Тёмный

BRIAN BANDA KUFUNSA MAFUNSO PAMAPERO PA CONVENTION 

HOT 265
Подписаться 78 тыс.
Просмотров 69 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

11 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 132   
@IvyMkhura
@IvyMkhura 24 дня назад
Peter Mutharika is so genius, amene anamuchalira kuti abweranso ku convention kachiwiri wauponda.
@isaihmagani5697
@isaihmagani5697 24 дня назад
Adatopa ndi achikulire
@WhiteRichard-cw2fo
@WhiteRichard-cw2fo 24 дня назад
Muthu waluza musamukwezi tima ayi musiyeni wafotokoza bwino kwambiri
@JustinLipipa
@JustinLipipa 24 дня назад
Kkkkkkkkk ndizakuchipani izi.
@augustMag
@augustMag 24 дня назад
Peter Muthalika ndi oganiza mozama sikuti kukula ayi koma pamenepa adani Ake anawaona Ndipo chifukwa CHOTI anthu omudzungulira amamukonda anamuuza kuti bwana pano sipokhala nyamukani Ndipo mawa musakabwere dzikolo linakakhala kuti Lili monga momwe linali muja imalamulira DPP m mbuyomu osusa amayenda pena Pali ponse mwaufulu mopanda mantha Bwezi Peter Muthalika akupezeka paliponse koma panopo mmmmmmm
@ishmaelsiffah9900
@ishmaelsiffah9900 24 дня назад
Peter muthalika ndiochenjera guys,kuteroku ndiye kuti oyedzeka anzao aja anamuchalilira lero auponda iye sanabwere 😂😂😂
@PetroKachingwe-jf7dh
@PetroKachingwe-jf7dh 24 дня назад
Nkhalamba zokhazokha osasiyila achinyamata bwanji Mbava izi Uyu George Chaponda anaba chimanga chonse ndalama za Admark Mbava iyi asakudziwa ndani Admark inatha chifukwa cha Anthu awa
@Victoriabwaira
@Victoriabwaira 18 дней назад
Mpakana Osayila kkkk
@SolokingChimzy-yt7dj
@SolokingChimzy-yt7dj 24 дня назад
Ndiwayankhile ine a Chaponda kukula komwe akula sizikutanthauza kut akhale pansi ai..azakhala pansi ntchito yao ikazatha pa Dziko lino..this is why we have a Old testament qnd new testament..
@FatimaUmali-pc8sy
@FatimaUmali-pc8sy 24 дня назад
Zoona zake ndi ZImenezo kuti a nawona adani ake alipafupi ndi munthu wankulu Peter akaona patali genius Peter ❤❤❤ mphechempheche mea njovu Salita awiri
@user-oc9vl9xz8e
@user-oc9vl9xz8e 24 дня назад
Koma Briane ukufuna kukweza BP munthu wachikulileyo Kodi komanso zakhala bwino akula azigwila ndi anyamata ntchito
@user-rk3gq7gd8f
@user-rk3gq7gd8f 24 дня назад
Koma Brian ndi azako muthu waluza koma mafuso ameneo muthu atha kukomoka
@user-xz3nz7dy1f
@user-xz3nz7dy1f 24 дня назад
Akulu ndi dambo mozimira moto ... Anyamata azikathamanga pa ground akolo azilangizi
@mayachikadewa7551
@mayachikadewa7551 24 дня назад
Zitheka bwanji Kuti president asapezeke potseka convention?
@user-wi9pe2hz7e
@user-wi9pe2hz7e 24 дня назад
Adani achuluka amaionela patali mkuluyu wachita bwin😊
@charleskazembe5728
@charleskazembe5728 23 дня назад
Brayan thanks you always make program sacessfull 😅😅😅
@mzezengamsiska2637
@mzezengamsiska2637 24 дня назад
Chaponda waledzera ndipo mutharika akupuma after ukalamba azigonagona
@MauriceMukona
@MauriceMukona 24 дня назад
Nonse amene mukunena zokalambazo mbolo zanu ndi nyini zanu mxiiiii.manamvapo kuti ukalamba ndimatenda?
