Тёмный

HOT CURRENT YA LERO ACHINA BRIAN BANDA AUZA MCP LIVE KUTI ASAMANAMIZE ANTHU KUTI BOMA NDI LOMWERI 

Makosana
Подписаться 90 тыс.
Просмотров 80 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

12 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 267   
@JackMtengo
@JackMtengo 18 дней назад
To be honest Hot current iyiyi yaonetseratu kuti Brian and Jona, you guys are truly investigative Journalists... I like your courageous presentation because you have hitted a nail by head. Ya Kabwira komanso ya Extended Credit Facility ndiye mwaing'aluladi... Kuswa Kuswa, kugaza kugaza, kubandula kubandula. Kkkk kkkk kufotokoza nkhani osati based on speculations but facts on ground. The media has a very important role towards politics, rule of law and good governance. Guys you are a leading analysts in Malawi, so far😊😊😊😊😊😊
@HesfordMathemba
@HesfordMathemba 15 дней назад
Brian aise Mulungu azingokudalitsa. You represent us the poor and voiceless people.
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v 18 дней назад
Koma Boma la Chakwera latipweteka amalawi
@ChejaliChirwa
@ChejaliChirwa 18 дней назад
My vote 2025 DPP 💙💙
@ConfusedClam-ov4mx
@ConfusedClam-ov4mx 18 дней назад
Opakuku akudya bwino ku times eee Masaya amenewo?
@GeorgeChitapapata
@GeorgeChitapapata 17 дней назад
Ulemu wanu brain .kuima pachilungamo kuzukuta kosekose .I'm really happy with this program
@NorahMangasanja
@NorahMangasanja 18 дней назад
Continue guys mumatiyankhulira opanda pakamwafe pitilizani
@Patricia-tr2vy
@Patricia-tr2vy 18 дней назад
Mcp yagwa nayo basi,ife tinalonjezedwa zosatheka ,koma abusa achakwera angatero ndithu,empty promise
@BizweckMbwindinga-uh6fq
@BizweckMbwindinga-uh6fq 18 дней назад
Guys kd muli ndi lawyers et chifukwa mukung'alulatu fans for brain let's here
@JeffreyKambwemba-zs7wy
@JeffreyKambwemba-zs7wy 18 дней назад
You just forgotten the word 😂(gather)
@MisheckAselo
@MisheckAselo 18 дней назад
Akabwira kuwawata ngati ngati hule wakumudzi 😂😂😂
@lucymakata9916
@lucymakata9916 18 дней назад
inde! inde! dad Chafumuka kuyankhula chilungamo chokhachokha.more fire🔥🔥🔥
@CharlesKachipanda-jz9jv
@CharlesKachipanda-jz9jv 18 дней назад
Timakunyadirani team times
@user-be5fc3ed1i
@user-be5fc3ed1i 18 дней назад
Boma la MCP lanunkha kwambiri ngati manyi eish chakwera akuchedwa kuchoka pampando
@anthonynkhoma4265
@anthonynkhoma4265 18 дней назад
Nothing wrong to say Boma ndi lomweri. And I repeat boma ndilomweri sitikusintha.
@josephmunthali2526
@josephmunthali2526 15 дней назад
Tell them bro
@GladesMhango
@GladesMhango 13 дней назад
Mwalankhula ndendende zomwe a Malawi , akufuna kuma lankhulaa km timàopa🔥🔥🔥🔥🔥🔥 ipatse 🔥🔥
@WakuMalawi
@WakuMalawi 15 дней назад
Zikomo kwambiri. Ine ndili kunja. Hot Current is the best. Keep going..
