Тёмный

JB kumuyamba dalaku Mumakhala mwapepetulidwa?, eeee? 😂😂 JB vs Morton Maghaya 🔥🔥 

Malawian Cameras
Подписаться 31 тыс.
Просмотров 30 тыс.
50% 1

Morton Baghaya anamunena Jb kuti ndi Rubbish amazinena kuti ndi Gangster komaso amabwera ndi Zamapemphero kotero Iyeyo Jb samuwaza
Apa mpomwe Jb Watulukira ndikumkumbutsa Morton Maghaya kuti ku Sukulu Morton anali zoba komaso Kape ndipo or chibwezi sanakhale nachoko Nchifukwa chake ku China aliko amangojambula mahule koma ndisathe mau
Taonerani video yi muli nkhani mmenemu

Опубликовано:

 

21 сен 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 221   
@dorcaslouisamwango2428
@dorcaslouisamwango2428 4 дня назад
Thanks JB for fearing God. We all have flaws but I like the fact that you acknowledge God.
@actuarialscience2283
@actuarialscience2283 5 дней назад
Mwambo wa Kusala kudya kuti MCP isawine uli motere: 1) Ku Thyolo osamwa tiyi wa buledi kufikira MCP itachotsedwa mboma 2) Ku Lilongwe onse okonda DPP tizidya meal imodzi kufikira MCP itachoka 3) Ku Zomba kudya mazulo okha. Kusalaku kukuchitika kwa 15 days mpaka pa 23. Just choose any 15 days. Zopempherera ndi izi: 1) Ma plan obera zisankho alephereke. Anthu a ku MEC amene akupanga chinyengo amangidwe 2) Ufiti wa MCP usagwire ntchito 3) Chakwera asgwiritse ntchito magazi a Chilima. Kupemphera katatu pa tsiku mpaka pa 23 mwezi wa mmmawa. Zikomo.
@TachikoMwanamanga
@TachikoMwanamanga 3 дня назад
Amen 🔥♥️
@BrandinaMphuka
@BrandinaMphuka 5 дней назад
Komatu JB ngakhale amatukwana koma penapaketu amayakhula zithu zazeru ndithu
@MalawianCamera
@MalawianCamera 5 дней назад
@@BrandinaMphuka zoona 😂😂
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 4 дня назад
Ndipo live
@MuhammadBAKILI-kl2mj
@MuhammadBAKILI-kl2mj 4 дня назад
😂😂😂😂😂motoni ndiwaukape mwina sakudziwa kuti Mavyeete tilipo kagulu JB ❤❤❤❤❤❤
@TheresaNtodwa
@TheresaNtodwa 4 дня назад
Jb zoona amene amapemphera ndiamene amapambana ❤ jb ndizimene walankhula amuziwe yesu magaya.
@AndryDTylos
@AndryDTylos 2 дня назад
Nde akuti amakhala ku China 🇨🇳 mene akuwonekeramo angokhala ngati ali kwachinsapo Amortonwo
@BistonMacheso
@BistonMacheso 5 дней назад
Yes JB mulungu mamuziwadi munrlthu amene umamuziwa mulungu umayakhula chonchi nkhani ndichisomo ambuye akudaliseni kwambiri JB
@yusufbakali
@yusufbakali 5 дней назад
I am with jb ❤jb
@JacklineNiwahereza-ni3pm
@JacklineNiwahereza-ni3pm 5 дней назад
Mavyete muwoneseni baghaya akuti sakhulupilila mulungu 😅😅😅😅😅😅
@BeckhamDavid-v6c
@BeckhamDavid-v6c 5 дней назад
😂😂😂😂 koma jb musiye zako wamuchapa kwakwana😂😂
@MalawianCamera
@MalawianCamera 5 дней назад
@@BeckhamDavid-v6c 😂😂😂😂
@UncleShopRite
@UncleShopRite 5 дней назад
JB wandiwaza powopa mulungu pokhapo ndiwe dolo ❤❤❤❤❤ you JB
@BenjaminMtima
@BenjaminMtima День назад
JB love you for respecting God
@Rometcma
@Rometcma 3 дня назад
Kabrauzi kena kake moton mutu ngati ndimu 😂😂😂😂😂
@shaddaimaonga5832
@shaddaimaonga5832 5 дней назад
America ndi America basi❤❤❤❤❤
@samdiverson9733
@samdiverson9733 5 дней назад