@stalickkafera3454
@stalickkafera3454 24 дня назад
Mutalika wantha mukumukakamza kugwirabe ntchito😂😂 Osamusiya apume bwanji Adzaferatu pa msokhano😂
@thomaswyson-e2q
@thomaswyson-e2q 24 дня назад
Iwe namachende asanafe peter ayambe kufa ndiabambo ako
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q 24 дня назад
Kkkkkkk koma anamalomba ndi achina Brian kkkkk
@UchizieFMtemela
@UchizieFMtemela 24 дня назад
A chair mwayankha bwino 😂😂alekeni chabe😂😂
@AlickChima
@AlickChima 23 дня назад
Maharaja nde mwawapanikizatu onyamata inu 😅😅😅 mpaka chibwibwi kudzitamandira ati Leader of opposition ndi power 😅😅😅😅
@CleverlyKanthyos-ds5sg
@CleverlyKanthyos-ds5sg 24 дня назад
DPP khalamba zokhazokha Zoyha mano
@thomphalavi5027
@thomphalavi5027 24 дня назад
Dpp yatsakha bwino mipando komaso mukutipasilanu mukulemphera
@InnocentEdasi
@InnocentEdasi 22 дня назад
Profe sikape guys ... , munthu uja amayiwelenga
@BrianMaganga
@BrianMaganga 24 дня назад
Adad akuyendani pansi, muona kuti mutani 😂😂
@christopherkamphinga
@christopherkamphinga 24 дня назад
Zayambika uku. Azizathawanso mu office ndi ukalamba.
@giftsululu4274
@giftsululu4274 24 дня назад
Malawi muno tupusitsana kobas
@83kwak
@83kwak 24 дня назад
I love Malawi,let's keep praying to Lord,Jesus Christ ...........
@LightonKamwana
@LightonKamwana 24 дня назад
Ukakamira nkhalamba.
@MphatsoZintambila
@MphatsoZintambila 20 дней назад
Mbuzi izi
@MahallaMinistries-fv1hw
@MahallaMinistries-fv1hw 24 дня назад
Atolankhani athu suffers from a certain condition
@KenAipa-r3r
@KenAipa-r3r 24 дня назад
Kkkkkkkk Kuchita kubwereza kuti Kodi aluza ????
@LewisJumbe
@LewisJumbe 24 дня назад
Conversation yayenda bullet,mafunso Anu,sapindula kanthu.lets look forward.
@VictoriaKumwenda-k6o
@VictoriaKumwenda-k6o 24 дня назад
Kukalamba munthu uja ndi nkhamba
@MzadziWanga
@MzadziWanga 24 дня назад
Kagwere uko pedegu iwe 😂😂😂 age is just a number
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 24 дня назад
😂😂😂😂😂😂😂 kodi 😅😅😅😅
@patrickmoffat9609
@patrickmoffat9609 24 дня назад
Iwe suzakula
@user-kt5bq2wg6v
@user-kt5bq2wg6v 24 дня назад
Zoona a mwene suti a piter niwoyipa ayi koma akamba nchito yi sangayikwanitse.
@Blessings-b7h
@Blessings-b7h 24 дня назад
Kodi Brian bwanji ukuwavutitsa anthu dpp? Munthu wamkulu akuphunzitsa ana ntchito.
@user-nt7cd9vo8u
@user-nt7cd9vo8u 23 дня назад
Kumangoduladula mau zobowa
@ChimwemweBottomani-hc5ju
@ChimwemweBottomani-hc5ju 23 дня назад
Age is just a number indeed...DPP my vote
@PreciousPhiri-l8w
@PreciousPhiri-l8w 24 дня назад
Koma chi peter chija osazachiphwekes chochenjera ❤❤❤❤❤❤❤❤❤
@user-sr4fe5bb2w
@user-sr4fe5bb2w 24 дня назад
Kodi Hon Mchacha alipo?
