Тёмный

BON KALINDO 27 JULY 2024 KUSALAZA KWA PA SATURDAY 

Malawi Trends TV
Подписаться 48 тыс.
Просмотров 25 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

17 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 124   
@AmosJere-ir4zr
@AmosJere-ir4zr 2 месяца назад
Awa a MCP ndimakape kwabasi ndipo ndi mbuzi za anthu, ife tili pa mbuyo panu a DC
@giftkayome3568
@giftkayome3568 2 месяца назад
Mwayankhula zoona akulu, The DC.
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 2 месяца назад
Big up Mr president we love u ❤
@MikeArthur-jd2ij
@MikeArthur-jd2ij 2 месяца назад
Ng'alurization😄😄😄 The DC 🔥
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 2 месяца назад
My president just imagine fertilizer cost 89,000 kwacha is this a way of life or a way of death
@RadsonTimoteo
@RadsonTimoteo 2 месяца назад
Kufa basi za moyo palibepo apa
@AngolanChinga
@AngolanChinga 2 месяца назад
Mmmm ndiponso
@scoltenroma6240
@scoltenroma6240 2 месяца назад
Koma DC adaaaaa😂😂✊
@GiftSoko-w4h
@GiftSoko-w4h 2 месяца назад
Koma iwe Bon kalindo usazafe uzangosowa wava ndipo iwe unforeseeable kuima uprezidenti uzawona Malawi 🇲🇼 kukuvotela umaganiza osati zisiru iziiiii
@lyiemax
@lyiemax 2 месяца назад
That's our beloved president ❤❤❤
@sarahmphande6108
@sarahmphande6108 2 месяца назад
Our angel from above
@KunyengaMoyo
@KunyengaMoyo 2 месяца назад
Chilungamo ichi cha nyooo, angogawa ndalama mopanda dongotsolo moti apange zoti zinthu zitsike mmmmm mukamva ndafa wandipha😂😂😂😂
@razackibrahim5880
@razackibrahim5880 2 месяца назад
Bon Kalindo ❤❤❤❤❤❤❤ I love you so much
@HopeLuwangakaunda
@HopeLuwangakaunda 2 месяца назад
Our president BON KALINDO ❤❤❤
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 2 месяца назад
More Fire 🔥 🤧......Bon Kalindo....Auze amenewo amvetsese...Chakwera wationongera Mother Malawi... People are suffering tindikwera kwa zithu zofunika kwambiri.
@LaikaSaidi
@LaikaSaidi 2 месяца назад
Athilen mau anthu osaopa Mulungu amenewo
@Kabwilachikangawa
@Kabwilachikangawa 2 месяца назад
Just meet the DC outside my home. What an honor to meet him...🤝
@BruceChirambo-ly8jm
@BruceChirambo-ly8jm 2 месяца назад
BOOOOOON KALINDO🔥🔥🔥🔥🔥💯💯💯
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 2 месяца назад
Ayi dzikoli ndilaiweyo kalindo, osamakhala ndi nsanje
@CalvinThomson-ys5zf
@CalvinThomson-ys5zf 2 месяца назад
Uniform mpaka muisoka zikizaki 😂😂😂😂😂😂
@YassinAmbali
@YassinAmbali 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂
@arthurkayuza
@arthurkayuza 2 месяца назад
Ndiye mwati chani "ng'alulazation"😂
@OwamiSimeon
@OwamiSimeon 2 месяца назад
West of west president in the world 🌎
@ghamagift4591
@ghamagift4591 2 месяца назад
Lets go.....umati tsegula mutu
@GeraldChikalema
@GeraldChikalema 2 месяца назад
😂😂😂 Ng'alulazation yomweyo kuti wawawaaaaa
@JonaZimpita
@JonaZimpita 2 месяца назад
Mbu🥵li iwe tang,aluluko chizungu
@MoeshahIbrahim
@MoeshahIbrahim 2 месяца назад
Alot is not going well amalawi tiziombela mmanja sitima 😂 ifeyo kodi aliyense amateurs galimoto aaah njala ndalama izipezeka
@GRACIOUSKENAN
@GRACIOUSKENAN 2 месяца назад
Hello our president bbboooonnnn kalindoooooo
@loneymagwera915
@loneymagwera915 2 месяца назад
Ng'alulasation🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@Mervic-vm8eo
@Mervic-vm8eo 2 месяца назад
Tilimu zimu wa chikangawa pano 🙌🙌🙌🤣🤣🤣🤣🤣
@AlinafeLinje
@AlinafeLinje 2 месяца назад
Mr DC mumakwana
@RitaKainga
@RitaKainga 2 месяца назад
Ng'alulaaaa!!!!!!! THE DC CCCCCV!!!!
