Тёмный

Bon Kalindo watuluka kundende. Chakwera ndi Dictator. 

Human Rights Consultants TV
Подписаться 10 тыс.
Просмотров 42 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

27 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 82   
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu 3 месяца назад
Koma a vice president panepo mwaikocha, Bon Kalindo akumanena zinthu zeni zeni zimene anthu akudandaula. I like that Mr. VP.
@ChaibishuSwadck
@ChaibishuSwadck 3 месяца назад
More fire VP usi mwaya bwino ntchito koma ndi mawu amenewo mudana ndi MR PRESIDENT
@RabeccaMpunga
@RabeccaMpunga 3 месяца назад
I like your speech mr vp 🎉🎉🎉
@rashidadan2533
@rashidadan2533 3 месяца назад
We always supporting you all freedom fighters in malawi , You encouraging us as Malawians to know our freedom without scare anyone We will fight our freedom together with you . We will continue to blame the stupid things from any government
@GrecianahmedMaulana
@GrecianahmedMaulana 3 месяца назад
bwinotu michauel usi. usowatu
@0wenNkhambule
@0wenNkhambule 3 месяца назад
The Dc bon kalindo tiyeni mademo Chakwela you mast go
@KondwaniNguleti-x1q
@KondwaniNguleti-x1q 3 месяца назад
A Vice President athu Dr Michael Bizwick usi I like ur speech iwe umandiwaza komano bola Lazaro waumphawiyo asakutume pa Ndege mkudutsira ku Chikangawa Forest
@NoelLangwani
@NoelLangwani 3 месяца назад
More fire 🔥🔥🔥🔥 kalindo ..... Michael usi ulemu wanu vice president pamenepo mwaonesa chikondi zikomo kwambili ❤❤❤❤
@YoungMwacho
@YoungMwacho 3 месяца назад
Please Bon Kalindo do not associate with Timothy Mtambo, he is a devil 👿 just like Chakwela, please do not trust him, please, please. He is MCP do not be cheated.
@JamesManjawira-yz4ji
@JamesManjawira-yz4ji 3 месяца назад
He knows bro.... The DC he is another story baba😂
@JoshuaNyirongo
@JoshuaNyirongo 3 месяца назад
True
@AngolanChinga
@AngolanChinga 3 месяца назад
Mulungu akudalisen iweyo polankhula mau amenewo timoth asamukhulupilile kwambili
@AngolanChinga
@AngolanChinga 3 месяца назад
​@@JamesManjawira-yz4ji❤❤❤❤
@joyahmedjoma4615
@joyahmedjoma4615 3 месяца назад
Ai zikom a vice president tikuona ngat tili limodzi ndinthu ndikuvana nazo bon kalindo it's the best ❤❤❤
@petermajor-mb2rb
@petermajor-mb2rb 3 месяца назад
Thambo sindumukhulupila Ine carefully born
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 3 месяца назад
I like manganya's speech keep it up bro
@masterchitabwino898
@masterchitabwino898 3 месяца назад
Mr Ussi well put keep it up.
