Тёмный

Honourable Kanyasho akufotokoza zomwe zidachitika posakasaka ndege ya Saulos Chilima. 

Malawi Page
Подписаться 78 тыс.
Просмотров 105 тыс.
50% 1

SUBSCRIBE here for more videos goo.gl/aYvIXK
Malawi videos in English and Chichewa

Опубликовано:

 

28 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 83   
@FredrickPhiri-vc6we
@FredrickPhiri-vc6we 3 месяца назад
😭😭😭 I'm still crying todate. Mulungu pakuti munalora chabwino,
@mikemakamo7360
@mikemakamo7360 3 месяца назад
Chakwela wayigwila ntchito under ground koma mulungu ngwamphamvu ziwululika
@maggie793
@maggie793 3 месяца назад
& even members of his party - why didn't they start making calls to inquire when the plane didn't land when it should have? When your boss is running late, you are supposed to be aware - communicate. When he is 15 minutes late - you start making calls inquiring where he is. You're supposed to be on your toes - time keeping.
@nathanphiri4029
@nathanphiri4029 3 месяца назад
Ndipo ku maliroko asapiteko ndithu😢
@johnkatapeh7182
@johnkatapeh7182 3 месяца назад
😢😢😢
@FloridaMwale-ft3uu
@FloridaMwale-ft3uu 3 месяца назад
Chilungamo chiyende ngati madzi 😭😭😭😭
@nelsonmorris4352
@nelsonmorris4352 3 месяца назад
Malawi tiphana sure
@YASSANWADO-jk4xp
@YASSANWADO-jk4xp 3 месяца назад
APresident akuziwapo kanthu musawope mwafufuze bwino or kumafusa fut uli pamutu pawo alongosola moveka bwino amene vuto ndilibe phavu ndikanagwila ndekha ine amen walah ndikanapha ine 😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭😭
@Memorykamanga-qb7eo
@Memorykamanga-qb7eo 3 месяца назад
𝐁𝐮𝐭 𝐰𝐡𝐲??😢😢
@StevenKamanga-ow6iu
@StevenKamanga-ow6iu 3 месяца назад
Chakwwera press briefing
@loveruthphiri6645
@loveruthphiri6645 3 месяца назад
Zowawa zopweteka
@HajiAbdul-w5n
@HajiAbdul-w5n 3 месяца назад
Musalole kuti akale nawo kumwambo wamalirowo
@hysonkayanja5696
@hysonkayanja5696 3 месяца назад
Mulowere uku?????
@Justman34_dislike
@Justman34_dislike 3 месяца назад
MCP chipani cha magazi...
@AggieBanda-o2b
@AggieBanda-o2b 3 месяца назад
Eeeh till today I cant believe he is gone
@DennisTobias-b4r
@DennisTobias-b4r 2 дня назад
Khulupilirani ndithudi he's gone forever
@Memorykamanga-qb7eo
@Memorykamanga-qb7eo 3 месяца назад
😭😭😭😭
@raytavares2256
@raytavares2256 3 месяца назад
Bwinotu sis kanyasho angakupweteni mmene aphera malemu CK.
@feehasaidid.r.d
@feehasaidid.r.d 3 месяца назад
Utsogoleli wachilendo umene anthu anathana nawo 1994
@Nai3-j5i
@Nai3-j5i 3 месяца назад
kuma hoyo shoga atakuja kufirwa musenge huyo na sisi tumeumi sana na tabia za huyo chota chakwera ndi pamunyelo × 100
@doreenkaliati3166
@doreenkaliati3166 2 месяца назад
Chilungamo chimanasura mmmmm koma ai mpaka lero mawu ndilibe
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 3 месяца назад
Good speash...even president him self mst not there we dnt need him
@HarrisonMwanga-xy4sc
@HarrisonMwanga-xy4sc 3 месяца назад
You must mix, with English bcs some people don't know chintchewa, God be with Dr chilima, soon the truth comes out
@GreyHauya
@GreyHauya 3 месяца назад
I enjoy my language sir i dont like English oky👀
@VegmanYiw
@VegmanYiw 3 месяца назад
Anawuza kuti asayankhule english
@phiri-tv
@phiri-tv 3 месяца назад
The truth shall set the people free. R.I.P Saulos Chilima 😢
@PatrickKhutuliwa
@PatrickKhutuliwa 3 месяца назад
Pali anthu 5 omwe akhudzidwa ndi ifayi modzi mwaiwo ndi chakwela, kunkuyu, zinkhale ng'oma ndi mkulu wa army
@alexmkolongo3089
@alexmkolongo3089 3 месяца назад
Akangoyelekeza kubwela zikhale aphedwa
@user-ii5ke9pc1q
@user-ii5ke9pc1q 3 месяца назад
