Тёмный

DR. GEORGE CHAPONDA KUKAMBA ZA DPP KOMASO ZA NANKHUMWA NDI AMUNTHALIKA 

THAT GUY TV
Подписаться 3,7 тыс.
Просмотров 32 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 86   
@jomochirwa
@jomochirwa 2 месяца назад
Akulu yawa adaphunzila simuwona kunena background wosakayikaso ayi.koma vuto kuphunzila kwambili ndi nkhani za ndale ndi zinthu ziwili zosiyana.kkk
@replacefruittreenursery
@replacefruittreenursery 2 месяца назад
Very true
@kennethmakweya3561
@kennethmakweya3561 2 месяца назад
Anthu awa timangowanyoza chifukwa sitiwadziwa
@sonicanduwa6363
@sonicanduwa6363 2 месяца назад
Well educated madhala
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 месяца назад
Big man ❤❤❤❤
@GeorgeKapito-um2wl
@GeorgeKapito-um2wl 2 месяца назад
❤❤❤❤
@Okalekale
@Okalekale 2 месяца назад
Kutanthauza kuti onse andalewa ndi mbava zokha zokhadi,akuti iwonso ndi a corruption koma awa anyanya,ngakhale akunama,DPP ndi PP ndi zimene zinanyanya.
@clintonhodda9830
@clintonhodda9830 2 месяца назад
Dpp ili ndi anthu ophunzira kwambiri simabulutu a congress
@peterchikwakwa8476
@peterchikwakwa8476 2 месяца назад
He is a learned Man
@nnmzakwachamzakwacha9405
@nnmzakwachamzakwacha9405 2 месяца назад
I like him...
@g_deonm5793
@g_deonm5793 2 месяца назад
Awa anayenda ngati Christopher Columbus ndithu...
@thomasmakata8861
@thomasmakata8861 2 месяца назад
Uyuyu ndikatundu nsaname pakungofunika kukhala mtsogoleri wadzikotu uyu akhoza kusintha zinthu uyu 😊
@gifted5262
@gifted5262 2 месяца назад
The voice ndendende Bingu and ADADI. Sipachibale anthuwa?
@ambrozonamazemba8986
@ambrozonamazemba8986 2 месяца назад
Anthu Ophuzira ife ndi choncho 😂😂😂😂😂
@VesterLuke
@VesterLuke 2 месяца назад
Bss Material
@HendrickBanda
@HendrickBanda 2 месяца назад
💪💪💪🔥🔥🔥🔥
@DigleDafter
@DigleDafter 2 месяца назад
Muthu wakulu uyu ozichepesa makhalidwe n kulakhula ❤
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 2 месяца назад
Kkkkk ndi mmene imachitira mbavatu imadzichepetsa kufuna kupusitsa anthu
@SheenahMwalabu-iz3pr
@SheenahMwalabu-iz3pr 2 месяца назад
Jonah siiwe mtolankhani okutha l think unangogwelamo zautolankhanizi sukutha olo interview yi aaa. Inenso ndingakuwidetu 😂😂😂
@andreabanda7838
@andreabanda7838 2 месяца назад
It’s not important. MCP is strategizing day and night. What strategies is DPP putting in place. Nothing. Pangani zoti opposition iwine chonde. Malawians need to freed from this turbulance .
@khwimamtonga954
@khwimamtonga954 2 месяца назад
Koma Ku constituency pa 17years mwapangako chani ?
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 2 месяца назад
Katundu wa dpp ❤❤❤❤ 🙏🙏🙏🙏🙏
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 2 месяца назад
❤❤ awa ndi akuyidziwa bwino bwino mcp
@MarthaMalopa-kw9xw
@MarthaMalopa-kw9xw 2 месяца назад
Ku Malawi kuno nsanje imatikokera pansi. Ife anthu omwe tisanapite ku school mokwanirafe, timanyoza anthu ophunzira powasemera zinyawu
@DicksonLutere-p9k
@DicksonLutere-p9k 2 месяца назад
Kukaphuzila kuba chi manga
@MosesShaibu-ee8hn
@MosesShaibu-ee8hn 2 месяца назад
Pofunika mtolakhani amene analemba khaniyanu yabozayi ameneyo mumusumile
@kelvinmphande3754
@kelvinmphande3754 2 месяца назад
He's smart
@yusufsadic2930
@yusufsadic2930 2 месяца назад
Maudindowo ndiy wakhalad kwatsal kukayankh pamaso pa Mulung kt ukayankhe
@LaquissonLebessoni-cn7pi
@LaquissonLebessoni-cn7pi 2 месяца назад
Sililani brian banda nde amadziwa kufusa mafuso
@BredamanJoe
@BredamanJoe 2 месяца назад
Komanso muzikumbukila kutukula komwe munabadwila Nkochitisa manyazi kulibe chituko olo
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw
@ChiyembekezoPhiri-sv8nw 2 месяца назад
Chaponda kunena zooona! Sorry to say that unity is no longer there in dpp
@MacfelsonMunthali
@MacfelsonMunthali 2 месяца назад
Very well schooled but kuba chimanga kukhalanso no:1 Pathetic!!
