Тёмный

BUNGWE LA MALAWI FIRST 🇲🇼 KULI PUNGWE PUNGWE PAKATI PA BEN LONGWE KOMASO BON KALINDO🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼 

TIDZIWE TV
Подписаться 8 тыс.
Просмотров 23 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2023

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 209   
@Nomthatha-rp1sh
@Nomthatha-rp1sh 9 месяцев назад
Mr Ben Longwe mudakayamba mwafufuza kapena kukambirana muzapha Munthu osalakwa kugwada Kwa nduna sizisonyeza Kuti walandila ndalama ayi ndichikhalidwe chathu akuuzaniwo akungofusa akudaniseni ndi a Bon Kalindo chonde upezeni
@wilsonkalipa2063
@wilsonkalipa2063 9 месяцев назад
Ben longwe Mutu mwakomo mulibe mzeru ungofuna kuwapusisa amalawi palibe chanzeru ukukamba😊
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 9 месяцев назад
Akuru u Comrade sitipangira ku dziko laweni....ndipo muthokodze kuti dziko la South africa siili pa ubale wabwino ndi dziko la malawi kamba ka nkhani ya bushiri ija bwedzi mutatumidzidwa kalekale kumudzi.....komaso ndikambepo za malawi first ...chiyambireni malawi 🇲🇼 first siinapangisepp mademo dziko .ndipo mademo onse amakhara akurephereka ...ndipo ngati kunali mademo ndi akalindo ndipo anadzungulira dziko lonse ....
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 9 месяцев назад
I like this so much magulu kapena zipani zikamayambana
@AufiJafiali
@AufiJafiali 9 месяцев назад
Kalindo emweyo bas iye Ali kumalawi uyu galu Ali Kuno kujoni💪
@AlvinJnr-rm6pe
@AlvinJnr-rm6pe 9 месяцев назад
Bon kalindo simunthu wamba anabadwa wachikhalidwe eyetu enawo ndi choncho kutukwana basi 😂😂😂😂😂
@simonpaul6567
@simonpaul6567 9 месяцев назад
Mr ben longwe all the time ndinu isokoneza kwambiri
@ernestovirgilio8790
@ernestovirgilio8790 9 месяцев назад
A beni inuyo muli dziko lina ndiye nkumati mukumenyera nkhondo a malawi? Kanyereni kutari komanso mwagulidwa ndi chakwera kuti mu ipitse boooooooooon kalindoooo ife wathu bon,bon bon bon kalindo
@user-mj3ms4jt3b
@user-mj3ms4jt3b 9 месяцев назад
Amalawi votu lathu timangoombera m'manja ndi mfiti zomwe. Anthu ngati awa ndi amene akupangitsaso ife osauka kuti tizisaukira. Anthuwa awa siomenyera ufulu anthu osauka akumenyera mimba zawo ndi mabanja awo. Ndipo Mulungu anthu awa awkantha chifukwa akufuna azipidula mudzina la amphawi. Tikhazikitsiso lamulo lomanga anthu ngati awa omanamiza kuti akumenyera ufulu anthu yet akudziwa kuti apidula ndi iwowo. Mose muja anayambilamu ndi ufulu uti omwe atimenyera?
@JamesMalango
@JamesMalango 9 месяцев назад
Mr bwanji osakambirana kumbali ngati anthu opita ku school, mwaonesa kut ndnu osowa khalidwe
@Lastonkabota
@Lastonkabota 9 месяцев назад
Ndipo zoona,,,awa akulilila udindo bas
@Lastonkabota
@Lastonkabota 9 месяцев назад
Ndipo zoona,,,awa akulilila udindo bas
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 9 месяцев назад
Koma ben longwe kusokoneza aaaaaiwetu uli jon aaaaa
@MtenjeHassan
@MtenjeHassan 9 месяцев назад
Olo atakhala kuti bon kalindo analakwisa Koma simumayenera kupanga zimenezo,mukanayamba kaye kukambilana nyumba mwanu...a Ben longwe mwalakwisa..grow up man....
