Тёмный

Hilco and Ching'axy - My Wife ( Plan B Season 1 Episode 3 ) 

Hilco
Подписаться 36 тыс.
Просмотров 506 тыс.
50% 1

Plan B, New Episode Out 🔥
#hilco #ching'axy #wakuba #ponit #malawi #trending #maluwa #hilco #ching'axy #planB #malawi #comedy #trending

Опубликовано:

 

1 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 624   
@AlickGobede-qx8wd
@AlickGobede-qx8wd 5 месяцев назад
Respect himself (Uzipase Ulemu wekha) kkkkk chingaxy fan tipangeni like tibwereso plz 😂😂
@SanteRamzey
@SanteRamzey 5 месяцев назад
Mpakana kukangana ndi nzawo wa madam kkkk akuti how many maminits kkkkkk nde avekere lero silachizungu kkkkmmm
@josephmawaya7408
@josephmawaya7408 3 месяца назад
Kkkkkk aliyense pa ntchito yake
@JoshuaJames-s5o
@JoshuaJames-s5o Месяц назад
Kkkkkkk koma
@FrancisNamaona-wh5to
@FrancisNamaona-wh5to Месяц назад
Muli bho guys km mupange zoti mukamalizise kameneka❤
@MillicaPhiri
@MillicaPhiri 5 месяцев назад
My wife my wife koma ukugona kumiyendo chingaxy 🤣🤣 like ndibweleso
@HenryPhiri-hq5jp
@HenryPhiri-hq5jp 5 месяцев назад
Umakwana Watching from Zambia 👠😅😮
@maryChidoola
@maryChidoola 4 месяца назад
I'm the guard
@HifaBusiness-p7j
@HifaBusiness-p7j Месяц назад
Umatha chingaxy
@LenadChelute
@LenadChelute 13 дней назад
@LenadChelute
@LenadChelute 13 дней назад
@Veronicaleman-eg7jd
@Veronicaleman-eg7jd 5 месяцев назад
Who comment and like before watching like me let's gather here
@SdjcNgophiShadreck
@SdjcNgophiShadreck 4 месяца назад
Ching,ax ndi dolo
@EmmanuelMoses-ut3zw
@EmmanuelMoses-ut3zw 5 месяцев назад
Ching'aning'an nd aktundu et am the head of controller 😂😂😂😂😂your flowers abambowathu
@OmahMalinga
@OmahMalinga 5 месяцев назад
Hilco fans let's gather here
@islamuidrissa
@islamuidrissa 5 месяцев назад
😂😂😂😂
@johncassimu5433
@johncassimu5433 4 месяца назад
ching'akise kkkk kma mungokwatilana bas kkkkkkkkkk
@NyumbaChifunilo
@NyumbaChifunilo 13 дней назад
Ise umati😂😂😂😂😂
@TsuzenThomas
@TsuzenThomas 5 месяцев назад
Respect him self ( uzipase ulemu wekha 😂😂😂 Hilco & Ching'axy fans let's gather here n give them flowers
@Dianabanda902
@Dianabanda902 5 месяцев назад
If possible include English Subtitles in the coming episodes, because this will hit an international level.
@HilcoMw
@HilcoMw 5 месяцев назад
Will consider that,thanks for the idea
@Dianabanda902
@Dianabanda902 4 месяца назад
@@HilcoMw most welcome 🥳🥳
@giftpenjankaungah8104
@giftpenjankaungah8104 4 месяца назад
Koma ka m'dara aka ndikochenjeretsa eeeeh
@peterblazio5293
@peterblazio5293 4 месяца назад
Ching'aning'ani fans let's gather here 💖❤️💖Hilco❤️💖💖 She got beautiful voice matchona watch from Greenland I miss Home 🇲🇼❤️❤️
@maxyfreeman9691
@maxyfreeman9691 5 месяцев назад
Lero ndi lachinayi silachizungu....kkkķk
@Mada_kay
@Mada_kay 5 месяцев назад
😂❤
@CharlesMuhammad-s3w
@CharlesMuhammad-s3w 5 месяцев назад
Komatu Hilco ndibomba
@maxyfreeman9691
@maxyfreeman9691 5 месяцев назад
Aise wayambatu zenizeni kkkk
@ANDIWOTCHIMedison
@ANDIWOTCHIMedison 18 дней назад
Komatu medisoni
@NaomiMushanga
@NaomiMushanga Месяц назад
Continue guys
@IssacBwanari
