Тёмный

Chakwera V Mutharika: 2025 Kuli Gule - Redson Munlo 

Nyasa VoiceBox
Подписаться 27 тыс.
Просмотров 10 тыс.
50% 1

On Nyasa VoiceBox, Redson Munlo asserts that His Excellency President Dr. Lazarus Chakwera faces no competition heading into the 2025 election. Tune in to hear his reasons.
Pa Nyasa VoiceBox, Redson Munlo wanenetsa kuti Pulezidenti Lazarus Chakwera sakumana ndi mpikisano pa chisankho cha 2025. Yang'anani kuti mumve zifukwa zake.
#malawi

Опубликовано:

 

13 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 303   
@JonathanMsiska
@JonathanMsiska 23 дня назад
Saulos Chilima ndiamene azawinise Peter Mutharika mawu anga sapita pachabe.
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 23 дня назад
Mesa chakwera ndamene Ali muboma chifukwa chan chilima yemweyo munamupha agalu inu
@ChrispineJonathan
@ChrispineJonathan 23 дня назад
Kuvotela chakwel ndichimodzimodzi kutseka kobibila mkumabibila kukamwa amuthalika my vote
@isaacchiwaula731
@isaacchiwaula731 23 дня назад
Ndie akutukwana kwake kumeneku nkumati inuyo mungadzalamulire kopanda tsankho? Alomwe inu!!
@garnetphiri
@garnetphiri 23 дня назад
Kkk ok kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkokkkkkkkkkkkkkkkkkk ok kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkokkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkokkkkkkkkkkkkkkkkkk kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
@AgnesMatola
@AgnesMatola 22 дня назад
Mbava za MCP izi
@AgnesMatola
@AgnesMatola 22 дня назад
Mwawononga dziko A galu inu 😢
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 21 день назад
@@isaacchiwaula731pamtumbo pako iwe ndiChakwera wakoyo chitsiru iwe
@Blessings-b7h
@Blessings-b7h 23 дня назад
Zoonadi kuti muthalika ndi Chakwera ndizosiyana chifukwa choti Chakwera ndi wakupha.
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 23 дня назад
Zoonadi ndi wakupha
@amosnyirenda-pl1ss
@amosnyirenda-pl1ss 22 дня назад
anapha bombo ako kape iwe mzazvutika nayo dpp yanuyo
@user-un6qv6sj3h
@user-un6qv6sj3h 22 дня назад
​@@amosnyirenda-pl1ssadapha chilima
@ellennchambalinja484
@ellennchambalinja484 21 день назад
Chilima rest in peace my dear
@DanNzima
@DanNzima 23 дня назад
APM my vote
@PollyLysonLutepo
@PollyLysonLutepo 23 дня назад
Popeza kuti makutu amamva chilichonse. Ndicho chifukwa timamva nkhani za m'nulo. Ine kuti ndidziwe kuipa kwa chakwera ndi mcp ndi m'nulo ndi ben longwe. Pachifukwa ichi ndikuti dzikomo a m'nulo. Ndalama yagwiladi ntchito pa anthu awiliwa..
@JoshuaMbewe-ff5mk
@JoshuaMbewe-ff5mk 23 дня назад
Iwe Redson mapwala ako a bambo ako mayi ako a village anu ndi mudzi wakwanu onse machende anu
@user-vz6lk1lc7s
@user-vz6lk1lc7s 23 дня назад
Pepani amwene chitsiru chili ndi mwini
@user-ww9rj2wx8d
@user-ww9rj2wx8d 23 дня назад
Machende ako plus mbolo yako yosadulayo wamva usalimbane ndi DPP wamva ife tinakutuluka kale kale ndipotu sitimakusowa gwape
@YellowmanMalawi-qe8zh
@YellowmanMalawi-qe8zh 23 дня назад
Poti anakupasa money,yang'ana ma comment a wanthu ngati mcp izawine kuposela kubera
@JuniorJone-v1g
@JuniorJone-v1g 23 дня назад
amutharika my vote 🇲🇼🇲🇼
@MercyNkhoma-b6h
@MercyNkhoma-b6h 23 дня назад
Koma a Munlo afikapo, umphawi wakukhadzulani achimwene. Mavuto amamupeperetsa munthu.