@StanfordMNthali
@StanfordMNthali 21 день назад
Chaka chino tiona maroza akariyati akupanga ubale ndi dpp ayiwala dpp amunyoza Chirima ndiposo kariyati kumbukirani mumene dpp yinamphela banja raTambala ku Lilongwe kariyati uribe Kodi Chirima anakhala kuti arimoyo mukanapita kumeko Mai opanda manyezi iwe
@KingsleyKunneno
@KingsleyKunneno 24 дня назад
Koma nkhalamba izi nazo 😂
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 24 дня назад
The question is unprofessional
@MoreenSemu
@MoreenSemu 24 дня назад
Akudwala Peter akungu mukakamiza
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 24 дня назад
Koma inusotu Chanel chanuchi ndiye gaga weniwenotu Madera bwanji ingoduka basi chimphwetelele
@samsonmtumbati4855
@samsonmtumbati4855 24 дня назад
Iwe chikangawa choka ap tulutsani report basi
@tasmania527
@tasmania527 24 дня назад
Iwe Namalomba, njala inabwera chifukwa ma leaders anu ammbuyo sanapange za irrigation kuphatikiza ndi ng'amba ya Southern Africa. Mwakhala mukunena kuti achina Mutharika ndipatali, nanga anayika madziko anji mu nthawi ya ulamuliro wawo kuti ku Malawi kusakhale njala ? Mulibe fundo koma kunama ndi kupusitsa anthu.
@DONNEXKhama-bk1gy
@DONNEXKhama-bk1gy 24 дня назад
Nice conversation
@CostanceLalli
@CostanceLalli 23 дня назад
Munthalika ndi dolo Mesa anthu amachachila kuti amupange zina ndi zina ndiye iyeyo wabanduka ndi dolo
@user-ub1vt2kq4s
@user-ub1vt2kq4s 24 дня назад
😂😂😂😂😂 koma Brian amanditsangalatsa❤❤
@Apostolic.faith7044
@Apostolic.faith7044 20 дней назад
These are elders supposed to rest for sure. Old to a point where they can't function to bring change in Malawi. People must accept they are old and tired, not even able to close a convention. They can't even see the difference of frail health on P. Mutarika. He did his best part in the past but must retire all these who are not able to see that they a madalas
@PreciousDzonzie
@PreciousDzonzie 24 дня назад
Agogo agogo agogo 2025 kotsutsa boma woooooo
@giftsululu4274
@giftsululu4274 24 дня назад
Ndipo nkhalamba izi
@user-ev6bi7jr7g
@user-ev6bi7jr7g 24 дня назад
Munthu wankulu posakhalapopo sanafune zopalana pakamwazo
@FainessMwanza
@FainessMwanza 23 дня назад
❤you Peter
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 23 дня назад
Sakumwa akutero ma ujeniwa 😂😂
@leonardmalirana7423
@leonardmalirana7423 24 дня назад
Brian osatero, osamuyankhulitsa chibwibwi munthu, Muthalika watopa akapumule
@AlihIbrahim-s7v
@AlihIbrahim-s7v 24 дня назад
Dpp yasankha bwino mipando yawo
@user-uc1pd1tc2x
@user-uc1pd1tc2x 24 дня назад
Ndipo koopsa zed bro❤❤❤
@ConlardNkhoma
@ConlardNkhoma 24 дня назад
Chipani chamagogo kkkkkk
@hassammaulana4529
@hassammaulana4529 24 дня назад
Koma guys akuti alipomwepana ali kubuyoko
@EmmanuelChirwa-z3n
@EmmanuelChirwa-z3n 23 дня назад