@SteveSangwa-tb7lk
@SteveSangwa-tb7lk 3 месяца назад
So Mr VP mutathauza kut a Malawi ndi amisala mwana wao kalindo ngwabwinobwino 😂
@Dee01papa
@Dee01papa 3 месяца назад
Nkulu wachimimbayo nde utinso😅
@samchibenene4458
@samchibenene4458 3 месяца назад
Good point Mr Vice President
@amontchuwa6876
@amontchuwa6876 3 месяца назад
VP zimene ukunenaz ndizoona km usatipusitse ai Ubwino wake the dc ndizako wenewene bola menyan nkhondo chakwera achoke Malawi abwerere pakale osat manyakawa
@princedetbozsmallboy1749
@princedetbozsmallboy1749 3 месяца назад
I like to see mutambo and bon kalindo together
@RadsonTimoteo
@RadsonTimoteo 3 месяца назад
Usi Michel nice one
@LuciasSimione
@LuciasSimione 3 месяца назад
Kkkkk naye manganyatu wabwelapo
@IdahKadewere
@IdahKadewere 3 месяца назад
Chakwera olo lero anakamwalira tatopa naye
@robenallie6985
@robenallie6985 3 месяца назад
Adala chemanganya twanyadire awechete chenene
@FrancisKalinde-wz7yd
@FrancisKalinde-wz7yd 3 месяца назад
Abon kalindo pathako panu mwava
@NicholasJames-cb7du
@NicholasJames-cb7du 3 месяца назад
The DC pangorin mwana wovuta kwambiri kwatuluka
@BrunoChakukuma
@BrunoChakukuma 3 месяца назад
A vice president mwayankhula bwino osati angangawo yawo ndiyomanga anthu 😂
@DoricaGoweka
@DoricaGoweka 3 месяца назад
Children Chakwera walephera Achike basi sakutha ayi . Kalindo more fire the DC . Unatiimiliraaaaaa 😅😅😅
@louisemsowoya8235
@louisemsowoya8235 3 месяца назад
Ambuye bwerani mwachangu kuzatipulumutsa 😭😭😭😭
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 3 месяца назад
Takondwera ndikutuluka kwa aprezdent anthu cakwera manyazi bwanji umafuna utawapha ngati momwe wapher chilima mulungu wakusekatu aprezdent athu atuluka amoyo litamandike dzina la yehova wamwamba mwamba kuno ku thyolo thekerani
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 3 месяца назад
A VP alankhula bwino komabe take care kulankhula kwawo kukonza kukhala pusi pusi a kalindo akuyenela kamasamala kwambiri
@PizoZopi-w2g
@PizoZopi-w2g 3 месяца назад
Apm my vote ✊
@zimmekapachika6784
@zimmekapachika6784 3 месяца назад
Chakwera udzipita sitikukufuna
@Lifestyle-q4k
@Lifestyle-q4k 3 месяца назад
Azipita kuti. Chakwera is not going nowhere
@GodfreyTSAMDOKA
@GodfreyTSAMDOKA 3 месяца назад
Avice president mwalakhula bwino kwambiri ngati mungankhale ndi masompheya ameneyo dziko liyenda bwino zikomo kwambiri
@spargomw
@spargomw 3 месяца назад
Lawyer wa Born Kalindo nae akufunika kumamuikiza m'mapepemphero kut Ambuye azimutetezera😂😂😂😂
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 3 месяца назад
Lawyer palibe vuto lomwe angampinge nalo chifukwa lawyer ndi ntchito chabe amayimira munthu aliyese akhoza kumuyimira
@YohanePatrick-lc2lq
@YohanePatrick-lc2lq 3 месяца назад
Avice akuwona dzolakwa dza chakwela mbudzi imeneyi ukamuwudze chakwela yo osadula mboloyo
@williammenard48
@williammenard48 3 месяца назад
Amoya akwa Golden ayankhula bwino monga VP
@MexcoJepter-p5f
@MexcoJepter-p5f 3 месяца назад
Akuwonetsa ngati aUsiwa akudziwa kuti amalawi tili ndiufulu woyankhula bola asakhale pusi pusi yemweyo
@MoosaSame
@MoosaSame 3 месяца назад
Ndipo chilungamo chokhachokha mr vp
@Uladimbwana-fr9ev
@Uladimbwana-fr9ev 3 месяца назад
Koma manganya apa ndiye wabaya ndithu
@ebenezerkamanga6016
@ebenezerkamanga6016 3 месяца назад
Manganya ikapitiliza izi iwe tigwilizana vice president azitero
@EdisonNakulenga
@EdisonNakulenga 3 месяца назад
Dasagalala Lelo diyako Sima potuluka Kumada adede kumwabakunenepe
@TalazanGamah
@TalazanGamah 3 месяца назад
We follow
@RashidRacc
@RashidRacc 3 месяца назад
Bhonikali ndo ulemuwanu 🦾🦾🦾🦿
@joicemumba3608
@joicemumba3608 3 месяца назад
Apo tageilizanananu
@robinfeb5684
@robinfeb5684 3 месяца назад
Mademo ayendeeee bas azaona ngat moyo ndi ophwekaaaa Timuziwe roya yo zina lake 💪💪💪💪💪
@HusseinMoffatt-mi1fl
@HusseinMoffatt-mi1fl 3 месяца назад
Bon kalindo ndidolo
@francebanda-du9yk
@francebanda-du9yk 3 месяца назад
Waturka. Zikomo
@ChinombaElvin
@ChinombaElvin 3 месяца назад
God is good all the wlc the DC 🙏🙏
@GiftHaward
@GiftHaward 3 месяца назад
Kumeneko ndiye kuyankhula Mr vp of malawi
@samueljuma4452
@samueljuma4452 3 месяца назад
Kodi iwe ntambo ukutani ndi mzako trapezie,mudayiwala ntchito yanu kodi?mademo alone m'bwalo
@FelixBoss-yn9pe
@FelixBoss-yn9pe 3 месяца назад
Iiiii sopanotu akuthamangitsani mukayamba kuyankhula zimenezo Che manganya
@SamsonSolomon-rc4ef
@SamsonSolomon-rc4ef 3 месяца назад
Wakambako Za dzeru Koma ndiwe kazitape manganya
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 3 месяца назад
More fire manganya
@WezzieChimuzi-ek7bk
@WezzieChimuzi-ek7bk 3 месяца назад
Achakwela alimmadzi ndipotu a manganya muikoke nkhaniyi osaphweketsa ndikuti mutha kutenga moandowo
@isaaczuze
@isaaczuze 3 месяца назад
Chakwera chimene akuchita sakuchiziwa ayi
@ChimwemweKondowe-nj4lx
@ChimwemweKondowe-nj4lx 3 месяца назад
I love what I'm seeing.