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 2 месяца назад
A Malawi tili pa mavuto oopsa kwambiri MULUNGU atithandize kwambiri
@SamuelKulimah
@SamuelKulimah 2 месяца назад
Shallomo Malawi shallomo 😂😂
@EmmaculateChadambuka
@EmmaculateChadambuka 2 месяца назад
❤❤❤❤❤❤I love you Mr. DC
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 2 месяца назад
Koma DC ndimakhala ndi chidwi ndi apolicewa iiiiiii unifom eti mpaka kuisokasoka eti
@GeraldChisokeza-er5cf
@GeraldChisokeza-er5cf 2 месяца назад
Nthawi yaathera bas
@MoosaSame
@MoosaSame 2 месяца назад
The DC ❤❤❤❤❤❤❤❤
@JohnAsendi
@JohnAsendi 2 месяца назад
Ukumba manda Achakwera adzakaitena Ukumba zisime kuti chizakhale chakuya tidzachite kunponya ngati galu😂😂😂😂😂
@EmmanuelNgambi-y6h
@EmmanuelNgambi-y6h 2 месяца назад
Tiyeni tipange ngati zaku kenya
@inamrigala
@inamrigala 2 месяца назад
Malawi idyan ndalama Za makape omuvotela tamuziwa kale ife
@MphatsoGamah-v3v
@MphatsoGamah-v3v 2 месяца назад
Big up Mr president!!
@watsonmhango8794
@watsonmhango8794 2 месяца назад
DC ukulasa mfundo zoveka bwino, ukulasa mfundo
@DavidJackson-ox4xm
@DavidJackson-ox4xm 2 месяца назад
The DC'S mwana woooopsa kwambiri akhalise Malawi chilungamo chiyende ngat madzi
@ThandiMbewe
@ThandiMbewe 2 месяца назад
Zikizaki indeed koma ndalama nde zikusakazidwa eish
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 2 месяца назад
Mzimu wa chilima
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 2 месяца назад
Boma iri likulangadi eeesh mbola ndithu mmm
@temwarachaelkhonje3733
@temwarachaelkhonje3733 2 месяца назад
Mwanza mwanza adaaa😂
@TapiwaKhwisula
@TapiwaKhwisula 2 месяца назад
The dc tiyeni paseu basi bomali latitola kwambili sizoona akuchitazi dzikoli silabuyao mmmm
@KingsleySitima
@KingsleySitima 2 месяца назад
Kkkkk welcome the DC Inu nd one tili pa mbuyo panu bwana
@Thewarrior7093
@Thewarrior7093 2 месяца назад
Akuti samalani oipa watsikira komweko
@ArchangelMdzinga
@ArchangelMdzinga 2 месяца назад
Osabayo ndi ndani? Olo iweyo sungathandize amalawi
@petrooverton6643
@petrooverton6643 2 месяца назад
Mzimu WA CHILIMA
@ViserKabango-jt1hs
@ViserKabango-jt1hs 2 месяца назад
Musamayiwale kuyikapo mau akuti achimwene aku nthochiiiiiii,the DC !!!! mukatsanzika
@DalitsoMichongwe
@DalitsoMichongwe 2 месяца назад
Kulankhula zoona zokhazokha....chilungamo chimawawa
@SaudhaKatete
@SaudhaKatete 2 месяца назад
Kumun'galula kumene Mr chikangawa more fire the dc
@PatrickNkumba
@PatrickNkumba 2 месяца назад
Bon kalindo amanena chilugamo
@Robertmkango
@Robertmkango 2 месяца назад
Mademowo akhàre omuchosa mpopano bas
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 2 месяца назад
Born kalindo ndi wa one auze chilungamo avetse boma lonyasa iri
@Emmanuelisraelsimbi
@Emmanuelisraelsimbi 2 месяца назад
Koma iwe DC ma demo aliko liti Kodi 10 days ija sinathe?