Jb ndi shasha Inu tamangodyani achulewo kumeneko
@PreciousChisale
@PreciousChisale 2 дня назад
That,s it JB , umakwana ❤❤❤❤❤❤❤
@ChristinaMdeza
@ChristinaMdeza 5 дней назад
😂😂😂😂 anaganiza bwanji? kuti alakhule chocho. aputira dala JB
@MalawianCamera
@MalawianCamera 5 дней назад
Kayasotu 😂
@educenter796
@educenter796 2 дня назад
Morton naye ndi goat aise mavyete achepa nazo amaona ngati awasiya siya azingotukwana
@AubreyBeniMbewe-bt1qg
@AubreyBeniMbewe-bt1qg 2 дня назад
Team JB. Ungochepetsa kutukwana kokhako
@peterthawi
@peterthawi 5 дней назад
😂😂😂mavyete...muwuzeni baghaya morton ma wise
@mohamedriazshreef8697
@mohamedriazshreef8697 3 дня назад
❤ number one jb, is more fire 🔥❤
@KennedyPhiri-h9h
@KennedyPhiri-h9h 5 дней назад
😂😂😂 koma JB ndi katundu simunthu womuyamba 😅😅
@MalawianCamera
@MalawianCamera 5 дней назад
@@KennedyPhiri-h9h 😂😂 eti kumamuyamba Jb? 😂😂
@MadalitsoKachelenga
@MadalitsoKachelenga 4 дня назад
Koma panalakwika mpaka Trash,,,,kod iwowo ndi maphunziro awo anapànga chani pa malawi pano, PhD, abwere azatukule malawi ngati ali dolo.
@MaggieNamaona-h1z
@MaggieNamaona-h1z 4 дня назад
Team JB
@TheresaNtodwa
@TheresaNtodwa 4 дня назад
Magaya ndi satana ..jb osalimbananaye ameneyo. mulingu amukatha wasala masiku ochepa magaya .
@Dellingsmunthali
@Dellingsmunthali 4 дня назад
Uyu ndiye mtumbuka waku USA😂😂
@JosephKuyeli-rc9on
@JosephKuyeli-rc9on 3 дня назад
JB Kodi ndiwe mwana wammudzi ...basi you have my support 🎉
@greychizaka4088
@greychizaka4088 5 дней назад
JB is a heavyweight kwasasambayo🎉
@FredNyalugwe
@FredNyalugwe 3 дня назад
I'm with jb number one for real
@Givenjnr
@Givenjnr 3 дня назад
Ngat JB chiyambile zakoz ngat wandilakhulira bwino nd vd iyi 💪💪💪💪💘
@sparkdymon3429
@sparkdymon3429 5 дней назад
Aaaa musamatibowe nose muliso makape ASA
@JibraanSharief-ol1yn
@JibraanSharief-ol1yn 2 дня назад
Jb number one more fire 🔥 😍
@AugustineChimaliro-e5i
@AugustineChimaliro-e5i 5 дней назад
Moto unandi Jb😂😂😂😂😂
@AlexBeluka
@AlexBeluka 2 дня назад
Jb kutukwanaku ndi nsena eti😂
@MaliGomani-z4k
@MaliGomani-z4k 5 дней назад
😂😂😂Baghaya wangoziyamba izi😂😂😂
@ThokohPrescotKalonga
@ThokohPrescotKalonga 5 дней назад
Kkkk JB mavyete amenewo 😂😂😂😂 osawayamba ayi
@YonaPearson
@YonaPearson 5 дней назад
Kkkkk chiuzeni chimenecho chimadya achule 😂
@saidiwilliam9832
@saidiwilliam9832 5 дней назад
Ndikuona ngat JB asamayakhe zinazi akuthu akumasaka potchukila 😂😂😂😂😂😂😂
@TachikoMwanamanga
@TachikoMwanamanga 3 дня назад
Social media imatipusisa. We thought JB sadziwa Mulungu kma akukamba zamzelu kuposa m'busa wina. I love JB amakamba chilungamo n zanzelu
@JonathanNankambe-o7d
@JonathanNankambe-o7d 4 дня назад
❤JB 100%
@smartnicodemus7778
@smartnicodemus7778 День назад
May God bless you for that
@HERMANMALIWA
@HERMANMALIWA 2 дня назад
Ma bade kkkk😂😂😂❤
@giftngombeyakuyera8703
@giftngombeyakuyera8703 День назад
Nde mwati khwangwala amkatani?? KKKKKKK
@HestingsZiba-d6k
@HestingsZiba-d6k 5 дней назад
I'm with JB 🎉🎉🎉🎉🎉
@Razarusmbavachakwera
@Razarusmbavachakwera 4 дня назад
2be honest amtumbuka ambili ndimbuli ngakhala amakonda school
