Ma goalkeeper trainer athu they're not doing well at all,, saphunzisa anthu positioning bwanji ma goalkeepers athu nthawi zambiri amachinyidwa coz of kuchoka pagolo nanga akufuna aputche mpira akugwa kuchedwaso kudzuka Ma reaction amavuta amakhala slow paziganizo ineyo i don't think Nyasulu will help us in with that problem coz with this goal he is below par yes amagwira ma penalty koma ngati akufuna improvement akhale odekha komaso osunga position