@NedsonKanjira-qj2ig
@NedsonKanjira-qj2ig 9 месяцев назад
I think nkhani Yoona NDI iyi Mr Ben longer akunena Chilungamo anthuwo alandiladi vindalama zankhani nkhani kuchokera KU Boma , ndibwino nonse mungosiya kudzuzula Boma chifukwa Palibe chimanga inu asiyeni amalawi NDI Mulungu yekha amene amenyere nkhondo Ife Amalawi 1992 Mulungu anatimenyera nkhondo kumuchosa Kamuzu kuzaika Bakili Muluzi so don't waste your time live it
@user-wd9yd1bg9n
@user-wd9yd1bg9n 9 месяцев назад
This is what ee call ntumbuka pa chilungamo ❤❤❤
@user-vh9uk1jy7w
@user-vh9uk1jy7w 9 месяцев назад
Ben longwe mbuzi iyii bwanji osapita ku Malawi ngat uli dolo
@innocentmusuli7380
@innocentmusuli7380 9 месяцев назад
Akuwopa amangoziwa kutukwana ndekaya atakhala president angakhale wotukwanatu
@linllychinyumba-gw1su
@linllychinyumba-gw1su 9 месяцев назад
Very good ..well spoken
@JamesThomu
@JamesThomu 9 месяцев назад
Ben longwe ndiwe kape kale ndimakutsata ndimaona ngat ndiwe wa nzeru koma pano ndakuona coz ukanakhala wa nzeru ukanabwela kudziko lako ndikumapanga zomwe ukunenazo tikanakukhulupila koma uli kwina nde ndikumati umazitsata assssaa ku mademo sumakhalako umangomva basi ndikumachuluka nzeru
@doreenkhembo7718
@doreenkhembo7718 9 месяцев назад
Ben vesira muli ndianthu ambiri amakusatilani inu koma zimene mukuchita pano aaaaaa anthu asiya kuvera message yanu khalani pasi nose mukambirane wachisisi zimakomatu lero zaipa chonde chonde message yanga lekani khalani pasi Hiooooo ❤☝️☝️☝️☝️☝️☝️
@LysonMtalika-tb6fk
@LysonMtalika-tb6fk 9 месяцев назад
Too shameful, I didn't expect Malawi First to be decided like this, if it's like this then who is going rescue us, we poor Malawians are going to suffer a lot
@RaphaelHara-tr9iy
@RaphaelHara-tr9iy 9 месяцев назад
Iwe Ben uliopusa kumenyera ufulu ulikuno Ngati ineyo azako akudya bonya pamalawi
@user-yh3dw6qu7z
@user-yh3dw6qu7z 9 месяцев назад
Popanda kalindo mungatani ku south Africa.inu mulingati kamulepo kalua amkateronso.nkhalani ndiulemu pochita zinthu
@alicephiri3706
@alicephiri3706 9 месяцев назад
Aben Longwe mwinatu munapupulumatu zopanda umboni mukhale pamodzi mukambirane ngat akulu akulu
@georgednthala-wh3pf
@georgednthala-wh3pf 9 месяцев назад
Nobody is wanted by either ICC or UNHCR Mr Ben we don't 've any problem with our leaders. Mr mphepo and Mr chipungu r very cool guy unless u have smthng against them
@IbrahimDailes
@IbrahimDailes 9 месяцев назад
Zachisoni ndipo zolilitsa sitimayembekezela kt mungamatidutse pasi chonchi after mutatiuza kt akubanja kwanu anakuyitanani kukuzuzulani kt musiye kumenyela anthu ufulu after mudabwela kutiuza kt simunalole muzafela amalawi nankha izi ndi ziti lelo tinakudalilanitu anthunu umodzi uja ndi uti nankha mmmm Malawi 😭😭😭
@umaliishumaeli9637
@umaliishumaeli9637 9 месяцев назад
Akuluwa aben Longwe ndopanda nzeru lyeyi amakhala south african bwanji osapita kumalawi kukapanga nawo ma demo ben Longwe ndi osokoneza
@user-hd6xc5ud2b
@user-hd6xc5ud2b 9 месяцев назад
Bwana kupupuluma abwana😅😅😅😅
@user-tu9oe5sv4b
@user-tu9oe5sv4b 9 месяцев назад
Bwana longwe kupupuluma sikwabwino.ngati muli dolo.pitani kumalawi muzikamenyela ufulu amalawi.kalindo ndi big amatiyimilila
@mathewsmbaluko8522
@mathewsmbaluko8522 9 месяцев назад
😂😂😂
@user-hd6xc5ud2b
@user-hd6xc5ud2b 9 месяцев назад
Abwana mungokambirana apa mwangowonesa uchisiru timakutengani ngati muli ndi dzeru
@husseinmoffatt
@husseinmoffatt 9 месяцев назад
Mwana oophwa kwambiri 🏃🏃🏃🏃🏃🏃🏃😆😆😆😆😆😆😆
@JerryChain-cz8ru
@JerryChain-cz8ru 9 месяцев назад
Ben ndinu osowa khalidwe
@user-xl1xn3jb2e
@user-xl1xn3jb2e 9 месяцев назад
Comrade bwana Ben Longwe phunzirani kukambirana ku ma office anu aMalawi first chifukwa chomwe mungadziwe, Malawi first mwatenga aMalawi onse kukhala m'manja mwanu ndipo aMalawi pano adalira inu ndiye ngati pa maudindo anu ngati musanamvetsetsane please pezani njira zina mpaka mumvane.
