Тёмный

DPP IDAONONGA INFRASTRUCTURE KU MALAWI - DR JOHN PAUL- TREASURE GENERAL WA MCP WAUZA BRIAN BANDA 

Amuna Misso Tv
Подписаться 31 тыс.
Просмотров 4,8 тыс.
50% 1

DPP IDAONONGA INFRASTRUCTURE KU MALAWI - DR JOHN PAUL- TREASURE GENERAL WA MCP WAUZA BRIAN BANDA

Опубликовано:

 

28 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 94   
@ChimwemweKamanja
@ChimwemweKamanja 13 часов назад
Brain boma agwesa yekha 😂😂😂😂😂😂 proud to Brian
@ChimwemweKamanja
@ChimwemweKamanja 13 часов назад
Aziyakha fuso amaneo osamagoti Dpp
@KhooMadex
@KhooMadex 13 часов назад
I think Brian banda is a blessing to malawi
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 13 часов назад
Kudzivuta ndi mtima uku... DPP ikubwera ndithu m'bomamo😂😂😂
@MakabaBauleni-c2i
@MakabaBauleni-c2i 13 часов назад
Kma uyu akunama Dpp ikubwelera m'boma ndipo ulira sunati ife olo titavota lero Dpp ikhoza kuwina ndi 89 % osalawo mutha kugawana
@PatrickMtira
@PatrickMtira 13 часов назад
Sakuyakha ma fuso uyo
@Kiyamachilipa
@Kiyamachilipa 13 часов назад
Tidzawonani pa mavoti
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 4 часа назад
Nose a MCP machende anu😢😢
@Kiyamachilipa
@Kiyamachilipa 13 часов назад
Achimwene Mudziwopa MULUNGU
@PrinceBlessings-bv5bs
@PrinceBlessings-bv5bs 13 часов назад
Amakanika kuyankha mafuso awa 😂😂😂 kumangodziluma
@stanleymollen7273
@stanleymollen7273 13 часов назад
Sangaloze zomwe current government yapanga..Chixungu chimaonesa ngati munthu akunena za mzeru..Garbage...
@KelvinPhiri-z9d
@KelvinPhiri-z9d 13 часов назад
Tiwawonera amenewo akungwa chagada😂😂😂😂 njanjiyotu ndiyamozambique asatisokose ameneyo
@BlessingPhiri-br5kv
@BlessingPhiri-br5kv 3 часа назад
Kd angokamba za DPP bwanji ayankhe ameneyo nkhan ndiyokut akuba misonkho yathu ife Malawi
@ShamimuBisani
@ShamimuBisani 13 часов назад
Padziko lonss lapansi chsru choyamba kapen chidebe chophikira makata kusimba ndye ichi osamaiwal chitukuko cha 16tillion ijatu muitchule njanji ndye siyan Joyce Banda anatiuza kale
@ChancyWilly
@ChancyWilly 13 часов назад
Zomwe mwapanga a mcp ndikubweresa njala komaso kugwesa kwacha zomwe anthu sazakuiwalani
@DavieAlumenda
@DavieAlumenda 13 часов назад
Kunama kopanda Nako manyazi ineyo ngwa ku nsanje komweko koma zomwe akuyamkha akuluwa nzabodza zokhazokha
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 11 часов назад
Iweyo udamwa nawo ndopa za anthu Aja mudaphera kuchikangawa
@ElizabethMtuwa
@ElizabethMtuwa 13 часов назад
Taziyakhani mafuso bwanawe njanji ndi yamozabque.
