Тёмный

BON KALINDO WABWERANSO NDIIZI TAMVERANI 05/09/2024 

Mpungwe-Pungwe mw
Подписаться 54 тыс.
Просмотров 34 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

15 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 56   
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 10 дней назад
The DC nenani chilungamo bas chiyende ngati madzi koma zonse tasiya manja mwa Mulungu bas ❤❤❤❤
@RobertPhiri-gt2cr
@RobertPhiri-gt2cr 10 дней назад
Bon kalindo umatiimilira Mbava zichoke 2025 muome mseu wa mugabe hiway mmene uliri zomvetsa chisoni ngati kulibe boma 111st ❤
@MariamJaffali
@MariamJaffali 10 дней назад
❤❤❤❤ boniiiiiiiiiiii kalindooooooooo the DC
@ThomasMwandila-tn7cf
@ThomasMwandila-tn7cf 10 дней назад
Wamisara akufuna chipani choti aroweuyu,siuyu wayamba kuyendandi U.D.F
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 10 дней назад
Mmmm!!!!!
@Outi-p7d
@Outi-p7d 8 дней назад
Palibe zokuti zonse tisiyile mulungu . Koma action can help so much . Chondechonde tatiyeni tionese mbanvu kuwanthu.
@KelvinJpchimphepo-sh6nc
@KelvinJpchimphepo-sh6nc 10 дней назад
Ada amenewa asapangeso ndale chifukwa one day akazapanga ndale azagendedwa
@KondaniPhiri
@KondaniPhiri 10 дней назад
Talankhulani bwana DC malawi ikugonabe apa. Timuphe naye anthu onse ndende akagwire
@ChimsyUlemu
@ChimsyUlemu 10 дней назад
Ndipo ndiye ndizoonadi Malawi anthu anapusa kwambiriiii aphedwenso nawo iyaaaa these duckies
@IsaacKamanga-cv8ec
@IsaacKamanga-cv8ec 10 дней назад
Ati kusowa nkhondo 😂😂
@RobertPhiri-gt2cr
@RobertPhiri-gt2cr 10 дней назад
Koma ndyetu tikuberedwa kumalawi
@user-ux3ed3ni1p
@user-ux3ed3ni1p 10 дней назад
Acommanda and chief akanika kuti teteza.
@KelvinJpchimphepo-sh6nc
@KelvinJpchimphepo-sh6nc 10 дней назад
Mgwilizano tilibe, vuto osogolera palibe kut anthuwa amangidwe komaso akubanja ndamene afookesa amalawi sakulakhura kut anthu akhare ndi mphavu anthuwa akana choka, akanayimisidwa kaye ntchito awonese chilungamo
@HaliJana
@HaliJana 10 дней назад
Kusachosako ndipomwe muziwe kuti ndi plan oseo anaphela limodzi sangachosani tichosa 2025 ndikuonanao zochita
@MustafarBridon
@MustafarBridon 10 дней назад
Dc boniiiiiiiiiiii kalindoooooooo
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j 10 дней назад
Munanena mawu a DC kuti amalawi siwowafera ndi chifukwa chake ziko lamalawi likupita aliyense akungoyang, ana tizionerani limodzi popeza tonse tili momwemu
@KelvinJpchimphepo-sh6nc
@KelvinJpchimphepo-sh6nc 10 дней назад
Basi khani ikhare tiwadikire 2025 Mesa kupusa ko tikunena ko anthuwa chaka chino akanayimisidwa akanayitanidwa ku bwalo lamilandu
@UthumanMwangala
@UthumanMwangala 10 дней назад
Amalawi ife tulo chomwe tkuzwa ndikudikila kut bakili tv kapena bon kalindo ayankhulalit pa social media tipange coment bas
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 10 дней назад
Pepani aprezdent anthu osauka pp asakhale mawo pa mgwirizano chifukwa ndi joyce Banda mmmmmm timamuopa
@Mustapher-fb4qp
@Mustapher-fb4qp 10 дней назад
Boni karindo warowa udf
@paulvan9306
@paulvan9306 9 дней назад
Zoona
@RobertPhiri-gt2cr
@RobertPhiri-gt2cr 10 дней назад
The Dccccc❤❤❤
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j 10 дней назад
