Тёмный

BON KALINDO - MA DEMOSTRATIONS ALIPO NDITHU 

MPUNGWE-PUNGWE MW
Подписаться 65 тыс.
Просмотров 8 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

20 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 36   
@GiftNgwira-e8l
@GiftNgwira-e8l 11 часов назад
Chakwera ndigalu kwabasi akutipatsa ma passport afake.Bon kalindo more fireee ndikudikira mademo
@MarryNyilongo-s5x
@MarryNyilongo-s5x 2 часа назад
Koma iweyoo dc ndikanakhala kuti ndimatha mayere ndikanangoaloza onse a mcp ndi kupangaso enawo angonena kut president wathu ndi bon kalindo umatiyimilira wokukumbira dzenje agweremo wokha in Jesus name
@dalitson3558
@dalitson3558 16 часов назад
Agalu Andalewa ndi amozi, zoti kumalawi kuli a opposition siziziwika yeti amalawife ndiye tikuvutika
@VictoriaBakuli
@VictoriaBakuli 16 часов назад
Zoonadi Blantyre kunthembwe sitinalandire ma ID
@chesterkumwenda
@chesterkumwenda 17 часов назад
Bola musasintheso
@Paul-q2p
@Paul-q2p 16 часов назад
Mumalankhula kuchoka January mupaka lelo za mademo koma tsitikuwaona mademo Pena tiganiza kuti mumadyapo mukalankhula za mademo mukalephela apapa muzalankhuleso za mademo chifukwa yangokhala nyimbo
@happynyirenda8790
@happynyirenda8790 13 часов назад
ma demo akhalekodi koma this time ku mzuzu asakhaleko chifukwa amatenga serious kwambiri ku mzuzu ndikuphana,ndiye akhale ku Lilongwe blantyre ndi ntcheu
@BoscoKalua
@BoscoKalua 16 часов назад
He was a national figure
@lyiemax
@lyiemax 17 часов назад
Powerful ❤❤❤
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 3 часа назад
A opposition ali zii osathandiza anthu a malawi.chifukwa onse ndi A ALLIANCE IJA YA ZIPANI 9 ZIJA @ ONSEWA NDI AMODZI.KUFUNA KUPHA A MALAŴI ONSE
@ephraimphalawala4720
@ephraimphalawala4720 2 часа назад
Nthawi yakwana panseu tsopano. Atizolowela kwambiri a Mcp
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 7 часов назад
Eeeeeish😭
@UniceSauli
@UniceSauli 16 часов назад
Kape uyu watitopesa akusongezera nkhondo chifukwa choti anamumana mpando zikutinyasa ndikhan make zongokolanakolana
@stunahethibwi1112
@stunahethibwi1112 14 часов назад
Mbole yako iwe
@MWASISAINI
@MWASISAINI 5 часов назад
Zomwe akunena zoti amalawi abwezedwa ndi mapassport a fake ndizoona kapena akunama?
@awettesfamichool5009
@awettesfamichool5009 17 часов назад
Timakunyadilani ❤❤❤
@CathyMwale-o6k
@CathyMwale-o6k 15 часов назад
Tiri konko stikubwelera m'buyo bora asakutsekeni pakamwa agaluwa!!!
@RusselleStanley
@RusselleStanley 15 часов назад
Chokaaaa iweeeee
@MulowokaBlessings
@MulowokaBlessings 15 часов назад
Misala uyu alibe nzeru kumango bwebweta siku lililonse mmmmmm olo kuyankhula ketelo mwana wako angamve ?azingoti hiii asiyeni aziyankhula tinawazolowela mmm ayi koma anakulozani yo kuti muzilongolola anayitha mmm ayi
@MWASISAINI
@MWASISAINI 5 часов назад
Zomwe akunena zoti amalawi abwezedwa ndi mapassport a fake ndizoona kapena akunama?
@OwenNyambose
@OwenNyambose 15 часов назад
Kalindo the DC
@ElizabethKamiza-s9l
@ElizabethKamiza-s9l 16 часов назад
Mukasitha a Dc tidana nanu
@YasmeenYalabi-b2c
@YasmeenYalabi-b2c 12 часов назад
The Dcccc
@MrMagombo
@MrMagombo 15 часов назад
A DPP ndi zipani zotsutsa alembeleni chipani chitakane ndiye kuti sitidzachivotela.
@IslamMapepa
@IslamMapepa 16 часов назад
Akalindo mukunena zoona Ena Zana abwelela paboda Kom ali ndipaspot ikukana sikan
@RusselleStanley
@RusselleStanley 15 часов назад
😂😂😂😂😂 kkkkk za ziiiii
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 3 часа назад
Kkkk kodi mwana wa chinyau chakudambwe LAZARUS CHAKWERA ANGAPANGÈ MAPASS PORT A EFFECTIVE? GULE WAMKULU MWANAYO NICK CHAKWERA .MBULI YOTHA NTCHITO
@user-ii9ch7oz8n
@user-ii9ch7oz8n 17 часов назад
Koma ndiye mulindintchito yosayendera zaziii
@SydneyMwale-u9w
@SydneyMwale-u9w 16 часов назад
Mwatalikitsa bwanji
@UniceSauli
@UniceSauli 16 часов назад
Sichiziwaso kuchulaso figer yandalama tachimven
@ThomsonShunga
@ThomsonShunga 16 часов назад
The DC
@Samuelsailesi-d6n
@Samuelsailesi-d6n 16 часов назад
bolani musasinde tilimbuyomwanu
@UniceSauli
@UniceSauli 16 часов назад
Patumbo pakoiwe wakhuta khanu
@stanleymollen7273
@stanleymollen7273 15 часов назад
Mkadeti...
@EmmanuelNgambi-y6h
@EmmanuelNgambi-y6h 15 часов назад
Tiyeni pamsewu basi tathopa nawo anthuwa
Далее
Handsoms😍💕
00:15
Просмотров 3,1 млн
Paint Projects
00:17
Просмотров 1,9 млн
Watching This On Loop ♾️
00:32
Просмотров 10 млн
Handsoms😍💕
00:15
Просмотров 3,1 млн