Тёмный

JB wayakhula chilungamo cheni cheni pa nkhani yokhuza black nina😁🤔 

HASSA YUSY MW
Подписаться 3,5 тыс.
Просмотров 12 тыс.
50% 1

Опубликовано:

 

22 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 24   
@FathimaMa2
@FathimaMa2 3 месяца назад
You the good man my brother
@AlexanderMisheck
@AlexanderMisheck 2 месяца назад
Kodi zanga umadyela kumazele kkkkkk umakwana
@SamurlStephen
@SamurlStephen 10 месяцев назад
A J B tigayireni forex kuno sizikuyendatu 😅
@hopembendela
@hopembendela 11 месяцев назад
Koma ndiye kutafuna ngati mwafika kumene ku Americakotu
@PrinceKachimanga
@PrinceKachimanga 3 месяца назад
jb😂😂😂😂😂😂😂respect
@PaulMkweza
@PaulMkweza 11 месяцев назад
Ineyo mwa adah awawa ndimapindulamo kwambiri
@AlickJinamu
@AlickJinamu 19 дней назад
JD timajwela kumanja ozati kumazele
@fredgabrielnyangulu
@fredgabrielnyangulu 11 месяцев назад
Mbuzi ya munthu iyi inu tawonani ali busy kuwonetsa anthu nsima ndie Nsima yakeyo kuda biiiiiiii ndipo wakulira ameneyu ndi kumadyera kumadzere ngati mwana woti akuphunzitsidwa kudya. Nkhani yaikulu apa ndiyoti awa ndi amene anamubera mwana uja nyimbo zake ndi kukula chimutu kwakeku😊
@GeorgeSinoya
@GeorgeSinoya 11 месяцев назад
😅
@FosterZulu-b3j
@FosterZulu-b3j 3 месяца назад
AJB tabwerani kuno kumalawi tidzakuoneni ka
@MOSESEVANSON
@MOSESEVANSON 11 месяцев назад
True
@mellipherjohn7158
@mellipherjohn7158 4 месяца назад
nsima yake yosaphikika angodyadi ngat wafika kumenedi kkkkkk
@BlessingsPhiri-l9s
@BlessingsPhiri-l9s 11 месяцев назад
Zikomo kwambili JB please please please please please please please please please please please please please usadzasiye kutisitsa information yemwe achinyamata amachita zopusa please please please please please please please please please please please please timakundalila kwambili chifukwa poponda iwe ayamata opusa wa zitipusitsa timayamika chifukwa sumadzikweza ndipo usasiye kutipatsa khani zabwino kwambili zikomo kwambili mulungu azikundalitsa kwambili
@inessmsiyambiri8517
@inessmsiyambiri8517 11 месяцев назад
Ndimmene akulowera satanic oyimbawa kutengekaa iiiiiii
@PrincePhiri-xv2dm
@PrincePhiri-xv2dm 2 месяца назад
Kukonda kudya ankolo
@giftkamwiyo9175
@giftkamwiyo9175 11 месяцев назад
💪💪💪
@SulaimanaWasi
@SulaimanaWasi 11 месяцев назад
😂
@wonganikaunda7704
@wonganikaunda7704 11 месяцев назад
Nzeru
@CobraTwaib
@CobraTwaib 11 месяцев назад
JB wayakhula bho black nina analakwitsa kusaina contact vuto la achinyamata akumalawi amangotengeka ndi zinthu zopanda pake aaaa mumandililitsa 😢ndisaname
@mordecaikachale2497
@mordecaikachale2497 11 месяцев назад
Awatu ndanzeru ❤❤❤❤❤
@deanmossiwa1415
@deanmossiwa1415 11 месяцев назад
Kungot mukudya nsima zinavuta koma nkhan mpka ikathere kugura mma usd
@jeanjiward952
@jeanjiward952 11 месяцев назад
So what's the way forward because him is crying, according to him he said he wants his video no matter whatever he spent he doesn't care care,to my understanding l heard that u are the richest but he got surprise u are falling to give him.for your information why u accepted him to sign when u know that it's not gud and why is keeping the video for him u were supposed to tell him before that use your 70 percent before signing.whats the benefit for him to just keep the video instead give it to the owner and advise him the advantages of signing mmm it's unfair.Anyway only God knows the best
@BusiBusisiswe
@BusiBusisiswe 11 месяцев назад
Zoonandi JB
@veronicanyirongo1314
@veronicanyirongo1314 11 месяцев назад
Choka iwe munthu oipa osauka mphawi iwe mpatse vedio yake nina
Далее
Malodza Akuchikangawa A Poem by Sir Michael Benjala
5:00
FRIDAY PARTY WE PARTY
10:43
Просмотров 20 тыс.
ZEZE,MAVYETE & JETU
1:31
Просмотров 1,6 тыс.
Rip Thomas Chibade
5:00
Просмотров 11 тыс.
USAUVER S07E03   AGALU
8:42
Просмотров 86 тыс.
Amalawi tidzameta maliro a Chilima 2025
7:57
Просмотров 68 тыс.