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 9 месяцев назад
Aaaa shem AAA Malawi first basi yagwaa
@simonpaul6567
@simonpaul6567 9 месяцев назад
Ben longwe we know very well you your like Chamillion
@KhimzyMike13
@KhimzyMike13 9 месяцев назад
Apapa chilungamo tichiziwa ndi lodson munilo basi kuti zikhala bwanji 😢 iiiiiiish zosayenda kwabasi
@charlesmpaso2383
@charlesmpaso2383 9 месяцев назад
Basi Malawi sazathekaso 😢sindinayembekezere kuti zikhonza kukhala zotere ku malawi first...my fellow Malawians let's just focus about our future don't trust these nosence called freedom fighters and politicians 🙌🙌
@AmusedDimSum-hd5yp
@AmusedDimSum-hd5yp 5 месяцев назад
Boooon kaliiiiiindooooo wowopsya kwambiri
@JacksonMacheso-hb3bm
@JacksonMacheso-hb3bm 9 месяцев назад
Ben longwe inuyo mungotokota muli kunja duuu ngati uli mamuna tabwelani tidzamenye nkhondoi limodzi
@samuelbrian3409
@samuelbrian3409 9 месяцев назад
😂😂😂Munthu uli ku south africa ife tikuzuzika ku malawi kuno, pamenepo ukumenyera ufulu ndani, kkkkkkkkk km a malawi anzanga😮😮😮😮😮
@neemahkapatamoyo9563
@neemahkapatamoyo9563 9 месяцев назад
Komatu munthu uyu akunena zowonadi kunena chulungamo kalindo amakonda ndalama utsi sumafuka popanda Moto Angakhele anthu enanu mukumutukwana Ben Longwe
@wilsonfelix6559
@wilsonfelix6559 2 месяца назад
Muziona nkhani zoika pa social media plz mukutithera bandle zaziii
@user-yt2op5rl2q
@user-yt2op5rl2q 9 месяцев назад
Akulu alongwewa penapake MMM ngaphuma ngat tuzi tosegula mmimba
@ernestovirgilio8790
@ernestovirgilio8790 9 месяцев назад
Wagulidwa ndi chakwera galuyu kuti aipisse bon calindo ussazabweretso ku malawi ndi zakumenha
@eliaskachali-xn2ve
@eliaskachali-xn2ve 9 месяцев назад
Ukunena zowona Ben Tawa uze chilungamo.kalindo akubayiza
@user-js3ds5qz4r
@user-js3ds5qz4r 9 месяцев назад
Ben longwe ndiwe opusa kwambiri ukadakhala dolo ukadapita konko osayamba mwakambilana bwanji ndalama zingapangitse mademo popanda anthu kupupuluma bwanji
@duncainjimmy
@duncainjimmy 9 месяцев назад
Bon Kalindo wayankha inde Koma Ben Longwe is right because Bon Kalindo sanatsutsepo Za kugulitsa mademo ndipo sanalowepo ai . Kwakulu wakana kulankhula momveka bwino kusonyeza Kuti ndi bodza
@BrayanMisomali-nj3hv
@BrayanMisomali-nj3hv 9 месяцев назад
Ndinuopanda Zelu Sujamukati urendo uno palibe atatidanise phuma siramwino kugigilika ngati manyi a mamawa
@JohnConar-kq4hi
@JohnConar-kq4hi 9 месяцев назад
eish bon kalindo 🤔🤔🤔🤔
@ibrahmdoka7486
@ibrahmdoka7486 9 месяцев назад
