Тёмный

BAMBO NDI MWANA APHEDWA NDI ANTHU POWAGINIZILA KUTI NDI FITI By gova 

Balanço semanal CK & Govate
Подписаться 21 тыс.
Просмотров 67 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

17 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 60   
@EmmanuelZiba-qz6ug
@EmmanuelZiba-qz6ug 22 дня назад
Am watching you from Lusaka Zambia 🇿🇲😢😢😢😢😢😢
@Mpungwe123
@Mpungwe123 2 года назад
Zinazi pena umazaona ngati ukulotatu....tisamatengere malamuro mmanja mwathu chonde government must wake up and shield her innocent souls.
@sergiopauloposse7610
@sergiopauloposse7610 2 года назад
Zoona.
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 2 года назад
Exactly
@ChisisiKamphambe
@ChisisiKamphambe 4 месяца назад
Zooona
@TiagoManuelBanhaBanha
@TiagoManuelBanhaBanha 2 месяца назад
Heee angonia é outro nível 😢😢
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 2 года назад
Nkhani yoziziritsa nkhongono. Zambirizi zikuchitika chifukwa cha mangawa,umbuli ndinso kaduka. Izi zipangitsa kuti anthu adzingophana ngati nkhuku chifukwa cha nkhani ngati zimenezi.
@sergiopauloposse7610
@sergiopauloposse7610 2 года назад
Balanço Semanal está melhorando cada vez muito mais obrigado pela informação. E muito triste.
@josuahkachali1489
@josuahkachali1489 2 года назад
Very sad watching live from Kuwait
@RuthMvula-kq2dd
@RuthMvula-kq2dd Год назад
Ambuye atithandize
@lazarusziyaya3997
@lazarusziyaya3997 Год назад
Kodi ku Mozambique malamulo a ufiti amati bwanji ?
@jazakalemani3127
@jazakalemani3127 Год назад
A balaco mwasowatu bwanji mwasiya kutipasira nkhani?
@osamabinraden9391
@osamabinraden9391 2 года назад
Keep up bansosamana👏👍
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 2 года назад
This is completely out of ignorance , civic education is greatly needed in these areas . Innocent souls are being killed.
@cynthiakananji1608
@cynthiakananji1608 Год назад
Umbuli akapolo umphawi Majerouse Sukulu ndiyofunika. Kupha anthu ngat nkhuku akapolo otembereredwa...
@promise3693
@promise3693 2 года назад
Anthuwo akanadikira ndipo choonadi chilamaululika ... ndiye iwowo apha ndiye wakufa winayo apezeka bwanji
@jvpondan4332
@jvpondan4332 2 года назад
😭😭😭😭😭komatu sibwino abale tapempherani iiii
@austinvincent773
@austinvincent773 2 года назад
Proud of you barancol
@mavuschitseko7757
@mavuschitseko7757 2 года назад
Mmmmmm tili mmatsiku otsiliza zedi😭
@EdwardGeorgeKasabola
@EdwardGeorgeKasabola Месяц назад
Koma zosayenda
@aleksawilliams710
@aleksawilliams710 2 года назад
🤔🤔Mozambique nkhani izi zikuchulukiratu
@frankmaluwa5120
@frankmaluwa5120 2 года назад
Aaaaaaa this is out of hand now ngati zinthu zikutere tsopano ndiye Kuti apolice kapena Kuti achitetedzo sakugwira ntchito yawo, Koma zikomo kwambiri Inu anyamata a balaco semanao mukugwira ntchito yotamandika
@MarcelinoManquena-ws8nd
@MarcelinoManquena-ws8nd Год назад
Inyo dine kalekale Kodi zimenezi zimakhala zoonadi timazionadi pa balaso semenalo
@halimahussein6571
@halimahussein6571 2 года назад
Chilungamo ndichakuti anthu aku Mozambique sagawa kamba ndi ankhadza nkhondo yinawalowa mmitima
@balancosemanalckgovate8464
@balancosemanalckgovate8464 2 года назад
Kkkk mpaka pamenepo?
@victoriawilliam4490
@victoriawilliam4490 2 года назад
Ndipo ndizoonadi
@pililanibuliyani7684
@pililanibuliyani7684 2 года назад
Za ufiti ziripo koma sibwino kutengela malamulo manja mwako boma lirowelerepo zikomo Agova
@rabeccagama4067
@rabeccagama4067 Год назад