@stanleymollen7273
@stanleymollen7273 13 часов назад
Doctor kukanika kuyankha funso... Mediocre
@HashimKanjanga
@HashimKanjanga 13 часов назад
Awa ndi achitsiru bwnj 4yrs azitiwuza zanjanji
@ThanksKamlanje
@ThanksKamlanje 13 часов назад
Amariza bwanji njanji ndarama atagawana mkudya
@francismungu7749
@francismungu7749 13 часов назад
Uyu ndising'anga akuoneka makani 😂
@LastbornEnd-r9c
@LastbornEnd-r9c 13 часов назад
Uyu machende ake
@MussaJafali-q4c
@MussaJafali-q4c 13 часов назад
Achisilu awa
@MussaJafali-q4c
@MussaJafali-q4c 13 часов назад
Achisilu awa
@GiftGeliati
@GiftGeliati 13 часов назад
Kkkkk DPP my vote
@BlessingsFredd
@BlessingsFredd Час назад
Kodi mbulutu ameneyi ndiye UTImuzitibwelesela athu oti atithandiza osati zozizila akukambazi mbava ndi chikangawa wakeyo
@TiyanjaneMkwate-we8gu
@TiyanjaneMkwate-we8gu 3 часа назад
Ndinkangoti ngati muthu Ali Dr amakhala wanzeru koma awa u Dr wao ndi opanda mawo nzeru,apa bola osaphunzilafe mwina tikhoza kubwera ndi ma facts, alibe so manyazi, DPP fertilizer 20 MCP 107, fuel DPP 850 MCP 2750 ,dpp sugar 750 MCP 2500,chimanga 20,000 MCP 50000+, ngati alipo otsutsa anditsutse
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw 13 часов назад
Koma Ka background sound always do touch my soul! Who did that sound
@amunamisso
@amunamisso 13 часов назад
YT LIBRARY
@beinhardkausiwa7107
@beinhardkausiwa7107 2 часа назад
4 kilometer ya njanji koma mmisonkhano ya mcp nkhani ndiya njanji njanji njanji eeeeee mcp muzichita manyaziii
@BlessingPhiri-br5kv
@BlessingPhiri-br5kv 3 часа назад
Km akuthawamafuso bwanji ngat akut dziko akuliendetsa bwino muwudzen ayankhe nkhan ya fetelezayo asathawe
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 3 часа назад
Alimi tasitha chifukwa cha chakwera fodya akugula chimanga tikugulitsa mitengo ya bwino
@WarriorKB-u3k
@WarriorKB-u3k 11 часов назад
Iwe ukuzitcha doctor ndi zako chikangawa ndinu dzisilu,mbuzi ya munthu MCP palibe chomwe akuchita zisilu za anthu DPP 2025 boma ovota ndife tiona
@juliochiwalo
@juliochiwalo 4 часа назад
Munthuyu ndi opanda nzeru chakwera walephereratu iyeyo akuziwa zimenezo ndipo an thu ndi okwiya akuvutika koopsa anthu sadya njanje
@MaxwellChiwaya-i8q
@MaxwellChiwaya-i8q 6 часов назад
Anthu sitidya njanji komanso ntchito zikusowa komanso zinthu zinakwera kwambiri ndiye umoyo wa anthu ukuyenda bwino bwanji
@KenAipa-r3r
@KenAipa-r3r 13 часов назад
Kod njanji yake yaku Mozambique akunyadilayo ????
@MustapherLino
@MustapherLino 11 часов назад
Ambuye mulungu tikupepha kuti mutichosera mcp mu boma, satanic awa chonde chonde achoke
@edsonnyasulu5394
@edsonnyasulu5394 4 часа назад
Kunena zoona palibe kusiyana mcp ndi DPP onse ndimbava anthu awa ndiamozi
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 11 часов назад
