2 дня назад
Pano mabodza ai. Zimenezo zonse mbava tikukudziwani anthu inu.
@DaudRashid-sp3sk
@DaudRashid-sp3sk 2 дня назад
Iwe ndi mwana zomwe ukhuyankhulazi zawonekelatu kuti ukupanga sukuziwa wakutha gayiwa wakowo uko wati uzatinyase apa
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 дня назад
Ai zikomo kwambri
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 дня назад
Mbava zokhazokha izi anthu inu kupepela bwanji kodi mpaka pano simunazindikirebo kuti anthu Andale amafuna kuzitukula okha
@DysonTummiesSajiwa
@DysonTummiesSajiwa 2 дня назад
Chisale mukumunena apayu yemwe uja anaba cement uja kapena wina aaaa tamankhalani serious ngati akulonjezani ndalama wayiponda anse
@AshanAlexx
@AshanAlexx 2 дня назад
Umboni mulibe khani unapita Ku court and mulandu anawinatu don't forget
@Maxwell-j2t
@Maxwell-j2t 2 дня назад
Zazzi
@EmmanuelRichard-k9k
@EmmanuelRichard-k9k 2 дня назад
Inu ndi achisilu
@YOUNGKIDS-k5d
@YOUNGKIDS-k5d 2 дня назад
Chitsilu ndiiwe sudziwa kanthu
@EmmanuelRichard-k9k
@EmmanuelRichard-k9k 2 дня назад
@@YOUNGKIDS-k5d iwe ndikape ao ndimaganizo ako osati amalawi
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 дня назад
Boma ndilomweri la congeresi basi palibe kusintha
@THANNAMTENDERE
@THANNAMTENDERE 2 дня назад
Osamangonyoza tayesaniko atupele mumuwone sizobwelela mbuyo pano
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 дня назад
Kwathu tisintha congress ai
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 2 дня назад
​@@THANNAMTENDEREAtupere odzimva u
Далее
На самом деле, все не просто 😂
00:45
РОК-СТРИМ без ФАНЕРЫ🤘
3:05:16
Просмотров 1,3 млн
ITZY 예지한테 AI 메이크업하기💖 #shorts
00:23
Ben Kay ft  APM  - DPP Moto NVB Visualiser
3:02
Просмотров 6 тыс.
A DPP Mwafulumila Kulira   Shafie Hassan
14:58
Просмотров 1,8 тыс.
На самом деле, все не просто 😂
00:45