@samsonchikopa2442
@samsonchikopa2442 17 дней назад
Pitilizani kunena chilungamo kwa adindo mmalo mwa aMalawi mwina section 12,30 ambiriwa samaiwerenga
@MexcoJepter-p5f
@MexcoJepter-p5f 18 дней назад
🔥🔥apaMkuku mwabwera bho ife tikuvutika munthawi yachakwera nduna zawozi sakuyenera kumaziwopa ,AChakwera ndiamene akutizunza
@user-rn7wv8ze3v
@user-rn7wv8ze3v 18 дней назад
@@MexcoJepter-p5f ndizowona kholo lanzeru siringasekere mwana wake akumenya anzake Apa zikuwonekerathu Chakwera ndiye amane akupanga zimeni izi kuzera munduna zake
@saidimwanyali8969
@saidimwanyali8969 18 дней назад
Kodithu achilima zanali kathundu Koma munthu osakwima pandale achilima kunena zoona akana Deka akanakala akathundu chifukwa chipani cha UTM ulendo unowo yikanawina 😢 Koma chovesa chisoni anatiponya kung'ona achilima akukululukile mulungu muzolakwika zanu Koma mwatisiyira mavuto chifukwa chofuna kulamula nthawi isanakwane mukanadeka 2019 anthu anakukonda ulendo Uno UTM yikanaliwa nboma payoka
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 17 дней назад
Keep it up to all yr team for gd job poor Malawians suffering today kapumen bwino
@user-tr4fv6ry9q
@user-tr4fv6ry9q 18 дней назад
Guys,Brian and others,mumatiyimilira,coz u talk about the truth,coz anthuwa akuzuza amalawi ndithu,
@NeemaMatewere
@NeemaMatewere 17 дней назад
Brian Banda mmatiimilira
@PearsonZachariah
@PearsonZachariah 18 дней назад
Aaa,osanama akuluakulu chilungamo mukuyankhur aChakwera zawavuta ndipo nthawi yatha sangakozenso
@user-ix4yv4rn1f
@user-ix4yv4rn1f 18 дней назад
ndipo zowona
@Vascomw
@Vascomw 18 дней назад
We are with you from Uk
@wisdomsadyalunda2001
@wisdomsadyalunda2001 18 дней назад
Jona is right I feel the same let's no t brame ma ministers president yu ndi is incompetent he has no sense of direction hence his appointment s are also poor... Good example is bingu He was sharp upstairs as results he had ma Ministers oziwaso chomwe akuchita
@YughozMw
@YughozMw 18 дней назад
Inuo guys mumandiwaza heavy🔥
@swadikimbwana7680
@swadikimbwana7680 18 дней назад
She is completely confused and mad pls MCP instruct her to stop she is denouncing your party mcp
@user-xd1cm7tm7t
@user-xd1cm7tm7t 18 дней назад
Brian ndikatund osat andevu zamway😅😅
@KendrickLuckyc
@KendrickLuckyc 18 дней назад
Ndevu zamwai kape
@josephmunthali2526
@josephmunthali2526 15 дней назад
Chifukwa choti awa akukwela DPP mwati ndiabwino, koma wonder poti amayi balancer mwati ngoyipa mxieeeeew
@PatrickSomanje
@PatrickSomanje 17 дней назад
Next year must think nice when we going to vote pls everyone knows now mcp not helping Malawians
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 18 дней назад
😂😂😂😂😂😂! Koma apankuku mwati pomaliza mwati who is a better devil kapena sinamve bwino kkkkk
@HassanHussein-x6o
@HassanHussein-x6o 17 дней назад
I really appreciate your speech guys mumatha inuyo
@LytonMatola
@LytonMatola 17 дней назад
Nice and lovely conversation guys keep it up.
@IssaJohn-cb8vn
@IssaJohn-cb8vn 18 дней назад
Sizingatheke kukonza nthawi alibe kwachuluka komwe awononga mazi Ada basi
@henryphiri6100
@henryphiri6100 18 дней назад
Osanamizira Nduna,vuto ndi President Chakwera amasankha dala incompetent ministers ndicholinga choti adziba.Bwanji Nancy Tembo alibe mbiri yonunkha ngati akapolo enawa
@user-eq8hr8li8h
@user-eq8hr8li8h 18 дней назад
Yesu akubwera mavuto onsewa adzatha amen
@GracianJames
@GracianJames 18 дней назад
Amen and amen God bless you brother or sister
@LuckyChsi
@LuckyChsi 18 дней назад
Atetezi a mkaka😂😂
@joegibsonzulu2599
@joegibsonzulu2599 17 дней назад
Program yosangulutsa iyi. Keep it up guys
@IssaJohn-cb8vn
@IssaJohn-cb8vn 18 дней назад
Anyamata awa akulu akulu akugwila chinchito chachikulu pa redio iyi tikukunyadilani achina brain banda
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 18 дней назад
Bola asazasinthe ena akazabwela
@christopherkuseli6190
@christopherkuseli6190 17 дней назад
Hot current at its on best ,Sponsors should consider a bottles of water.