SKC lived and died honorably. But if not careful many of his inner cycle will live and fie in disgrace
@Nai3-j5i
@Nai3-j5i 3 месяца назад
kuma hoyo shoga atakuja kufirwa musenge huyo na sisi tumeumi sana na tabia za huyo chota chakwera ndi pamunyelo × 100
@KamizaElizabeth
@KamizaElizabeth Месяц назад
Ape ndipamene pakanayambika nkhondo but we Malawian we are very stupid..........😢😢😢😢😢
@GiftJulius-gx2kb
@GiftJulius-gx2kb 9 дней назад
Mwana olo mbuzi ikasowa anthu sakhala pansi kufufuza.vp kugwa ndenge yake .ayitiimike kufufuza mpaka mnawa ayindithu
@GreyHauya
@GreyHauya 3 месяца назад
President akudziwapo kathu
@thondoyaenterprise3795
@thondoyaenterprise3795 3 месяца назад
What does he know ?
@chrisschikozera7271
@chrisschikozera7271 3 месяца назад
He knows everything.....that president is evil man of God ​@@thondoyaenterprise3795
@Betty-fe9ql
@Betty-fe9ql 3 месяца назад
The truth ​@@thondoyaenterprise3795
@rashidadan2533
@rashidadan2533 3 месяца назад
Don't ever and ever trust president chakwela plz , don't Soon you will believe me on this .
@Betty-fe9ql
@Betty-fe9ql 3 месяца назад
Kongelesi mwampweteka Chilima mwalaka kwambiri
@Nai3-j5i
@Nai3-j5i 3 месяца назад
Chakwera ni mfiti uyo atimaliza mumpheniuyo uzafa ni ntima I've mnyelo
@RuptureBear8501
@RuptureBear8501 3 месяца назад
Crocodile Chakwera wadya mzakeyo ...Boma lankhanza ili
@SibusisoMlenga
@SibusisoMlenga 2 месяца назад
Anthu akupemphaso mmeneri wa mulungu mmalo mwa mulungu
@Furnituremaker-vt8ku
@Furnituremaker-vt8ku 3 месяца назад
May his soul rest in peace
@maggie793
@maggie793 3 месяца назад
Something smells fishy. The plane fell not far from houses. You mean in all those houses there's no-one with a cellphone who could have phoned someone or sent a video? What happened to curious onlookers? In Malawi everyone is a reporter, why couldn't they report this one? Some of those people in the plane could have been alive but because of the unecessary delays........ Their cellphones, the blackbox in this case it didn't burn. Probably it would have helped for autopsies to be performed on their bodies as well.
@LeendaDeborah2005
@LeendaDeborah2005 3 месяца назад
One of the villagers narrated exactly what happened but he was cut off
@maggie793
@maggie793 3 месяца назад
@@LeendaDeborah2005 That's not right. Allowing them to talk about what they saw etc etc will bring healing and closure to the family and the nation rather than leaving everyone with a buch of questions for a week now.
@collennyadile8179
@collennyadile8179 3 месяца назад
mcp will never change amene akusapota mcp ndi satanic fiti zoyipa kwambiri kupha munthu chifukwa cha udindo ngati mukanawina popanda chilima
@apatsachintengo
@apatsachintengo 3 месяца назад
Am shaking 😢
@Angelchinse
@Angelchinse 3 месяца назад
Panyapake chakwera ng'undu wake
@richardkamundi2965
@richardkamundi2965 3 месяца назад
Fog yomwe inapha Chilima siyokhalitsa
@chirwaellace1093
@chirwaellace1093 2 месяца назад
Zoophyatu ndi bomali
@wilsonfelix6559
@wilsonfelix6559 3 месяца назад
Musamati president akudziwapo kanthu muziti wapha anthu osalakwa satana
@Coach-Viv
@Coach-Viv 3 месяца назад
The man has been assissinated. Malawi has lost a great leader.
@FrankTsabola
@FrankTsabola 3 месяца назад
MHSRIP
@GIGSTUDIOS-tf2hx
@GIGSTUDIOS-tf2hx 3 месяца назад
Rest in in Doc.saulos chilima
@victoriachapweteka6704
@victoriachapweteka6704 3 месяца назад
Iiiii abale kulakwa😢
@HumphreyWillima
@HumphreyWillima 3 месяца назад
Kodi iwe Kanyasho, umatha kuona chikangawa yonse at once kuti kulibe asilikali kwinako?...kapena ukunena zakomwe Iwe unali?