Chokani mwakalamba oba chimanga inu🤣🤣🤣
@user-ik5sz8hc6f
@user-ik5sz8hc6f 23 дня назад
Zomwe akuyankhulazo ndidziwona chomwe chinachititsa kuti msonkhano uwonjezeledwe matsiku Malo motha tsiku le ileni ndichani?which means adani amakonz a chiwembu.President adachita bwino kungolemba note yotsekela msonkhano wawo basi
@GiftJulius-ro9ev
@GiftJulius-ro9ev 24 дня назад
Kkkkkkkkkkk koma yah😅😅😅😅
@user-yh3dw6qu7z
@user-yh3dw6qu7z 24 дня назад
Iwe Brian peter amaopa kuphedwa ndi dzigawenga dza mcp
@MaikNkhoma
@MaikNkhoma 23 дня назад
Kkkkkkk yadwala nkhalamba ija
@ChrispinEdward
@ChrispinEdward 23 дня назад
Iwetu brain Banda ndikuwona umadana ndi dausi
@peterwhite3782
@peterwhite3782 24 дня назад
❤❤❤❤ Dpp
@charitykalulu
@charitykalulu 24 дня назад
Kusakhalapo osati chifukwa chokula kapena
@user-gd7xm7xr9v
@user-gd7xm7xr9v 24 дня назад
Wadwalika ndi kutopa gogoyu. Siyirani anyamata. Alipo ambiri anyamatakumeneko. Milandu ya malibino yinathera pati, atatchulidwa ku kothi pamodzi ndi Ntaba
@douglaskayira8362
@douglaskayira8362 23 дня назад
Nice
@RonnexNyezule
@RonnexNyezule 24 дня назад
Brian ati get away tu😂 atero George 😂
@bisweckchimphamba8497
@bisweckchimphamba8497 24 дня назад
You are dreaming
@MosesShaibu-ee8hn
@MosesShaibu-ee8hn 24 дня назад
Muthalika ndiwochenjela wayenda kwambili uja ndiwozindikila
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q 24 дня назад
Kkkkkkkk Brian Banda usadzafe udzangosowa
@OwenDubbyflitz
@OwenDubbyflitz 23 дня назад
Mbwerera zeni zeni
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 24 дня назад
Peter wakula sangakwanitse kulamulira azalamulira ndi getrude ndi chisale yawo ija
@gradsonmayira9336
@gradsonmayira9336 24 дня назад
Brian banda😂😂😂😂😂
@RABSONSIKELO
@RABSONSIKELO 23 дня назад
Mr Maize gate ur wounded
@JonesManyeka
@JonesManyeka 24 дня назад
Iiiii musiyeni munthu akagone
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 24 дня назад
😂😂😂😂😂😂😂 madala party zachisoni kutha kwachipani ndikomweku basi
@JacklineNiwahereza-ni3pm
@JacklineNiwahereza-ni3pm 24 дня назад
Kkkkkk koma nde mwamuwonjeza chaponda kkkkkkk
@SolokingChimzy-yt7dj
@SolokingChimzy-yt7dj 24 дня назад
Nothing is was wrong Muthalika posamaliza nawo zochitika..bola alemba babawo zoyankhula zawo
@JohnBanda-ux9fy
@JohnBanda-ux9fy 24 дня назад
Munthu wamkulu APM anachoka lero mmawa chifukwa anadziwa Kuti Ku dpp kulibe kukhapana ngati achita chikangawa party..anachezera convenshon .. Koma kurephera kukayang,ana ndege Ku chikangawa 😂😂
@yusufsadic2930
@yusufsadic2930 24 дня назад
Chapond sakuyankh funso mwaluz ndiy muzit ndil ndigalimot ndiy kt chiyan anthu akukanan
@RabiaNotes-ql8cf
@RabiaNotes-ql8cf 24 дня назад
😂😂😂😂Dr George Chaponda
@johnchicoti
@johnchicoti 24 дня назад
Peter wadwalika ndichifukwa chake sanabweleso
@EnerstBanda-m4s