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 23 дня назад
Eyaa uphawi sizinthu ndaonera munulo
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 23 дня назад
Kodi mumafusilaji kuti chakwela ndi apm iwe redson uzagovotela chakwela koma ine wanga ndi madala APM
@HappyAbyssinianCat-xt2bm
@HappyAbyssinianCat-xt2bm 23 дня назад
Iweyo ndwe kape olo atapanda kugona km ndi wakhupha peter ndamene tikumufuna ife atiphure pamoto akuphawo sitikuwafuna anamupha chilima anthu oyipa iwe munulo machende ako wamva
@MaxwellMbesa
@MaxwellMbesa 23 дня назад
Sitikuvotera zaka koma kuthekera kwa munthu iweyo khara ndi mcp chikangawayo
@UseniMailosi
@UseniMailosi 23 дня назад
Ife tinavotera chakwela koma pono sindingakufotere
@ChrispineJonathan
@ChrispineJonathan 23 дня назад
Utafe ndiwe palibeso Cha zelu ukulankhula kapena iwe
@user-jb5yb9wq3y
@user-jb5yb9wq3y 23 дня назад
Kape iwe anaukugula ndalama zingati? Kape
@Drmuhammadchiwona
@Drmuhammadchiwona 23 дня назад
Gwape uyu
@eddiesilika618
@eddiesilika618 23 дня назад
Thawi zina ndibwino kukhala tchete ngati ulibechonena chazelu,chakuti chako buzi,ingodikila uwone angagwele Lazalo wakoyo
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 21 день назад
Muthu kulephela ivini kutsekela nsokhano wake wa conversation ndeno angakhale president wadziko,,,kulifunila dziko la Malawi ubwino aii guys khalani Sirius plz
@DanielDoctor-t3p
@DanielDoctor-t3p 23 дня назад
Iweyo nzeru ulibe nkhani ndiyoti Anthu atopa ndi mr chikangawa mukamalankhula muziganiza wava iweyo garu
@JusticeKawilira
@JusticeKawilira 23 дня назад
Zoti MCP idzawina mukunamizana ku MCP komweko tapitani kumidziko mukamve maganizo a Malawi akumudzi APM my vote
@AdamNapwanga-ff2wm
@AdamNapwanga-ff2wm 23 дня назад
Gwape weni weni za ziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii8iiiii chule
@AbdulmalikAmanu
@AbdulmalikAmanu 23 дня назад
Yes is better kuvotela Peter muthalika ndikuvotera chikangawa bola Peter ntchivukwa chikangawa ndimunthu wakupa anamupa mzake chilima kuyiwalira kuti anamuwinisa bola Peter ngakalekuti ali wa mkulu is no problem
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 21 день назад
Munlo singing for his supper. Ndale zaku Bagamoyo adakonza.Maluzi amamusintha munthu.
@ThomasStephan-tg6ng
@ThomasStephan-tg6ng 23 дня назад
Iwe pachende pamako pamozi ndi chipaniakowo ndi chakwera wakoyo😊
@PlanzaWisiki-cv2fs
@PlanzaWisiki-cv2fs 23 дня назад
Mapwala ako amunulo
@pauljosephmakaula6835
@pauljosephmakaula6835 23 дня назад
Mudzadzimuka Mutharika asakuyima kutabwera mnyamata wa Economics...
@LehmanManere
@LehmanManere 21 день назад
Line up doesn't matter all we want is change and good governance
@LenardWillard96
@LenardWillard96 17 дней назад
The game is president muthalika he's ahero in Malawi Government for sure.MCP Government they know nothing more especially president.That's why muthalika's family we call them ngwazi.