Boma linayenera kutengapo gawo sizoona amalawi umunthu tinausiya kuti Nkhani zogopeka plus maudani aaaaaa amalawi pliz tiyeni tikondane ndithu komaso pena zimaonesa umbuli nanga mene awaphamo chisithe chani mudzimo maliro asiya kumwalira ana awo a malemu mwapasa picture yotani nakakonda atamagidwa anthu amenewa aaaaa munthu kumumpha ngati galu
@martaarauio1347
@martaarauio1347 2 года назад
Afela zawo amenewo kumoto Basi
@ririvilla1423
@ririvilla1423 2 года назад
Apolisi sakugwila ntchito yawo anthu apha anthuwa aphedwenso
@louiskk100
@louiskk100 2 года назад
Umbuli wachuluka...Mukatero muyambe kumenyana,nkhondo sinakukwaneni eti?
@lucysimbani3971
@lucysimbani3971 2 года назад
Zosayenda ayi anakangowamenya mkuwasiya mwina osati kumphelatu ayi mwina akanasiya ufitiwo
@MarcelinoManquena-ws8nd
@MarcelinoManquena-ws8nd Год назад
Oooo pepani kwambili
@majendauzananilimitedi2049
@majendauzananilimitedi2049 Год назад
Pitilizani kumatipatsa actualizações ❤
@promixphotography8056
@promixphotography8056 Год назад
Ndikuti uku mwati
@MrnjiwaNjiwa
@MrnjiwaNjiwa 8 месяцев назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@ancientnkhata1137
@ancientnkhata1137 2 года назад
Nsanje and kaduka
@HarryUmarih
@HarryUmarih Год назад
Mumakwana
@iangama35
@iangama35 2 года назад
enanu mukut zalakwika km muzazindikila ufitiwo mukazakumana nawo.....ufiti ulipo guys wake up.......ine ndalhulupilira nkhaniyi...
@ClementWanja-f4k
@ClementWanja-f4k Год назад
Anakumana ndi zukwa
@aliciabanda3656
@aliciabanda3656 2 года назад
Mmmmm koma abare inu sambi
@ibrahimalfred6539
@ibrahimalfred6539 2 года назад
Komano afiti awonjeza serious anthu amafika potopa abale osati anthuwa olakwa chifukwa even ukapita ku police uva zilibe umboni ndiye anthu atani kutopa ngati amfumu akuyankhula chocho afiti polani moto chifukwa anthu atopa
@chifunirogoliat4630
@chifunirogoliat4630 Год назад
Sopano ngat mukut ufit kulibe mfiti zina zimafika poulura kunena zokha kut zimatamba ndikupha anthu muufiti..zimakhala kut ndichan
@sulaimanabanda9605
@sulaimanabanda9605 Год назад
Apolsi akulephera ntchito yawo
@lydiaamos4214
@lydiaamos4214 2 года назад
Danger in the Last days
@fatimahluis6450
@fatimahluis6450 Год назад
Koma kumeneko mkuti
@JosephBanda-fl5ss
@JosephBanda-fl5ss Год назад
Please pitiliza ni kutipasila
@bonifaciosimao8620
@bonifaciosimao8620 2 года назад
Zovetsa chisoni kwambiri 🥲
@peterbanda7003
@peterbanda7003 2 года назад
School anthu awa ikufunika kwambili
@jvpondan4332
@jvpondan4332 2 года назад
Koma simukufunikira mudziranga anzanu choncho
@jvpondan4332
@jvpondan4332 2 года назад
Komatu ndikanakonda ndikadakhala mudzi umenewu
@mariamhalid9185
@mariamhalid9185 2 года назад
Eeeee abale ndi chian kwenikwen...tili mmasiku omaliza
@victorbanda7546
@victorbanda7546 2 года назад
This is very bad izi ndi nkhani zopanda umboni kodi munthu wakufa amalakhula?apa mwapha anthu osalakwa kunali bwanji kuwatengera ku police kusiyana ndikuwapanga khaza ngati zimenezi,boma likuyenera kuchitapo kanthu
@zainabchikakuda6297
@zainabchikakuda6297 2 года назад
Boma lichitepo kanthu anthu tikutha ,
@nelsonmwanache8692
@nelsonmwanache8692 2 года назад
This is very bad
@marianyirenda
@marianyirenda Год назад
This area is too much primitive ,these people they must go to school they are still living old fashion ways they believe in witchcraft
@miloslundu6366
@miloslundu6366 2 года назад
a police sanathandize sanapeleke mau oteteza banjali
@dakasaul3111
@dakasaul3111 Год назад
Mmmmmmmm mavuto aakulu zedi zikomo balaçio
@armandojohn7641
@armandojohn7641 2 года назад
,,,,
Далее
tikupirizabe
14:18
Просмотров 36 тыс.
ZOMWE ALANKHULA A DR JOYCE BANDA KU CHIKWEWO, MACHINGA
30:53
CRUISE5 WITH MAYI NAYERE
1:30:20
Просмотров 12 тыс.