@nicolsley995
@nicolsley995 4 дня назад
😂😂😂 inu ndabodzatu ..... Fufuzani bwino
@fortunenthala4042
@fortunenthala4042 2 дня назад
Atumbuka ndife ophuziratu mukuti chani inuyo
@chikublea8982
@chikublea8982 3 дня назад
Mangochi Boyz musale mavyete abweratu kwa mereka mkoko
@SolomonNjolomole
@SolomonNjolomole 5 дней назад
Zina umangoona utaziyamba 😂😂😂😂
@MalawianCamera
@MalawianCamera 5 дней назад
Eeeeh koma ndiyetu😂
@GiftMwachande
@GiftMwachande 5 дней назад
American vs china😂😂😂😂
@AmidyMudani
@AmidyMudani 5 дней назад
Kkkkkkkkkkkk JB 😂😂😂😂😂😂 muwuse
@MalawianCamera
@MalawianCamera 5 дней назад
@@AmidyMudani 😂😂😂
@JacklineNiwahereza-ni3pm
@JacklineNiwahereza-ni3pm 5 дней назад
JB eishiiiiiiii 😂😂😂😂😂😂 koma adaaaa koma ndasekatu ati ntabaluka bayayaaa tamunvetu jolly juice 😅😅😅😅
@MalawianCamera
@MalawianCamera 5 дней назад
@@JacklineNiwahereza-ni3pm 😂😂😂
@samdiverson9733
@samdiverson9733 5 дней назад
Jb ndi nsena otchena umakwana bagaya ndi kape kwake mkudya achule akakhuta mkumati kulibe Mulungu
@OdalaKamwendo
@OdalaKamwendo 2 дня назад
Morton ndi dolo kwambiri akamadzi inu, JB doesn't speak facts amangotukwana basi mwina u don't know koma waphunzila kena kake.
@munashemoyo4190
@munashemoyo4190 5 дней назад
Tabaluka koma kudya Anathesi bas 😂😂😂😂😂😂
@IqrahOmar-x6w
@IqrahOmar-x6w 5 дней назад
Ife tili kumbuyo kwako jb big man wamkulu muthile fire
@AllickChilala
@AllickChilala День назад
FACT!!!!!!!!!!!
@chitchohistorical1036
@chitchohistorical1036 5 дней назад
Vyeteee ndi machine bulasa😂😂😂😂
@DanfordMkalimbaBanda
@DanfordMkalimbaBanda 4 дня назад
Ali odara odalira yehova chifukwa adzathandizika mu msautso yake. JB is a real G
@YamikaniMunyawa
@YamikaniMunyawa 3 дня назад
Wukunipulikiza iwe
@PRECIOUSMKUTE
@PRECIOUSMKUTE 4 дня назад
Mtopola at its best 😂😂
@AshrafuKalimula
@AshrafuKalimula 4 дня назад
Jb fire
@FredNyalugwe
@FredNyalugwe 3 дня назад
Magaya ndi zoba ndikape sangafane ndi jb or fredo kiss
@henryhenry6632
@henryhenry6632 4 дня назад
Who’s JB, kodi amalawi ndinu dzitsilu eti mmayamikila ma kape chifukwa chan,
@gizzykondwani865
@gizzykondwani865 5 дней назад
😂😂😂😂😂😂 JB 🔥
@Jayleezbond
@Jayleezbond 5 дней назад
Hahaha 😂😂 ati ine ndi ntsena ndee samatopatu hahaha 😂😂😂😂
@MalawianCamera
@MalawianCamera 5 дней назад
😂
@Friday-o4u
@Friday-o4u 3 дня назад
Ulem wanu jb ❤❤
@Paul-q2p
@Paul-q2p 5 дней назад
Anthunu wina aliyese tsibwino kumyamba dala nkhakhale inuyo tsangakuyambeni dala otsati JB tsimunthu womuyamba wina aliyese tsiomuyamba dala
@JawaduShafie
@JawaduShafie 5 дней назад
Ntabaluka!😅
@YamikaniMunyawa
@YamikaniMunyawa 3 дня назад
Kkkkk pakana chitumbuka mmmmm kkkk
@mohamedriazshreef8697
@mohamedriazshreef8697 3 дня назад
Mumakhwana man auze awa wokudya nkhonowa
@blackwellblackwell6337
@blackwellblackwell6337 4 дня назад
Morton alije zeru
@RodgersKanyasko-dh3cy
@RodgersKanyasko-dh3cy 3 дня назад
Kkkkkkkk koma JB ndi 1
@Alfred-lb4jw
@Alfred-lb4jw 3 дня назад
JB fire fire
@dumiharawa
@dumiharawa 4 дня назад
JB sangafike pa Morton,mukungoyamikira kutukwana akulu and zikuonesa kuti muli ndi mbali