@EnerstBanda-m4s 24 дня назад
Please abale athu a Dpp tamumverani chisoni Gogo wakula munthu sangakwanitse kulamulira dzikoli ndi munthu okalamba kwambiri his a good President sibodza but tasakhani munthu weniweni wamoyo osati izizi Please mukulimbana ndi chipani choti chili m'boma kale woke up Malawians we can't continue ruled by old person 85yrs or muli serious
@YusufMapata
@YusufMapata 24 дня назад
amuthalika akuchita kukakamizidwa kuti ayime koma munthu uja mafupa atopa popeza mtima sukalamba
@thomaswyson-e2q
@thomaswyson-e2q 24 дня назад
Mafupa akalamba ndiabamboako kapeonyozamakoloako iwe mboliyakonso
@husseinjabu8866
@husseinjabu8866 24 дня назад
Poor quality of coverage improve guys
@EmmieChikuseKoreya
@EmmieChikuseKoreya 24 дня назад
Zokalamvazo ndiye usanene iweso osakalamba iwe unkhoza kufa kumusiya okalambayo komaso kukalambako ayamba ndi mai ako ndi bambo ako
@user-wg8tp8in1v
@user-wg8tp8in1v 23 дня назад
Wakalamba uyu
@GladsonBanda-m3e
@GladsonBanda-m3e 24 дня назад
Nkumati tiyendetsa Boma pumani mwakula kukanika kukatseka msonkhano ngakhare campaign idzawavuta
@LightonKamwana
@LightonKamwana 24 дня назад
Abanda muziva chisoni ndi agogo.
@user-lp2sd7lt8b
@user-lp2sd7lt8b 24 дня назад
Koma zitithandiza??????
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 24 дня назад
Tizakalamba koma ngati tizizakakamila mpando
@GavanaradagarasiDagarasi-bu6le
@GavanaradagarasiDagarasi-bu6le 24 дня назад
Wakomoka amenewuja akudwala
@RabeccaMkandawire-i9j
@RabeccaMkandawire-i9j 24 дня назад
Akapume amenewa ndi amene anayambitsa quota system
@violetkamvanthupi2443
@violetkamvanthupi2443 24 дня назад
UTM my vote
@MsondaBanda
@MsondaBanda 24 дня назад
This old party, with old experience
@GeorgePhiri-ub2of
@GeorgePhiri-ub2of 24 дня назад
Madala madala madala madala
@omicloans
@omicloans 23 дня назад
Use proper internet
@DavieChiwale
@DavieChiwale 24 дня назад
Brain uzioona mikoko yogona iwe
@aligrayjeo1071
@aligrayjeo1071 23 дня назад
Rubbish some audios are skipped
@OwenJambo
@OwenJambo 24 дня назад
Kukakamila mpando
@solobertkamunga2826
@solobertkamunga2826 23 дня назад
Next time Dont post video yot ikuduladulA, azungu azititseka
@Lingstone-r3z
@Lingstone-r3z 24 дня назад
Brain that is issue to close covetion,
@ishmaelimani3779
@ishmaelimani3779 24 дня назад
Khangati mitu sikugwila amalawi chomwe timachifuna sitimachidziwa
@finchiadriano
@finchiadriano 24 дня назад
Koma chipani chopanda m nyamata
@JamesMpinda
@JamesMpinda 24 дня назад
wakulu uyu avomeleze
@tebogomaake9375
@tebogomaake9375 24 дня назад
Inu simudzakalaba
Далее
ФОКУС -СВЕТОФОР
00:32
Просмотров 211 тыс.
Times Exclusive featuring Sameer Sulemani - 13 April 2024
1:00:14
INTERVIEW YA MATHEWS MTUMBUKA
30:11
Просмотров 1,5 тыс.
ФОКУС -СВЕТОФОР
00:32
Просмотров 211 тыс.