Тёмный

Dalitso Kabambe wagulidwa ndi MCP. Dan lu wapasidwa 500Million. MCP yagawa mfuti 

Jay Kawere TV
Подписаться 21 тыс.
Просмотров 29 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

21 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 137   
@PatrickMakina-c2w
@PatrickMakina-c2w 3 дня назад
Mr Ntanyiwa! Yes we might blame opposition parties pazomwe zkuchitikaz but on other side we might also blame ourselves as a malawians pomangotengeka ndzlizonse. Who changed the government is it APM or a Malawi? If yankho yake ili yot a Malawi ndamene anasintha government, so why we are busy now blaming APM kut akungoyang'anila? Kodi Mesa ndtomwefe amene tinkamunyoza APM akutiuza ife kut tisayelekeze kusintha boma koma ifeyo kusanva. Lelo akuvutika ndndan pakat pa APM nd ifeyo?
@ChifuniroInnocent
@ChifuniroInnocent 2 дня назад
Penapake osamangotinamiza zilizonse n then the funny thing is ppl jst get convinced over everything .iwenso ntanyiwa ukakhala chete ppl can say akupatsa chibanzi,BT aliyense can hv his own decisions at the end of the day basi
@EmmaOsman-w3p
@EmmaOsman-w3p 2 дня назад
Ndpo sitikuenela ku mu brema Peter cz anthu ndi omwe anasakha so chomwe anasakha ndikuchiika Pampando tomwefe ndiomwe tingavote moyenela posakha munthu emwe azathandize amalawi vuto LA amphwawife timangonvela zilizonse relo ndizi
@OusmanBen-f4o
@OusmanBen-f4o 2 дня назад
Ifeyo anthu ovotafe ndamene tikuvutika ndithuu! kuposa APM,kusamva kwathu kwatipwetekesa heavy
@HamanjaManyela
@HamanjaManyela 2 дня назад
Ifeyo bwana amalawi tikumva pain
@StevenTaulo
@StevenTaulo День назад
Can you send us that list of Unga and the attached Benefits. Post it to the famous papers of Malawi
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 3 дня назад
You're the best, ndipo simandiphonyatu. Ilike Limpopo so much!!!
@EvanceRazaki
@EvanceRazaki 3 дня назад
Zoona Dan lu ndye kt za poison zija mwina zinal zonamat umafun usapite ku kovechoni ya dpp ija anal atakukopa a mcp yeti.why malawi wathu.ambuye chitanipo kathu chonde.
@DanJohn-ws5gl
@DanJohn-ws5gl 2 дня назад
Ndalama ndi satana ankolo
@samdiverson9733
@samdiverson9733 2 дня назад
@@EvanceRazaki tisadandaule kanthu God will fight for us mmene tili
@SabitWililson
@SabitWililson 2 дня назад
Zozisiya zimenezo awafunse amzawo kut alikutko? Ndalama ndisatana pajatu inampereka Yesu.
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 3 дня назад
Mzimayi wacita zowamangitsa a Shumba ndiwe wa tsoka
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 3 дня назад
A comrade Inu conde conde, musatokose njoka kudzinje,,musadzabwere kumaconvetion,,azitiwuza zocotika ndani 😭😭
@FrancisMbewe-xn2pl
@FrancisMbewe-xn2pl 2 дня назад
Loud and clear boss mthanyiwa
@LoveKasema
@LoveKasema 39 минут назад
I don't see any reason i can blame Dan Luh. The money is too much and iyeyo ntchito yomwe imamubweletsela bread ndikuimbako. So, in this case i feel like Dan ali ndichipani chomwe akuchidziwa ndipo kumupatsa ballot paper lero akudziwa omuchonga yekha muntima mwakemo. Ukuku akugwilako ntchito yake yomwe amadyela. 500mk olo mukanakhala inu mukanatani? Big up bambo a Daniella. Iyaaa
@zondanitzulumusicfly.5202
@zondanitzulumusicfly.5202 2 дня назад
Only part in Malawi which can put Chakwela in prison is UTM. That's why agula anthu kuti aphe chipani , chakwela knows that.