@LuciasSimione
@LuciasSimione 3 месяца назад
Inu anthuwa akudziwana yawa😅😅😅😅
@samuelmoyo2650
@samuelmoyo2650 3 месяца назад
Powerful
@Mervic-vm8eo
@Mervic-vm8eo 3 месяца назад
Wayitha vp
@MarthaMbewe-uk5nn
@MarthaMbewe-uk5nn 3 месяца назад
A VP alankhula bwino komabe take care kulankhula kwawo kukonza kukhala pusi pusi a kalindo akuyenela kamasamala kwambiri
@AlgentChilanga
@AlgentChilanga 3 месяца назад
Michael usi as our vice president pamenepo ulemu wanu kumeneko ndiye kuyankhula kp it up.aboni kalindo akungonena zinthu zomwe akuziona ndimaso zomwe boma likuchita samaonjezera koma poti iwowo akulankhula chilungamo that's why amcp ndizimene amadana nazo .koma l love your speech 🎉🎉
@IbrahimDailes
@IbrahimDailes 3 месяца назад
The dcc mulungu alemekezeke basi, km chilungamo chizaziwikabe ine ndili pambuyo panu forever
@AbrahamLLoyd-xb2xc
@AbrahamLLoyd-xb2xc 3 месяца назад
Zoona zimenezo
@marryphili5419
@marryphili5419 3 месяца назад
Ndawakonda avice president keep it up muli ndi zeru kuposa chakwera zomwe akunena born kalindo ndimene anthu amadandawura
@AleksaWilliams-qc6cn
@AleksaWilliams-qc6cn 3 месяца назад
Vp wayankhula bwino,keep it up bon kalindooooo
@LawranceNkuliwa
@LawranceNkuliwa 3 месяца назад
Kodi Amanda munali kuti muphula dzikotu inu chilungamo mukuchiziwa
@augustMag
@augustMag 3 месяца назад
Thanks GOD for helping you Mr DC ❤
@JackMvura-ik2td
@JackMvura-ik2td 3 месяца назад
Mitsonkho ya amalawi kunsewera nayo
@YasinMusa-ym8lp
@YasinMusa-ym8lp 3 месяца назад
Chakwera achoke simtikuvuna
@cjaylucky
@cjaylucky 3 месяца назад
VS WAYAKUL KUT THE DC SAKULAKWISA TIYEN PASEW BAS GATI KUKENYA NO PAIN NO GAIN
@LawranceNkuliwa
@LawranceNkuliwa 3 месяца назад
AVP ndinu katundu ulemu wanu zikomo
@ElizabethKazambwe
@ElizabethKazambwe 3 месяца назад
Mr vp mwayamba bwinotu
@MemoryKaunda-js9qv
@MemoryKaunda-js9qv 3 месяца назад
Manganya mwayakhulatu
@enockdaisi1306
@enockdaisi1306 3 месяца назад
Asamale
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 3 месяца назад
Awesome,ndidzomwe,tikudikila
Далее
We finally APPROVED @ZachChoi
00:31
Просмотров 6 млн
TIKUFERANJI 01 AUGUST 2015
25:43
Просмотров 355 тыс.