Mandota video yako za zulo ndinapanga dissapoint sinaionele koma usiku ndalota titakwatilana koma sumagula ndiwo Sima timadyela tomato ndi anyezi dairy ndi sabola ndi zomwe umagula umandiuza kuti zimakoma ndiposo zimapeleka ma vitamin thupi😂
@@CHEMANDOTACOMEDY ndipo ndikanakhala pafupi ndikukufotokozela story yose mene inalili ku maloto ikakhaladi video yobeba mpaka ndimazifusa nditazizimuka kuti koma zikukhala bwanji eish I can't believe it