@IssacBwanari 10 часов назад
Ching'aning'ani ndi katundu omanga ndi mawaya😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@EkariRestaurant
@EkariRestaurant 4 месяца назад
😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂😂
@bonifacelipenga6315
@bonifacelipenga6315 5 месяцев назад
Madala chinga'ning'ani akuti kaya gate yi imayenda bwanji hahaha 😂😂😂😂😂😂
@jezalakaphuka7325
@jezalakaphuka7325 5 месяцев назад
Wosokoneza kwambiri
@AungunKadzinja-wv2uc
@AungunKadzinja-wv2uc 4 месяца назад
Chphanya more fire umativesa kukoma Koma musamachedwe kutulusa Guys
@nalisonkaimba3400
@nalisonkaimba3400 5 месяцев назад
Head of controller 😅😅😅
@ShafieMwaleabiyoni
@ShafieMwaleabiyoni 4 месяца назад
Lkkkkk chingaxy
@mphatsolupiabanda6910
@mphatsolupiabanda6910 5 месяцев назад
Kkkkkk ngat camera man waseka ine ndinda😅😅😅😅
@MosesShaba
@MosesShaba 5 месяцев назад
Mwabwera boiz🔥 camera man anaseka pena
@stevengwiranipansi21
@stevengwiranipansi21 3 месяца назад
Ndipo akumaseka heavy azitolere
@AubreyKasonga
@AubreyKasonga 4 месяца назад
Ine olo zivute zitani Chingaxy sangakhale nzanga chifukwa sachedwa kunena ma fact 😂😂😂😂😂
@SylviaMsukuma
@SylviaMsukuma 27 дней назад
Chief security ,,eti undipase zakudya ,ndizophakaphaka ,,ma conflicts 😂😂👍💥,,Ching'axy
@YamzyNedson
@YamzyNedson 4 месяца назад
I'm the head of the controller 😂😂😂😂😂Ching'axy fanz we have a meeting paselipa.
@2023edition6
@2023edition6 5 месяцев назад
Ching'axy sazatheka
@Ishmaelmsash5598
@Ishmaelmsash5598 4 месяца назад
Ma guys enawa apange improve acting skills.....koma zili boh
@LanwellJangiya
@LanwellJangiya 5 месяцев назад
Et ukuonela zee world...km pa tv amaonesa ku Starlife...they thought we will never know AAA Malawi sazatheka
@PatrickTembo-lm1ih
@PatrickTembo-lm1ih 20 дней назад
Kkkk 😂😂😂 kusamalira ntchito 😂😂😂😂
@JumaDollo
@JumaDollo 5 месяцев назад
Respect himself 😂😂😂
@LukeManda
@LukeManda 4 месяца назад
Komatu imeneyo amaonera UPILE si Zee World ndi Starlife AIDA watinamiza
@ZephaniahMajamanda
@ZephaniahMajamanda 5 месяцев назад
ching'axy mwalakwitsa kumulowetsa nkaziyo pa gate, amakujeda ndi sister wake was hilco🤣🤣🤣🤣🤣
@GeofreyDyton-eg7ty
@GeofreyDyton-eg7ty 4 месяца назад
Bwanji osangoponya video yonse anthu awonele Koma kumangoyidula zachamba
@LimbikaniNyirenda
@LimbikaniNyirenda 5 месяцев назад
Ching'aning'ani tsopano, uli ndimphanvu et? Mpaka kukankha munthu wathupi choncho??
@STEVENMPONDA-o6r
@STEVENMPONDA-o6r 2 месяца назад
𝐂𝐇𝐈𝐍𝐆'𝐀𝐗𝐘 𝐖𝐚𝐩𝐚𝐚 𝐆𝐀𝐓𝐄𝐄 𝐲𝐚𝐤𝐞𝐞
@MacdonaldMasamba-e2x
@MacdonaldMasamba-e2x 5 месяцев назад
Km ching'axy mpaka head of states😀😀😀Head of the Controller 😀😀
@CollinsChimsendenji
@CollinsChimsendenji 4 месяца назад
Chizungu wachiyambitsa yekha ching'ax nde nzake wayankha chizunguso bas avekere lero sila chizungu nd lachinai limene kunadutsa satana kkkkkkk
@victoriamambusha5362
@victoriamambusha5362 5 месяцев назад
😅😅😅ching'axy fans let's gather here😊😊
@InnocentKatius
@InnocentKatius 4 месяца назад
😂😂😂 dolo
@STEVENMPONDA-o6r
@STEVENMPONDA-o6r 2 месяца назад
𝐂𝐇𝐈𝐍𝐆'𝐀𝐗𝐘 𝐔𝐦𝐚𝐤𝐰𝐚𝐧𝐚𝐚 𝐨𝐬𝐚𝐦𝐩𝐡𝐰𝐞𝐤𝐞𝐬𝐚 𝐍𝐓𝐂𝐇𝐈𝐓𝐎 𝐲𝐚𝐭𝐡𝐮𝐮 𝐢𝐦𝐞𝐧𝐞𝐲𝐨
@francismanda
@francismanda 4 месяца назад
😅😅😅😅
