Тёмный
No video :(

BOMA LIKUFUNA KUZENGA MULANDU A BON KALINDO WA ALBIONⓂ 

TIDZIWE TV
Подписаться 8 тыс.
Просмотров 13 тыс.
50% 1

Tidziwe tv

Опубликовано:

 

26 авг 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 56   
@user-mc8gk4xv3f
@user-mc8gk4xv3f 8 месяцев назад
Mulungu achite nao anthu onse amene akumufunira Bon Kalindo zoipa, kuphatikiza Ben Longwe ndi Lerdson Munlo. Mulungu achite nao onsewa
@thesocietynews3181
@thesocietynews3181 8 месяцев назад
Pempho kwa a Malawi onse: Tiyeni tipereke support kwa PRESIDENT wathu the DC Bon Kalindo.
@patrickmacheso5062
@patrickmacheso5062 8 месяцев назад
That's true my brother, let's support him and show Chakwera that he is a failure.
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 8 месяцев назад
❤❤❤❤ameen ndipo zoona may Allah protect bon kalindo
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 8 месяцев назад
Mwachoka kutali Mr kalindo Ana achepa mulungu wakhala nanu nthawi yayitali ndipo alinanu komanso adzakhala nanu osaopa nkhondo amenya yekha .
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd 8 месяцев назад
Ooowo mtanyiwa tamapezekan limoopo
@thesocietynews3181
@thesocietynews3181 8 месяцев назад
Long live the DC, Bon Kalindo
@lovenessmuthiya3513
@lovenessmuthiya3513 8 месяцев назад
May God protect Bon kalindo
@Goliath461
@Goliath461 8 месяцев назад
Kalindo must be protected ❤
@lyiemax
@lyiemax 8 месяцев назад
May God protect and take care of the Dddddd Ccccccc
@user-bv3hk1zn7k
@user-bv3hk1zn7k 8 месяцев назад
Tilipambuyo panu mr kalindo mulungu achitepo kanthu
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 8 месяцев назад
Mulungu akuwona zonse ndipo chilango chili pansi pmpano sure
@KondwaniMwasinga-rs6kv
@KondwaniMwasinga-rs6kv 2 месяца назад
Atolankhani alimpopo mumakwana 🎷🎷🎷
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 8 месяцев назад
Kudalira kumanga mmalo mowapatsa anthu akumudzi chakudya muli busy kumanga
@ChikumbutsoJohn-rs4tt
@ChikumbutsoJohn-rs4tt 8 месяцев назад
My lord protect Bon kalindo's situation
@GustavoBoloi-kz8js
@GustavoBoloi-kz8js 8 месяцев назад
Asaope kalindo
@user-dk6yc8pl2m
@user-dk6yc8pl2m 8 месяцев назад
Mulungu apitilize kuteteza Mr kalindo
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 8 месяцев назад
Eeeee koma DC mmmmm simukugonetsa anthu tulo
@user-si7po9sd5i
@user-si7po9sd5i 8 месяцев назад
You're protected Mr DC
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 8 месяцев назад
Simunthu wamba DC
@alicehananiya
@alicehananiya 8 месяцев назад
Mr kalindo osaopa mulungu Ali Nanu pomwe mulipo satana Alibe mphamvu angoyamba koma sangamalize
@mustafahaji2599
@mustafahaji2599 8 месяцев назад
Tiripambuyo panu Mr boni karindo murungu akusogorerani osadandaura🙏🙏
@user-jp5mo2qf3h
@user-jp5mo2qf3h 8 месяцев назад
Zachamba kalindo alibe chifukwa
@CedricMdala
@CedricMdala 8 месяцев назад
May god protect you
@kelvindickson
@kelvindickson 8 месяцев назад
The DC simunthu wamva sizitheka mophweka
@user-ti2ct8ts8d
@user-ti2ct8ts8d 8 месяцев назад
Zabwino zonse a president athu a kalindo❤
@alexjeremanuel2541
@alexjeremanuel2541 8 месяцев назад
Which means there's no human right in Malawi specially with the current government of MCP and tonse alliance
@gladysbonongwe1038
@gladysbonongwe1038 8 месяцев назад
