Тёмный

Asilikali 62 a Rwanda alowa mdziko la Malawi motsogozedwa ndi General wamkulu kwambiri. 

Bakili Muluzi TV
Подписаться 133 тыс.
Просмотров 87 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

15 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 231   
@lyiemax
@lyiemax Год назад
Mmm MCP itipweteketsa ndithu, go deeper our own informant, love you, proud of you always 🔥🔥🔥🔥🔥
@onester4946
@onester4946 Год назад
This journalist is genius. Umafufuza aise. Big up. I like how you use deep knowledge to research news. Chakwera is killing refugees.
@bernadakim6544
@bernadakim6544 Год назад
Kod ndinu muli ndi ka RU-vid Channel kanu kopepela mumakatcha bakili muluzi 🤣🤣🤣, zot kutali pass out week yatha ya ma cadet simumaziwa? Zot kunafika ma general from different countries like Zambia, Rwanda, eswantin, Mozambique,Kenya, Tanzania pamwambowo chifukwa ena mwa omwewa amapanga pass out are from those countries simukuziwa iyayi? Page iyiyi yazaza NDI ma bulutu.. very foolish, stupid and ignorant.. ka school kaja pena pake kamathandiza
@devlinebhema2729
@devlinebhema2729 Год назад
@@bernadakim6544 bulutu nd iwe aise palibe akukukukamamiza kut uzinvela
@obimonegev5579
@obimonegev5579 Год назад
Anthu ngat iweyo ndiyamene akufunika kumakhala dziko muno, receive your flowers 🎉
@francistonysanena5349
@francistonysanena5349 Год назад
I don't think that the government has to review everything to the public
@TONYJUSTIN-cx7yt
@TONYJUSTIN-cx7yt Год назад
Iweyo ase the best of the best history in malawi 🇲🇼 👌
@thomassimbaya197
@thomassimbaya197 Год назад
Watching from Zambia muchinga province God bless you,you are the best,
@LUCKYM4787
@LUCKYM4787 Год назад
Ohoho thanks very much bg mn respect ndawi zonse
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 Год назад
This journalist is very great.
@EmmanuelThom2-xf6ij
@EmmanuelThom2-xf6ij Год назад
More thanx bro 4 keeping us updated
@misianguisheraufi4803
@misianguisheraufi4803 Год назад
This is nice narration, evidence based journalist
@mathiasmajamanda5797
@mathiasmajamanda5797 Год назад
This is great and well explained
@honourablemcgregorysc97tv
@honourablemcgregorysc97tv Год назад
One of the best Channel🔥🔥🔥🙏🙏😍
@mateyudyton4739
@mateyudyton4739 Год назад
Good work brother keep on informing us
@successngoma
@successngoma Год назад
Malawi 🇲🇼 God help us
@matamandonkhoma8163
@matamandonkhoma8163 Год назад
You stand for Us Boss
@argentchilanga3246
@argentchilanga3246 Год назад
Zikachitika timvera Kwa inu big man give us more zomwe zikuchitika mziko lathu from South Africa
@davenchimadzi6529
@davenchimadzi6529 Год назад
Asazakunamizeni chakwela sanali m'busa wa mulungu. Awawa ndmaplan omwe akupanga kukhomzekela zisankho gyz tisamale kufa anthu kuno😭😭😭😭
@ManuelMalunga-fl3vq
@ManuelMalunga-fl3vq Год назад
Yaaaaah oooooh!! Point iyi zedi thanks brother Wanga 😢😢
@wilsonsawasawa3794
@wilsonsawasawa3794 Год назад
You are the best! Big up
@yasinkamwendo-jf7sc
@yasinkamwendo-jf7sc Год назад
Big up brother King 🤴 of history ❤❤❤
@andersonmaster8055
@andersonmaster8055 Год назад
Best chanel than ever
@ahmedmsume1489
@ahmedmsume1489 Год назад
Koma ase iweyu u can rule Malawi coz u know history alot
@ManuelMalunga-fl3vq
@ManuelMalunga-fl3vq Год назад
Ndipo zedi brother ndidolo uyu zed
@johnchavula3282
@johnchavula3282 Год назад
Thanks but please do Hosni Mubarak
@WilliamChopika-d1z
@WilliamChopika-d1z Год назад
Inuyo munadalitsika boss much respect, izizi nde zikufunikila mu dziko lathu lino
@irenechirwa9710
@irenechirwa9710 Год назад
Brother bwanji mungopanga zoti muzapikjsane nawo pa chisankho cha upule tizakuvotelani ife pls.