@JTUPHIRI
@JTUPHIRI 5 месяцев назад
koma mukumachedwatu mpaka ma followers kukuyiwalani? tamaponyaniko mwina pa week kamodzi bobo, nanga mpaka 2months tkumakuyiwalanika
@FredKhembo-m7j
@FredKhembo-m7j 2 месяца назад
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@AndrewKaumba-gq1vb
@AndrewKaumba-gq1vb 4 месяца назад
Nkhani yavuta ndi ya zolowa ndi zotuluka
@AliJackson-gf3wj
@AliJackson-gf3wj 5 месяцев назад
muli boh vuto kakufupika komaso zikutenga nthawi yayitali kuti ibwere yina komaso try mawu azimveka bwino bwino kumakwezako look line ya mahope ako voice ya nyatwa koma line ya akazinu mukabisa voice ndinayesela volume mpala 200 ndimayesa mwina vuto ndi phone yanga ayi ndithu
@yolamujrdikamdimajr
@yolamujrdikamdimajr 4 месяца назад
Ili bhooo koma try to change angles isamakhale ngati mukujanbula pa stage
@troychikhwaza-Mw
@troychikhwaza-Mw 4 месяца назад
Kubwela kuno undipatse minyama chingaxy umatha
@AmirGhafoor-bk2le
@AmirGhafoor-bk2le Месяц назад
Kod sister firm imeneyi ikupitirira kapena ayi please tiudzen kungowonera part 1 end of two bas amateur cc
@ANDIWOTCHIMedison
@ANDIWOTCHIMedison 18 дней назад
Kkkkkkk medisoni usi MALAWI kani yabwino yosakalasa
@NgomaRaheem
@NgomaRaheem 5 месяцев назад
Chifi sekilite kkkkkkkkkkkkk
@Ashlyzanel-kb4km
@Ashlyzanel-kb4km 4 месяца назад
Head of state kkkkkkkkk
@MtalimanjaMulawo
@MtalimanjaMulawo 5 месяцев назад
Koma sister wa Hilco mmm❤
@piliranikasambara3066
@piliranikasambara3066 4 месяца назад
Muli thako2😂😂🙌🙌😂😂😂
@GovatiNickson-h7c
@GovatiNickson-h7c 3 месяца назад
zoona tikulandira phunziro pitirizani kuphunzitsa nthundu wa Malawi
@kellsonOfficial
@kellsonOfficial 4 месяца назад
Apatu your not kulowa eish....😂😂
@QassimMuhammad-ol2td
@QassimMuhammad-ol2td 4 месяца назад
Mukufupikitsa kwambiri ikutha isadatikwane thanks
@hastingsphiri3071
@hastingsphiri3071 4 месяца назад
Ching'aning'ani sukuopa thupi lonselo😂😂😂
@AndrewKaondo-f7n
@AndrewKaondo-f7n 11 дней назад
😂😂😂😂😂 amapanga choncho ndiwa ntchito kd😅
@VincentMisiasi
@VincentMisiasi 4 месяца назад
Kod simungangotulutsa tose pakamodzi😂
@stormchatepa134
@stormchatepa134 5 месяцев назад
Camera yabwino I lyk apa mukuti head of controller
@Gracendau-d3l
@Gracendau-d3l 4 месяца назад
Zili bwino koma mumachedwetsa abale mpaka kuyiwalako ife
@LexmanPhiri
@LexmanPhiri 4 дня назад
Kkkkkkkk
@edsonmghandira4648
@edsonmghandira4648 4 месяца назад
Ndangosangalala mmene wamubwezera dutuyo
@stevezunda1944
@stevezunda1944 4 месяца назад
Koma ichi? Ati iwe walowa bwanji apo pa gate pakakhala munthu,,,Ali iyeyo
@northbusymw
@northbusymw 5 месяцев назад
It's too short plz,thawi mkanaonjezerako pang'ono
@ANDIWOTCHIMedison
@ANDIWOTCHIMedison 18 дней назад
Agogoaka akuonele oipa wapopano
@GiftLajah
@GiftLajah 9 дней назад
Migration yoona zotuluka ndi zolowa kkkkk
@MayraThaund
@MayraThaund 6 дней назад
Km upil nde ndiwangat ndapang kal plan yaukwat
@MikeBanda-rr2fo
@MikeBanda-rr2fo 5 месяцев назад
Mukumachedwa kuturusa ina
@JosephPhiri-dg3ps
@JosephPhiri-dg3ps 5 месяцев назад
🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣
@JOSEPHPHIRI-ve6ls
