Sindimakonda kupeleka comments koma ndangofuna kuyankhulapo pang'ono. Nyimboyi ndi hit and it deserve more views . Koma zomati uku kuponya uku kuponya it seems like sizinthu za bwino let's help oyimba athu popanga views Nyimbo zawo pa u tube, ngati kuli kuponya pa Facebook try to use link kuti anthu azizayiwonera pa u tube pomwepa Palibe support yomwe tingawapatse oyimba athu than kupanga view Nyimbo zawo pa u tube.
He is basically saying our love story will end in penalties, once u try to disappoint me I will bewitch u, if u know u can't love me perpetually u should dismiss me b4 I love U more, but if u wanna use and disappoint me I will not revenge by beating or insulting u I will just bewitch u, am tired of being used, this our love story will end in penalties.