@macnellnamanja6698
@macnellnamanja6698 17 дней назад
Koma pa Chilima pokha paja anatilakwila
@JustinMpunga-c8b
@JustinMpunga-c8b 17 дней назад
Plz connect your line properly coz breakdown communication
@Costance-nf7ue
@Costance-nf7ue 16 дней назад
Watching from johansburg
@ALEXAlli-ck8lj
@ALEXAlli-ck8lj 17 дней назад
Times ndi katundu auzen anthu zoona tatopa
@jameslweya-eo1uj
@jameslweya-eo1uj 16 дней назад
Azidandaula Ma americans about our malawian welfare…pomwe akumipandowo they cant see
@HenryChiwaya-u8l
@HenryChiwaya-u8l 18 дней назад
The trueth free
@ishmaelsiffah9900
@ishmaelsiffah9900 18 дней назад
I remember tsiku lina pa Sana mu Lilongwe kunabwera Richard kungokhala mgalimoto akuti akatero amwenye amangotuluka kuzapeleka ndalama n day imeneyo anachedwa,komatu mzibambo anaulephera mtima watsika kukathira fire mkati muja,mungangondikhanzika panjapa ine,do u knw whom i am ine shaaaa🤔🤔🤔
@veronicamustafa305
@veronicamustafa305 18 дней назад
Amakatani mu Sannah mo
@wisdomsadyalunda2001
@wisdomsadyalunda2001 18 дней назад
Chithyola wa community development kumpasa unduna wa za chuma how do you expect him engenier the economy? Jona hold that vuto wankulu ndi empty tin.
@FrancisNyayi
@FrancisNyayi 18 дней назад
Dennis mahata the new party basi though sitikumiziwa ahhh we know bingu coz of bakili and ahh
@KingsleyChiphwanya
@KingsleyChiphwanya 14 дней назад
Awona kupweteka monga mene atipwetekela ife amalawi 2025 tiphwanya MCP
@LysonMkomadzinja
@LysonMkomadzinja 17 дней назад
APM ndikuvotela chifukwa ukawina umusiila Kabambe as president utm boma.
@knoxymaulidimaloya4174
@knoxymaulidimaloya4174 16 дней назад
Ine kwanga ndikuyamika chifukwa cha Tv imeneyi ya Times ndi Tv yokhayo imene imatithanndiza kuunikila zambuyo komanso zakusogolo, Pitilizanikutisegula mmaso ife achinyamata. vote UTM
@CollingsMweniteteNgilania
@CollingsMweniteteNgilania 16 дней назад
Akulu akulu inu Mmatiyimilira kwambiri .Bishop munali kuti nthawi ya kumbuyo ?.Jonah apitilire kukhala nsukuludzi pamenepo ukanakhala mpira bwenzi tikunena kuti striking force is strong like Mbape ,Vinicious jr and Bellingham.kkkkkk
@LysonMkomadzinja
@LysonMkomadzinja 17 дней назад
Ubwino wainu simukhala ndimbali mumayankhula CHILUNGAMO dzisiyeni dzitsilu dzidzikunyozani koma dtikufunani 2025
@ishmaelkassim539
@ishmaelkassim539 18 дней назад
Kod yemwe amakhalira zithuzi kujambulitsa ku HD ndindan guys 😂😂😂😂😂
@MerryWayson
@MerryWayson 14 дней назад
Inutu ❤❤❤❤❤ more far🎉🎉🎉🎉🎉🎉
@Amgwagwa
@Amgwagwa 18 дней назад
Koma akuluakulu ❤❤❤❤
@ChisomocaxstonStima
@ChisomocaxstonStima 14 дней назад
Mumakwanira kuposa ma TV station enawa, mbuli ndiiwowo inu simbuli ayi.yabaya kkkkkk
@user-os4iz4tn9z
@user-os4iz4tn9z 18 дней назад
Over expenditures disregarding financial crisis that Malawi is passing through, Germany, Mozambique uyo Italy
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 18 дней назад
Olo face ya akabwilawo iiiiiiii ngati ufiti alibe matewela okha amadya alipo angopo mziko muno azimai ngati amenewa, oipisisa osati masewela asatana enieni.