@AlickMuliya
@AlickMuliya День назад
end of the age , people are loving money than life, love already went out . this is indeed crazy world.
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 3 дня назад
Koma anthu ife tinatani kodi amalawi ife anthu omvesa chisoni Danilu amutenga ndalama ndizomwe azafele awa
@TimothyNkhutembaChirwa
@TimothyNkhutembaChirwa 3 дня назад
Muzipatala mankhwala mulibe ndalama kumangogawana A mcp chame
@samdiverson9733
@samdiverson9733 3 дня назад
Comrade ntanyiwa ndi one koma bakili mulizi tv Ali kuti koma?
@DanJohn-ws5gl
@DanJohn-ws5gl 2 дня назад
inu Balkili muluzi TV wabwelelanso
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 дня назад
Waponya audio dzulo
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 2 дня назад
Waponya audio dzulo
@GodfreyMzembe-b3n
@GodfreyMzembe-b3n 3 дня назад
Brother muyankhureko za Bakili muluzi tv
@AroushMussah
@AroushMussah 3 дня назад
Nkhanga zaoooooooona❤❤❤❤❤❤❤❤
@TakondwaSulani
@TakondwaSulani 3 дня назад
Eish God have mercy
@eunicemacdonaldkaipsa9705
@eunicemacdonaldkaipsa9705 2 дня назад
Nde mwati 500 MITA? Koma bomali Lili ndi ndalama zoseweretsa anthu akudya xitedze mmm
@McDonaldbeketeNkhata-n4l
@McDonaldbeketeNkhata-n4l 3 дня назад
Mayeso awa kodi tikulemphera kukoza mavuto aziko ndiumbuli bwanji kuwononga choma chaboma ndikugula anthu alowe chipani chankhaza Kumapeto kwa izi kuzakhala nkhondo muziko
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh День назад
Mesa mukati chakwera wamudyetsa poison Dan luu nanga bwanji walowaso MCP alomwe matako anu
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 дня назад
Chitsiru nanunso antanyiwa simungabwere ku Malawi inu ,muli ku exile
@QassimuMitawa
@QassimuMitawa 3 дня назад
Dziko la asatana (Malawi)
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh День назад
Wabodza iwe chitsilu ku UNGA anayamba ndi chakwera mesa zinayamba ndi UDF, DPP
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson Час назад
Ndiwe wekha otsutsa kuonetsa kt ndiwe wamisala...galu
@ziwani3682
@ziwani3682 2 дня назад
Ndalama xikungothera kugula anthu ndikuyenda yenda koma fertilizer ochipa mtengo uja mubweresa? Alton chirwa international airport mumanga? Ma passport a 14000 yabwera liti? Amalawitu tatopa nanu
@chifundokachola7532
@chifundokachola7532 2 дня назад
Komatu sirius anthu simukugona kufufuza zimwe abomawa akupanga ...u really do your best informing the public but i think the only solution we have to this problem is voting otherwise kumangolankhula zizitipwetekesa mutu...
@KennyThindwa
@KennyThindwa 3 дня назад
A Malawi 🇲🇼 conscious alibe ,kuno ku Malawi too slim.