@JOSEPHPHIRI-ve6ls 4 месяца назад
I am the Head of controller 😅😅😅
@MagretSaid
@MagretSaid 5 месяцев назад
Mukumachedwa kutumiza chonchi bwanji
@LovenesLovenes
@LovenesLovenes 4 месяца назад
Respect himself emweyo ching'akisi iwe ndi one
@goodsonkhulani7470
@goodsonkhulani7470 5 месяцев назад
Ma criminal 😂😂😂😂😂😂
@abduhrwahmaansilverbanda4908
@abduhrwahmaansilverbanda4908 5 месяцев назад
Ching'azy uyu akanakhalamo mnyumbo ija thithu uchita ufusa tea aaaaaa
@AmadumtungasudiSudimtungaamadu
@AmadumtungasudiSudimtungaamadu Месяц назад
Hilco am fine zokukhalan inuo bc❤❤❤❤🎉🎉
@SydneyChilipa
@SydneyChilipa 5 месяцев назад
Komatu ching'axy unali serious
@JoshuaJames-s5o
@JoshuaJames-s5o Месяц назад
Koma chingax ati mutu wabanja iyeyo KKK 😅😅
@alfredpower2334
@alfredpower2334 4 месяца назад
Ati kungochoka uko criminal basi😂😂😂
@rebergiftmaniwa8291
@rebergiftmaniwa8291 4 месяца назад
😂 🤣 🤣 🤣
@FYNESBEATSRECODS
@FYNESBEATSRECODS 8 дней назад
Kkkkkk
@SheriffAbduh-tv8sn
@SheriffAbduh-tv8sn 4 месяца назад
The last man akupanga manyazi why? Mr chiduntu
@EvansMakwinja
@EvansMakwinja Месяц назад
Koma sister wa Hilco ndi katundu waboma
@macdonaldkainga
@macdonaldkainga 2 месяца назад
Ching'aning'ani head of controller 😂😂😂
@genesiomiguelmiguel7777
@genesiomiguelmiguel7777 5 месяцев назад
kkkkkkkk🤣🤣🤣🤣
@alicechilembo7101
@alicechilembo7101 4 месяца назад
Ati, "respect himself"azizipatsa ulemu😅
@FrankBoti
@FrankBoti 11 дней назад
Kkkkkkk
@ThandieHarry
@ThandieHarry 4 месяца назад
😂 akut ngati Tomas didimu osakhulupilira
@Jaliwe--jally---hy3tf7bl9w
@Jaliwe--jally---hy3tf7bl9w 4 месяца назад
Vuto lake ma episodes waaa mumachedwetsa kutulutsa
@MajiduAsick
@MajiduAsick 4 месяца назад
𝐊𝐨𝐝𝐢 𝟒 𝐢𝐭𝐮𝐥𝐮𝐤𝐚 𝐥𝐢𝐭𝐢 𝐡𝐢𝐥𝐜𝐨
@maxwelllevison6398
@maxwelllevison6398 5 месяцев назад
😂😂😂😂😂
@EniaChicco
@EniaChicco 5 месяцев назад
😂😂😂😂😂
@HamzaAyame-ch3et
@HamzaAyame-ch3et 5 месяцев назад
😂😂😂😂😂
@ezralevison
@ezralevison 5 месяцев назад
😂😂😂😂😂
@PeterChinoko
@PeterChinoko 5 месяцев назад
😂😂😂😂❤❤
@RahimKamisoni-up8bo
@RahimKamisoni-up8bo 4 месяца назад
Nkhani za tea zikuyenda bwanji 😂😂😂😂
@jackbello2170
@jackbello2170 4 месяца назад
Ma criminal mufuna kupanga chipongwe madam
@LucianoZebe
@LucianoZebe 12 дней назад
Mumakwana mutu wanyumba ndine😂😂
@BeyardThenifod
@BeyardThenifod 14 дней назад
Abambo athu phokoso heavy😂😂😂
@alexmajanja3179
@alexmajanja3179 5 месяцев назад
Kaya imayenda bwanji? Munthu umayendetsa daily 😂
@phillimongulumba1918
@phillimongulumba1918 4 месяца назад
Koma onjezerani ma minutes kakuchepa ,
@TroubleRichard
@TroubleRichard 4 месяца назад
❤ ❤ ❤❤❤❤
@benardphiri4465
@benardphiri4465 4 месяца назад
🤣🤣🤣🤣
Далее
KHASU-Malawian movie_PART 1[Akila films official 2024.]
1:06:28
ХОМЯК ВСЕХ КИНУЛ
10:23
Просмотров 583 тыс.
Top 9 Ya  Anthu Olemela Kwambiri Kumalawi
8:17
Просмотров 84 тыс.
MFUMUKAZI COMEDY  SERIES 21/12/2022
27:04
Просмотров 162 тыс.
Usauver S09E02   AKAZANU ASOWA
16:28
Просмотров 218 тыс.
RESERVE BANK - Episode 171
9:15
Просмотров 29 тыс.
MILANDU PA OKALA....Episode 24
11:54
Просмотров 311 тыс.
Mr Jokes "WACHAKE COMEDY SERIES" episode 6 (Full Video)
15:12