@emmanuelkhosa-ze6fl
@emmanuelkhosa-ze6fl Год назад
Please tell us about the story of the people leaving in moon
@rashidstamburi2705
@rashidstamburi2705 Год назад
Big up 💪🏻
@farookousmane715
@farookousmane715 Год назад
King of history!
@martinkhozombah
@martinkhozombah Год назад
Keep up the good work boss
@chitimbethegreat-pc1bp
@chitimbethegreat-pc1bp Год назад
Chakwera ndi mzake chilima have change Malawi to den of robbers
@khamaneizarif4491
@khamaneizarif4491 Год назад
Good job
@drbanda6105
@drbanda6105 Год назад
Bbe up♥️♥️♥️
@ziwani3682
@ziwani3682 Год назад
BIG 👍
@chekiamaabdul5083
@chekiamaabdul5083 Год назад
Asilikali a Malawi ndiye kuti ntchito Samatha??? Mpaka kuwabweletsela asilikali adziko lina aaaaaa shame
@josuahkachali1489
@josuahkachali1489 Год назад
Keep it up Mr
@innocentissah2636
@innocentissah2636 Год назад
Chakwera khala serious osaononge dziko la Malawi ndi nkhondo, ona ku DRC nkhondo yemwe amalimbikitsa ndi Kagame yemweyonso,kulira kulowetsa zigawenga m'dziko zoona, watitopetsa ndiwe munthu osaganiza.
@nickmagola278
@nickmagola278 Год назад
You are a machine in history
@isaactembo6164
@isaactembo6164 Год назад
Tikhale ndi airport ya asilikali payokha iyo ndi public airport, sikofikila asilikali.
@dhaoudhiabedinegomaseko2363
Ndipo kwambiri zoona ada koma MCP ayi zikomo
@anafieintuka8090
@anafieintuka8090 Год назад
Inu ndiye mozi kwa history
@YunusuOfesi
@YunusuOfesi Год назад
Mumakwana big ❤
@titomethiwa4213
@titomethiwa4213 Год назад
Ndimakunyadilani big man koma ndimafuna ndifunse zikuwoneka kuti kangame ndimuthu oipa kwambiri koma sangakusakeni inuyo chifukwa ndimuthu oipa
@ManuelMalunga-fl3vq
@ManuelMalunga-fl3vq Год назад
Amakhala Kuti iyeyonso Ali well safeguarded by his people boss
@nelsonmacken7662
@nelsonmacken7662 Год назад
Koma bwanji Mr president Alola zimenezi
@daviemafunga
@daviemafunga Год назад
Munabadwa masiku okwanira brother mumakwana heavy
@levisondaka6392
@levisondaka6392 Год назад
This is true story I remember well my friend from Rwanda who were taken to that country they were killed by this guy's truly you can feel bad what I Saw that time please work up Malawi
@JeanMarieNsengiyumva-qu9vm
@JeanMarieNsengiyumva-qu9vm Год назад
😭😭😭😭😭yoooooohhh Mulungu Tetezelani ana akoo
@promisemakawa1556
@promisemakawa1556 Год назад
Atsogoleri aku Malawi ndi zitsiru
@ChembeSolomon
@ChembeSolomon Год назад
Never give up
@professorsafuta3936
@professorsafuta3936 Год назад
Mmmm koma ndiye zosakhala bwino ndithu, eeish
@gesinasutherland9241
@gesinasutherland9241 Год назад
ndakugomelani..ndipo umantha...abusa sadapange bwino ndipo asilikali amenewa anyamuke
@HakeemSilaji
@HakeemSilaji Год назад
Pena ndkaikhala ndi kumawona ngati kamuzu anasiya buku lina rake kuchipani cha m.c.p lophuzitsa dza ulamurilo wawo 😢😢
@andrewkapanga-jo2cj
@andrewkapanga-jo2cj Год назад
Exactly the way i think.