Pangani gwilizano nonse mwatchulidwa apawa ma udindo oyamba akulu akulu muzapereke mofanana pozasata ndi m, mene chipanicho chizapezere ma percent ake
@SamuelLiwonde
@SamuelLiwonde 10 дней назад
surely ma guys aku defence ndye anayenera kuimitsidwa
@ChimsyUlemu
@ChimsyUlemu 10 дней назад
Kkkkkkkkk akakomoka kumangowathila acid basi Malo mwa madzi
@user-ps5tv4hq3c
@user-ps5tv4hq3c 10 дней назад
Yes ❤❤❤❤❤❤
@RobertPhiri-gt2cr
@RobertPhiri-gt2cr 10 дней назад
Malavi onfire
@Cubotenterprise
@Cubotenterprise 10 дней назад
Amangidweee onseeewa
@Biath-m4b
@Biath-m4b 10 дней назад
Koma iwe wayankhula bwino bwanj mpake tikuti ndizopangana bwanj sanamangepo olo mmodzi apa zikumveka koma so akuthawa chian mdziko muno kukakhala ku china akusowa mtendere uyo
@ChisomoBanda-g5s
@ChisomoBanda-g5s 10 дней назад
🎉🎉🎉🎉🎉🎉🎉😢😢😢😢
@user-wx1jt5fd2j
@user-wx1jt5fd2j 10 дней назад
President chipani China vice chipani China secretary chipani China ndimaudindo ena zipani Zina mwina malawi angazaoneke kusintha
@williamlyton8016
@williamlyton8016 10 дней назад
the DC mwana owopsa kwambiri
@violetpotani
@violetpotani 10 дней назад
Uyuyu muti president yu asatiphwanyitse mutu tingoonda nazo izi
@mlimipatsogolo7323
@mlimipatsogolo7323 10 дней назад
Zikuti pweteketsa mutu tasakani mfundo zina zowawuza amalawi
@KingstonMahamba
@KingstonMahamba 10 дней назад
Likiliki nanuso nda opposition kani
@UthumanMwangala
@UthumanMwangala 10 дней назад
At wina azangokomoka😂😂😂😂😂😅
@user-cp4qt9hs8w
@user-cp4qt9hs8w 9 дней назад
Anthu nde mwayankhula km sizikusintha pangofunika kumukolaso mdege yakeyo chakwela
@DalitsoTanganyika
@DalitsoTanganyika 7 дней назад
Nkhondo yathu tayisiya mmanja mwa Mulungu
@FrancisKamwendo-p2i
@FrancisKamwendo-p2i 10 дней назад
Go deeper.ang'alulidwe basi
@NeemaMatewere
@NeemaMatewere 10 дней назад
@jamesjolichi2026
@jamesjolichi2026 10 дней назад
Bornnn kalindoooooooo
@Cubotenterprise
@Cubotenterprise 10 дней назад
Pagan comment smnuye
@Cubotenterprise
@Cubotenterprise 10 дней назад
Agalu a MCP
@AuphieBannet
@AuphieBannet 10 дней назад
Diiiiiiiiiiiisiiiiiiiiiiiiiiiiii
@BarnettKathumba
@BarnettKathumba 8 дней назад
imfa ya chilima siizaiwalika
@AlickChima
@AlickChima 10 дней назад
Kodi a born kalindowa anaphunzirapo za ndegeso?? Anahwiraposo ku army¿? Aaaaa zili zonse komenti. Asiyeni ma xpert azikamba zinazi za sewero la ADRAzi sizikuthandiza atah
@EmmanuelZiba-qz6ug
@EmmanuelZiba-qz6ug 10 дней назад
😢😢😢😢😢
@SalahMhone
@SalahMhone 8 дней назад
Vuto lake chilungamo chimawawa
@LidyaGoodson-fb4tt
@LidyaGoodson-fb4tt 10 дней назад
Kkkkkkkkkk
@HendrickBanda
@HendrickBanda 10 дней назад
🔥🔥🔥🔥
@VincentAndrew-p8l
@VincentAndrew-p8l 7 дней назад
Panyopako
@humphreyskasonde7096
@humphreyskasonde7096 8 дней назад
Iweyo ukazangopeza anzako ena atatu olimba ntima ngat iwe dziko lizasitha
@BICHALIDAYSON
@BICHALIDAYSON 9 дней назад
😂,
@AbgirlChinheya
@AbgirlChinheya 10 дней назад
🎉
@ClementWellos
@ClementWellos 10 дней назад
The DCccccccccccccccccccccc
@CHIFUNDOVINTULA
@CHIFUNDOVINTULA 7 дней назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
Далее
9월 15일 💙
1:23:23
Просмотров 1 млн
@HolyBaam ультанул в конце 🧨
00:34
Просмотров 156 тыс.
КОГДА МАМА НАШЛА ТЕБЕ НЕВЕСТУ
00:55
FREDO MASINTHA
12:07
Просмотров 18 тыс.
TIMES TV KUING'ALULA MBC TV - APWETEKANA AWA🙌🙌
30:44
9월 15일 💙
1:23:23
Просмотров 1 млн