Osayakhula mwamwatama mcp si chipani chafuko fuko lake liti. Ndipo ndikunenesa kupanda chilima ndi zipani zina mcp abwezi simunalowe muboma. Mcp yazaza ndimbuli magesi akuzimazima kunu ku mzuzu akulamula ndindani Brian banda uziona anthu owaika pa times chimene ukulankhula nacho chili ngati sikizi. Ngati dpp mavoti anakubwera inu akambwe bwanji chisankho chachiwili munabwera mugwirizano ndi zipani zina.umbuli tikunena kuti ku mcp kuli ziwanthu zoti mumuto muli ambuye tengeni. Ngati dpp inakuberani kachiwili aliyese akanayima payenkha ndipamene tikanaziwa kuti ddp inakuberani koma zipani 9 zimene munabwera nazo muchisankho chachiwiri pano munene mopumbwa mcp yinawina ndizoona kuti munthu wopanda zeru saziwa chimene chamufikisa pamene ali. Shame mcp muziweni Mulungu osanena mochachalika motumbwa mwamatama
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 11 часов назад
Osatenga anthu oti mutu ndiwozungulira amawona ngati ndiwochenjera kupusisa amalawi ayiwala kuti akuzipusisa okha koma Mulungu akuona
@IkirahTwaibu
@IkirahTwaibu 11 часов назад
Akulu muli mpingo wanji koma mmapemphela inu kunama olo mwana wa zaka zitatu akhoza kukugwilani bodza lanulo mukunama kuti chichokeleni kamuzu njanje kunalibe Iyaaaaaaa ndinu abodza kwambiri ndipo DPP ndi boma lomwe anthu mukuyidayo ndiye boma lomwe china chilichonse chidali chotchipa koma inu ndi umbava wanuwu komanso kuyipa mtima muli nakoko kosaganizila anthu amdziko mmmmmmmm chokanipo tatopa nanu mwamva muuzane
@kingstonekalonga8435
@kingstonekalonga8435 13 часов назад
Brian mumatha akukanika kuyanga galu ameneyo angamuvotere ndani mbuzi yamuthu chakwera ndindani
@Davis-qo4qp
@Davis-qo4qp 5 часов назад
Ndimaganiza kuti Dr amakara ndi nzeru koma pano zadziwika kuti ndi opsa
@HestingsZiba-d6k
@HestingsZiba-d6k Час назад
Galu uyu kwabasi machende ake pati...
@TiyanjaneMkwate-we8gu
@TiyanjaneMkwate-we8gu 3 часа назад
Mumuziwe yesu ndi ophunzira ake 12.
@AlickyMatola
@AlickyMatola 12 часов назад
Brian doctor uyu akusepa mafuso😂😂😂😂 dpp 2025 boma
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 13 часов назад
Koma abale tikuziwa kuti ana anu akusangalala muziyankhulako zoopa mulungu plz plz ulendo wanjanji ife tizipita nazo kutiko
@CassimMbalaka
@CassimMbalaka 4 часа назад
Aaaaaaa akukanika kukuyakhani mafuso ndi mbuli ya muthu sitidya jaji
@mphatsomalenga
@mphatsomalenga 13 часов назад
Chabwino njanji ikugwila vepi koma zasintha moyo motani?
@BarwickSalanje
@BarwickSalanje 4 часа назад
Munthu uyu wadya ndalama za mcp kuti alankhule za mcp
@Milanzi-nb5fv
@Milanzi-nb5fv 4 часа назад
Mcp simungawinenso😅😂 mukuziwanso ap
@ElizabethMtuwa
@ElizabethMtuwa 13 часов назад
Mwamuna wadzeru sabrama mwamuna wakare mukaone oterewa dziwani banja lamumvuta basi
@FortyoneHarwa
@FortyoneHarwa 13 часов назад
Inu. M. C. P kwanu nkunama basi tidzakutchotsani m boma inu dzitsilu inu
@WakisaNjeghenje-i2n
@WakisaNjeghenje-i2n 13 часов назад
Dpp itenga boma chikwangwan ndizinkhale ng'oma
@PhillipAcquaron
@PhillipAcquaron 12 часов назад
Njanji yake iti zoba ameneyu a Malawi angadye njanji chitsiru ichi
@giftmakwale-n5d
@giftmakwale-n5d 8 часов назад
A mcp akudzikwata ndi chala ndipo akulu awawa akungoyankha za mmutu mwao
@petrokagona1708
@petrokagona1708 13 часов назад
Kkkkkkkk. Ndiye ma indicators kuti zinthu zikuyenda bwino ndi ati?
@AmirGeloo
@AmirGeloo 13 часов назад
Kodi amenewa amadziwa zimene akuyankha kapena akungoyayankha kuti akome kwa mabwana awo ?
