ZIKUONEKA ZABWINO NDITHU , koma muzilimbikitsa ma mission opindulitsa , ngati za xool, pakhale ambiri opita kuxool, ena zichita za sound , za mipira, pakhale ma technician okonza zinthu ndizina zotero kuti anthu aziphunzira za phindu , ndikaona story line yanu mukungolimbitsa UHULE basi,