@rexnyalugwe4910
@rexnyalugwe4910 17 дней назад
"the more things change, the more they remain the same"😢
@YatoRoy-kt4lh
@YatoRoy-kt4lh 14 дней назад
Koma anthu inu ma Jesuit mukuwadziwa? Amenewa ndi amene amayendetsa dziko not president
@ChundaLackson
@ChundaLackson 18 дней назад
ngati mcp yakanika nde palibe chipani choti chingakwanise
@user-xt2gu9yt9q
@user-xt2gu9yt9q 17 дней назад
Boma silomweli musatikakamize kuti likhale lomweli ayi awa ndi manyaka aboma boma linapitalija
@Littlefair7
@Littlefair7 17 дней назад
A bishop nawonso suit yodula chonchi tiwafufuze.
@laurentbutao4084
@laurentbutao4084 17 дней назад
Atsogoleri asamanamizile convid,,Chakula ndikudzikonda okha
@user-cq4gr1tq6u
@user-cq4gr1tq6u 18 дней назад
Akakhala azungu atinyanyala ngongole satipatsaso😢😢😢😢😢😢
@ussimasi2458
@ussimasi2458 16 дней назад
kkkk😂😂 azungu atigwila ufiti 😂😂
@wisdomchilanga723
@wisdomchilanga723 18 дней назад
Koma lero ndiye mwang'aluradi guys
@MasterBlack-r2n
@MasterBlack-r2n 15 дней назад
best TV. not MBC tv
@shaibukamwendo4868
@shaibukamwendo4868 16 дней назад
musamanamize athu agaru inu boma ndilomwelo la mcp basi
@user-eq8hr8li8h
@user-eq8hr8li8h 18 дней назад
The govt has failed to deliver angochoka sakudziwa chomwe akuchita amaona ngati kuyendetsa boma ndi masewera
@Yungjoe786
@Yungjoe786 18 дней назад
Koma mpaka a Nansonjora?😂
@WillmotChiuimia-vr6ou
@WillmotChiuimia-vr6ou 15 дней назад
😂😂😂 zeni zeni zomwe zayankhulidwapa yaa ndikuva bwino ndithu
@user-ju9lg5pg5g
@user-ju9lg5pg5g 18 дней назад
Awa ndi azungu akufuna tingwesetso kwacha
@user-jk8sh7fh2d
@user-jk8sh7fh2d 18 дней назад
Vuto la usogoleri opusa opemphapempha basi azibusa ndi kukhala kwao ndie ndikukhalaso nsogoleri wa ziko aah basi m'mitu mwake ndizopempha basi kuendeza church ndi ziko nzosiyana system yake so asakaniza ati ndi yofanana to be honest kwa chakwelayu zativuta kwambili more problems
@VincentMtambo
@VincentMtambo 14 дней назад
Boma ndi lomweli ofunika kungosintha chipani ndi mtsogoleri
@UchizieFMtemela
@UchizieFMtemela 16 дней назад
😂😂😂😂😂😂😂Mai kabwira azitengeratu zinthu pa mngong'o
@MercyHassan-p4e
@MercyHassan-p4e 17 дней назад
Keep it up 🎉❤
@AkimuKindsonchirwa-j7l
@AkimuKindsonchirwa-j7l 18 дней назад
Ngati a DPP akufuna kuwinaso must follow your advice and guidance another thing vice President must be Enock Chihana and Atupele Muluzi finance minister and next President agreement
@josephmunthali2526
@josephmunthali2526 15 дней назад
Mesa a Dpp, amayimba Kuti lozani zanu, nde a MCP asalodze zawo, a Brian ndi Jonah pena pake mmakondela DPP iyaaaah, Simufunila Dziko lino zabwino, koma Mufuna DPP yanu yokupha Ma Albino, Ma black outs aja, Miseu yogumuka ija Aaaah, inu nga DPP basi komanso mwatatsa poti Wonder ndi Bayana Chunga palibe. Aaaah inunso mumakondwela ndi DPP yanu ija iyaaa ndipo simunati, Chakwera ndi Mpakana 2030 wooooo!!!!
@GraceLakatika
@GraceLakatika 14 дней назад
Tiyeni nazoni 🙆
@thomasmcbanda9794
@thomasmcbanda9794 15 дней назад
Inu ndimadoro koma number 1
@chisomokotamu7563
@chisomokotamu7563 12 дней назад
Koma mwaziziwa kuti kuseliku aneba anu akukukambilanani???
