And Fredo he got the vision for young generation for Malawi 🇲🇼 same like the way he was thinking the let vice president Saulos Klaus Chilima. and SKC always he was thinking about the youth.
Don't come here to attack the ideologies of your friends. Come with what people can support you with. What Khad is doing can put the government under pressure and achina Fredo awo apeza mwayi. MCP sukuyidziwa bhobhoo dolo. Political ground ya Malawi pali peace????
Akulu akulu ife amalawi sitidziwa chimene tikufuna, ndife anthu osochera that's why a lot of people are manipulating us, the reason is one timadzikayikira that we can develop this country, two we don't love our country, three we are not creative and productive ndife anthu a ulesi chimenecho tizidziwa four multiparty is not a tribal thing boma timayisadutsa zaku nyumba, remember blood is thicker than water. We, as malawians, we are compromised. What am edging you malawians, please let's be patrotic,loving,creative, let's not worry too much we are wasting time, Politics shouldn't limit your ambilities, Rest in peace Chilima and God bless malawi
If the youth can rise up and unite to save this country, i don't doubt Fredo. Currently the youngest president in Africa is only 35 and akupamga zinthu zokupsya kuposa nkhalamba zinazi ,,more fire Fredo 🔥
Iwe iwe galu iwe iweyo sizikuwawa cifukwa amene anafa si abale Ako dikilani muona zi tipange ku siteti house ndi ku parameters tagwilizana kale ndi zigawenga zamailo ena tiotcha parameter pamodzi ndi steti house agulu cifukwa chani mumadana ndi chilungamo
Some how it makes sense, this is freedo and wachinyamata and he is kind and he is responsibility to fight for Malawian people, we youth can rise if this guy will be in power because he will also consider us. SKC was a youth leader as well , 75% of SKC 's heart was to achinyamata. Let's trust freedo my thought naneso
Mukudziwa TV, you are saying the truth. Ma social media group mu and pa RU-vid pano, enake agundika kukamba zinthu zambiri, zosamveka zopanda ma umboni, zinthu zopanda logic. Ambiri akungoti a Chakwera achoke koma kuwafunsa, tsono muyikapo ndani a chakwera akachoka answer zero. Koma basi mphuzo, mwatumidwa inu, ana njoka inu, eh inu akupatsani zingati a MCP. Ife sitidya za MCP koma zimasakomele mbuzi kugunda galu, timakonda kunena kuti boma lidzitiyankha mafunso kuti ndalama zayenda bwanji, eh chakuti apanga bwanji, nde ine ndikuti ku opposition, ma activist, mabungwe, anthu tidzifunsanaso mafunso. Inu awuje mukati boma lapha a uje ndipo muti muli ndi umboni, tiwonetseni umboni aliyense awone, mukamati boma lisapange chakuti, inuyo boma lipange chani kapena inuyo munakapanga bwanji? A ambiri tikumangonyoza boma mchigulugulu. Mungoona ma comments ali pamudzi pano. Stop and think for yourself individually, research for yourself, musananyoze boma kapena kubakila munthu amene akunyoza boma chonde a Malawi.
Can I be honest with you? Peace is what has brought us problems in the first place. When I say peace I say the art of not actions against these old politicians. It hurts me when we youth allow these elder generations to dictate our lives. We were told by them that we are the future so why are they in our future now? Malawi wake up. Stop talking about peace and get to the real deal we youth need to take over by all means the time for listening to these politicians make promises is over, we should bring change. Am not saying let's be violent or do more protests but I am lets take action on taking over the country and start fixing it ourselves. Take it or leave it but I have started making moves for overtaking these old thieves
leadership comes from God the almighty so don't be confused with the age of man. you can be educated or older still more you are not the leader. i personal don't like people who rush to condemn someone without having enough time to analyze what someone says. we call issue based analysis
Iwe usatipangilire zochita naweso,,wausiru etii mapwara ako wafuna ifeyo timvere za iweyo nde wanzeru tiye uko galu,,,siukuziwa anthu tili ndi nkwiyo Apa nde daily iwe uzingotukwanidwa ukamabwera ndi manyaka akowa
And Manganya they fired him already from UTM party so why Chakwela he want Manganya to be the vice president and that's nonsense. am asking you mr murder Chakwela just put Fredo on this position. and don't put Manganya on this position for vice president because even him he is evolved of this accident for SKC the let vice president. Thanks to all 🇲🇼 Malawian and let's put this flag to Fredox .❤
Fred is intelligent enough yes but in politics he's prematured, ndale nkanyimbi kanyama konunkha zedi musiyeni Fred aziphunzile ndale first bwino lomwe I understand your narrative and it does make a reason and I support it but at this stage Malawi requires well experienced leader to pull up and stretch the broken bones together at least then wachinyamata azagweremo 2030😢😢
Aaaa koma iwe nde ndanitso AGALU A MCP NDALAMA ZAMAGADZI AKUKUPASANI A MCP IDZI MUDZAFA IFA YONVETSA CHITSONI NDE MAYETSA NDINU MUMWA MUMAWONTCHA ZIPATALA KATUNDU KATUNDU WAANTHU KUPHA WA POLICE KUWONONGA DZINTHU LELO MUDZIWAUDZA ANTHU KUTI DZIWONETSELO SIDZAMBINO AAAA IWE GALU KWABASI NDI MCP YAKOTLYO ANTHU AMAGADZI