@user-do2cs8nf4b
@user-do2cs8nf4b 14 дней назад
Amunilonso ndinu achitsiru mwasowa zokamba basi kulimbana ndi Dpp munya muwona mwayiwala kuti mumatulutsa ma audio anu womutukwana razalo, lero ndalama zafika pa inde Inde la 40 lidzakwana pangatalike Maka dpp woyeeeeee ❤❤❤❤❤❤❤ angasapote Mcp ndi mbuli wa mbuli zonse, chifukwa ngakhale mwana akudziwa kuti Mcp ndi chipani chokhetsa mwazi
@Georgemphamba-to1ik
@Georgemphamba-to1ik 15 дней назад
Che mmunlo mukuzinamiza nokha. Kodi ndi ndani amend Amati, Tamita mumsika wa Limbe ukanene kwacha kwacha ngati sugendedwa. Anthu adzasankha Poona mfundo ndi pa ground pali bwanji . iyi sinkhondo yomenyana ndi manja kuti ifuna mphamvu za thupi ayi. Usapeperetse a Malawi akuziwa omuvotera. Inuyo simungauze anthu chochita. Zidyani ndalamazo zikatha muzatipeza
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 22 дня назад
Umuze Chakwerayo akuyembekeza Ku ndende,ukuseka chapa Kati cha Mako,umuze Chakwerayo lipoti lachikangawa lituluke, Amalawi akufuna Wanthu amzeru achikondi Osati Okupha koma iweyo Panyero pa Mako
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v 22 дня назад
Mzanga iwe akutuma Chakwera kadya ndalama izo akupasa koma mawa uzalira
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 15 дней назад
Mankhwala a Redson munlo sangafike zaka za APM, Mayankhulidwe ake chinafa kale ichi
@hagayichiluwe
@hagayichiluwe 21 день назад
Munthu wazeru dziko lonse lapansi 🔥🔥🔥🔥🔥🔥💯
@SuzgoMkandawire-ss4kh
@SuzgoMkandawire-ss4kh 19 дней назад
Chikangawa party ndi yanzeru?
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 21 день назад
Kuvotela Peter Mutharika zili ngati muthu amene sakuona matso kapena tinene kuti wakhungu,,,,,taonani manja a Peter Mutharika akulephela olo kugwila bwino pepala basi muthu kumu ponyela vote zoona zimenezo,,,ngakhale zitavuta motani sindingavotele DPP.
@MussaZakeyu
@MussaZakeyu 23 дня назад
Ndilibe mawu ambili km wekha uone ma comet okhawa ndi mavoti kale 😂 ndiye uzikati chakwela awina 😂😂
@alfredhanleck9043
@alfredhanleck9043 17 дней назад
Mapazi ako iwe munlo, si iwe wemwe umkat pano sungapite munsika wa Lizulu ndikut kwachaaa ! Suyankhidwa
@user-ph3zy9ox7d
@user-ph3zy9ox7d 18 дней назад
Litembeleledwe thako la mzimayi anakankha chimutu chakocho ubongo wake osakanizana ndi mamina Dpp my vote
@rashidadan2533
@rashidadan2533 21 день назад
Musavutike ndi mtima , MCP palibenso kubwelela m'boma . Redson munlo alibe mzelu zotiuza amalawi
@michaeltchuwatchuwa5699
@michaeltchuwatchuwa5699 22 дня назад
You are very mad person my vote is going to dpp
@user-oq8js5fd6u
@user-oq8js5fd6u 21 день назад
Peter my vote
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 23 дня назад
Chakwera umkamutukwana za mkabudula ndi ben longwe wako uja lero mwakoma chakera woyee tione ngati anthu sakutibula mu msika achitsiru inu.
@JamesRoben-dy7bx
@JamesRoben-dy7bx 22 дня назад
Muthalika ndi chakwela sangafanane zoon muthalika alibe mbili yokuba kupha kuba nkhadza alibe muthalika koma chikangawawa mmm waonjeza kuba kupha khadza mmm ai chakwela mm out in Jesus name
@EvanMchere-qf8fs
@EvanMchere-qf8fs 23 дня назад
Chakwera ndi Munthalika ndizosiyana kumene chifukwa chakwera ndi mubusa or ndi church chomwe chinamumvuta kuyendetsa peter tu paja anali president tinaona kale ntchito zake inuyo ngati ali a mcp ndi zanu vote yamunthu imakhala mu mtima mukungomvutika ndikulakhula a mcp munadzipanga dekapeni nokha pomupha chilima,
@user-vg1lj5gs4z
@user-vg1lj5gs4z 23 дня назад
Nthawitu yotsata anthu inatha ,ife tikufuna tidziwe za SKC ,campaign ya Peter anapanga kale a Chakwela tsiku lomwe SKC anamwalila lija okey
@user-rk3jx3kg8i
@user-rk3jx3kg8i 18 дней назад
Maphala Ako iwe, chikangawa sangawine, zingodyani ndalama zamishoko ya Malawi
@DanielChisaka-tg1il
@DanielChisaka-tg1il 21 день назад
Iwe redson Kaya ukufuna chakwela akupaseni ndalama zina wauponda DPP ikuwina ndipo uzathawa Malawi iwe chifukwa cha manyazi
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 21 день назад
DPP ayiiiii plz a Malawi,,mudzakulukuta manoooo
@user-pf5hu2pd2b
@user-pf5hu2pd2b 23 дня назад
Iwe ndi mphake wa chikangawa machende ako ndithu iweyo ndi bambo Ako achikangawa mudzalakalaka kulowa pansi pa nthaka palibe angadzavotele MCP ndipo mudzakhawula ndithu mudziwudzana ndi nzako Ben Longwe wakoyo anthu oputsa ngati inuyo dzipumi ngati akwiri .
