Тёмный

CHAKWERA AMUDZUDZULA KUSELIKU LIMODZI NDI CHIPANI CHA MCP 

Malawi Extra
Подписаться 15 тыс.
Просмотров 14 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 137   
@AbdulsharifulKalipinde-m6u
@AbdulsharifulKalipinde-m6u 3 дня назад
I greed with you True spoken Misewu sitingadye Olo atamanga ngati kwa america simungawine Anthu akufuna chimanga ndi fertilizer,zipangizo za kumunda ndiye munkhoza kuwina
@hamiltonsolomon3756
@hamiltonsolomon3756 2 дня назад
Powerful Speech Brother ❤❤❤
@CourageBanda-d1g
@CourageBanda-d1g 2 дня назад
Nice message
@YamikanMasiye
@YamikanMasiye 2 дня назад
8:45 I humbly respect your views mr u r number 1 ,, palibe chabwno angachte ngt njala sakuithesa kapna kuichepesa
@ernestjuniormbanga3370
@ernestjuniormbanga3370 2 дня назад
Powerful words fadah ...truth baba tell them....akunamizana
@marthansaliwa7732
@marthansaliwa7732 2 дня назад
Ife a UTM tilibe nthawi yovotera Chikangawa.
@osmanmdala-uh7xw
@osmanmdala-uh7xw 2 дня назад
Eee brother salute....Good advice to mcp koma sangakumvereni.....
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 3 дня назад
Kodi inu, ena nanu or mukuti ndi a chakwera mukunena zoona dziko li likuyenda bwino, tamawopa Mulungu inu, chakwera ndi munthu wolephera kwambiri, kuba, kupha, kumanga anthu, osalakwa, a comrade inu Mulungu wathu, akudalitsen powawuza chilungamo. awa, anthu osavawa, anthu sakuwafuna, awa, God bless bro
@SamsonSelevasio
@SamsonSelevasio 2 дня назад
Perfect said boss mumakwana inuyo
@AhmadIsmael-l5q
@AhmadIsmael-l5q 3 дня назад
inu dpp sugar 500 kwacha fertilizer 18.000 nchele unali otchipa chimanga chinali chotchipa ife amalawi tonse tivotela dpp kufuna osafuna ife bolani dpp
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy 2 дня назад
Yes ,, DPP boma ,,mtendere wathu otsagula ndindalama lero tilibe what kind of man chakwera ,, rubbish man
@mathiusbizinesi2482
@mathiusbizinesi2482 2 дня назад
Well said brother
@AhmadIsmael-l5q
@AhmadIsmael-l5q 3 дня назад
mcp ndichipani cholephela kuchokela kale mcp isazinamize ife tonse tivotela dpp dpp dpp basi nothing else
@Chikwawa
@Chikwawa 3 дня назад
Ife a UTM tivotera dpp.
@NewtonTembo-q4t
@NewtonTembo-q4t 2 дня назад
Point number 1
@stuartsangaloti8461
@stuartsangaloti8461 3 дня назад
Very true much respect
@usherjamson174
@usherjamson174 2 дня назад
More fire misewu samadya pamenepo tiyimepo ndithu tsindikani ndithu zisilu zanthu😂😂
@AchinaKellz
@AchinaKellz 2 дня назад
Koma kumanena chilungamo apa tili ndichitsiru😢
@Esa-u3t
@Esa-u3t 2 дня назад
Powerful message big🙏🙏🙏
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 3 дня назад
Powerful speech auze brother
@ShakiraJackson-x8w
@ShakiraJackson-x8w 2 дня назад
This very true
@raphaelsamala3792
@raphaelsamala3792 2 дня назад
Ndine waku Lilongwe komano zinthu zikudulilamu boladi dpp yomweija
@MathewKalinkhu
@MathewKalinkhu День назад
Koma ndiye waitha MCP, zoona zokha zokha, anthu sangadye misewu ayi. Better APM ndi DPP basi. Chimwendo Banda ndi Kunkuyu akumunamiza chakwera.