@MartinNyirenda-wf5oz
@MartinNyirenda-wf5oz День назад
Amuthanyiwa yesesani kutiunikila xose zimene akukambilana a mcp
@ThivadoartistDyson
@ThivadoartistDyson Час назад
Mbuz zina zayamba ma comment ya negative pa voice ya mtanyiwa koma chosecho sakudya nawo ndalamazo ubakha okhaokha
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh День назад
Mwayi wawo umenewo mawa uzapita ndiwe sanje njeee MCP boma
@ChicoBanda-kq7py
@ChicoBanda-kq7py 2 дня назад
Ambeye azikudsni ntanyiwa mukugwila ntchito yotamandika
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 3 дня назад
Koma abaleeeee????ine zikundisowetsa mtendere zikucitikazi,,atimanga mu jumbo ndithu,,anthufe kungokhala ngati zidole?? Anthu akudya nyika,zitedze,eish,,mfuti zawozo ziawombere okha ndithu in Jesus Christ name
@YamikanAbubakary-my4ie
@YamikanAbubakary-my4ie 3 дня назад
😂😂😂😂😂 Km galu uyu gusy 👉🐕
@isaaczuze
@isaaczuze 5 часов назад
Dziko lomvesa chisoni ....achakwera azipita kwa akabudula
@kekeaufi9834
@kekeaufi9834 3 дня назад
*Zomvesa chisoni Malawi wathu*
@Musa1828-l5d
@Musa1828-l5d 2 дня назад
Ntanyiwa ponyani ma audio apa tivele nawo nkhombe ndichitsiru kwambri ndipo Ntanyiwa osapanga chibwana chowasekelela agulu amenewa
@LusunguKondowe-r4w
@LusunguKondowe-r4w День назад
Ndalama ndioopsa.. Kukana nkovuta chisisi akuchiziwa okha
@GbossMw
@GbossMw 2 дня назад
Mulungu akuona zonsezi😢
@Ronaldmtonga-j8c
@Ronaldmtonga-j8c 2 дня назад
Anthu ngati awa amangofuna kukhutisa mimba zawo amalawi tsegukani maso ,simunazindikirebe ? Uyu akapeza ndalama simudzamuvaso azizakhara akudya ndi mawaja awo chenjerani A Malawi azanga ,asiyeni andale azipanga okha
@DuncanGatoma
@DuncanGatoma 3 дня назад
Ife tinaziwatu kt awa mumat a Dan lufan adyaso kenakake
@INNOCENTMOFOLO-io8tg
@INNOCENTMOFOLO-io8tg 2 дня назад
ndikutha kuona kut dziko lamawi likulamulidwa ndi anthu asatanic yooooo komatu ndalamazo azazibweza ndimagazi awo
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 дня назад
Achita bwino kwambiri kumanga chitsiru chotchedwa shumba ichi
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 2 дня назад
Boza ilo nanunso a ntanyiwa muli ndi chani inu aliyense wa ma audio kuzitama kut ndiyo khwima zilomwe inu
@KaulembeMavuto
@KaulembeMavuto 2 дня назад
Awa amtanyiwa akugwira ntchito Yolanda pake kunamiza anthu zabodza izi mpaka anthu 6000
@samanthamuller7643
@samanthamuller7643 3 дня назад
atanyiwa inuyo musatisiye ife asatana awa iiiiii ine mr chikangawa uyu
@MillicaBanda
@MillicaBanda 2 дня назад
Dan lu alibe umunthu satana alibe manyazi mulungu amukathe
@FebbieNjewa-g3k
@FebbieNjewa-g3k 3 дня назад
Koma kabambe ngati waterodi? Siwe munthu wabwino ndiwe opepera
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 2 дня назад
Musiyeni apite adzikamwa magazi ife sitikusintha maganizo APM our vote chisilu chimenechi ndachitaya nyimbo zakezo sindimavela
@giftsululu4274
@giftsululu4274 3 дня назад
Antanyiwa msuzi ukusukukatu tsopano pompano timva Mwalowa mbakuwaku
@TomasDzifoole
@TomasDzifoole 3 дня назад
Kothela kabambeyo kumeneko,
@WhiteKasungu
@WhiteKasungu 2 дня назад
Dan lu ndilibe nayetchito ameneyo
@LukaEthibwi
@LukaEthibwi 2 дня назад
Ngati amupasa ndalama achita bwino
@KelvinJpchimphepo-sh6nc
@KelvinJpchimphepo-sh6nc 2 дня назад
Koma ndalama mmm siyikhutidwa mmmm anthu chifukwa timafa chifukwa cha zilakolako zambili
@gladysmanthimba7851
@gladysmanthimba7851 2 дня назад
Ndalama zimenezi zikuchokera thumba iti mankhwara akusowa mzipatala
@FadweckLifa
@FadweckLifa 2 дня назад
Timanjadila kwambiri. nkhanga zaona. Koma nati ndipemphe kuti nkhanga zaona zizitilukanso. Nchinelezi. Ndicholinga mayiko ena Azim a nkhanga zaona.
