Wapanga bwino kuyimba ndi jetu wamva nda download chifukwa Cha feat ndi jetu osaziwa kuti iwe Fred mw muli uthenga ndukupanga follow Zowonadi mvuto ndi nyumbamu nkhani ndi nyumbamu Favorite song Zowonadi anthu amakhala masiku atatu osapanga even ka 4times kamakwana km eeh Fred mw
I was in min bus this other day,, nyimbo iyiyi ndiyomwe inayamba kuimba I was just smiling 😁..the story telling chemistry between you two was just wow... this is good song Man Fred
Overall, there is a big difference with your previous songs.. Hard working pays brother .However ,your far to reach there but wth dedication and perseverance you can reach there our young star.... Take note that there are ups and downs in a every industry , therefore focus on your hustle and move . Proud of you 🎉