@MalawianCamera
@MalawianCamera 4 дня назад
@@dumiharawa Maghaya vuto sakhulupilira Amene anamulenga koma muzinthu zina ndi dolo ndithu
@mosessemuh9681
@mosessemuh9681 4 дня назад
​@@MalawianCameraNdi dolo
@AchinaKellz
@AchinaKellz 5 дней назад
Komadi ma vn ake ndiopepera😂amandibowa I think ndichitsilizira kwawo
@MalawianCamera
@MalawianCamera 5 дней назад
😂😂😂😂
@KavutaChancy
@KavutaChancy 3 дня назад
Big dog 🐶 Morton
@AlexSymon-he1vt
@AlexSymon-he1vt 5 дней назад
jb mofaya ❤
@MartinMajola
@MartinMajola 5 дней назад
Jb uma kwanaa
@StephanoSonkho
@StephanoSonkho День назад
Jb l❤ you bro
@KettieNathaya
@KettieNathaya 5 дней назад
Amuna sayambana zaziiiiiiii nonsenu ndinu osadzindikila mkufuna kutchuka mwina
@BlessingsmadalitsoShumba
@BlessingsmadalitsoShumba 5 дней назад
😂😂😂😂🤣🤣🤣 waying,alura tu jb
@DanielGeorge-l4h
@DanielGeorge-l4h 5 дней назад
Wathawatu ntabaluka uja 😂😂😂😂😂😂😂
@GloryLouis-x2l
@GloryLouis-x2l 5 дней назад
JB guys Born fire
@KavutaChancy
@KavutaChancy 3 дня назад
Team morton
@EliaThomas-vp9jz
@EliaThomas-vp9jz Час назад
Amen
@AliNtolera
@AliNtolera 5 дней назад
What is happen with your cape my friend Malawian camera kkkkkk
@thomasmcbanda9794
@thomasmcbanda9794 4 дня назад
Kodi enawoso nde uti 😅😅😅😅 angooneka ngati mchikumbe
@JibraanSharief-ol1yn
@JibraanSharief-ol1yn 2 дня назад
Rubbish ndi wokudya nkhono mboli yamako
@FridayChibalo-l1q
@FridayChibalo-l1q 4 дня назад
Mavyete kuyooya chomene
@nicolsley995
@nicolsley995 4 дня назад
Koma JB sanali pa poly 😂😂
@SarahMusama-eu7wt
@SarahMusama-eu7wt 5 дней назад
Ndasekaa
@AlinafePililani
@AlinafePililani 3 дня назад
😂😂😂😂 Walala a Jb
@peterthawi
@peterthawi 5 дней назад
ati morton wambula mahala...😂😂😂😂
@dalitson3558
@dalitson3558 5 дней назад
JB all the way we like him
@giftsululu4274
@giftsululu4274 2 дня назад
A jB mwZindikira liti kut kutukwana munthu osalakwA ndi ntchimo.. Pomwe dairy mutukwana mtsogoleri wadziko lino LA malawi
@suprianomgalla5512
@suprianomgalla5512 5 дней назад
The fact is JB ndi otchuka pamene Morton's IQ is better than JB
@AllanMwakalenga-wn5ib
@AllanMwakalenga-wn5ib 5 дней назад
Akuti chizungu chanu ndichokokera
@EdwardMguwela
@EdwardMguwela 5 дней назад
Mvyete ndi machine osati okudya nakalizi uja
@MalawianCamera
@MalawianCamera 5 дней назад
😂
@FrancisKalavina
@FrancisKalavina 4 дня назад
Fact
@BensonJugah
@BensonJugah 5 дней назад
JB is my ...........✍️ 💪🇲🇼
@RuthChilobwe
@RuthChilobwe 5 дней назад
Ku China anthu ake samaria mulengi yesu mkhristu..ndiye mzimu woyera unamuleka chifukwa chokanirira macimo. Ndiye Baibulo limati..: Ntchimo.losakhululukidwa ndi Mulungu .ndi tchimo losamvera mzimu woyera..amen ..Non God feareres and non God lovers expect to be thrown in he'll fire !! Amen
@MalawianCamera
@MalawianCamera 5 дней назад
Ma Chinese anamupusitsa
@HamanjaManyela
@HamanjaManyela 3 дня назад
Moton mfana wachikape kwambiri
Далее
NKHONDO YAPAKAMWA - MORTON BAGHAYA KUBWENZERA JB
1:35:14
Распаковка Monster High Potions №4
00:46
Просмотров 111 тыс.