@HakeemSilaji
@HakeemSilaji Год назад
Sirius
@ManuelMalunga-fl3vq
@ManuelMalunga-fl3vq Год назад
Fact brother
@wensleyshumba8205
@wensleyshumba8205 Год назад
Chakwela ndichitsiru kwambili angalole bwanji asilikale alowe mu mziko ngat muli khondo , Nundwe naye angokhala ngat alibe mutu zautsilu kwabwas nkondo yili ku ukraine not ku malawi
@idrissaeliassa
@idrissaeliassa Год назад
Politicians ndi anthu onyasa zochitika zawo
@NeversonGonthi-fg3zm
@NeversonGonthi-fg3zm Год назад
Chitetezo cha Malawi chalowa mbola,aganiza bwanji abusa?
@AlexKaunda-ir6rz
@AlexKaunda-ir6rz Год назад
Chakwera mbolo yako sure Ngati dziko lakurephela zisiye panyapako😂😂😂❤
@sumanmedson6068
@sumanmedson6068 Год назад
Koma adaha😄😁😁😆😅🤣😂😂
@kamwendoderek6567
@kamwendoderek6567 Год назад
TRUE GOD IS GOING TO FIGHT FOR THIS ARMY,
@alfredbanda886
@alfredbanda886 Год назад
Chakwela alionetsa Zinthu Dziko Lamalawi
@justicenyirenda2049
@justicenyirenda2049 Год назад
Timva zinthu🙌
@HestingsBellow
@HestingsBellow Год назад
Crying for my mother Malawi
@evancenasoro922
@evancenasoro922 Год назад
Mwatisuka mmaso apa boss 🎉😊
@eunicemoyo6024
@eunicemoyo6024 Год назад
Chiopsezo chiliso kwaife pamenepo dziko lilibe security ili😣😣
@BenadetaChisale-z9t
@BenadetaChisale-z9t Год назад
😢😢
@DicksonMulinde
@DicksonMulinde Год назад
Abusa sakuchitadi bwino Dr chakweka
@kubengovender6996
@kubengovender6996 Год назад
Chakwera ndichitsilu mbolo yamake wakupha!! Guys we vote for wrong person , chosadzi nafenso!! Big up my brother for your good research!!