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 2 месяца назад
Mnyamata uja waiphula kwabas
@PatrickViyache
@PatrickViyache 2 месяца назад
DC inuyo mumatiimilila ife amalawi?
@BenNgreziman
@BenNgreziman 2 месяца назад
And Malawi ambiri anali ndizoyankhula kma timaopa kukadyela mgaiwa pawindo big inuyo mumatiimilira ulemu wanu
@FunnyKatchenga
@FunnyKatchenga 2 месяца назад
Our president ❤❤❤
@G00dwillPhiri
@G00dwillPhiri 2 месяца назад
Mmakwana mbwiye
@billymhoni9527
@billymhoni9527 2 месяца назад
Utm moto
@FrancisMazamba
@FrancisMazamba 2 месяца назад
Ulemu wanu bwana
@Dentera215Music
@Dentera215Music 2 месяца назад
😂😂😂😂chimwana choopsa kwambiri
@AustinBornface
@AustinBornface 2 месяца назад
The DC!
@ajudyaustine984
@ajudyaustine984 2 месяца назад
The DC 🔥🔥🔥
@GanieAlidih-gu7no
@GanieAlidih-gu7no 2 месяца назад
Zimu wagadama
@JosephLemani-qq1is
@JosephLemani-qq1is 2 месяца назад
Mbambande bon kalindo ndipo ife tili nanu nanupaka zinthu zizasunthe 💥💥💥💥💪
@KennedyKanyama-ce8lb
@KennedyKanyama-ce8lb 2 месяца назад
Mbambande bon kalindo auze
@prettytambala5687
@prettytambala5687 2 месяца назад
Koma the DC 😅😅😅😅😅😅
@ALEXKAUYE-it9os
@ALEXKAUYE-it9os 2 месяца назад
Kodi, DC wamanidwa dollar to, ndiye mwayamba kuululakkkkkmm
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 месяца назад
Ndiwe opusa iwe eti ukuona ngati The DC ndioshota ngati iwe pita uzikakanda uko mbuzi
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 2 месяца назад
Chakwera zomwe akuchita Atha kukuchimwisa ndithu kod ulamuliro wanji umeneu
@GospelSoldiers-sr7np
@GospelSoldiers-sr7np 2 месяца назад
Ndipo zomvetsa chisoni kwambili komatu kuli Mulungu ichi ndiye asamaiwale ay
@DalitsoMbalanje-n2p
@DalitsoMbalanje-n2p 2 месяца назад
Mmakwana apule
@JoelMwenegamba
@JoelMwenegamba 2 месяца назад
DC chilungamo ngati madzi amu lake Malawi.
