Thank you very much bakili muluzi zimene zikupanga boma lachakwera akuziwa ndimulungu ngat tinawalakwira kuwavotera watching from Mozambique never give up bg brother timakunyadirani kwambir potiwululira zisisi zambavazi
Is this man king of voice? a Malawi nsanje ndiye unakula, ndipo kusangalatsa andale. ine I do support zimene Dr. Michael Usi amanena ndi kuchita. And ulemu wanu olemekezeka a Vice president Dr. Saulosi Chilima,you soo gentle and calm.
Tsopano lesson yanji ku malawi.inde tikufuna kusinthaso mtsogoleli koma sitingavotele 80years reader kuti chiyani.msaka,mwanamveka ndi ena alipo but why 80yrs 😢