@ManuelMalunga-fl3vq
@ManuelMalunga-fl3vq Год назад
Very bad my Malawi😢😢😢😢😢
@NgaboJeanvier-iw4yu
@NgaboJeanvier-iw4yu Год назад
Great documentary from intelligent man... true story of best killer in our continent..big up man
@jaykar-issa706
@jaykar-issa706 Год назад
Gen Nyakarundi Vincent is Army chief for intelligence, Imachedwa Department Military Intelligence ( DMI)... ndi anthu oopsa zedi! 😢😢😢
@AlickNyirongo-cp1dn
@AlickNyirongo-cp1dn Год назад
chakwela sure bt niphala la munthu angalowese asilikali a ku ruward sure
@jermahkell8538
@jermahkell8538 Год назад
Zomvetsa chisoni, ku mchinji anachita kubwera asilijali nkumamatchola ma shop nkumauza anthu kut azitulutsa katundu, God over everything
@eunicemoyo6024
@eunicemoyo6024 Год назад
Shaaaaa kom zomvesatu chisoni mpakana kwatengela zinthu mushop pali uzimu apa
@ManuelMalunga-fl3vq
@ManuelMalunga-fl3vq Год назад
Mmmmmmmm zachitika litiro zimenezi?😢😢😢😢😢 Koma Chakwera guys ai zikomo 😭😭😭😭
@ManuelMalunga-fl3vq
@ManuelMalunga-fl3vq Год назад
​@@eunicemoyo6024Ndagwetsa nsonzi inee😭
@josephychisoni8628
@josephychisoni8628 Год назад
Ndiye mvuto ndichani mesa akutenga akwawo Ngati akutenga a Malawi 🤷🤷
@maxgulani1391
@maxgulani1391 Год назад
Chakwera ndi Mbuzi yamunthu ameneyi angobwerera Ku church basi
@georgekalichero7829
@georgekalichero7829 Год назад
Mmmmm kagame ndiwachabe
@bayview4554
@bayview4554 Год назад
Koma chakwerayu ndi buzi yamunthu akulolawesa zigawenga ziko zoo a
@rosseshaibu1576
@rosseshaibu1576 Год назад
❤❤❤
@oscarkachale9234
@oscarkachale9234 Год назад
Live them
@wensleyshumba8205
@wensleyshumba8205 Год назад
Munthu wogwila kuchipiku angalamulire dziko anazolowela kunyamula mathumba akamba bas mbuz yeniyeni
@frankmajawa528
@frankmajawa528 Год назад
Km iziz sizabwino these ppo came here bcoz they wanted peace and they hav sweat alot fo them to get wat ever they hav now penapake ndbwino kumaganiza kut ndtakhala ine ndkupangidwa zimenezo ndnganve bwanj, God must be the only helper
@marthankhoma1063
@marthankhoma1063 Год назад
Akuyanjana ndi anthu oipa kufuna kusokoneza bziko la Malawi
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera Год назад
As malawian citizens I will never allowed this nonsense to happen m"boma liyenela kuwasiya anthuwa tizikhalanawo mwantendele ngatimene timakhaliramu osamati kumazuka ndikumasawusa mitima yaanthu osalakwa
@georgechikafutwa1334
@georgechikafutwa1334 Год назад
Funso nkumati kodi ma Hutuh kwao ndikuti ngati akukhala mothawathawa dziko laku Rwanda?
@Rafiki-pk7hw
@Rafiki-pk7hw Год назад
Chakwala ndikamukonsa koma mmmm ndaona kuti ndi manyi amuthu
@jacquesnsabiyaremye3166
@jacquesnsabiyaremye3166 Год назад
Apapa zayambika, Chakwela akusewela ndi team((Rwandan Solders) imene sakiyidziwa. Anthuwa amalora kupeleka ndalama iliyonse cholinga aketse mwazi(Blood) basi. Mukaitsatila bwino nkhani mupeza kuti boma la Malawi lalandira ndalama za nkhani nkhani cholinga Ma Refugees asowe mtendele basi. Si izi Zayayambika ku Chileka ndi madela ena ndi ena.
@JeofreyNamalima-yn4tj
@JeofreyNamalima-yn4tj Год назад
Bingu samanvera iz kma awaw mmmmm mawu ndilibe
@ManuelMalunga-fl3vq
@ManuelMalunga-fl3vq Год назад
Usandikumbutse malemu wathu wabwino ujaaa brother or Adzungu kunoko amanena Kuti amalawi ndiife zisiru tinkalimbana ndi munthu wanzeru yemwe anakalemeletsa Malawi
@pastonmoda-pk4uj
@pastonmoda-pk4uj Год назад
Koma mulungu akuwaona sangasanglale muthu akuvutika chocho
@mathewsmwale20
@mathewsmwale20 Год назад
Lazarus chakwera is not fair why can he allow such people to enter his country maybe he knows something and they offered him some money
@AlexKaunda-ir6rz
@AlexKaunda-ir6rz Год назад
Zikhare ng'oma mbuzi yamunthu mulizelu m'menemo Mutu unangokula 😂😂😂❤
@NeoMaphango
@NeoMaphango Год назад
😢Yo
@greychizaka4088
@greychizaka4088 Год назад
be an advicer to our govt officials eish......