@WanangwaMfune
@WanangwaMfune 2 дня назад
Sitsani fertilizer, tsitsani mtengo ya zinthu basi zotse zoyankhula anthu zinthu. Koma zinazo mmmmm titsanane.... Kukwela kwa katundu Ndi D compen mawu angawa mdzaakumbu muasunge
@IsaahLobern-x2u
@IsaahLobern-x2u 3 дня назад
Wayakhula zanzeru bro
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 2 дня назад
🤞🤞🤞🤞
@Abel_uniquejson
@Abel_uniquejson 2 дня назад
Komano this man akuyankhula ichi ndichilungamo osat zandaleso ayi
@SamuelKhumbiwa
@SamuelKhumbiwa 2 дня назад
Brother mwalakhula mau. Basi musawauzire mayeso amenewa kwao kwantha.ause mumtendele
@JacksonMoyo-tm8dv
@JacksonMoyo-tm8dv 2 дня назад
There is no vote for MCP in Northern region I'm telling you I'm tumbuka by tribe
@NgeyasjuWadeya
@NgeyasjuWadeya 2 дня назад
Anyani awa chomwe akudziwa iwo ndikuba nde akuona ngati amalawi sakuona kuti azisekerera zopusazii,mchifukwa chake akufuna kubwera zisankho.
@RoseMsonkhoMalele
@RoseMsonkhoMalele 2 дня назад
Ndipo onse a mcp mmmmm ngati mbuli zonkha zonkha , ndipo iwe ukunena zowona live live
@RoseMsonkhoMalele
@RoseMsonkhoMalele 2 дня назад
Udf inanthanso kale, kale, akunamidzila amenewaaa
@FunnyKalimwayi
@FunnyKalimwayi 2 дня назад
mbamande boss
@ElizabethKoopa
@ElizabethKoopa 2 дня назад
Where is Our food security
@JoaquimElidioChiwisse
@JoaquimElidioChiwisse 2 дня назад
Ifé sitingataye nthawi kumakavotela mcp zaugalu
@PriscillaKhumbanyiwa-i1d
@PriscillaKhumbanyiwa-i1d 2 дня назад
Ife Tina vota UTM sinavote mcp
@amillalickalkymond
@amillalickalkymond 2 дня назад
Yankhula koma kumeneko brother
@MarryNyilongo-s5x
@MarryNyilongo-s5x 2 дня назад
Nzoona anthu akufa miseu zizayendamo ndi mbalame njala akuionaasiyeyeni anzaona mbwanza in Jesus holy ghost fire
@andrewmandawalaphirithepillar
@andrewmandawalaphirithepillar 2 дня назад
I gree with you
@MattinGold-l9w
@MattinGold-l9w 3 дня назад
Am agree with you
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 2 дня назад
Dpp my vote 💙💙
@ShillahLawrence
@ShillahLawrence 2 дня назад
Ndakhala ndikuwauza awa a MCP kuti asinthe zochita ,inetu ndatukanidwa mu 2020 chifkwa chainuyo ,inetu ndinapeleka Voti yanga b,coz of SKC ;
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 2 дня назад
Kumanga misewu it's good
@EvansEgra
@EvansEgra 23 часа назад
Nkhani yabwino zedi, ndipo ikumveka, koma nzomvetsa nchisoni panopa anthu akufunanso kuyika mbuzi yomwe inavetsapo kuwawa kale anthu, kuti akhalenso pampando.