@MacDonaldkachala-cm5gc
@MacDonaldkachala-cm5gc 2 месяца назад
I thought he want to tell us that he is old, and doesn't want active politics, he want fresh blood to take over
@Okalekale
@Okalekale 2 месяца назад
Mbava zimene zaononga dziko izi,DPP,UDF ndi PP,zipani zokupha ndikuba.Madala awa dyera ndalama za chimanga sizinawakwane or anaotcha, akalambanso m'malo momakasewera ndi zizukulu zawo akufuna kukafera mu ofesi achinyamata ku DPP alipo.
@AnnaPhiri-b8t
@AnnaPhiri-b8t 2 месяца назад
Nyau yabodza nthawi ya DPP, pachaka m'makumba zimbuzi ka 4 panopa toilet yatha 4years simunakumbe 🤣🤣
@lazaruschitsamba8394
@lazaruschitsamba8394 2 месяца назад
this jeonalist is westing time ndizintu zakakalekale wosayakhula za lero
@BrightZionga
@BrightZionga 2 месяца назад
Komano achaponda inuyo ayi bola Navicha uja amakwanitsa kwambiri
@SmilingFishingRod-zc4wx
@SmilingFishingRod-zc4wx 2 месяца назад
Ndagwilizana Nanu. Navicha anakatithandiza. Km a Chaponda ayipwetekesa DPP akunva zomwe anzao akupangira, akutidoda koma a Chaponda angoonerera. A born kalindo, mthanyiwa onsewa akuyesera kuuzira mayeso kt mwina a Chaponda azuke maganizo km aaaaa mbola bola a Navicha akanayesesa.
@ArnoldKhandeya
@ArnoldKhandeya 2 месяца назад
wakulu, kuyamkhura akumwetulira
@LeonardPetro-ky6dq
@LeonardPetro-ky6dq 2 месяца назад
Ulemu want bwana anamkumwa nga dyera basi
@chiletsokazembe-ri4ic
@chiletsokazembe-ri4ic 2 месяца назад
Nchifukwa chake mumakatenga anthu ku mozambique kt azidzavota kuno et ndinu anthu akuba chimanga cha amalawi pot inu ndinu anthu akumozambique
@robsontyg3928
@robsontyg3928 2 месяца назад
Mr maize gate, chimbava ichi, chindere chakufikapo
@sheikhjaffarwhyte2688
@sheikhjaffarwhyte2688 2 месяца назад
Ndiophunzira zedi sanavinepo nyawu muja muchitira muja
@kelvinmphande3754
@kelvinmphande3754 2 месяца назад
The competent Court of law aquitted him, who are you?