Bon Kalindo is a hypocrite He is now worse .He is cursed
@chekiamaabdul5083
@chekiamaabdul5083 9 месяцев назад
minyelo yamanu agulu inu.osawukafe sitimadya m,makwanu anamachende inu mikongo yanu
@tonemuyaya6284
@tonemuyaya6284 9 месяцев назад
Ben longewe Mach ndi chimoz moz reroso ndi chimoz moz ali ndi ufiti 😅😅😅😅
@AlvinJnr-rm6pe
@AlvinJnr-rm6pe 9 месяцев назад
Kuli ntchito zikatelo mumati yangawana nzida 😂😂😂😂😂😂
@user-yi4oc4xz4v
@user-yi4oc4xz4v 9 месяцев назад
😂😂😂😂 chilungamo chinakupweteka ase
@umalimaganga
@umalimaganga 8 месяцев назад
Iwe Ben longwe umangolimbana ndi Bon Kalindo ndiwe opusa kwambiri chitsilu Ben longwe
@shuraimuwamama2349
@shuraimuwamama2349 9 месяцев назад
Mwatigwetsa ulesi kobasi chifukwa mu Malawi first ndimomwe timati muli chilungamo,mtendere,ulemu ndi chikondi osati mbwelera zomwe mukubwera nazozi
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 9 месяцев назад
Chipasupasu ku Malawi first.
@user-nf3ik3ff6y
@user-nf3ik3ff6y 9 месяцев назад
Zaululika Malawi sazatheka😂
@dysonkhofi-gv4uy
@dysonkhofi-gv4uy 9 месяцев назад
Ben Longewe uchite Manyazi, Ngati uli dolo ukanabwera pa ground. Ndiwe osokoneza.
@Nomthatha-rp1sh
@Nomthatha-rp1sh 9 месяцев назад
Azisogoleri nonse a Malawi First a Malawi ochuluka amakukonda I Komanso amakusatani ndiyeno mukayamba kutosana chonchi ndiyeno a Malawi athawire Kuti chonde anthu akuvutika
@user-hs5xv6bk2f
@user-hs5xv6bk2f 9 месяцев назад
Kodi Ben umati umamenyela ufulu Ife tinakuwonako kumademo ati made no umapangawo ndiati mwina umamenyela ufuluwa anthu akujoni omwewo Ife kuuno kumalawi sitimakudziwa Kuti udziwe lelo
@MilikaKilion-tn1bn
@MilikaKilion-tn1bn 9 месяцев назад
Pitani komweko amkolo ufulu sitimenyela tili Kwa eni Ake azanu akugwila mbendela any time akhoza kuphedwa inu mukulumbwa muli kutali
@amabhohlela.3492
@amabhohlela.3492 9 месяцев назад
Mwana oopsya kwambiri ndi chitsiru kwambili,,kumangidwa kosekuja mpaka kumakafika Dwangwa aaaah ine sindimakhulupilira kuti amamangidwadi!!!!kapena kunalikomakalandila Ndalama..
@simonpaul6567
@simonpaul6567 9 месяцев назад
Mr ben longwe ndinu waphuma munatikhumudwisa poyamba
@henrychauya713
@henrychauya713 9 месяцев назад
Mukutimbwambwanisa anthu inu 😱😱😱
@christopherphillip4718
@christopherphillip4718 9 месяцев назад
@Iweyo simunthu wabwino walandila ndalama zingati usiye palibe vuto ukumawapatsa anthu zakudya ngati tili kale pamavuto chifukwa cha zitsilu inuyo
@victorauwana7258
@victorauwana7258 9 месяцев назад
Mmmmm muli ku jonz?