@moseskavalo3304
@moseskavalo3304 13 часов назад
Scandal after scandal...By the way which indicators , coz when we talk of inflation nde eeeeeehhh zosakambika
@Davis-qo4qp
@Davis-qo4qp 5 часов назад
Zoona Brian waona kuti udokitara wa uyu kulibepo
@YasinAdam-pn4bh
@YasinAdam-pn4bh 12 часов назад
Akuluwa atichimwisapo apa bola ndisunde kaye aaaaaa
@LemieMwalendo
@LemieMwalendo 5 часов назад
We don't need information,we need delivery shupit
@Victoriabwaira
@Victoriabwaira 3 часа назад
Ameyo ndiopusa kwambiri
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 12 часов назад
So angokamba za Dpp why malo moyankha mafutso? 🤔
@AlexKaunda-ny2eg
@AlexKaunda-ny2eg 4 часа назад
Sukulu munachita Koma mulibe nzelu
@CarolyneGunda
@CarolyneGunda 13 часов назад
Anthu akuba awa akuzinamiza kuti awinaso kkkk koma MCP kkk umbava wakeo
@GerladMingu
@GerladMingu 13 часов назад
Khani ndi pa ground not on papers such as,he talks about minister of transport,what is that?
@WilliamBandaWili
@WilliamBandaWili 11 часов назад
Iwe chimutu chako mcp yakoyo fwetseke
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 3 часа назад
Ndipo dpp sindiyifunaso kuva
@WilsonKaomba
@WilsonKaomba 2 часа назад
Uyu ndi mbuzi ya chitsilu
@PhillipAcquaron
@PhillipAcquaron 12 часов назад
Vuto nd ndalama chitsiru ameneyu
@Davis-qo4qp
@Davis-qo4qp 5 часов назад
Uyu si Dr ndi mbuli yachabe
@WakisaNjeghenje-i2n
@WakisaNjeghenje-i2n 13 часов назад
Maboza basi tatopa ndizaboza a mcp azaona 2025
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 13 часов назад
Koma ma doctor aku mcp abale 😂😂😂😂😂
@AnusaChiwale
@AnusaChiwale 13 часов назад
Akulu yankhani funso straight
@JosephMalizani-u7s
@JosephMalizani-u7s 2 часа назад
Uyo ndiwamisara
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 11 часов назад
AAA MCP ndi DPP bola DPP. Aaa
@Kiyamachilipa
@Kiyamachilipa 13 часов назад
Abwana muli ndi wabodza
@UmaliIshmael
@UmaliIshmael 12 часов назад
Anthuwa ndi oyipa awa
@MeriaMasinga
@MeriaMasinga 5 часов назад
Dpp 2025 boma
@JosephMalizani-u7s
@JosephMalizani-u7s 2 часа назад
Alibefundo
@Kiyamachilipa
@Kiyamachilipa 13 часов назад
Yankhani chilungamo
@mphatsofost
@mphatsofost 13 часов назад
Awa ndiwupenga
@WilsonMbendela-d4o
@WilsonMbendela-d4o 13 часов назад
Achisiru awa
@MussaJafali-q4c
@MussaJafali-q4c 13 часов назад
Chizilu inu
@DjshukulanGift
@DjshukulanGift 11 часов назад
Jaji yake it?
@LobertSamuel
@LobertSamuel 13 часов назад
Awa amatha mr brian
@LobertSamuel
@LobertSamuel 13 часов назад
Kkk
@rabsonDimba
@rabsonDimba 2 часа назад
😊
@kingsleyhopematchaya5184
@kingsleyhopematchaya5184 3 часа назад
Fertiliser siwondula brain iwe alimi tikugulitsa 2bags ya chimanga kugula thumba la fertiliser koma 2020 timagula 21000 koma timagulitsa chimanga matumba 7 panopa kwa alimi fertilizer siondula
@AndersonChinkwapulo
@AndersonChinkwapulo 11 минут назад
@@kingsleyhopematchaya5184 koma iwe udapita ku school? Chimanga ndi feteleza choyenera kudula ndi chani? Wekha ukuti umagulitsa matumba 7 chimanga kuti ugule feteleza, pano matumba awiri achimanga kugula fetereza
Далее
Chakwera Will Not Win The Elections - Samuel Lwara
22:19
CRUISE 5 WITH BLACK MISSIONARIES
1:05:27
Просмотров 83 тыс.