Тёмный

Aqīdah Kwa Akazi - Day 29 

Free Online Madrasah
Подписаться 1,3 тыс.
Просмотров 156
50% 1

Lero asilamu ena mu gulu la akazi akumapita mwa abusa nkumakapempha chithandizo (kumapemphereredwa, kupatsidwa madzi oyera, ndi zina zotero); ena mwa iwo akupita kwa asing’anga kukaombedza mu nthawi yomwe mavuto awagwera; ena akukhulupirira mu nyenyezi (horoscopes); ena akukhulupirira mwa mizimu pamodzi ndi ziwanda; ena akumapita kwa ma sheikh kukachititsa matalasimu; ndipo ena akumapempha omwalira ku manda. Kenako akachita ntchito imeneyi, iwo akumabwera m’mizikiti yathu namapemphera tsiku ndi tsiku. Enanso afika pomakhulupirira mbali imodzi ya Qur’ān ndi kumakanira mbali ina. Mtumiki wa Allāh (ﷺ) amamutsata pakamwa pokha koma osati mu ntchito zawo.

Опубликовано:

 

13 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 2   
@ShaId-qc9bh
@ShaId-qc9bh 2 месяца назад
Jazakala khaila.mashaallah zikomo kwambr
@UthumanDaudi-f2g
@UthumanDaudi-f2g 2 месяца назад
Ma shaa Allah
Далее
Aqīdah kwa Akazi - Day 30
1:10:49
Просмотров 211
hadith ke17: Hadith 40 Imam Nawawi  - ibnu rijal
56:51
Просмотров 2,9 тыс.
IPGM KTHO - PROGRAM BUDAYA AL-QURAN BIL. 35, 2024
59:43
Aqīdah Kwa Akazi - Day 28
54:59
Просмотров 181