Тёмный

BON KALINDO LERO PA 31 OCTOBER WATI AKUYENDA OKUFAIFA NDIPO SAKUOPA OLO AMUPHE BORA CHILUNGAMO 

Makosana
Подписаться 118 тыс.
Просмотров 14 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

31 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 35   
@MafavukeJere
@MafavukeJere 17 часов назад
The DC💥🔥🔥✅
@patricknthakomwa5613
@patricknthakomwa5613 20 часов назад
Pope came 1989 during Kamuzu Banda regime and in 1990 waves of multiparty started to spread across the country.
@IbrahimDailes-j6y
@IbrahimDailes-j6y 6 часов назад
Zoona timakunyadilani Mr Bon kalindo the dcccc tiling nanu nanu
@SiseoRakesh
@SiseoRakesh 19 часов назад
Mwana oopsya kwambiri frm njeza village
@JaneBandah-v6u
@JaneBandah-v6u 17 часов назад
The DC
@StenDuma-o7h
@StenDuma-o7h 17 часов назад
Apolice Manyiiii awooooo
@EliphaKamanga-jv5sh
@EliphaKamanga-jv5sh 16 часов назад
Ndipo tikukanikad kuti tibwelele kwanthu apolice kuno mumene akutivutisila eeee koma akanasinthe😊
@PraiseMt-l6f
@PraiseMt-l6f 5 часов назад
The DC..💥💥💥💥
@ANDYSabola
@ANDYSabola 15 часов назад
Mumakwana Boss
@MthusaniKingstonMpofu
@MthusaniKingstonMpofu 19 часов назад
The Dcc ❤❤
@PhyllisMambo
@PhyllisMambo 13 часов назад
Zoona DC masiku awiri amenewa ndi akulu kwambiri mu mpingo kuzera mwa anthu oyera amenewa nafeso timayelesedwa koteloko mapemphero anthu amayankhidwa mwachangu pamaso pa Mulungu and anthu amene anatisiya timawakimbikoraso ndipo mizimu yawo imakhala nafe pafupi kuteteza kuteteza nthawi zonse Kwa adani athu
@bridgetmajor3646
@bridgetmajor3646 12 часов назад
The dc 🔥
@ChifundoGawanyemba-tj9zl
@ChifundoGawanyemba-tj9zl 21 час назад
MR CHILUNGAMO❤❤❤❤🎉
@FalesiFrank
@FalesiFrank 16 часов назад
Akalindo munthu waumunthu amaika anthu osauka patsogolo ndichifukwa chiyani atsogoleli a Ku Africa amakhala odzikonda,adyela ankhaza ndi ophwanya malonjezo. Painfa vise president imene ija Malawi 🇲🇼 tinataya masomphenya,chitukuko komaso kuthetsa katangale manyazi kwaonse okhudzidwa paimfayi mulungu awakanthe mowirikiza asasiyeko olo mmodzi
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 15 часов назад
Nkhni yapa Jonz ndye usachite kufotokoza zovuta kwambri Mulungu yekha atithandize
@Olivabanda-l1o
@Olivabanda-l1o 13 часов назад
The DC umakwana
@CharityHayaKaunda-q5d
@CharityHayaKaunda-q5d 17 часов назад
😂😂 Koma ichi eish
@DavidKanyemba-n2s
@DavidKanyemba-n2s 15 часов назад
Satana anatinyengelera😂
@DavidKanyemba-n2s
@DavidKanyemba-n2s 15 часов назад
The DC Bon Kalindo
@SboneloMhlanga-m3s
@SboneloMhlanga-m3s 7 часов назад
Uremu wanu boss ndripambuyo panu
@JamesSingini-t4j
@JamesSingini-t4j 19 часов назад
The good thing,,,MCP sizawayankhaso awa kkkkkk Boma ndilomweli
@PercyRoos
@PercyRoos 18 часов назад
Ndipo ndizabwera kumalawiko chakwera atatula pansi udindo
@NEBRA-lm7ji
@NEBRA-lm7ji 18 часов назад
Mashallah 😅
@TenganiObety
@TenganiObety 20 часов назад
Bola usadzitaye panjila koma sunalume chingwa?
@patricknthakomwa5613
@patricknthakomwa5613 20 часов назад
Papa came 1989 not 96
@GodfreyNdhlovu-rm5uj
@GodfreyNdhlovu-rm5uj 12 часов назад
Kuyenda ofaifa kkkkkkkkk
@chikumbutsozipirana
@chikumbutsozipirana 18 часов назад
Nthakati
@MaduyaPatrick-v6h
@MaduyaPatrick-v6h 20 часов назад
Zoooona chilungamo auuuzeni😊
@FalesiFrank
@FalesiFrank 16 часов назад
Moto Kuti buuu!! Ndine JB mchewa weniweni mmodzi mwaachewa omwe sakukondwa ndi bomali. Ndimatsatila kwambiri ndale komano boma laleroli landionjeza ndisanachoke munchaka cha 2019 ndinavotela DPP chonde amalawi sinthani boma anthu tibwerere kumudzi
@FundoNdeketeya
@FundoNdeketeya 20 часов назад
Kulibe zochita kumeneko kumalawi ndibwino tizikhala kunja kuno
@SteveJulio
@SteveJulio 21 час назад
Umakwana kma
@GodfreyKamphiripiri
@GodfreyKamphiripiri 18 часов назад
❤❤Fireeeeeeeeee Fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee fireeeeeeeeee DC
@YohaneChipande
@YohaneChipande 8 часов назад
Kkkkkk mumatiimila boss
Далее
skibidi army returns (skibidi toilet 77)
00:49
Просмотров 2,6 млн
Expelled EFF member Mphahlele: we'll not be silenced
16:36