Тёмный

CRUISE 5 WITH GEORGE KALICHELO - Inventor 

Joab Frank Chakhaza
Подписаться 66 тыс.
Просмотров 21 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

25 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 43   
@josephkuleti1548
@josephkuleti1548 Год назад
even kuyankhula kwake so gentle mwanayu ndiwanzeru & he looks so humble may Good Lord bless you George Kalichero
@giftmlangeni8350
@giftmlangeni8350 2 года назад
Big up, this is hidden wisdom and this man needs support on his effort.
@patrickmuliya2736
@patrickmuliya2736 2 года назад
1 year down the line. How have we utilized this rare gem? Guy is a genius. We're sleeping on this unutilized talent.
@josephphiri519
@josephphiri519 3 года назад
Nde Mwati kalichangu amakwana encourage this young boy
@selinamvula1350
@selinamvula1350 3 года назад
This is truly development for the community. He needs support.🙏
@ibrahimmtotomeka
@ibrahimmtotomeka 3 года назад
Congratulations to this brother, m'bale ameneyi zingakhale bwino atapitilizadi maphunziro pamapetoko pake ndi kuchita ubale ndi anthu a business amene angamuthandize kumapanga zinthu zoti akhoza kumagulitsa kwa anthu ambiri. Popanda kuchita business sangapindule, koma kuti adalile boma kapena mabungwe azangochidwa, ama bungwe ndi a boma amangochedwetsa munthu ndi ma paperwork basi. #wesupport you bro.
@retsobanda7807
@retsobanda7807 2 года назад
This is awesome long liveee George Kalichelo
@ririvilla1423
@ririvilla1423 3 года назад
William kamkwamba made it mpaka movie was made in USA atapanga windmill this guy needs help a Tonse Alliance mumuthandize mnyamata yu. He is gifted
@rossbank7248
@rossbank7248 3 года назад
He even married black American and he'graduated in university in U.S.
@promisemakawa1556
@promisemakawa1556 3 года назад
Uli bhoo mfana. We r proud of u. Mwina zozimazima magetsi zingakhale history
@chrisozil5723
@chrisozil5723 3 года назад
Joab mwanayo Alindi luso tisanve kuti mwanayo luso lija lafa ai remember mbuyomu alipo anazapangapo airplane koma boma linakaniza kuyesa kumati ipha anthu ndiye timadandaula kwambili tili ndiana aluso koma boma limapondeleza so uku ndi kumulanje mwapitaku sizopondelezana ai Big up George
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 2 года назад
He is talented, Ambuye akuona kuti luso lako lipite patali.
@amonbanda6977
@amonbanda6977 3 года назад
Dude is genius all he need is our support...
@lamackbanda6869
@lamackbanda6869 3 года назад
Nkhani yayikulu ngati ife anthu okuda osati a Malawi okha ayi koma tonsefe ndi kufooketsana kupanda sapoti kwa mzathu. Chifukwatu zinthu zina ukaziyamba ndikupezeka okulimbikitsa umakala ndimphavu. Chitsazo mphaulayi ndi yabwino koma ikutsowekela mzelu pang'ono kuti itsamagwe, ndizina zambiri koma zimene zili zofunika. Koma wina aliyetse akabwela ndikuona azipeleka maganizo ake koma nthawi zonse timafuna mzathu alephele tizimunena. Nthawi zonse tikamapeleka maganizo chofunika kuchita umusapote kumuyamikila pantchito yakeyo, ndiye tizipeleka maganizo athu osafika ngati ndiwe oziwa sizofunika. Ndikukupempatso Joabu muyamikile Munthu komatso ngati uli ayidiya inayake upatse ndikumulimbikitsa mokoma. Ndimakunyadila kwambiri ❤❤❤
@caletian
@caletian 3 года назад
this interview is one of the many interviews made with him. I started seeing him kali kamwana than now koma he is still a village champion mpaka lero. Why Malawi
@akonligomeka9869
@akonligomeka9869 2 года назад
The fact that ukutafuna nandolo, just like Ntedza, wow I never knew kut nandolo amatafunidwa uncooked
@dannymangawa7511
@dannymangawa7511 3 года назад
Good initiative, this boy just needs support so that he can improve
@cedrickpatrick4852
@cedrickpatrick4852 3 года назад
Wow Interesting, Joab #thebest
@stanleymlenga8606
@stanleymlenga8606 Год назад
Bwana Joab, what was the aftermath of Mr George. Where is he now?
@rafickcpaul3659
@rafickcpaul3659 3 года назад
