Mulungu akadamakhala kuti amalankhula live,,,akanatilankhula ndithu,?mwapemphela kumutchula Mulungu kupempha chikhululuko kwa munthu wakufayo then mukubweletsaso zida mkumayimbaso nyimbo bwanji koma A malawi,,,Oh paja mmati kuyimba ndiluso lokupasani Mulungu eti
Ndizomwe ananena mwini wake kuti pa maliro ake anthu azakodwe not kulira Rest Well Mr Banda tidzaiwala koma chikumbumtima chidzakhalapobe mpaka Kale ❤❤❤❤❤❤
Maturity kwanu konko coz they are just celebrating a life of a hero and that's what Soja always wanted and that's y amati aliyense zintchito Zake zimamuchitira umboni
Aliyense ntchito zake zimamuchitira umboni n Soja ntchito zake zamuchitira umboni, John was just celebrating a life of his hero nothing more nde maturity kwanu konko
Bro munthu uja anali oyimba osamayiwara nde it's must Kuti pa mwambo wake pakhare ngati show ndi zomwe munthuyo amakonda, even nfumu ikafa anthu amatenga maliro kupita nawo pa bwalo