@WonganiKatchale
@WonganiKatchale 22 дня назад
Auzeni akuzinamiza
@SuzgoMkandawire-ss4kh
@SuzgoMkandawire-ss4kh 19 дней назад
Chikangawa party
@ebenezerkamanga6016
@ebenezerkamanga6016 22 дня назад
Ndi chifukwa munamupha kuona ngat mutenga ma vote awo unya ovota ndife si iwe ndi kabwira wakoyo
@wisdomchilanga723
@wisdomchilanga723 23 дня назад
Koma DPP chilowereni muboma ma vice sanaphedwepo ndimumozi yemwe. Koma MCP kwawo ndikupha,Kuba, maboza,kaduka,Njala, Corona, sankho koma mwalipha dziko ndinu you will never wine
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 21 день назад
Awudzeni mwina akhodza kunva,,,,ngati sakunva asiyeni akwele yakubwa tayala,,,, ubwino wake kaya afune kaya asafune chakwela akupitilidza kulamulila malawi,,, uthenga ndi umenewo.
@StephanoMaganizo
@StephanoMaganizo 15 дней назад
Umbuli umenewo kuphuzira sindiye kuti ndiwe wanzeru zedi nkhani ndi thinking mbuzi iwee
@AndersonChiponola
@AndersonChiponola 18 дней назад
Redson Mutu wako sumayenda bwino kagone ngati wankhuta mbewa
@GiftChitsulo
@GiftChitsulo 23 дня назад
Iwe ASE ndikukulonjeza ngati suganiza bwino kuchipani chako cha MCP Cho sungawineso kwanuko pa mp
@user-mt1su7li6z
@user-mt1su7li6z 22 дня назад
Chakwera ndiwoipa kwambiri okudya Matewera
@IsmailTambula
@IsmailTambula 23 дня назад
Ulibe kuganiza mulo chikwa ngat ndawi ya mutalika timagula chimanga 7 yachakwela 50'000 zikutsiyana kwambir ndiye aliyese akufuna kugula dzindu mochipa komaso chakwela pemene anazitembelela yeka powasiya anthu 9 kichikangawa paka mawa kwiyo waanthu ulipamenepaja kuluza kulipo muzingozipasa minyama komaso munthu amene amatukwanidwa amawa ukapemba chele komweko ndipo mutalika ukamamutukwana mukumupasa mwayi omwina ndipo mulungu mwin kusoza ozikweza ngat inu
@MussahBamusi
@MussahBamusi 21 день назад
Ukunama munlo chakwera ikamazakwana 11koloko usiku achakwera titayezeka ndipo amunlo ndi opepela
@KnowledgecGodwin-xo4pw
@KnowledgecGodwin-xo4pw 23 дня назад
Tangonenani kuti ndalama zatha akupaseni zina Achisiru anxanuwo, amasikini inu.
@SuzgoMkandawire-ss4kh
@SuzgoMkandawire-ss4kh 19 дней назад
Redson machende ako pamoz ndi chikangawa party
@kingstonekalonga8435
@kingstonekalonga8435 23 дня назад
Aise mapwala ako aise ndiwe wakumba akufuna akutame achakwera akupase ndalama panyopako aise akukuyo machende aka achakwera machende aka iweso manyi
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 23 дня назад
Kunena zoona malawi ikanakhala ndi añthu oganiza ngati anthu akumupotò bwezi andalewa akawona polekela chifukwa anthu akumupoto safuna zibwqna akafuse Aford alibe nayo ntchito 2025 akumupoto alibe chipani choti achivotele kufa kwa chilima ku mpoto basi kuvota kulibe
@IvyMkhura
@IvyMkhura 21 день назад
Ukuti line up ya mcp ilibwino, azavote ndi achina Jessie Kabwira akowo? Ovotati ndi amphawi amene ali mmidzi, amene akuzunzika ndi njala mmidzimu. Mbuzi yopanda mzeru iwe.
