Тёмный

Kodi Malawi Adzasintha Liti - Bon Kalindo 

Nyasa VoiceBox
Подписаться 28 тыс.
Просмотров 14 тыс.
50% 1

Today on Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo asks, when will Malawi change? He is asking this alongside many other questions such as:
When will malawi you stop being used for terrorizing political opponents?
Why can’t malawi opposition parties work together with one agenda?
As a country are we comfortable with our country being governed by injunctions?
Lero pa Nyasa VoiceBox, Bon Kalindo afunsa, Malawi isintha liti? Amafunsa izi limodzi ndi mafunso ena ambiri monga:
Ndi liti a malawi mudzasiya kugwiritsidwa ntchito poopseza otsutsa boma?
Chifukwa chiyani zipani zotsutsa ku malawi sizingagwire ntchito limodzi ndi mfundo imodzi?
Kodi ngati dziko tili okondwa kuti dziko lathu likalamulidwa ndi ma injuction?
#malawi

Опубликовано:

 

3 окт 2024

Поделиться:

Ссылка:

Скачать:

Готовим ссылку...

Добавить в:

Мой плейлист
Посмотреть позже
Комментарии : 56   
@edwinchimbuto
@edwinchimbuto 7 месяцев назад
vuto kumudzi kuno ndi court.... i dont blame mcp or dpp,i blame judges
@ShabaniKuswere-cp7ss
@ShabaniKuswere-cp7ss 7 месяцев назад
Zoona panopa Malawi wamezedwa ndipo akuyendetsedwa ndi judiciary.Ma judge ndiamene akusokoneza dziko lino kwambiri
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 7 месяцев назад
Nkhanitu ndindalama basi ma judge athuwa
@MaggieRoseKaunda
@MaggieRoseKaunda 7 месяцев назад
Thank you sir my God bless you first,, plz can you mobirais the churches and ask this,and play to God in all, can you see Malawi, take care malawi
@thulanimpphiri6873
@thulanimpphiri6873 7 месяцев назад
Mr DC always umanena zoona vuto ndifedi a Malawi tikuganiza Mombwambwana. Mcp ndi falawo ndiye Mulungu adatichosa mwafalawo koma amalawi kupupuluma ndikubwereraso kwa falawo mistake yayikulu.
@HannaBanda-pj8vr
@HannaBanda-pj8vr 7 месяцев назад
Malawi first please yambisani chipani mupulumuse Malawi tikuvotelani ine voti yanu yoyamba pls pls pls Mr bon kalindo .
@esthermalixani2244
@esthermalixani2244 7 месяцев назад
Zoona bon karindo
@HildatoweraMhango-et4mz
@HildatoweraMhango-et4mz 7 месяцев назад
Zoonadi malawi ino anthu ndife opusa tinakaimadi pamodzi kupita ku court cause anthuwa akulandira ndalama zathu za misonkho ndiye tili ndi ufulu opita ku court kukatenga injuction nafeso kuti parliament iyime kaye
@ishmaelsamuel2199
@ishmaelsamuel2199 7 месяцев назад
Yes go konko Ku court
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 7 месяцев назад
Iweyo Kalindo umati ndiwe omenyera ufulu koma ntchito kutukwana usana ndi usiku. Chakwera umamutukwanayo naye ali ndi anthu ake omutsatira omwe akhala chete kwanthawi yaitali panopa afika potopa nanu nde muona nyekhwe...this is just the beginning
@tingamasi106
@tingamasi106 7 месяцев назад
Kwagwereni uko ndi chakwera wanuyo, Bon kalindo more fire
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 7 месяцев назад
@@tingamasi106mulira kwee! Simunati..pano game yalowa zikwanje
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 7 месяцев назад
Watukwana pati bon kalindo? Tamaganizani nanunso zaziiiii
@ziyamporoma377
@ziyamporoma377 7 месяцев назад
@@VictoriaWilliam-ms2ft ukuyenera kuganiza ndiiweyo coz you're following Kalindo who persuaded you to vote for Tonse alliance only to turn against them chifukwa sanapatsidwe udindo. Malawians open your eyes
@VictoriaWilliam-ms2ft
@VictoriaWilliam-ms2ft 7 месяцев назад
@@ziyamporoma377 who is following kalindo?
@chipi892
@chipi892 7 месяцев назад
Our judiciary is killing us. Our dziko is being ruined awa court failed us big time
@MosesBanda-ef6fj
@MosesBanda-ef6fj 7 месяцев назад
Galu chakwela walephela komanso watikwana
@mariezorgen7735
