Nooo nooo nooo even you Brian you know what exactly is on the report and what Mr chikangawa said to Malawian on his first bliefing is exactly parallel to this carrent report and the second thing is Mr chikangawa azaziwikabe
@@ShemieMavuto If you are Malawian make sure and don't miss to 👂👂🦻🦻 Limpopo FM, Bakili Muluzi tv and The DC Bon Kalindo.Anthu andale kodi simumakhala ndi chifundo pa anthu anu aumphawi,osowa,ovutika ndi amasiye?
Even the president himself knows that Malawi has many parties and their signs ,so why moving out frags of the other parties to me this must stop just let the president to address the people at any time he wish even at aplace where flags of other parties hungedup
This accident will be talked from one generation to the other till the end of the universe.... whether chikangawa is out of leadership or not... people will never stop talking about it
The camera 📸 man has to do better next time please. & Also when watching from this channel most of the time the videos jam, 😊 you need to improve on that.
no one has the right to stop people from crying. let the mourners cry unt they finish. And these leaders must know that they lead different people of different like/choices. In order to be good leader u must reespect different choices
Amene adalakwitsa ndi amene adamulola(adamuwuza)munthu kuti akwere ndege yosakwanira zipangizo ameneyo ndi amene adalakwitsa.Anthu amene damwalira pamalopa ndi anthu amene amathandiza pachitukuko cha dziko lino.
Wondar Mskiska please if you don't want to talk about the pain death of Chilima which was caused by jealousy people, do not bother yourself in defence of these killers
Koma pa zonse mukumbukile kuti a President ananena kuti ndege anayibweza ku Mzuzu (Pamenepo) Funso: 1-Kodi ku Mzuzu anayibweza ndindani?. 2- Anamuwuza President ndindani?. 3-Why they decide to lie to Malawian?. Ndege kusowa 10am akufufuza kuyamba usiku 5pm?. Still mare question coming.
Brain, Brain your question about why the president, chimwendo and Nancy spoke is very unfortunate.. You know very well a bout the serious allegations, So my question is" do you want or expect MCP just to remain silent on these serious allegations ??????
Unbelievable politicians they have no shame no integrity no conscious they don't think of others apart from their own. Imagine after all sorts of insults Jefu Wa Jefu said to Chakwera and mcp today she can stand and say kwacha kwacha!!!! For real??? U think u can fool us??? Fine and good chiona ndi chipande poomola
Bereavement takes time for other it takes one year and others two years even threes to give years depending upon the therapeutic sessions, but with other people's reactions they may be taken to a mental level acute for clinical depression because they have not received closure inparticular cases where the families which have lost their beloved ones via first degree murder or homicide during court proceedings where they take about years for the judge to deliver a verdict. Looking at the case of jinkid and Mellys the rapper in usa or shanquila Robinson. People have the right to mourning their beloved ones who have passed away.
Za ndege kungoyiwalako,,,akapanda kalindo kupachika moyo wake kuti achititse mademo..mkuyembekezera chani 😢😢😢ndiye akuti final report 10-12months 😢😢😢 obvious azatulusa after ma voti 😅😅😅😅
Wonder I was watching you yesterday when you were asking Chakwera questions after the rally you were asking with fear as you visibly seen and you did not continue to him questions which made you to ask two questions only, explain why you were afraid of him or should we say munadyeratu bans? Koma ma Prezident enawa mumawaphaphalitsa ndi mafunso apa nanga mumaopa chani? Ndiri ndi observations pa Inu a Msiska
Pali kusiyana kwa makambidwe pakati pa chikangawa kunkuyu wankulu wa nkhondo ndi kulephela kwa achitetezo were confused guys it can not be end this until when we know exactly what was happening in chikangawa to those 9 malawi who killed including our let vp
It’s all political, ena azibale awo amwalira last week yomweyi apanga move on koma akuti akulira chilima, ndani apa asakugona kukhalira kulira kuti chilima anamwalira. Andale onse akugwiritsa ntchito chisoni cha anthu kuti apite patali kugwiritsa ntchito imfa ya chilima. It’s all politics, vama candle ivi, how many people lost a close family member after chilima that are lighting candles for their loved ones. Even his own family has accepted and we are not letting them move on. The way MCP was ready to betray chilima while he was alive we can say they killed him twice, but politicians should not fool us that chilima was their hero because he’s dead.
Discussing Nsete zokha zokha yet you know ma statement opusa adayankhula chakwela n Valentino Phiri which illustrated lies n contradictions Kaya mwapasidwa chani Kaya kuti mudzipanga zansete zanu mukupangazi
Ndale za ku Malawi nzautsilu or ikanakhala mcp bwenzi pano akuchita zomwezo. Kodi a Chakwera sankaonetsa kuti iwo sadzaba pano akutani??? Ankati katangale atha pano bwanji??? Kudzakhala ma mega farms ali kuti??? Pano anthu a kudya chitedze why a Malawi simumatha kulankhula chilungamo. We are tired of the leadership of Malawi. 😭😭😭😭😭😭😭 Amayoooo God where are You??? A blood shade country. No love in our nation. Sagrigation, cruel leaders. We need God's intervention
Imfa ya chilima anthuwa salinayo ndi chisoni ayi,koma they are happy cz the political parties are looking to benefit out of his death .trust me anthuwa sichisoni ayi nooo!
Chakwera ndi president wa dziko, ndalama zomwe amayendera ndi za a Malawi azipani zosiyanasiyana, asamapite ku malo nkumakatumbwa za chipani chake, azitha kusiyanitsa chipani ndi boma
Zomwe zikuchitika kumalawiko kuli ngat kuno ku SA president atathothola papando kalekale sadikilaso kut afike term yake anthu vote amalawi tinapusa kwambir apapa tikuti bolaso nthawi ya DPP anthu samadya chiteze tikusiyanisa kwambir zithu zina pano ndi kale lija
A Times timakudalirani mumalankhula chilungamo of cause Koma penanso mumaopa kuvaya pa point because a Malawi sitingasiye kukamba olo kulira Ngati boma likuzemba, likukanika kufika poyera pakafuku fuku chilungamo chioneke anthu tiisiya bwanji kuludza anthu 9 pa kamodzi plus VIP timve bwanji bwino nazo izi tikumva kuwawa