@alexsumani6823
@alexsumani6823 Год назад
Awa atipwetekesa sure
@NeversonGonthi-fg3zm
@NeversonGonthi-fg3zm Год назад
Agalu awa atipwetekesa.koma za UN akuziziwa ?
@rickiez
@rickiez Год назад
Im afraid to comment......Zikhale Ng'oma ndimunthu wabwino.
@Mohamedkotwal
@Mohamedkotwal Год назад
But the question is How many richest people are leaving in out of the country? Chakwela please treat well the pples
@nyararaishumba9288
@nyararaishumba9288 Год назад
Chakwera walandilapo ndalama pamenepo afuna aphese Anthu bas
@ManuelMalunga-fl3vq
@ManuelMalunga-fl3vq Год назад
Kwambiri zedi iye wadyapo miyoyo yathu ikupululuka😢
@yampanyamulenda9377
@yampanyamulenda9377 Год назад
Whaooww 😲😲 I can't believe that in Malawi you have such brilliant journalist 🤔🤔 Tell them, teach them 😂😂😂 Many people don't know exactly what we be the consequences of the presence of this rwandeses on the Malawi land
@lewisbonongwe8518
@lewisbonongwe8518 Год назад
Malawi lero Ali pa mpeni vuto ili Matsatatsata Amalawi lero ndi izi Ntchito Qne million zija ma Mega farm aja Kudya katatu kuja ndikumeneku amalawi kususuka lero ndi nkhondo iyo
@nashoniclifford172
@nashoniclifford172 Год назад
Wait Malawi idzazindikira bwino patsogolo
@LimbaniYassin
@LimbaniYassin 2 месяца назад
Umakwana bakili muluzi tv
@henrymunthali1280
@henrymunthali1280 Год назад
Kkkkkkk pot ndi akuda akanakhala ogalukila achizungu mukana khala chete
@mansonchinkhuzi
@mansonchinkhuzi Год назад
Marefugees sakhala pakati padziko ayi uyu amalandila ndalama kuti azitchuka ndi zinthu zopweteka amalawi azake mtayeni
@mansonchinkhuzi
@mansonchinkhuzi Год назад
Zikhale asabwerere mmbuyo kufikila awavachoke basi akakhale ku chitipa pakati padziko ayi ati takana amalawi amasomphenya
@molicieeosama8877
@molicieeosama8877 Год назад
Kagame He going mad naw
@MikeSungitsa
@MikeSungitsa Год назад
Umakwana nkani zakwatu umazitsata hv
@ibrahimatibu8784
@ibrahimatibu8784 Год назад
Malawi kwathu bass ndi mbili yakale palibe chabwino misonzi yokha kumangotuluka
@GraceBeza-d7o
@GraceBeza-d7o Год назад
Chakwera akuononga nziko 😢😢
@gladysbonongwe1038
@gladysbonongwe1038 Год назад
Kobasi
@MaidakaisiNkota-oo5tz
@MaidakaisiNkota-oo5tz Год назад
Mesa ma social midia mumapempha nkhondo ya friendly ndiye abweratu
Далее
Silent Hill 2 - Мульт Обзор
07:26
Просмотров 260 тыс.
Cool Parenting Gadget Against Mosquitos! 🦟👶
00:21
КТО БОИТСЯ КЛОУНОВ?? #shorts
00:20
Просмотров 575 тыс.
Nancy vs Che Nkope - Apatseni moyo wautali
11:05
Просмотров 4 тыс.
GWEDE GWEDE PA MALAWI | 11 October  2024
26:26
Просмотров 4,3 тыс.
Assista na íntegra o Balanço Geral 16/10/2024
Просмотров 1,2 тыс.