@LysonMkomadzinja
@LysonMkomadzinja 17 дней назад
12:45
@HaloonChikoko
@HaloonChikoko 18 дней назад
Atsukuluzi mukambazo ndizowona APLE wa alindi ndivuto
@JoiceNkhoma-s1m
@JoiceNkhoma-s1m 18 дней назад
Brian hot current ipatseni 3hrs sure olo even do it everyday. Please
@RodrickMwakatundu-gl6yo
@RodrickMwakatundu-gl6yo 17 дней назад
Ufa sakandira ndi madzi owira,mcp nthawi yatha
@StiveneChikafa
@StiveneChikafa 18 дней назад
Brian ndi anzanu awuzeni atsogoleri azipani zonse kuti asamati anthu akutifuna koma aziti ndikufuna kulamula kuti zofuna zanga zitheke
@MexcoJepter-p5f
@MexcoJepter-p5f 17 дней назад
Mai kabwira polani moto,Boma silomwelo inde
@FatimaAyami
@FatimaAyami 16 дней назад
😂😂ndinachoka ku south africa kupita ku bluenfornteen ,,,,k kkkk mesa bluenfornteen ndiye south africayo,,,ok koma abusa mumatinvetsa kukoma lets go!!!!
@DanMhone-iw6xg
@DanMhone-iw6xg 18 дней назад
Boma silomweli zona zake
@corretabanda7685
@corretabanda7685 18 дней назад
MCP must go for Malawians to survive. Ambuye tsegulani maso ndi mitima ya ma sapota a mcp onse kuti adziwe choonadi.
@paulphalandwa3133
@paulphalandwa3133 12 дней назад
Apankuku ndi Abanda musadzafe mudzangosowa
@constancemkandawire7378
@constancemkandawire7378 18 дней назад
Ndalamazo nde zikumapezeka ku zambia,no one to be held accountable No arrest no nothing ......aaaaaaaash why malawi every thing looks like is falling apart instead of fixing the economy ali besy kutukwanana mumisonkhano aaaaaaaaaa fwiti iyo ili kulowa malawi i think njanakazi iwenge yanalume nthe yagowoka Lord come rescue us
@eliffagondewe8214
@eliffagondewe8214 18 дней назад
So sad 💔
@yusufbakali
@yusufbakali 17 дней назад
Imf must must go out of Malawi
@user-xt2gu9yt9q
@user-xt2gu9yt9q 17 дней назад
Thawi yachepa sakwanisa kukoza zithu thawi yomwe ayiononga yachuluka kuyambila 2020 kufika 2024 kuononga x100 ng,ooooooooo
@LeyvanSamuel-pe5tc
@LeyvanSamuel-pe5tc 18 дней назад
Madolo awa amatha ndipo amayima pa chilungamo 💪💪💪
@InnocentChunga-jg8te
@InnocentChunga-jg8te 18 дней назад
Koma ngati wina samva apa, kayaaa!
@KikaImran
@KikaImran 15 дней назад
Eti nkumati boma ndi lomweli? Mutikakamiz bwanji?😂😂. Mwatitolatu a malawife😂
@LightonNdala
@LightonNdala 17 дней назад
Apa ndiye hot current yasukuluzadi. Wokumva wamva.
@freddyndzukuma1357
@freddyndzukuma1357 18 дней назад
To times .check what dpp says kumisonkhano yowo .amaloza zinthu anapanga ndi iwowo yet ndimitsonkho ya amalawi. Don't look one side here I think she is answer the dpp party. Onsewa angosiya zoloza zomwe zikuchitika zonkhudza boma. Or dpp isiye nyimbo ya lozani zanu
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 18 дней назад
Palibe chanzeru mwakamba apa nanu nkhani ndi kagwilitsidwe ntchito ka misonkho yathuyo coz sangatenge zamuthumba mwao amaloza zomwe apanga pamene enaso apatsidwa mpata omweo km zikuwakanika tsono kumaganiza kmso kumazindikira zinthu.
@MarthaBango
@MarthaBango 18 дней назад
Bwanji?mwadwala?
@YohaneKaluzi
@YohaneKaluzi 18 дней назад
Brian usachoke pa hot current ,a ndevu za mwai akabwela mwapase mpando mbali inao coz amasisititsa kwambiri.
Далее
TPM - Como lidar?!
4:20
Просмотров 2
Kenny Kunene's take on the GNU's performance thus far
19:08
BON KALINDO LERO WANG'ALULA MWA NYOO 13 September 2024
13:25