NUMBER ONE JOAB 100% UMATIMVESA KUKOMA
@josephchisomo7450
@josephchisomo7450 3 года назад
Fantastic joab
@m.ak.a8401
@m.ak.a8401 3 года назад
Luso lilipo koma dziko lakelo mmmm zithera pompa ,akanakhala maiko ena amenneyo bwezi atalemera
@jamesmark9298
@jamesmark9298 2 года назад
Joab i love your work , but can you please try to approach the government and ask them why we keep on wasting our own talent ? it was like the same with Kankwamba till the Americans saw his talent and gave him opportunity now maybe he might not come back to Malawi again. we should not repeat the same mistakes with this guy. we are talking about climate change and green energy this guy is a national assets but its up to the government to believe in our talent, if we send this guy to school and upgrade his knowledge its the National that will benefit from this. Government please help this guy
@yamikanimdala5955
@yamikanimdala5955 3 года назад
Hahahahahah George kali changu ndi genius.... Bigup uncle Joab mumatha zinthu
@estonmnthali3719
@estonmnthali3719 2 года назад
Kkkkkkkkkk kalichangu wakwana
@osamabinraden9391
@osamabinraden9391 3 года назад
😁😁😁😁Koma Frank ndiwe wachimbwana😁😁😁😁😁
@lamackbanda6869
@lamackbanda6869 3 года назад
Komatso unacheza ndi aku MRA zinatha bwanji? Ndinaonela yoyambilira yoka ndinkhani zofunika kwambiri kuzidziwa zilipati tiponyeni
@medsonboti1984
@medsonboti1984 3 года назад
Kudya Nandolo wamuwisi Joab.
@osamabinraden9391
@osamabinraden9391 3 года назад
CRUISE 5 💪💪👊
@emmanuelmhango5655
@emmanuelmhango5655 3 года назад
Mr joab ulemu wanu
@chrisbanda8520
@chrisbanda8520 3 года назад
Good job bro komabe I don't get it pa mbaulayo kut pali connection lanji nkhuni ndi mota ilikupasiyo I'm still confused coz moto ukayaka ikuyenera kutetha beside those motors 🙆🏻‍♀️☺
@joabfrankchakhaza
@joabfrankchakhaza 3 года назад
Akuti they are used to fan the flames. So you can use it to increase or decrease heat.
@chrisbanda8520
@chrisbanda8520 3 года назад
@@joabfrankchakhaza okay chabwino ndimaganiza kut kuchepa or kuchuluka kwa nkhuni ndikumene kungapangitse heat kuchepa or kuchuluka mu Kachangu wakeyo kkk anyway he talented ife sitingakwanitse🙏
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 3 года назад
Kodi mumadya nandolo wauwisi? Saladi wachigwada mumadyanso?
@chigomileiichannel3717
@chigomileiichannel3717 3 года назад
Nice
@fulachisisili6186
@fulachisisili6186 3 года назад
The boy just need some advice and support.. Otherwise to use a electricity to power mbaula and kugwiritsa ntchito nkhuni.. not a good idea.. Maybe magesiwo tizingogwirisa ntchito to power a stove, ti saver nkhalango..
@shareefchimbali765
@shareefchimbali765 3 года назад
Munthuyi boma limupase support apitilize ma phunziro ake
@nkhwalamkwala6483
@nkhwalamkwala6483 2 года назад
Kuno Ku Malawi anthu alipo ndithu
@issahsabitilawey2091
@issahsabitilawey2091 3 года назад
Kkkkkkk kali changu kufoka kugwa poto palibe
@nyanguoipa6996
@nyanguoipa6996 3 года назад
ZAbwino zonse nyamata pitiliza ntchito zamanja ako
@charliealieck6490
@charliealieck6490 3 года назад
Koma ndi chamba chimene ukuchita apa chi😅😅😅
@bsowani5645
@bsowani5645 3 года назад
Nandoro ndi Makaka 🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@franciscofranciscojose696
@franciscofranciscojose696 2 года назад
🇲🇿🇲🇿🇲🇿
Далее
CRUISE 5 WITH SPY CHESA - THE SNAKE SELLER
1:00:23
Просмотров 82 тыс.
Cruise 5 with Moses Mwalabu   Former Street Kid Part 2
48:39
CRUISE 5 FRANK WASHON - BANANA FARMER
1:09:35
Просмотров 18 тыс.
CRUISE 5 WITH RASTA GALAWANDA   KAWALE NYABHINGHI   PART 1
46:20
The 21st century | An age of Creation and imagination
17:04
CRUISE 5 WITH ALLELUYA BAND
1:17:41
Просмотров 17 тыс.
CRUISE 5 WITH CONSTABLE HAMID VASCO 8 OCTOBER 2023
1:14:55
Cruise 5 with Joshua Chisa Mbele
51:40
Просмотров 30 тыс.
CRUSIE 5 WITH CHIMWEMWE MWENYEMASI
1:34:40
Просмотров 21 тыс.
EXCLUSIVE INTERVIEW WITH SIMBI PHIRI ON ZODIAK TV
1:27:07