@verinachiponde6922
@verinachiponde6922 2 дня назад
Eya auzeni zoona amenewa
@SaidiBaneti
@SaidiBaneti 2 дня назад
vote 🗳 yanga ayi Wales chakwela
@mercymalenga1884
@mercymalenga1884 2 дня назад
Amen brother
@DavidPhiri-o6w
@DavidPhiri-o6w 2 дня назад
Anavotera chilima. Mavote a utm ndi another 7 parties ... MCP is going
@NgongireMwakasungula
@NgongireMwakasungula 2 дня назад
Ankanena fertilizer tizasisa ali pa 40000 pano ali pa 125000 chi president chuzungulira mutu ichi atilanga ife alimi osati masewera
@Dellingsmunthali
@Dellingsmunthali 2 дня назад
Miseu mkunena mesa timaona alemba china chani kaya"ndarazo sizawo
@KikaGray
@KikaGray 2 дня назад
Boma lapita ili MCP palibe angazaivotere olo zitavuta maka ndipo sizizatheka
@JohnAmanu-p5d
@JohnAmanu-p5d 2 дня назад
Chakwera ndi anthu ake mitu sikugwira nditu big
@SaidiMtira
@SaidiMtira 3 дня назад
Komatu chakwera ndi bale wanu, m'chimwene wanu weniweni. Musavere manong'onong'o. Asatana. Ameneyo ndidani wanu owonekera. Muzilankhura moganizirana
@AmosScott-z9x
@AmosScott-z9x 2 дня назад
Mwayankhula chilungamo man zamphamvu hope kumkuyu ndi chimwendo uthenga wamufika
@AdaMussah
@AdaMussah 2 дня назад
Zoona mwauze anvesetse
@YusufuChalamanda
@YusufuChalamanda 2 дня назад
Kumeneko kumeneko ndiye kuankhula komwe a Malawi akufuna
@NewtonTembo-q4t
@NewtonTembo-q4t 2 дня назад
Kuyakhula kumeneko ulemu wanu
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 2 дня назад
Chakwera chinyini chamake
@YasenYasen-q9g
@YasenYasen-q9g 2 дня назад
❤❤❤❤utenga wabo
@JacksonMoyo-tm8dv
@JacksonMoyo-tm8dv 2 дня назад
People are starving
@KikaGray
@KikaGray 2 дня назад
MCP yatha y
@GreyShadreck
@GreyShadreck 2 дня назад
❤❤❤
@aubreykamwendo4315
@aubreykamwendo4315 2 дня назад
Komaso atakhoza zithu nothing can change anthu awawa aononga just imagine soya pieces anali 70k panopa 450
@FunnyKalimwayi
@FunnyKalimwayi 2 дня назад
panya pawo awa azambili siziwa
@ChiyanjanoKuwani
@ChiyanjanoKuwani 2 дня назад
Wamveka big
@RoseKapalamula
@RoseKapalamula 3 дня назад
Awuuuze amvesese
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson 2 дня назад
Choyamba mukadakwanitsa kuthana ndi njala kenaka miseu yanuyo ,tikukamba izi chifukwa anthu ambili amakhala ku mudzi omwe amadalira ulimi kuti apeze chakudya, koma inu mukut mwapanga chitukuko chamiseu pomwe anthu akuvutika ndi njila chakudya chakwela, feteleza wakwela izi ndizomwe anthu mamiliyoni okhala kumuzi omwe amukupangitsan kut mukhale pomwe mulilipo amazidalira ,zakutuni kut kuli maloboti kaya kuli bulinji la mwamba alibe nazo ntchito bola iwo akhute so that's why bingu adaika ndondomeko ya chakudya pa tsogolo zina pambuyo ...
@mabvutomichaelpanagona1949
@mabvutomichaelpanagona1949 3 дня назад
Koma mwayankhula mau ogwira mtima zikomo kwambiri
@NewtonTembo-q4t
@NewtonTembo-q4t 2 дня назад
Ulemu wanu akulu
@SymonMwingitsa
@SymonMwingitsa 2 дня назад
Kulakhula kwa mzeru zayekha umawoneka ngati wamzeru kuchita bwino kumayambila patali chakwela sakufuna voti chifukwa chamsewu kapena chimanga iye akupanga zokomza dziko la malawi
@HerbertTchautchau
@HerbertTchautchau 2 дня назад
Ngatitu akumva pamenepo kmuyu ndfiti basi
@SymonMawaya-b6o
@SymonMawaya-b6o 2 дня назад
