I love utm president ndi time wanga onse, Mulungu akutetezeni sogolo lo Wala Lili mu manja mwanu vice president Usi. Inu kukhala president no doubt Malawi will be really Malawi we want
Mukusewera ndi mizimu ya SKC and all the other beloved citizens of this land who died in Chikangawa, trying to divide the party koma simufika nazo patali.... God will surely punish you.
Zopusa ukanaziwa kuti ndi zakutha why you killed chilima ur days are numbered unachenjera mozitama kwambiri hiyaaa koma kwa ine ndinasiya kukukonda full stop pati