@user-lj7lm6ly7z
@user-lj7lm6ly7z 22 дня назад
Mwina mudzachite kuberatu koma paulere ndakaika,APM my vote
@EmmanuelSambani
@EmmanuelSambani 15 дней назад
Ndimaona ngati uyakhula za nzeru koma popeza maloto salesana
@SymonNamalomba-sh3fu
@SymonNamalomba-sh3fu 21 день назад
Iweyo wabwerA ngati wa MCp ndipo ukuwauza ma members a MCP not amalawi
@user-hk4sp5tp9g
@user-hk4sp5tp9g 21 день назад
Achakwera akupanga chani lwe munlo
@anusahjenala1063
@anusahjenala1063 23 дня назад
My vote is munthalika
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 21 день назад
Iwe amene amakuvela ndizitsiru pamtumbo pako munlo
@JamesRoben-dy7bx
@JamesRoben-dy7bx 22 дня назад
Fuso ndilakut akufuna chakwela kut atan walephela wagwesa kwacha wapha athu oziwa ndiye akufuna atan plz chakwela sazawinaso olo half
@ErnestChansa
@ErnestChansa 23 дня назад
Chakwela ndi kumataku iwe ndiwe wa MCP ponyelela pako Inu a MCP ndinu akupha anthu ponyelela pako ayise chisiru iwe zolakhula thawi yina uzakhumudwa
@MaryNgwira-s5z
@MaryNgwira-s5z 21 день назад
Dpp my vote
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 21 день назад
Olo kumwa katchatsoyo ku votela DPP basi muthu kukhala pa line yovota uku votela DPP
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 23 дня назад
Iwe mumlo udzingodya ndalama akupatsazo,,APM akadzawina tisadzakuone uli khwekhwere kisendera konko
@ellennchambalinja484
@ellennchambalinja484 21 день назад
Chilima rest in peace 😢
@user-gx8or3yz9u
@user-gx8or3yz9u 23 дня назад
Ifetu tikudziwa kuti adad akula koma chikuni chachikulu chimasunga moto ife sitikufuna anyamatayi adad akulowanso mmboma ndipo mudzalakalaka kulowa pansi chifukwa chamanyazi
@MathiasVictorBanda
@MathiasVictorBanda 23 дня назад
DPP oro itakhara osapanga kampeni ndiyowina kare,anthu akudzwa ndipo akuona okha mmene Dziko likuyendera
@MathewsEnamu
@MathewsEnamu 21 день назад
Zopusa bc inu mmene yachitira 5 years yawot angazagonjetse alliance DPP, UDF, UTM , AFORD eee? Mwayamba chibwana tisiya kukutsatan
@IvyMkhura
@IvyMkhura 21 день назад
Kodi inuyo kupanda Chilima mukanatenga boma? Ndye uchitsiru wake mukukaphanso munthu amene anakuikani pa pando, palibe amene angavotere chipani cha magazi, muyambe kupakira ku State house ko.