@tonemuyaya6284
@tonemuyaya6284 9 месяцев назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂. Iwe ndi cho cho
@simonpaul6567
@simonpaul6567 9 месяцев назад
Ben long if you tired of malawi first you can go out but mr bon kalindo hes president of malawi first for food we can not trust you mr ben longwe
@chimwemwemorris6827
@chimwemwemorris6827 9 месяцев назад
Ai bwana musasiye dziko lilipamotoiri tikudalira inuyo abwana
@omanm2919
@omanm2919 9 месяцев назад
Ben longwe umafunika ubwele ku Malawi konkuno chifukwa umangotokota uli kunja uko. Ngati akupatsa kathu ena ife sikufuna usatisokoneze mitu
@husseinmoffatt
@husseinmoffatt 9 месяцев назад
Ben longwe your right
@user-mc8gk4xv3f
@user-mc8gk4xv3f 9 месяцев назад
Molalo imene amalandira Bon kalindo imakupweteka..umafuna azikupatsa iwe molalo chonsecho iwe umangoziwa kubwebweta monyoza no action pa ground.
@jonesnezara4294
@jonesnezara4294 9 месяцев назад
Mokupemphani akalindo pangani ubale ndi anthu omwe amapezeka pa ground, enawo amangotukwana akuziwa kuti alikutali zimakusalirani inuyo, akudwara mutu ben longwe mtayeni mwangomkakamira anayamba ndikale kulimbana nanu
@user-lx5dp1pd4e
@user-lx5dp1pd4e 9 месяцев назад
ben longwe galu iwe
@ChimwemweMagombo-kq8nl
@ChimwemweMagombo-kq8nl 9 месяцев назад
Machende ako Ben longwe
@sydneyngoma2356
@sydneyngoma2356 9 месяцев назад
Mwapupuluma a bwana kharani pamozi a Malawi
@AlvinJnr-rm6pe
@AlvinJnr-rm6pe 9 месяцев назад
Kalindo palibenso ndipo ben longwe uchedwa phuma kuyakhulayakhula
@elizamaster2168
@elizamaster2168 9 месяцев назад
ABen longwe inu simumamenyela ufulu amalawi mukadakhala kt mumamenyela umfulu amalawi mukadabwela kumalawi kokuno, km mumangoyakhula amayenda mademo nd abon kalindo mukunenawo
@ernestovirgilio8790
@ernestovirgilio8790 9 месяцев назад
Choka ukusokosera iwe ulibe khalidwe zimene ukuyankhula akunva ambiri ndiye uzinena zankabudula izikhala ndi ulemu ndi anthu chitsiru khala konko ku jhoniko.
@user-rv5tk4rp9s
@user-rv5tk4rp9s 9 месяцев назад
chitsiru iwe ben longwe ukutani kupita ku malawiko wabodza iwe ufuna kusokoneza anthu bs kape iwe
@dysonkhofi-gv4uy
@dysonkhofi-gv4uy 9 месяцев назад
Ben Longwe ndiwe osokoneza, ukhale chete!