Owazungulira omwe akudya nao bwino akuwanamiza achakwera kuti bwana mukuyendetsa bwino zinthu onse akukukondani, ndipo mmalawi mmene zinthu zilili akumamuti ndiwa DPP Kapena otsutsa boma ,kunena zoona a Malawi akubvutika
@ClementsKamanga
@ClementsKamanga 2 дня назад
Zoona manganya zot adatuluka ku utm tidadziwa kalekale sitingamuvotele or pang'ono
@LafickDickson
@LafickDickson День назад
Kkkkkk
@Samson-ve5rs
@Samson-ve5rs 2 дня назад
Wayankhula bwino kwambiri
@ThembaniJikah
@ThembaniJikah 2 дня назад
Ndipo zosatHeka😂😂
@MayesoBikefa
@MayesoBikefa 2 дня назад
Mau amenewo pa ground sipali bwino
@HildaSingin-vm2tr
@HildaSingin-vm2tr 2 дня назад
Dpp🎉🎉🎉🎉 bas awatso palibe kukhoza aliphela basi
@TimothyNkhutembaChirwa
@TimothyNkhutembaChirwa 3 дня назад
Tavulala A Malawi kwambila kuba to much Mcp
@ChibakuliKaisi-cm3hn
@ChibakuliKaisi-cm3hn 2 дня назад
Dpp boma
@ClementsKamanga
@ClementsKamanga 2 дня назад
Zoona auzen mwina akumva
@MiddayDeleza
@MiddayDeleza 2 дня назад
Kodi boma la mcp lidzafunanso anthu akumudzi kuti adzawambvotere? Fetereza, kudya chitedze eishhhhhh manyazi akugwireni ndithu
@FunnyKalimwayi
@FunnyKalimwayi 2 дня назад
chikhalidwe chonpha athu
@BrazioNtondo
@BrazioNtondo 2 дня назад
Komatu munthu uyuyu, akuyankhula chilungamo akuluakulu.Mutatenga malangizo awawa Zitha kukuthandizani achina Kunkuyu
@JosephChatha
@JosephChatha 2 дня назад
Voice
@Eric-gb9ms
@Eric-gb9ms 2 дня назад
Zoona big mukunenedzo
@HevenChiwaya
@HevenChiwaya 2 дня назад
Akunamiza ndi Chimwendoyo
@RaffickAllie
@RaffickAllie 2 дня назад
Tangopereka # ya mpamba or Airtel Dollars.warankhura zibambo uyu guys
@samdiverson9733
@samdiverson9733 2 дня назад
Ndipo uyu awona saona vote oloko imodzi
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 дня назад
Boma ili kuba ndi kupha basi ndi chomwe akuziwa
@WilliamNhlane-fd9hi
@WilliamNhlane-fd9hi 3 дня назад
Anthu wozungulira mutu kuti boma ndilomweli 😅
@SliviaJosephy
@SliviaJosephy 2 дня назад
Kwanuko ndilomweli but me no DPP boma
@Alice-z7t4z
@Alice-z7t4z 2 дня назад
Akulu mwayankhula zoona ndithu fundo zabwino
@CorneliusSande
@CorneliusSande 2 дня назад
Boma amayendetsa bwino ndionerera ngati Inu talowani inuyo osamabwebweta apa.
@DEXSTALLONEKAWAMA-s4g
@DEXSTALLONEKAWAMA-s4g 2 дня назад
Ulibe zelu mbale wanga
@AnitaLikado
@AnitaLikado 2 дня назад
Iweyo plus amako
@GeraldMkwewu-gd5eb
@GeraldMkwewu-gd5eb 3 дня назад
Umakwana bg man zoona zake osamubisa chikangawa
@MchachaGoodson
@MchachaGoodson 2 дня назад
Akamuna chilungumo chimamasula awuzeni.
@RoseThindwa
@RoseThindwa 3 дня назад
Zoona n boma ili likuononga dollar kugula anthu ,kuba Malo mopanga fix mavuto ochuluka mdziko lathu
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 2 дня назад
Ndipo live mawu abwino awa
@DixonChimanya
@DixonChimanya 3 дня назад
Uthenga wabwino kwambiri Anthu akumudzi pali pamavuto kwambiri
@PortiaDaveson-f8u
@PortiaDaveson-f8u 3 дня назад
Awa akunama kwambili amalawi akumaona
@ISMAELNKWATULANKWATULA
@ISMAELNKWATULANKWATULA 2 дня назад
Koma munthu uyu wayakhula bwino kwambiri inu ndiye tikuyendera limozi
@EvasiJafali
@EvasiJafali 3 дня назад
Ausilu ameyo sakusiwa chimene akupanga
Далее
Ubale Wa Timothy Mtambo Ndi Dpp... Watutumusa Gulu
6:23
ANA A KUMPANDA - Pastor Frackson Kuyama
26:40
Просмотров 14 тыс.
BON KALINDO 22 OCTOBER 2024 KUNG’ALURA PA TUESDAY
16:51