@mariezorgen7735 7 месяцев назад
When is ideation hiii so far!
@grantjossam
@grantjossam 7 месяцев назад
DC ndi legend 💪💪💪
@McDonaldBeketeNkhata
@McDonaldBeketeNkhata 7 месяцев назад
Munthu woyamba kusangala ndi achakwera Catherine Gotani Hara
@RobertLuka-wy9cl
@RobertLuka-wy9cl 7 месяцев назад
Kumalawi ma court ali pa bisnes sakupanga za amalawi ayi kom mulungu tsiku lina azatimenyela nkhondo
@DonaldPonda-p2q
@DonaldPonda-p2q 7 месяцев назад
President wanthu
@LysonKumwenda-v1m
@LysonKumwenda-v1m 7 месяцев назад
Zoba iyi
@harrisbanda5891
@harrisbanda5891 7 месяцев назад
Name bon usatimnyasepo apaa wamva iweee, ukuti koma abale mcp zizatheka abaleee, ife sitinakuwuzeni mthawi imene ija kuti don't try to vote for mcp coz its crocodile party, chipani chakupha, ndankhanza . Lero nde msatinyasepo apaa agologolo inu. Inenso adpp musalire nthawi yanu ija simumkagwilika ayi mcp and dpp nonse mapwala ndi nyini zamanu, mmsandilakwisepo ine apaa shut upppp . Nanga ndatukwanapo apaa ine?
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd 7 месяцев назад
koma andale si athu guys
@PreciousDouglas-d7v
@PreciousDouglas-d7v 7 месяцев назад
Mavuto alimo mmalawi muno
@greychizaka4088
@greychizaka4088 7 месяцев назад
Mau🎉
@GeshoMwakitwile
@GeshoMwakitwile 7 месяцев назад
Ine ndine chitsiru Cha munthu kumenyela ufuru wa a dpppp kut angabwelelenso mboma
@alfredmphande4930
@alfredmphande4930 7 месяцев назад
Tizazindikila bwino pasogolo amalawi. Vuto sitingaliziwe pano km ikazayamba
@WilsLimited
@WilsLimited 7 месяцев назад
Satana analowa mwachakwera ngati mmene analowera mwa njoka mmunda mwa ideni muja nkona anagwa mmanja mwa yehova
@zioneTembo-v2p
@zioneTembo-v2p 7 месяцев назад
Ndipodi onse azititadi
@Yahiya-wm8nd
@Yahiya-wm8nd 7 месяцев назад
satana koma guys atigwela dzikumuno
@giftdulamkalenga7344
@giftdulamkalenga7344 7 месяцев назад
Nabola kubwere nkhondoyo kusiyana ndi kuphedwa one by one silently
@HusseinAnthony
@HusseinAnthony 7 месяцев назад
😂😂😂😂
@johnchicoti
@johnchicoti 7 месяцев назад
Bon kalindo iwe ndiye kape wamunthu iweyo bwanji nyumba yako unayiphanda
@HusseinAnthony
@HusseinAnthony 7 месяцев назад
Ndi kape chifukwa akuyankhula chilungamo
@ShareeJali
@ShareeJali 7 месяцев назад
Iweso ndiwe galu
@HusseinAnthony
@HusseinAnthony 7 месяцев назад
@@ShareeJali galu amako opanda mano aja
@Homeofpeace321
@Homeofpeace321 7 месяцев назад
Akakhala a DPP Amenyeni Kwambili Apanikizeni Amazuza Kwambili Boma lawo, kunali achina jomo. Aliyense ovala cha DPP iphani. Azipani zina asiyeni. Ndalamula
@IbrahimWezely-qd4vj
@IbrahimWezely-qd4vj 7 месяцев назад
Uyu amatumidwa ndi chilima, ndipo kaya utani no chance. Zaipa poti akupanga ndi a mcp??? Zopusa
@salimmkumakumakitombi-yc7pw
@salimmkumakumakitombi-yc7pw 7 месяцев назад
Osamapereka comment musanavere uthenga akulu..tamvetserani bwino.bwino..kumva kwanga .munthuyu akudandaura chitidwe okhapana kuvulana zomvala kumenya .zomwe zikachitikaso munthawi ya DPP ndipo kalindo Nkukuyu anali limodzi pothawa nthawi imeneyo. nde munthuyu akudzudzula kuti zimenezo ayi.not kuti kalindo akakondwa nadzo munthawi ya DPP ... ndipo kalindoyo anamenyeswaso kuotvheredwa ma galimoto ndimasapota A DPP nde angakondweso ndiidzi
@robsontyg3928
@robsontyg3928 7 месяцев назад
Malawi adzasintha Peter munthalika ndi Bon kalindo akamwalila
@Dee01papa
@Dee01papa 7 месяцев назад
Shut up
@JoyceBanda-k8t
@JoyceBanda-k8t 7 месяцев назад
Umwalire ndi iwe mulungu akuibe wamva
@YoungMwacho
@YoungMwacho 7 месяцев назад
Rubbish comment
@christophermukaka7403
@christophermukaka7403 7 месяцев назад
Waganiza bwanji
@RiteRoderick
@RiteRoderick 7 месяцев назад
Umwalira ndiiweyo ndipo Chaka chino sichikuthera
Далее
Chakwera Will Not Win The Elections - Samuel Lwara
22:19