Ndizakhala osangalara ndikazakugwira panopa ndinawe busy kukufuna funa iwe I will do nkhondo ya golira basi, mulungu akandilange because of you mfiti wamunthu iwe. Ndipanga chothekela until to hunting you kuti mtundu wanga udzakhale osangalara tsiku lina
Munthu oipa iwe kugulisa dziko la Malawi kwa munthu oipa wa ku pha alubino ,mukungu adzaimba nawe mulandu chilungamo ukuchidziwa idya ndalama koma ulube mtendere kutsongoloku
Iwe ma xool onse washula wa.chizungu chake chimenechi. ndi chimene wumayakhula kuma court .tapanga copy chizungu chanyamatayo.iwe ndi mbutuma et osamangoyakha chichewa bwanji. Chimene umatha ndi kuba basi. ndi kuyakhula chizungu cha ku gahna cho basi.oyipa iwe