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 2 дня назад
Gyz chikangawa akudziwa kuti 2025 sakuwina akupita ndichifukwa angoba ndrama kumangogawa malawi akuzuzika inu simuona?
@ChristopherJohn-u5i
@ChristopherJohn-u5i 3 дня назад
Soka Kwa iye otama mkono wanyama
@MaxonKambazithe
@MaxonKambazithe 2 дня назад
Kuimba kwa oimba Dan lulu afuna ndalama apite ifeee amalawi tooonse ambiri sitivota chifukwa cha oimba aiiiiiiiii
@DominicNantowa-t4d
@DominicNantowa-t4d 2 дня назад
Ndikapanda akunvela antanyiwa a born kalindo ndi wa Bakili muluzi TV ndimadwala komano pano ndikudandaula kuti wa Bakili muluzi TV alikuti?
@LovmoMwanxa
@LovmoMwanxa 2 дня назад
AMBUYE safuna anthu omangolira ndizoona AMBUYE akubwera................ zoona koma paja ananeneratu kuti ndukusiilani mtendere ndiposo MAU a MULUNGU akutiso adatipasa ife pansi pano ufulu,,,,,,,,,,,,ndiye chomwe tingachite nkukhala ndi mapemphero amphavu AMBUYE alowerela zikatelo
@josephchisale4143
@josephchisale4143 3 дня назад
Ine ndikukudabwa kodi inu simudzafa zinanatikwanatu za maliro amuthu modzi yekha yekha athutu amafa koma muzingotiliza amatelo 😢😢why Malawi sindikutsutsa ayi koma podyela panu ndipomwepa koma ayi muzikhalako serious
@mishecksipolo7153
@mishecksipolo7153 2 дня назад
Sizikuvekatu izi
@chimwemwenkute3839
@chimwemwenkute3839 2 дня назад
Welcome comred mtanyiwa
@AyandaPhungula-bg9ql
@AyandaPhungula-bg9ql 2 дня назад
Eish Malawi wanga satanic yafikapo ..... thanks to you brother ntanyiwa
@HarveynsonthiNsonthi-u4n
@HarveynsonthiNsonthi-u4n 2 дня назад
Kodi ndalama zomwe akuononga kumagula ma MP. oluza akuzitengakut , Kodi khalidwe limeneli mukunzimva mphamvu yochita chilichonse kumwambako muliko mukuona ana anu akubvutika chifukwa chamunthu modzi
@justinmalala-e4o
@justinmalala-e4o 2 дня назад
Anthu 6000? Tamakhalani serious. Mukapanga masamu ndalama zomwe zingagwile ntchito ndi zingati? It's not possible. Mukayamba kumanama zizivuta kukukhulupililani
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q 2 дня назад
This man ntanyiwa eeeeeesh
@Rab2sope
@Rab2sope 2 дня назад
Koma mabodza ena awa ngati mukuuza mbuli tuu
@InnocentnMbale-zq8pk
@InnocentnMbale-zq8pk 2 дня назад
Best ever tv
@MosesSolomoni
@MosesSolomoni День назад
Kabambe sangapange zimenezo mwayamba bodza
@EdwardChimpukuso
@EdwardChimpukuso День назад
I'll) opl
@tawongakamanga-v9n
@tawongakamanga-v9n 52 минуты назад
Mtima wanga ukuwawa
@MakeSunshine100
@MakeSunshine100 2 дня назад
A Ntanyiwa nkhani ya Dalitso Kabambe ine sindikuikhulupilila. Nkhani imeneyi ndiyofuna kugawa mavoti ku convention. Ma voti akachoka kwa Kabambe (amene akuoneka ngati akutsogola), MCP ikufuna kuti ma voti apite kwa manganya. Please investigate carefully.
@MazonMatias
@MazonMatias 2 дня назад
Kkkkkkk iwe ndiwe wabodza kwabas mot anthu 6000 ayenda bwanji? Osamanamiza a Malawi chifukwa chot ulimbali ina ayi.