@user-mp5ir1qw1e
@user-mp5ir1qw1e 9 месяцев назад
Yadya ndalama ndiwe Ben longwe
@user-od6ln7gj8z
@user-od6ln7gj8z 9 месяцев назад
Inu simungakhare mu group la anthu munateloso ndi juma
@user-ne1kt6hx5w
@user-ne1kt6hx5w 9 месяцев назад
Ben ndiwe nzibambo opanda nzeru . Kodi anakupempha ndani kuti uzimenyere ufulu amalawi, miyoyo yathu ilimmanja mwamulungu ndipo ndiyekhayo adziwa mawa lamalawi... phunzirani kuyankhula mosanyoza bambo opusa inu
@LyfodKesten-he3fr
@LyfodKesten-he3fr 9 месяцев назад
mmmmh mbola guys
@NaasifJacobs-ou6rc
@NaasifJacobs-ou6rc 9 месяцев назад
Nonse mukulimbana chifukwa cha ndalama . Phindu palibe mukungosokosela
@user-tw2zf7bj3e
@user-tw2zf7bj3e 9 месяцев назад
Zinthu zikachitika muziyamba mwakambilana musanabwere nayo pa gulupa
@stevembama751
@stevembama751 9 месяцев назад
Ben wabodza uli ku jozi kuno ukukhalatso munkhunkhu ine ndimawona ngati uli kumalawi kkkkkkk Ben ndikape kkkkkkk za redson munuro ndi kalindo there together as one
@patiencetebulo
@patiencetebulo 9 месяцев назад
Mr Ben longwe that is solution
@stevembama751
@stevembama751 9 месяцев назад
Beni longwe usaputsitse anthu look your staying in South Africa koma kumakamba zakumalawi we know you Beni longwe u like to mess up things eshiii you know God knows kalindo alimumalawi momwemo redson munulo alikotso kumalawi koma Ben longwe uli kuno ku joni hahaaa alekeleni redson ndi awiniko amenyele ufulu anthu
@user-uq7cz1to2i
@user-uq7cz1to2i 9 месяцев назад
Son mukumakangan nokhanokha nde anthu okusatilan azit chani ukuku nde ndkupus sopan ndmakusatilan koma ndaona kut zalow chibwan guys
@omanm2919
@omanm2919 9 месяцев назад
So shamed to u Ben longwe, look at u where u are u just talking too much but u are out side the country we love mr bon kalindo
@user-xv6si8pn3e
@user-xv6si8pn3e 9 месяцев назад
Ben Longwe ndiwe mbuzi, coward,ongoyankhula pa Air pomwe Bon k the DC amamenya pa ground,Redson munlo ndi wamantha sangathe ku yenda pa nseu.....ine ndi the Dc viva Bon kalindo.
@EllaMohango-qd1pg
@EllaMohango-qd1pg 9 месяцев назад
Kape uyu mwee
@user-zj1xx1ic2m
@user-zj1xx1ic2m 9 месяцев назад
A Ben Longwe penapake tamakulani, MA audio anu ndinayamba kuwamva kale kwambiri ndipo ndimakutsani kwambiri koma Pena Pake kupupuluma sibwino, inu ngati vice president and president wanu walakwitsa mkungofikira PA air mwatani??
@ritabani274
@ritabani274 9 месяцев назад
Nonse ndi zitsiru zokhazokha inu Mlungutu amamenya nkhondo kuombola anthu ake inu ndi anthu akuba mukungofuna mudzipeza chakudya chanu
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 9 месяцев назад
Kalindo wadya ndalama zambili from MCP ku Mount sochi
@user-xv6si8pn3e
@user-xv6si8pn3e 9 месяцев назад
Zilibe ntchito,bon kalindo the DC timamukonda heavy.....Ben longer ndi manyi
@simonpaul6567
@simonpaul6567 9 месяцев назад
Mr boni Kalindo can not do that
@tingamasi106
@tingamasi106 9 месяцев назад
zitaye kumene if u want come home and fight apo biii nawe zikanda mashabwada ako kumeneko
@wilsonkalipa2063
@wilsonkalipa2063 9 месяцев назад
Ben ndi galu weni weni akunyoza anthu oti amapezeka pa ground
@user-hu8vp4wt7j
@user-hu8vp4wt7j 9 месяцев назад
Kom mukupanga chani a Malawi fast ife timakunyadilani tuu kut mutimenyela nkhondo ife a Malawi takhalani pasi mukambilane ndikuvesesana 😢😢
Далее
Вы чего бл….🤣🤣🙏🏽🙏🏽🙏🏽
00:18
OG Buda -  Лазерный
02:27
Просмотров 72 тыс.
🎙ПОЮ твои ЛЮБИМЫЕ ПЕСНИ💥
3:10:10
Chilungamo Chiposa Zida Zankhondo - Ben Longwe
34:28
Просмотров 3,1 тыс.
NTCHITO YODZUKUTA SPEECH  YA ACHAKWERA YAYAMBIKA |
33:43
Jomo wamukana Bon Kalindo
4:20
Просмотров 59 тыс.
Ben Longwe kuyankhulapo pazaimfa ya oimba..
35:04
Просмотров 14 тыс.
Вы чего бл….🤣🤣🙏🏽🙏🏽🙏🏽
00:18