@SprianoJeke
@SprianoJeke 2 месяца назад
Azanyamula makala Kwa kalulu ku Dedza
@Robertmkango
@Robertmkango 2 месяца назад
Ndipo live umakwana DC
@geraldgomati9624
@geraldgomati9624 2 месяца назад
Mzimu wa Chilima
@YoramChimtakabanda
@YoramChimtakabanda 2 месяца назад
Inu mulibe zelu Ife tupindula nazo
@ZioneMkwanda-y6i
@ZioneMkwanda-y6i 2 месяца назад
Winawe olo manyazi ulibe, ukulimbana ndi Bon Kalindo apa , CHOTI udziwe Bon Kalindo ndi president waife osauka ndipo izi akuuza ife, iweyo abale ako nda a Chikangawa Party takudziwa shame on you! Our president please more 🔥🔥🔥 Tell them the truth, winawe uziluma pa mchombo, wekha- wekha- kunyoza Bon Kalindo yaaa , Useless boy
@dytonmoyo4629
@dytonmoyo4629 2 месяца назад
🔥🔥🔥🔥
@DixonChimanya
@DixonChimanya 2 месяца назад
Kubwera kumeneko tawauza bwino
@SimonBanda-b1f
@SimonBanda-b1f 2 месяца назад
Ayiwala kuti ndalama zo agule fertilizer NDI mbewu za subsidy kuti mwina anthu alandile mwachangu komanso anthu ambiri Koma azapeleka mbewuzo February chaka chamawa
@DixonChimanya
@DixonChimanya 2 месяца назад
Dyson @tasona mbolo yako sukukuoa kuti ku Malawi pano kwafika nyasi Pantumbo pako Ngati ukamadya za kape wakoyo chikangawa udzingodya
@Geraldmkwewu
@Geraldmkwewu 2 месяца назад
Mumakwana madara chakwera chikangawa watikwana kd ndalamazo muzipatara mulibe makhwala katundu wadura nde atagure zake ndani bznesiyo chakwera akanafa km amanganya nanuso mungoyenga ngt wamisara muzayaruka nxt year
@prettytambala5687
@prettytambala5687 2 месяца назад
😂😂😂😂😂😂
@JamesKhengemussa-t1d
@JamesKhengemussa-t1d 2 месяца назад
Big man,asyene kunga'alula
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 месяца назад
Ndipo mutipase number yanu bwana tizikuuzani zambiri zomwe nguluwezi zikuchita
@MaryPanje
@MaryPanje 2 месяца назад
❤keep it up
@GeraldMustafa
@GeraldMustafa 2 месяца назад
The DC ❤❤❤
@EMILYKAWALANGA
@EMILYKAWALANGA 2 месяца назад
Ndipo kukasiyako akuchita kulandila ma 1 milion koma chikhalikenicho kwinaku analemba kut anthu azilandila 150 paka pano ndalama anthu sanalandilebe koma kwao anthu akuva kukoma munthu woipa uyu akungoona kwao konkha
@EstherChinkhata-hn8mf
@EstherChinkhata-hn8mf 2 месяца назад
Munthu oipa uyu ing'alure basi the DC ulemu wako
@valenceemmanuel74
@valenceemmanuel74 2 месяца назад
Ng'alulization 😂
@gracemkandawire8769
@gracemkandawire8769 2 месяца назад
Zoona ndi Mizimu ,,a Joyce Banda Nyumba anamanga
@Aisha-db6ds
@Aisha-db6ds 2 месяца назад
😂😂 mzimu wa mgadama
@capitalaction4107
@capitalaction4107 2 месяца назад
Ng’aluration😂
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 2 месяца назад
Ambuye Kodi chakwela afa liti tipume?
@EMILYKAWALANGA
@EMILYKAWALANGA 2 месяца назад
The DC fire mabomba
@SamuelAntone-mz6nq
@SamuelAntone-mz6nq 2 месяца назад
Yakhulani bwana timakunyadirani bigy
@priscillamangata4023
@priscillamangata4023 2 месяца назад
Ine ophika zakudya zakumademo
@RemitterFlik1130
@RemitterFlik1130 2 месяца назад
Kkkkk iwe zakudya ine madzi othira mutu
@williamalvis6028
@williamalvis6028 2 месяца назад
Munthu wankulu mumatitsegula mitu
Далее
Wildest 10 SECONDS OF HIS LIFE 🤯 @TomIsted
00:14
Просмотров 4,8 млн
Maloto A Bon Kalindo
14:07
Просмотров 9 тыс.
BON KALINDO 18 OCTOBER 2024 KUNG’ALURA PA FRIDAY
16:20