@giftjimu6685
@giftjimu6685 3 месяца назад
Chakwera mwini game
@MustaphaCassim
@MustaphaCassim 3 месяца назад
A utm plz finyeni chakwera mosese chimwendo ndi henly wakulu wa silikali akudziwapo kathu plz ngati mumakonda chilima osalandi bazi chifukwa panopa chakwera akhala bussy kugawa ma bazi .
@Kenji_Trupa
@Kenji_Trupa 3 месяца назад
12 soldiers must be special forces ndekuti
@WizBanda
@WizBanda 3 месяца назад
Nde inu bwanji aimudapitilize kupanga search panonkha?
@sokojane4015
@sokojane4015 3 месяца назад
I magine kuchita kuwauza kuti mulowere uku, anaziwa kuti akapanda kuwauza choncho akawapezelera sanathane nawo. Kufa kwa anthu amenewa ndikuthaso kwa MCP, mwina poti ndiakupha azayendaso njirazina zobera komano mwachilungamo sangazawine ndipo sakanawinaso kukanapanda SKC. Alakwira mtundu wa Malawi chiwembu cosasimbika anthu onsewo kuphedwa ntchito inalipo
@forexfuturemalawi
@forexfuturemalawi 3 месяца назад
💔
@JanetPhiri-b9x
@JanetPhiri-b9x 3 месяца назад
God fight for us please stiy😭😭😭😭😭
@Mother47
@Mother47 3 месяца назад
Terrible incident God knows 😢
@FishanNgwila
@FishanNgwila 3 месяца назад
Life always its complicated
@NsengiyumvaNoel-cj7dd
@NsengiyumvaNoel-cj7dd 3 месяца назад
Kagameso asapezekeso kumalilo dzikomo
@dalitson3558
@dalitson3558 3 месяца назад
Chakwera ndi munthu wakupha please Malawians lets wake up this regime must fall
@faithchinjala9335
@faithchinjala9335 3 месяца назад
God fight for this
@Gracekamanga-kt3tr
@Gracekamanga-kt3tr 3 месяца назад
Chakwera kulakwa
@Gracep.Maseko
@Gracep.Maseko 3 месяца назад
Athu woipa apaga dala
@lawrencekauwa8005
@lawrencekauwa8005 3 месяца назад
Zamanyazi ku MCP
@HassanJameskananjie
@HassanJameskananjie 3 месяца назад
Ng'ona za mmabango
@JamesMulale
@JamesMulale 3 месяца назад
Anenezo zoona VP samaduwala
@LynessAnord-hx4pq
@LynessAnord-hx4pq 3 месяца назад
Choyakhura Kusowa mmm😭😭😭😭
@DoreenMyaba
@DoreenMyaba 3 месяца назад
😢😢😢😢😢
@AminaGaffer
@AminaGaffer 3 месяца назад
Chakwera satana
@KasimuMaulana-mu8we
@KasimuMaulana-mu8we 3 месяца назад
Achinyamata ambiri takhala tikunena kuti mcp yokupha inali yakale ya akamuzu nanga lero bwanji pamenepa, anthu 12 tsopano amene aphedwa ndi mcp yatsopanoyi, kuyambila sidick Miya,Raph kasambara komanso Achilima ndi onse anali mundege imeneyija, be wise and be warned.
@DIRECTORJARVMACK
@DIRECTORJARVMACK 3 месяца назад
Nanga martse
@Okalekale
@Okalekale 3 месяца назад
Afufuza kale umboni wapezeka kale?.
@WinerdShadreck
@WinerdShadreck 3 месяца назад
MCP yakupha 😡😭 RIP chilima
@TwalikiWisiki
@TwalikiWisiki 3 месяца назад
My deep and sincere condolences to all the families of that lost their lloved ones, may the Lord comfort you,, munthawi yowawitsa ngati iyi,, ndiri okhuzudwa kwambiri ndiri ndi chisoni kowopsya,,i cant believe this koma Mulungu atithandize,, pempho langa kwa mabanja onse amene mwataya abalenu,ana anu,amuna wanu, abambo anu,amayi anu,,mtsigoleri wanu chonde chonde chonde chonde ndagwira mwendo musavomeleze kuti achipani cha MCP ayendetse mwambo wa maliro,,in English please please do not allow any MCP government authorities to temper with the body of His Excellency Dr Saulos claus Chilima,,they are goin to block any form tests not to be done,they are willing to spend billions and billions to make sure that results of the test should not be released, they have paid the relevant people not to release any medical report that can implicate them,
Далее
Se las dejo ahí.
00:10
Просмотров 2,2 млн
How the Most Elite Spy Agency Operates
22:42
Просмотров 1,4 млн
Se las dejo ahí.
00:10
Просмотров 2,2 млн