@robsontyg3928
@robsontyg3928 2 месяца назад
@@sheikhjaffarwhyte2688 nyini yamako refugee ndati dzipitan kwanu ku Mozambique
@robsontyg3928
@robsontyg3928 2 месяца назад
@@kelvinmphande3754 pathako pamako refugee dzimachende dzanu ma refugees
@HamitonFrank
@HamitonFrank 2 месяца назад
Iwe simmalawi galu mbolo yako
@GeorgeKapito-um2wl
@GeorgeKapito-um2wl 2 месяца назад
Awa nde ofunika osati mbavazi
@GiftWilliam-sk2zc
@GiftWilliam-sk2zc 2 месяца назад
Kma mulanje is blessed land
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 месяца назад
Chaponda amasewela civo kapena noma
@TisopeMkozo
@TisopeMkozo 2 месяца назад
Kuyankhula kwanzeru
@casilasjawadu1586
@casilasjawadu1586 2 месяца назад
Anthu oipa awa kuukira udf
@LeonardPetro-ky6dq
@LeonardPetro-ky6dq 2 месяца назад
Palibe zomwe tonse yachita 2025 bola DPP basi
@SaidiMbawa-st6bj
@SaidiMbawa-st6bj 2 месяца назад
Chilungamo ayakhula madalawa
@robsontyg3928
@robsontyg3928 2 месяца назад
Dzi anthu dza ku Mozambique, nkhondo inatha mudzibwelela kwanu agalu inu
@BenjaminKamanga-p8w
@BenjaminKamanga-p8w 2 месяца назад
Gaaaaaaaluuuuuiwewweeee
@robsontyg3928
@robsontyg3928 2 месяца назад
@@BenjaminKamanga-p8w kwanu ku Mozambique dzipitan ma refugees
@kassimwalusa
@kassimwalusa 2 месяца назад
Dolo
@MATTHEWSANDREWMANDUTU
@MATTHEWSANDREWMANDUTU 2 месяца назад
Eeeee koma kulu uyu ink anamwa ,koma akuyankhula mwanzeru ndithu,,
@yusufsadic2930
@yusufsadic2930 2 месяца назад
Ndiwakul komanso mukut ndiophunzir Koma funso ndilakut wathandizanj Amalawi chiyambiren ali ndi maphunzir ameneo
@BrightZionga
@BrightZionga 2 месяца назад
Nalo funso ❤
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 2 месяца назад
Kkkkk komanso akt 13 years in cabinet ministry km chitukuko kulibe kwao
@ambrozonamazemba8986
@ambrozonamazemba8986 2 месяца назад
Mwina mwabadwa kumene. Nde ndikupempheni mufufuzw bwno. Awawa. Ndi fada timawati Bull-dozzer. Each ministry he held. Mbiri imacta kuzaza. Yozaza Chanco library
@GenWealth728
@GenWealth728 2 месяца назад
So successful🎉🎉🎉
@YamikanBanda-z7z
@YamikanBanda-z7z 2 месяца назад
Akatundu omwe anamwako ink
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 месяца назад
Kani ndinu aku Mozambique now your talking
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 месяца назад
Chaponda tchaya iwe kupakana matope ku DPP
@ChifundoZimba-jh7dh
@ChifundoZimba-jh7dh 2 месяца назад
Kkkkk DPP akuti zasokonekera no unity
@damianokachingwe3531
@damianokachingwe3531 2 месяца назад
Mbava yaikulu ija yabweranso kd kkkkkkk
@NikolasNanawe
@NikolasNanawe 2 месяца назад
iwe mbava kwambir😂😂😂😂😂😂
@kelvinmphande3754
@kelvinmphande3754 2 месяца назад
Ati ophunziranso
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 2 месяца назад
Chaponda mchimanga
@yusufsadic2930
@yusufsadic2930 2 месяца назад
Ufa bwanj kumachit kt umadziw choona mumtim mwakom
@Lingstone-r3z
@Lingstone-r3z 2 месяца назад
Please tell us which,, you want to tell us, not where ever you go,, no ,,,kkklkkll
@usherjamson174
@usherjamson174 2 месяца назад
Mwanena zoona muthu wakulu awa anyanyadi
@AlickChima
@AlickChima 2 месяца назад
Katundu
@paulmanyamba5437
@paulmanyamba5437 2 месяца назад
Amenewo ndiye anthu oyendetsa boma osangoti ndinali mkulu wampingo kwachisindo 😂😂😂
@Okalekale
@Okalekale 2 месяца назад
@@paulmanyamba5437 Anayendets boma kwa zaka zambiri zoona,koma nkhani ndiyotu panopa Malawi alipati?,wasintha kapena ayi?,palibe chimene anapangila aMakawi mbava izi,kuphunzira kuphunzira chani l?,kwatipindulira chani kuphunzira Kwao?,anthu okanika kuyendetsa dziko,kwawo ndikuba chimanga basi.Binfubyekhabndi amene anali ophunzira kwa phindu komanso kuli anthu ophunzira kwambiri kuposa manyakawa ku Malawi chabe samapanga nawo nyansi za ndalezi,wake up man.
@giftmwale8475
@giftmwale8475 2 месяца назад
Kani ndinu aku Mozambique abakha inu😂😂😂
@henryphiri6100
@henryphiri6100 2 месяца назад
Kufotokoza mosabisa
@EkaliKapito-y8q
@EkaliKapito-y8q 2 месяца назад
Dolo
Далее
I tricked MrBeast into giving me his channel
00:58
Просмотров 4,6 млн
Kodi A Nankhumwa Akulowela Kuti - Richard Mphepo
26:50
Cruise 5 with Msulira Mathews Sapemba Tisatayane
58:13