@AdamAhamad-k2i
@AdamAhamad-k2i 23 дня назад
Line up ilibe ntchito nkhani ndiyoti ndianthu angati amene akumufuna chikangawa munthu okupha
@user-sf7sd1hb4g
@user-sf7sd1hb4g 23 дня назад
Kodi Mesa iwe umati wasiya zolankhula ifetu sitiyiwala komanso sife opusa
@Edoliwonde
@Edoliwonde 23 дня назад
Umphawi cwaabwino otherwise tingocya kukukhulupiliran agalu inu kuyakhulana konseko mumafna dollar
@SmarshChikwanah
@SmarshChikwanah 23 дня назад
Achisiru inu
@user-db3mh9wr9v
@user-db3mh9wr9v 23 дня назад
MCP inazichita decampain pamene adapha Chilima anazionongera mbiri Chikangawa party musazivute A munlo ingokhalani chete
@PaulMwachande
@PaulMwachande 23 дня назад
OPOILA IWE BWANJI OSANGODIKILA CHISANKHO CHICHITIKE BWANJI UZIPANGA ZAKO NDI CHIKANGAWA WAKOYO TIONESANA 2025 ASE MUGWA CHAGADA INU
@ChristophrMaiko
@ChristophrMaiko 22 дня назад
Koma ameneyi ali ndi azibaleako ku malawiko chifukwa anakati azimuzuzula pazomwe akuyankhulazi vuto azingozitukanisa komanso azibaleakewo pamozi ndi ana ake samapasidwa ulemu mr mulo zisiyeni izi taonani mmene mwatukwanilidwa mmmmm ai ndithu
@user-vg1lj5gs4z
@user-vg1lj5gs4z 23 дня назад
Mavoti akubwelawa anthu adzafuna kudziwa chomwe chinapha aChilima ,choncho olo popanda campaign anthu sangavotele aChakwela ayi ,coz ife tikufuna tidziwe choonadi
@KenChitete-pg3ws
@KenChitete-pg3ws 21 день назад
Awooo asiyeni awine pa FB
@ChristophrMaiko
@ChristophrMaiko 22 дня назад
ulibe ndundo galu iwe inatha kale basi zinakuvuta iwe mutharika 2025 boma
@dondamissonchdziwe3958
@dondamissonchdziwe3958 22 дня назад
Iweyo munlo Ndi MCP yakoyo mazinyini,manyero azimai wanu,ukuona ngati Wanthu akui wonera MCP kukondwa Wanthu adafa Ku Chikangawa aja ukuwona ngati zinali mbuzi, Panyero pa Mako wamva Mavudzi Ambuye wako mbolo yaifupiyo mkazi wako Ndi amene ama kuwulura akamachindidwa kunja machende ataliwo,usaza yankhulenso zovunda, Chakwerayo nyero ya mache adapha Chilima ankhandwe Inu Mimbulu matuvi anu muzafanso nyini za makolo anu
@IsmailTambula
@IsmailTambula 23 дня назад
NDipo chisiz chamulungu mozachiona siku lovota ngat mulungu anamuika pamenepaja zinsovuta kumuchoza munthu ozikweza ngat boma limeneli mwin chison alinsoza muzakayikeso
@user-sf7sd1hb4g
@user-sf7sd1hb4g 22 дня назад
Iwe umaonangati ochenjela kodi school inakupangila chani iwe umangoti unaphuzila munthu osowa zochita ngati iwe
@ClaudinaAugustoAugusto
@ClaudinaAugustoAugusto 20 дней назад
Koma siwewemwe umabwela pano Kumatukwana mcp?? Pano chifukwa adakupatsa ndalama kumabwela kumankhula zopudazo ulibe manyazi kupepela kwenikweni kupusa uchitsilu mulibe manyazi komaso umunthu iweyo ndi Ben longwe abakha mbuzi
@MathewsChitsulo
@MathewsChitsulo 22 дня назад
Akulu Inu ndi wopusa kwambiri mulibe nzelu akukutumani ndi atsilu pitani mukayambileso. Mbudzi ukuyinenayo chakwela alive ndi mzeru zomwe ungayelekedze ndi anthu ena? Ndichifukwachake akungopha athu amene akuoneka anzelu
@Bernardwisck
@Bernardwisck 23 дня назад
A red many munlo pa mtumbo panu mudyeretu mbuzi ya munthu
@KondwaniNguleti-x1q
@KondwaniNguleti-x1q 22 дня назад
Iwe Munlo panyapako palibe chomwe ukudziwa
@user-lw4hw9ce4w
@user-lw4hw9ce4w 23 дня назад
Kodi achisiru inu ìfe owina n APM muzanyera limodzi n mbuzi zinzakozo
@EmmyYafete
@EmmyYafete 21 день назад
iweyo ndiwechitsilu sunganiza,mbuzi iwe, munthalika boma 2025
Далее
Chakwera Vs Mutharika: Osewa Ndi Olephela - Mr Bura
11:54
REPORT LA NDEGE LIJA MU CHICHEWA CHOMVEKA BWINO
2:18:14
Exclusive Interview with Reverend Alexander Kambiri
30:56