Kumalawi kulibe ufulu
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 8 месяцев назад
Bon kalindo is good guy the DC is good guy
@joicemartin-ji5zu
@joicemartin-ji5zu 8 месяцев назад
Ladzaro ladzaro ladzaro conde musiyeni prezdent wathu bon kalindo amalawi tikamuona kalindo Kapena kungova mau ake amatilimbikitsa amatitothoza
@GeorgePhiri-rk6ei
@GeorgePhiri-rk6ei 8 месяцев назад
Bon kalindo wakulakwilani chiyani MCP ndi tonse alliance palibe chanzeru chomwe mukuchita ndipo mzika za dziko la Malawi zilibe ufulu olopang'ono ndimmene mukupangila .
@BeatrizUlanda-ht2th
@BeatrizUlanda-ht2th 8 месяцев назад
Murungu wakuru akudariseni Mr bon karindo
@sarahkamphanga
@sarahkamphanga 8 месяцев назад
Brother kusowa bwanj
@LowrentReman
@LowrentReman 2 месяца назад
Zawusiru bas
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 8 месяцев назад
nkhani yama albino ili mmanja mwa president. APM anaturutsa report la commission equal linapita kwa chakwera kuti liudze dziko .now its 2 years koma kuli ziiii amabitsa chani
@Michaelaliemapira
@Michaelaliemapira 2 месяца назад
Kod lopmpopo AFM ndidzinalokha la? Radio or iliku fumpi ndi limpopo river? It good Radio station kobas
@amabhohlela.3492
@amabhohlela.3492 8 месяцев назад
Man mulipo kodi!!ndimaona ngati mwaphedwatu bro!!,,,kapena zatha Ndalama.
@ririvilla1423
@ririvilla1423 8 месяцев назад
Boma ili layenjeza
@mbaliehaward947
@mbaliehaward947 8 месяцев назад
Chakwela palibe chimene ukuchita nthito yako ndi kuba ndi kumanga anthu okudzuzula pa zinthu zimene ukulephela iweso thawi yako izakwana
@user-pn7lx1oo1l
@user-pn7lx1oo1l 8 месяцев назад
Km Atanyiwa musamasowe kwambir
@chipi892
@chipi892 8 месяцев назад
Boma ili.lasowa chochita zedi
@user-qv3bc4rv7q
@user-qv3bc4rv7q 8 месяцев назад
Zabwino zose a president athu akando
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd 8 месяцев назад
Munlo koma azitenge bwino
@user-pc7tl2cb2m
@user-pc7tl2cb2m 8 месяцев назад
Y Lord will protect him
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 8 месяцев назад
Tikupenya
@Pangolinimw
@Pangolinimw 8 месяцев назад
born kalindo DC 🫶🫶❤️❤️
@khalifacalvinajass9998
@khalifacalvinajass9998 8 месяцев назад
The DC dangerous The most dengerous child
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e 8 месяцев назад
My Allah almighty protect him
@yusufbanda4980
@yusufbanda4980 8 месяцев назад
Aamin aamin aamin
@tonemuyaya6284
@tonemuyaya6284 8 месяцев назад
Zikhara bwn bwana the DC
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 8 месяцев назад
Kodi Ndichifukwa Chiyani Pa dzina loti Susan palibepo Z ?
@chrisboyce229
@chrisboyce229 8 месяцев назад
My Lord protect Bon Kalindo
@user-qm1qb2jp4s
@user-qm1qb2jp4s 8 месяцев назад
Guys bwanjinso a Malawi a chakwera mukuipitsabe mbiri yanutu
@marryphili5419
@marryphili5419 8 месяцев назад
God protect our people
@user-gk3bb8dx1m
@user-gk3bb8dx1m 8 месяцев назад
Bone kalindo we pray for you
@amoschataika1284
@amoschataika1284 8 месяцев назад
These Idiots of MCP asowa zochita and Munlo ndi Longwe are the influencers.
Далее
BON KALINDO LERO PA 27 AUGUST 2024 |
17:02
Просмотров 12 тыс.
Jomo wamukana Bon Kalindo
4:20
Просмотров 63 тыс.
Times Exclusive featuring Bon Kalindo - 6 January 2024
1:03:20
Vuto Si Anthu Andale Koma Ife A Malawi - Bon Kalindo
15:27