@CathrineRamseyJafaal
@CathrineRamseyJafaal 2 дня назад
Inetu ndinaziwa kuti oyimbawa akupasidwa ndalama ndi chikangawa party
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 2 дня назад
Dziko la MALAWI ndilomvesa chisoni kwambiri
@MsondaBanda
@MsondaBanda 2 дня назад
Where is proof Mtanyiwa? give us the proof please
@ChikumbutsoMaluwa
@ChikumbutsoMaluwa 6 часов назад
Iwe galu kwa bas
@JaphetSakala-u5j
@JaphetSakala-u5j 2 дня назад
Votolanu mmazichemelela nokha. Kuposa nkhani zoti ife tive palikusiyana pakati pa inu ndi bkm tv
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo 2 дня назад
Munthu wamantha iwe mtanyiwa umangolankhulila Kuno bwanji azako alikumalawi iweyo kumango namiza anthu basi
@innocentwingolo8724
@innocentwingolo8724 2 дня назад
Kuona anthu akutibera misonkhowo nkhope zawo zosamva ndalama, olo kusintha ayi
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 2 дня назад
Ntanyiwa ndi number 1
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 2 дня назад
Mkazi ndi nyambo yoopsa kwambiri wadya ndalama mkazi ameneyu
@265995451885
@265995451885 3 дня назад
Information makhala nayo yabwino kwambiri koma mudzitha kufutokoza mfundo zikukulu mopanga summarize.
@ChristopherManase-s1f
@ChristopherManase-s1f 2 дня назад
Bodza ilo. Sizingakhale zooona kupita ku Unga ndi anthu 6000
@TressLuka
@TressLuka 2 дня назад
Game on Mtanyiiii 😅😅
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 2 дня назад
Ndikutha kuona kumalawi kuno kukubuka nkhondo straight
@ChifundoZayenda
@ChifundoZayenda 2 дня назад
Mumakwana👍👍
@JusticeSalema
@JusticeSalema 2 дня назад
Dan Lu why???????? 😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅😅
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh День назад
Eya tizakawavotera
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 2 дня назад
Atupere angopanga mgwirizano ndi Apeter Mutharika bas straight tu
@FadweckLifa
@FadweckLifa 2 дня назад
Zizitilukanso za chongelezi. Nkhanga zaona
@DeenesNurudMeke
@DeenesNurudMeke 2 дня назад
Ntanyiwa watitsuka mmaso straight
@EmanuelChilemba-d2v
@EmanuelChilemba-d2v 2 дня назад
Mtanyiwa katundu bambo.
@petroszgambo9949
@petroszgambo9949 2 дня назад
Anabel mutalika ndiye utiso mutanyiwa
@DanJohn-ws5gl
@DanJohn-ws5gl 2 дня назад
Kuli ndalama ku MCP
@DianaMmagisa
@DianaMmagisa 2 дня назад
A bwana tilipambuyo panu
@AlexKamowa-u7m
@AlexKamowa-u7m 2 дня назад
Zoona
@StellaMichael-s4d
@StellaMichael-s4d 2 дня назад
Asataniki awa musadabwe muluzi wa galu ndiumodzi
@YusufJames-f5f
@YusufJames-f5f 8 часов назад
😢😢😢😢😢
@AvicckyBanda
@AvicckyBanda 3 дня назад
Wa bakili tv naye walowa mcp
@HerbartKaphamthengo
@HerbartKaphamthengo 2 дня назад
Koma anthu ena muzalangidwa maboza amenewa
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 3 дня назад
Umbuli sizithu sure 😂😂😂
@DalitsoMatope
@DalitsoMatope 3 дня назад
Inu mmene mukuonekela mungakhale ozindikira
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 дня назад
@@DalitsoMatope kwambiri kuposaso iweyo chifukwa munthu sangamavele zabodza ngati zimenezo
@FionaKhoma
@FionaKhoma 2 дня назад
M c p wautali 2025
@AnusaNkhoma
@AnusaNkhoma 2 дня назад
Mumakwana inuyooo bigy
Далее
GIANT Gummy Worm Pt.6 #shorts
00:46
Просмотров 47 млн
How to split your drink
00:45
Просмотров 1,2 млн
DPP ndi Comrade Timothy Mtambo agwirizana.
1:31
Просмотров 17 тыс.